Malawian woman burns her husband’s private parts

Advertisement
Police

Kanengo Police in Lilongwe city are keeping in custody a 33 year -old woman for burning her husband’s private parts.

Deputy Public Relations Officer for Kanengo police Salome Chibwana identified the suspect as Juliet Chiwaya from Dedza district.

PoliceAccording to Chibwana, Chiwaya burnt her husband’s private parts after hearing that he was in a love affair with another woman.

The suspect boiled some water and poured them at the man’s private parts, burning her husband’s manhood in the process.

According to Chibwana, if the suspect is found guilty she will serve a maximum of seven years imprisonment with hard labour.

Police have since warned people to avoid solving conflict using violence. The security providers have also urged Malawians to report such matters to police before making stupid decisions.

Juliet Chiwaya hails from Malindama village in the area of Traditional (T/A) Authority Kaphuka in Dedza district.

Advertisement

391 Comments

 1. Pa nkhani iyi ndikupempha ma bungwe kuti achitepo kathu mpaka nkhani iyi ithe macilungamo mayiyo alangike ndithu.Kupanda kutero izi zipeleka nkhaza kwambiri kwa azibambo.Nzopweteka kutimwamuna wapwetekeka azimayi azipanga coment zonyasa.Mwamuna ndi mkazi azifanana mzose osati kumati Gendar pomwe mukukondera mkazi.

 2. Pa nkhani iyi ndikupempha ma bungwe kuti achitepo kathu mpaka nkhani iyi ithe macilungamo mayiyo alangike ndithu.Kupanda kutero izi zipeleka nkhaza kwambiri kwa azibambo.Nzopweteka kutimwamuna wapwetekeka azimayi azipanga coment zonyasa.Mwamuna ndi mkazi azifanana mzose osati kumati Gendar pomwe mukukondera mkazi.

 3. Waganiza bwanji? Bola kungochoka ena akanakutola koma apa mmmm wafa kawiri waluza mamuna kumangidwaso pompo olo mamunayo atakhululuka ukhala Naye bwanji zamanyazi

 4. Ngati azibambo akuwonjeza nanunso musiye kuchinditsa. Stupid. Akakupangirani nkhanza mwamuna ndiye nkhani muma radio ndi manyuzi pepala monse. Apa poti wachitiridwa nkhanza ndi mwamuna ndiye mukusekerera. Koma chonsecho ngati mukulandira ulemu ndi chifukwa cha mwamunayo. Akanapanda mwamuna amene muli nayeyo bwanzi muli ndani inu? Osangothokoza kuti mamunayo anakuvuwulani mu nyansi za uhule munkapanga uja. Nayenso mwamunayo akachira adamuwotchenso kumaliseche mkaziyo tiwone ngati kudzakhale kokongola.
  Makomenti enawa akutosonyezeratu kuti akuchokera mkamwa mwa mahule.

 5. Mai ameneyo 2points,amuna akuonjeza,atangommangira kusata lamulo koma zoona zake wacita bwino kuotcha cikumpangisa matamaco,kkkkkkkk

 6. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

  1. To hell u go,,, do u think we are too blinded to be fooled by ur stupid posts? Cheat ur fellow Nigerians not civilized Malawians! Never post ur nonsense on this page again! Mxiew

 7. Mkazi waonjeza uyu mmmm ngati mwamunayo samamufuna osangochokako iyeyo bwanji kapena wapanga izi chifukwa cholira ndi kunyasa kwake kapena?

 8. Well, for a woman to come to such a conclusion, sometimes amakhala watopa nazo. Amayi ndi munthu opilira.amakhala wayankhula kwa nthawi but no action taken. Nde amunanu mukamapanga zibwenzi ndi bwino kusaiwala kusamala pakhomo..mwina nkhani zoterezi zitha kuchepa..

 9. Mabungwe Zikanakhala Zandale Mudakava Kt Tivale Zofiila Tonse Tiyende Mmisewu Koma Apapa Dzili Cheteee! Panyapanu Amabungwe Tatapa Nanu Mmakonda Ndalama Kuotchedwa Staff Mpakana Mm

 10. Muwona nkhani imeneyo ithera m’malere popanda kuchuluka zoyangula pa media amabungwenso pamenepo ndei angoti ziiiii koma akadakhala wachitidwayo ndi nkazi pang’onong’ono wayangula amabungwenu ndalama zizakuphaaaa.kapena umafuna kunena kuti dzikoli ndi la akaziwaaaa????????????.

