Mipingo ku Zomba yachita ziwonetsero zodana ndimathanyula
Mipingo yosiyanasiyana motsogodzedwa ndi mpingo wa Katolika Lachinayi yachita ziwonetsero zodana ndimaukwati amuna komanso akazi okhaokha (mathanyula) mu mzinda wa Zomba. Ku zionetserozi kudafika anthu ambiri ndipo zidayambira pa bwalo la Zomba kudzera ku St… ...