Ati kwawo kwatha. Ngati kuli kusolola, asolola basi ndipo amaliza. Tsopano ndi nthawi ya Kongeresi.
A Sidik Mia amene analowa chipani cha Kongeresi auza anthu a DPP kuti alongeze katundu wawo mmboma chifukwa 2019 kulibe kubwelelamo.
A Mia amene akuyembekezeka kuzakhala wachiwiri wa a Chakwera pa chisankho cha 2019 ati Kongeresi itenga boma basi.
A Mia ati a Chakwera ndiwo akhale Mtsogoleri wa dziko lino kuyambila 2019 ndipo achita zitukuko zodula mutu.
Iwo anadzudzula boma la DPP ati kamba kolephera kutukula dziko lino mu zaka zinayi zomwe akhala pa udindo ndipo m’malo mwake ayamba kujijilika pano kuyala miyala ya maziko.
“Pa zaka zinayi alephera kupeleka mwayi wa ntchito ku achinyamata, alephera kutukula dziko lino ndiye lero akati tiwavotelenso? Akunama,” anatelo a Mia.
A Mia ananena kuti boma la Mutharika tsopano likuyenela kulongeza katundu wawo ndikuyamba ulendo osamuka mmboma.
Eya Mia sakunama za Dpp ndi mbava zaba ndalama zamalawi osauka m’kumagawana ma k40 million pamene m’malawi wosauka wakumudzi akuvutika ndumphawi wadzaoneni wina am’vekele koma Dpp udzikondabasi zachambabasi pamene mankhwala nzipatala mulibe anthu ambiri tidakamwalira padakapanda ma private clinic piter atsanzike watibela mokwana.
Uyu alibe mbali Ali ngati hule mu ndale so anthu a nyakula mwatengeka naye mwayesa akuolotsani river Jordan eeissh mavuto alipo.
Zoona tione zina tatopa nanu.
ndalama ndi umunthu zonse zayenera kwamunthu kma mphatso ya utsogoleri ndiyakwamulungo 2019 tiligu mmatumba,namsongole kumoto¥¥¥¥¥¥¥¥¥¥
2019 Dpp boma again
mcp iz very maviful.u will never do what u wish.
in politics,people May become famous and second they become foolish people and finally they in devil peace ✌.only following Jesus is the best way so we can emulate Dpp,mcp or other parties but we are nothing to them so we should follow where we are going coz we don’t know a good leader but we should mulling over something when we shall voting in 2019
Mia usavutike ukaonjeza mwano even ndi MP omwe suzawina,DPP boma
MCP boma
Mia political prostitute,ungatiuze chani iwe… Nonse ndi mbava
kongeresi lero! Nthawi ya MCP inatha kalekale and chipanichi chinapita ndi kamuzu
aaah amia asaxipusiE makaladi tuwaziwa ife palibe game amasewela osaikapo juga azavoteledwa ndi asena nda chewa ananjoya nthawi ya gogo wankhaza uja
DZUKA MALAWI DZUKA……….ANTHU MUMENE MUKUVUTIKIRA KUMALAWIKO BASI MUDAKALI KUSAPOTA DPP????? OOOOO SHAME ON YOU PLZZZ………WINA WACHITA KULEMBA KUTI DPP YIZALAMULIRA MUPAKA 1000 YEARS …….MWINA YIZALAMULIRA AGOGO AKO STUPID!!!!
Mr Mia Tsekani Kamwa Yanu Musathe Mau Mwayenda Zipani Zingati Inu?
Pandale aliyese amayakhula zimene aķuona kut angathe kutero chocho amia anena mbali yao kuti awina ndio ndiye nao a dpp akut nafe tiwinaso ndie inu o komenta zikumaoneka kut aliyese akukokera mbali yake apa koma sinu andale mumangovota osewa anal chipani chimozi achita kumasitha ndie tieni tidikire 90mins
IWE MIA MANYI AKOWO UZIWAUZA AZAMBUYAKO
Amalawi 24 werengani ma Vote APA tiwone amene waluza! Zikuwoneka kuti A mia agwa nayo!
Kumbwambwana
MCP all the way….2019 osalakwitsa…
DPP titchecha ndi mitsitsi yomwe ovotafe tiliphee tingonola zikwanje zathu.