 11. Muwona nkhani imeneyo ithera m’malere popanda kuchuluka zoyangula pa media amabungwenso pamenepo ndei angoti ziiiii koma akadakhala wachitidwayo ndi nkazi pang’onong’ono wayangula amabungwenu ndalama zizakuphaaaa.kapena umafuna kunena kuti dzikoli ndi la akaziwaaaa????????????.

 12. ngati sitikumvetsetsana m`banja ndibwino kungolekana mwachilungamo kma osati kuonongana miyoyo`enanu mukuti amuchita bwino alingati brother wanu mungamve bwa shame on you

 13. ngati sitikumvetsetsana mmbanja ndibwino kungolekana mwachilungamo kma osati kuonongana miyoyo`enanu mukuti amuchita bwino alingati brother wanu mungamve bwa shame on you

 14. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life, this is what i caused myself, for allowing my fiance make sex to me unsecured without protection, although i never knew he is HIV positive. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the traditional healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.

 15. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life, this is what i caused myself, for allowing my fiance make sex to me unsecured without protection, although i never knew he is HIV positive. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the traditional healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.

  1. To hell u go,,, do u think we are too blinded to be fooled by ur stupid posts? Cheat ur fellow Nigerians not civilized Malawians! Never post ur nonsense on this page again! Mxiew

 16. As I always say nothing good will come out from our country so called the warm heart of Africa everything there is amess

 17. As I always say nothing good will come out from our country so called the warm heart of Africa everything there is amess

 18. Ngati pali chokhumudwitsa pa moyo wangawu ndiye ndimkazi,kulibwino kumangotenga ma takeaway,cash n carry basi akazi abanja anatha zinatsala ndizigawenga za akazi,amabngwe kuli ziiiiiii,zitsilu za anthu.

 19. Kusagula ndiwo pakhomo kumakhalila kanyenya mujumbo wakewake ndizimenezo, azimotolako juliet kkkkkkkkkkk wasalawinawe umbombo shupt konko

 20. I cn see tht malawi is goin to be on fire vry soon, why in our days peaple take fire as best weapon to deal with peaple who do wrong to the them? The one thn u hv to knw is that” muyeso umamuyezela mzako pangatalike bwanji jst knw tht someone wil use the same measure.

 21. Kkkkkkkkk nde waotcha machine osokela zovala!! Nanga zovala zikang’ambika asokela chani!!! Koma ma boko-haram achuluka mumabanja amatsiku ano shhhhiiiiiitttttt!!!!!

 22. iiiih ziotchanani mesa paja munavomereza kuti pamavuto mtendere mudzakhala limodzi,,,,kaziotchanani ….koma #yona’s wife anali woupedzatu #ThreeDays yona ali mmimba mwa #nsomba koma mkazi sanamuchite kalikonse,,,koma azimai amasiku anooo mmmm….ziotchanani !!!!!!!

 23. iiiih ziotchanani mesa paja munavomereza kuti pamavuto mtendere mudzakhala limodzi,,,,kaziotchanani ….koma #yona’s wife anali woupedzatu #ThreeDays yona ali mmimba mwa #nsomba koma mkazi sanamuchite kalikonse,,,koma azimai amasiku anooo mmmm….ziotchanani !!!!!!!

 24. kkkkkkkkkkkkk zofuna mkazi wakeyo samamukwanira n if he neva wanted her amaleka kupanga divorce nkumakapanga phada wakeyo bwanji

  1. Kkkkkkkkk.ndikachiyani cc* wangayo sakukwanila? ndiwe wadyera eti uzikhutitsidwa.zomwe wakambazo zonse mesa ndimomwe alili wakoyo ndiye ufuna mzulu bwanji?

 25. Mkazi wachita bwino,kuotcha shaftyo imagwira ntchito ndazimai ena.Go ahead sister,burn more.Azimai enanu ngati aziMuna akukuzuzani burn Shafts .

 26. Mkazi wachita bwino,kuotcha shaftyo imagwira ntchito ndazimai ena.Go ahead sister,burn more.Azimai enanu ngati aziMuna akukuzuzani burn Shafts .

