Musachite ziwonetsero mawa, a Polisi akhala otangwanika – Boma liuza Namiwa
Boma, komanso akuluakulu a polisi apempha wamkulu wa bungwe la CDEDI a Slyvester Namiwa kuti ziwonetsero zomwe akonza kuti zichitike lachinayi pa 21, November asachite kamba koti a polisi akhala otangwanika. Iwo apempha a Namiwa… ...