Mia chilimikani kwambili tili mmbuyomo 2019 MCP boma basi enawa apite akalime ku ndata.Abe anthu ma alubino akhale ndimntendele paumoyo wawo
Dpp or zinthu zitavuta maka singawine, oziwa ndale amawelengela,NOTE DPP IZAWINA KU THYOLO NDI MULANJE PANG’ONO BASI.you will mark my words.
This z wat we call old school politics…dissing each other cant helf .Mr Mia just tell wat u will to wen u takeover the goverment…
Amia asathe mau
Mia ndiodwala.bola azinena azizakeo. ndipo Mia ndiwa business osati ndale .
Ndipo zoona zake zimezo
Hahaha azikamba ena osati bambo MIA
Zoona
Kodi nkhaza munkapanga zija mukuganiza ngati anthu anaiwala? Nchipani chiti chimene chinkawaponya anthu mu ziwe la Ng’ona…#MCP. Nchipani chiti chimene chinkawqkhazika azimayi oyembekezera panseu chifukwa chopanda Card? #MCP. Nchipani chiti chimene chinkamenya anthu ndikuwqchita nkhaza popanda chifukwa? #MCP. Ndie mukuganiza kuti munthu wanzeru zake oganiza waumunthu akavotere MCP. ZIPHYERA za Mabala omwe Munawazunzira anthu Sizinafufutike zikadali mumitima mwawo. Akakumbukira AMADA NAWO KUKHOSI ULAMULIRO WANU WA MCP .
Kodi nkhaza munkapanga zija mukuganiza ngati anthu anaiwala? Nchipani chiti chimene chinkawaponya anthu mu ziwe la Ng’ona…#MCP. Nchipani chiti chimene chinkawqkhazika azimayi oyembekezera panseu chifukwa chopanda Card? #MCP. Nchipani chiti chimene chinkamenya anthu ndikuwqchita nkhaza popanda chifukwa? #MCP. Ndie mukuganiza kuti munthu wanzeru zake oganiza waumunthu akavotere MCP. ZIPHYERA za Mabala omwe Munawazunzira anthu Sizinafufutike zikadali mumitima mwawo. Akakumbukira AMADA NAWO KUKHOSI ULAMULIRO WANU WA MCP
Eeeti alibe manyazi chani wachake ndi wachake basi akuganiza kuti zomwe ankachita kale aleka??mesa it waz written and alinazo dongosolo lonse yoyendesera chipani akunama man kungowina adzayambiranso zawo zija.
Fisi ndi fisi ngakhale umutenge akakhale ku mudzi azigwirabe mbuzi basi kkkkkk
Zoonadi Bro aaah,
Inu munaliko
Paja mia NDE kuti?
Mia ndiyemwe uja analephera ku pp chachilendo ndichani
Hahahahahahahaha chipani chake chitinso choti uzikaima pagulu makolo anthu anavutika ife sitifuna kuona zomwe anaona makolo kkkkkkk
paka amia kumalimba mtima kt alowa m’boma sii uphungu uwu tionana 2019
Tivinaso “Atibela Volume 6” amia mungot duu
Mmmmm I Doubt. U Cant Just Defeat This Mighty DPP on a silver plater. they are all over the country unlike MCP. Lets Wait And See Mwina Mia Waiwelenga DPP Which in real sense i doubt.
Lindani Madzi adutse mudziti mwadala
Mbuz iyi itiuza chan! mcp sdzawinapo bola DPP
Malawi Congress Party again? Mmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmnmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmm ‘yalakwatu pamenepa’ Nkhuku zanga zapita basì!
wakufa sadziwika, tiyeni tingodikira pang’ono. Kusankha ndi anthu omwe sadalankhewa ndi amene adzaika pa mpando munthu yemwe akufuna!.
Magogo akapume basi
Kkk
Kikkkkkkkkk ba Mia chabwino ndakumvani
We take some of these empty sentiments as kicks of a dying Buffalo. MCP is a big threat and you may already having sleepless nights. Remember in the last election DPP and MCP were neck to neck. What more this time when DPP has lost penetration power especially in the central. You have to understand that this is the toughest campaign for DPP.
Nop! DPP IS POWERFUL PARTY &HE STEAL ROLLING GOVERNMENT OVER 2019.
