Ukadaulo ndi ukatswiri ndi yankho ku Chitukuko- Chakwera
President Lazarus Chakwera wati ukadaulo ndi ukatswiri mwa achinyamata ndiofunika kwambiri pa chitukuko cha dziko la Malawi. Pa chifukwa ichi, Chakwera wati mpofunika kuti maganizidwe akuya mdziko muno apatsidwe chilimbikitso chokwanira. Poyankhula pa mwambo okumbukira… ...