
Aphungu adutsitsa bajeti ya mchaka cha 2025/2026
Pomwe nthawi imati 6:30 usiku uno aphungu a kunyumba ya malamulo tsopano adutsitsa ndondomeko ya zachuma ya mchaka cha 2025/2026 yokwana 8.076 trillion Kwacha (K8, 076, 667, 784, 858) yomwe nduna ya zachuma a Simplex… ...