Nanunso ambiri sanavote timkangoti dpp wawina maka ku lilongwe city chiwoko anthu wolembetsa analipo 4000 wovota 459 nde muona ulendo uyu tikavota
Kkkkkkl,apakire_bas
maloto saletsana kulota.
maka ka program akumakaonesa pa mbc kaja sorry (sapita kawili)
Zoona zake mwaba kwakwana
Ndani munthu wamzeru angavotere MCP? MCP singawine 2019 zivute zitani, DDP ikhala ikulamulilabe up to next 1000 years.
Hapana Chisingapere oyimba waku Zimbabwe anayimba choncho meaning PALIBE CHOSATHA ndipo DPP mukuiti izalamula mpaka mpaka ZOSATHEKA ZIMENEZO ndipo muzaona ngati kutulo DPP iri kunja kwa boma….
DDP izasiya kulamula Yesu akazabwela.
UDF imatero koma ali kuti pano
Amenewo nde maloto bro ukunama siufumu tatopa nanu alomwenu
DPP izilamulira mu nyumba mwanu mpaka zaka 1000
Believe you me, mufune musafune DPP ikhala ikulamula up to next 1000 years. MCP sidzawinapo presidential elections.
Mcp Sizalamulira Malawi. Chimenecho Mudziwe, Mufune Or Musafune.
Zaziiii
Dpp izingopitiliza coz never again
I cant comment,am too busy dreaming about my next oresident…
I cant comment,am too busy dreaming about my next oresident…
Hon.Mia Behaviour is like of himself.Kuchipembedzo matama ake ndiomwewo.Amafuta atakhala Mtumiki Muhamad zimangovuta.Wanena bwino kuti abweretsa chitukuko chodula mutu.Muyambenso kutidula mitu
Mia kumbuka za Patel kwa Bvumbwe anawona zokoma chifukwa cholimbana ndi Boma.Mbuzi ndi ng’ombe zako zitha.Uyenda pansi.Umatsogolera kutukwana MCP lero ukufuna kutisikonezera chipani chathu.Ife sitinasinthe chipani.Koma iwe ukukhala ngati galu wachiwewe.Mpando ukufunawo ndi wa Msowoya ;Munthu wophunzila bwino ….aaaaa Mkaladi alamulile dziko la anthu akuda.Abakana ANgwazi zimenezo.Ife ayi .
Kodi apapa sipoopsezelana ai aliyese akuyenera kulankhula kodi mukati ndiokuba ndiye wabwino osabawo alikuti? mu dpp chaponda bwaa wabwino tiyambe kuwachula apapa aaaa inu anthutu akuona inutu mudikile kaye muone kuti kumwera kutuluka chani? come 2019
Iiiiiiii inu pakana mbudzi amatero ai chitukuko chache chiti? akunene iwecho aaaa unene zina bwaa
Mia usazanenenso,takukhululukira chifukwa ukamba iwe sukuziziwa.Mwana wachepa.
Kkkkkkkk mia wakhuta mkaka wa ng’ombe et kagwere uko ….DPP woyeeeee!
Kodi Paja a Mia Ndi ndani?
Ambuye tiomboleni awaso akuti yakwana thawi yawo yosolora tithawila kuti amalawi amzanga timaona ngati aziti thawi yobwezelexa ndalama mchimake koma kkkkkkkkkkkk mia ndiwakubadi eti
Kkkkkkkkk zovutatu
Apa ambuye alowelele basi kkkkkkkkkkkkkk
Ulikutali iwe…. #mia
Misala Siposa apa
Koma Mia Anayamba Waona Dpp Itagonja Pa Chsankho?
MCP sizawinapo
ovota ali phe!! pano tisanamizane nkhani zili paliponse ndiza Mcp,ikuwina basi ndiye apa tiyeni tizingochezapo ngatinso timavota nawo
Machende ake mia
Mia ufune usafune DPP bomaa!!!!!!!! siza MCP zakozo apa tiziti chitukuko sukuchiona mbuzi
Khongiresi..?? Never again..!!
Kikikiki! Asosola eti? Musandiseketse inu ndithu. Koma ali m’mavuto a chipani cholamulira no wonder they want to make a coalition with the other party
Koma kumeneko,wina athawa pa Malawi
ndi nthawi ya Congress kuti isololenso? Oh my God, aMalawi fe tili pa ‘mavuto
Azikasolora kwawo ku india
NEVER AGAIN !
