M’malawi ndi ena atatu akunja amangidwa ku South Africa
Apolisi m’dziko la South Africa amanga nzika ya dziko la Malawi ndi anthu ena atatu akunja powaganizira kuti anaba ma galimoto awiri a mtundu wa Toyota Fortuner ndi Mercedes Benz zomwenso amafuna azizembetse kutuluka nazo… ...