![People from Msakambewa at the Kamuzu International Airport](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/09/Screenshot_20230920-0643302-235x176.jpg)
Anthu a ku Dowa awonetsa chikondi pa mwana yemwe akupita ku Israel
Anthu pamasamba a mchezo ayamikira anthu a kwa Msakambewa ku Dowa chifukwa cha chikondi chomwe awonetsa pa mwana wa m'mudzi mwawo yemwe akukapitiriza maphunziro ku Israel. Anthu a kwa Msakambewa anatutana kupita ku bwalo lokwerera… ...