Anthu 8 amwalira pa ngozi za panseu tsiku la khilisimisi
Apolisi mdziko muno ati anthu asanu ndi atatu amwalira kamba ka ngozi za pa msewu pa tsiku la khilisimisi chaka chino. Wanena izi ndi wachiwiri kwa ofalitsa nkhani za apolisi m’dziko muno a Alfred Chimthere… ...