 27. Kukambilana could be the best way not killing each other maka khani za banja izi mmmmm titengepo phunzilo amene sitinaotchedwe ife

 28. Kukambilana could be the best way not killing each other maka khani za banja izi mmmmm titengepo phunzilo amene sitinaotchedwe ife

 29. Masiku omaliza ano tiyeni tisamale kuli zambiri zochitika kwabasi azimai analimba mitima.ife azibambo tili patsogolo kungofunika kudalila moyo uyu sagula kaya

 30. Masiku omaliza ano tiyeni tisamale kuli zambiri zochitika kwabasi azimai analimba mitima.ife azibambo tili patsogolo kungofunika kudalila moyo uyu sagula kaya

 31. Wat kind of woman is ths 1, if a man did somthng wrong, u suppose 2 sit down en dicuss abt de matters,wat is zat 2 burns him? Wat did u get after ?stupid lady eeeeish ??????

 32. Wat kind of woman is ths 1, if a man did somthng wrong, u suppose 2 sit down en dicuss abt de matters,wat is zat 2 burns him? Wat did u get after ?stupid lady eeeeish ??????

 33. Mkazi ameneyo ingomgamulani mulandu wa trizon basi coz she’s bushit she can’t burn her husband like so mxiewwwwwwwww !!

 34. Mkazi ameneyo ingomgamulani mulandu wa trizon basi coz she’s bushit she can’t burn her husband like so mxiewwwwwwwww !!

 35. Amuna Musamatenge Ngati Mulonda Wapankhomo Komaso Azimayi Kumeneko Sikulanga Koma Kuonjezela Mavuto Mayiakukagwila Yosalipdwa Vuto Kuana

 36. Amuna Musamatenge Ngati Mulonda Wapankhomo Komaso Azimayi Kumeneko Sikulanga Koma Kuonjezela Mavuto Mayiakukagwila Yosalipdwa Vuto Kuana

 37. Mai Woipa Uyu Bwanji!!! Kuotcha Engine Ndi Chimodzimodzi Kuthamangitsa Kazembe Kkkkkkkkk!

  1. Zaka 7 zachepa, tisanamizanepo apa, adakakhala mchimwene wa2 bwezi tikumva bwanji

 38. Hahahahaha! this seem to be simple, but trust me on this one, these women will be the ones to rule us soon. you won’t hear activist fighting for men’s rights. you will find someone saying that she should not be given a stiff punishment coz she is a woman bt had it been it’s a man,,, munakamva achina zodiak akukoka nkhani imenei

 39. Thus not punishment woman you have.
  Yet you have accumulate an offen guilty to yourself.
  Even when you seek presence of God. That guilty of what you have done will always be in your mind.
  Devil is your master using you woman.
  See now what benefit have you gain.

 40. mkadziyo amaganiza chani akaonongeka ku engine amati zida zokhonzera zizichoka kuti poti zomwe zimamukhonza ndi izi wazipanga ngati kanyenyazi shame on her

 41. munyanya azimunanu, mumatenga mkazi wapakhomo ngati wopusa, simuziwa kuti nafenso ndi boko harram. kip it up go a head mwina kuphwanyisana mutu kungathe

  1. Kupanda mbolo ndi machendewo a Harriet bwenzi mutakwatiwa inu?ukukhalila zomwezo pabanjapo ndiye uzisekelela zopusazo muotchetu wakoyo tione ngati ungakhale osachindidwa

 42. Muli inu mungatani mutanva wa chikondi wanu ali ndi chibwezi?Ndichinthu chopweteka komanso chowawa fukwa ndinjira imodzi yosakilana matenda.

 43. Nkhani iyi wakanakhala kuti wapanga ndi mwamuna ndikukuuzani kuti ikanavuta kwambiri,bwezi iri m’maradio station onse mdziko muno ndikunja komwe.

 44. Dats Already Killing Dem His Lifo! Kutetha Engineeeeeeee…Hiiiiiiiiiiiiiiiii~! Zoona Fiti Zazikazi Ndizolimbadi Heartmtimaaaaaaaa!…Achaaaaaaaaaaaaamwatiphaaaaaaaaa!

 45. Dats Already Killing Dem His Lifo! Kutetha Engineeeeeeee…Hiiiiiiiiiiiiiiiii~! Zoona Fiti Zazikazi Ndizolimbadi Heartmtimaaaaaaaa!…Achaaaaaaaaaaaaamwatiphaaaaaaaaa!

