Chakudya cholandira osadya moononga – Usi
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi alangiza anthu amene akulandira chimanga kudzera mu ndondomeko yothandiza anthu amene akusowa chakudya kuti akalandira chimanga asamale posadya moononga chifukwa ndi chochita kupatsidwa. A Usi ati… ...