Tsiku lofika mapepala oponyera voti lasintha
Bungwe loyendetsa zisankho mdziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) lalengeza kuti pali kusintha patsiku lomwe ma pepala oponyela voti pachisankho chapadela afikile mdziko muno kuchokera ku Dubai komwe akupangidwa. Izi ndimalinga ndi mneneri wa… ...