Anthu ku Mzimba alembera chibaluwa phungu wawo
Anthu okhudzidwa ochokera ku dera la Solola m’boma la Mzimba alembera kalata ofesi ya mkulu wa boma ku khonsolo ya M'mbelwa kuti awapatse tsatanetsanane wa momwe ndalama za thumba la aphungu (CDF) m'mene zidagwilira ntchito… ...