 46. Ku dedza kulibe akazi a banja nanutso,ambiri timitu tawo sitiyenda bwino.

 47. Malawi sali safe amwene lero ndi izi mamuna waotchedwa shaft ….not long ago wina kwachimseu ake mabatire anachita motafunidwa ndi brother wake ….kukhalako tizitero

 48. sanalakwitse wachita bho iye ama cheater ali ndi mkazi kupanga zibwenzi osathetsa banja ndikumnayenda ndi enao bwanji big up mama nxt adzaganiza kawiri ngati adzapangeso

  1. Thats queit amazing mzimai wandibebera uyu sanalakwitse ai men of today r taking women as trash isaaaa mmene munkamutenga nkumuika pa door ma side chicks anali kutiko?? Y didnt u marry them?? Mashalabwadawo ndi omwe amawatuma azibambowa nde wachita bwino THUMBS UP MAMA i lyk that

  2. U must think as a human being that’s y mmalephera kupeza mabanja u’r thinking capacity is very very low & i dont think this u’r coments can come from some1 with 6 senses may be u were abnornomal sometimes ago & u r not yet recovered shame on u

  3. I agree wit u Winford this is inhuman..Am a woman and i cudnt go this far that’s barbalique .if the man was cheating there are many ways of solving the issue or better still let him go his way osati mpaka pamenepoThis woman is capable of taking someone’s life

  4. kkkkkkkkkk ulibe mzeru ndi iwe wekha osaganiza. sory paja uli ndi 15yrs ukadzakula udzaona ululu wake munthu akamaku cheater while u r duing ur best to plz dat person

  5. nonsenu mzelu mulibe kuthetsa kwa mavuto a m’banja sikulangana chonchi mkadziyu mzeru alibe ngati banja linamukwana ndi kwabwino anakangomanga adzipita kwao kunalembedwa kuti mwamuna deserves to have more than one wife akadzinu khalani omvera mwamuna wanu…

 49. Time of the end. If she was being abused or the husband had affairs why not leave the bustard alone and just WALK AWAY FROM THE MARRIAGE PEACEFUL?

  1. Emmie usadzayankhulenso mau amenewo ukudziwa kuti kumoyo kumeneku,ndiye madzi amoto umawadziwa bwinobwino iwe.samala ndi macomment ako opusawa

  2. Amunawo akumakapanga uhule ndi mitengo ukamati anyanya??kodi mamuna amatchedwa hule??udaonapo amuna akuima mminseu atavula ukamati anyanya uhule??Undiyankhe nsangansanga mafuso angawo ndisanakwiye kwambiri kkkk

  3. Chabwino wamuotcha nanga azanyenganso ndikupha kumeneko walakwisa ngati amaona kuti mamunayo akulakwisa banja linakangotha basi pamenepo sazakwatilanso komanso sazabelekans ndindani amene angamakhale ndi munthu oti olo nkutota komwe sakutota akamati awa sabeleka amakhalat akumachindana nyumbamo koma mwayi wa ana pamakhala palibe ndiye watch out ndi timakoment tanu topusato ngati ndinu anzelu

 50. malawi each and everytime tikumamva nkhan zotero….. anyway nzimai ndi olimba ntima mpaka kumuotcha zida + ma batry mwamuna shame….

  1. Sikulimba mtima koma kuipa mtima. Simunthu ndi chirombo mfiti yotheratu. Otere ofunika amugamule kuti ngakhale atatuluka asakwatilane ndiwina koma yemweyu. Zomwe waotchazo adzazisowe yekha. Shupit woman!

  2. Sikulimba mtima koma kuipa mtima. Simunthu ndi chirombo mfiti yotheratu. Otere ofunika amugamule kuti ngakhale atatuluka asakwatilane ndiwina koma yemweyu. Zomwe waotchazo adzazisowe yekha. Shupit woman!

  3. kkkkkkkkkkkkk. #dian thats true walankhula ngati siiwe nkazi. kulankhula kwabwino. iyeyo azikadyana ndi zomwe waotchazo kkk

  4. kkkkkkkkkkkkk. #dian thats true walankhula ngati siiwe nkazi. kulankhula kwabwino. iyeyo azikadyana ndi zomwe waotchazo kkk

  5. ya kkkkk nanga iye akumuotcha mwamuna nde mkumuthawa ndupeza mwamuna wina nde ootchedwayo asiila ndan akhale wake basi

  6. kkkkkkkkkkkkkkkkk better that because mwamunayo achitavkukana yekha bt chomwe ndaona ine sangakwatile nkazi wina because zakudya zaotchedwa apa nde winayo azapanga ulesi kudya zootcha wina

 51. That is too bad to burn someones private parts. Judgement is not like that

 52. Mwina Dhilu Kapena Ndiwo Zankhwiru Anatenga Nthawi Asanadye,aPolise Mphuma Bwanji?

Comments are closed.