MIA UDALI KU PP BWANJI SIMUDALOWE M BOMA
Amia uzani mtundu wa amalawi zimene mudzachite mukadzalowa m’boma 2019 kuposa zomwe zilipo panopa.Amalawi panopa anachenjera kotero simungawapusitseso ndi kumawatuma kuti kandipheren brown mpinganjira ndikupatsan 5pin aliyese kulibe.Musasiye mlomo
Auze …
Pakamwa Sipasiyambuyake Akufa
foolish government of muthalika tawonani 3440 000 000 000 zimene adalonjeza kuti apatsa amene akane electoral reforms beaure ndipo zadziwika tsopano misonkho yamalawi kuchitanayo zovetsa chisoni malawi akupita kuti?mmalo mopanga chitukuko ndalama mkumapatsa zidzete zama mp kuti zizikana ma bill chimenechi ndicho chazelu adapanga amuthalika ?Atule pasi udindo uku ndikupha dziko, supit zanu fulken u muthalika.
Kodi iwe nkhani ikhala imodzi chaka chosechi kapena ukutithandiza kampeni
A mia wakutumaniyo akupweteketsani chifukwa yemweyo 2014 adagwa chagada. Kodi mukatchalenja a Msowoya za u vice president mukuona ngat ndi mungatchalenjenso a president adziko lino? Mmm musamatero a Mia ine changa ndichisoni kwainu
apulezident ake ati pitala?
Yes chifukwa ochakwera adagudubuzidwa ndi Pitala yemweyo 2014 ija
mark my word
A Mia akamati ndi nthawi ya MCP akufunaso kuzasolola nawo, never again
Mia usathe mawu poyankhula MCP singawine mark my work coz ili ndi mbiri yoyipa yakupha anthu
MAN TANG’ANANI KUCHIPANI CHOLAMULACHO NGATI KULIBE WAMAGAZI MMMANJA ? AND ONSE AMENE ANALI MAMAFIA NTHAWI YA MCP NDI AMENE ALI KU DPP NDIYE MUKT CHAN
Ndizakale zija zophana masiku ano ndi demokilase abambo, iwalani. MCP is a changed party.
Mark ma work yomweyo hahahahadaaaaa
Munthu akafera ku Police Mbiri imaipa ndiya Police Yonse ngakhale individule Yemwe adapha Munthuyo atachoka ndikukayamba uphuzitsi
Mark my work?
UKUPHA NDIWE
DJ Dzidzidzi ayamba kale ayamba kale kunjenjemera kkkkkkkk ndale sungazimvese
kkkkk eeeish
Atsogoleriwo ali bho koma vuto ndi chipani chomwe akwelacho mkovuta kuwina “kongelesi( mcp) musandikumbuse kale ndalila”
Mia galu wa ciwewe ngati iwe angakumvere ndani hule ungofuna mpando uyambe kaye wayang’ana ku mtundu kwanu ngati kuli wanzeru osamakangodya athese bwanji wayesa APM Nidi nzako eti ndipo ameneyu abwenze Cold storage ija galu wakuba uyu nadyanzi sukuona chitukukochi . Uli minister wa tranport unapanga cani iwe manyazi ulibe masaize ako ndife wamva
Keneth Jere, why commenting ngati Sidik Mia amalankhula za kunyumba kwanu? Its people like you who destroys the good history of the party.
Mwenye wa ku india atisokonezera dziko wabweletsa mpungwepungwe mu mcp upakire uzipita kwanu ku lndia
Size yako Mia. Hehehedeeee uli anthu mumafuna kuzinyozetsa
Anyamata akuthyolo kkkk makape achabechabe mia angakhale size yako munthu okanda ngt iwe
KKKKKKKK! Are u mad don’t tell us ur nonsense
Failed Mcp
CHITINI CHOPANDA MADZI PHOKOSO KWAMBILI, MIA KAVUWE VUWE KAYA CHAMBA CHIKUMUPWETEKA. ALONGEDZE NDANI NDIMAYESA IYE NDIYEMWE ANALONGEDZA DYELA. OVOTATU ALIPHEEE KUDIKILA TSIKULO DPP KUMABWELELASO M’BOMA.
Awuzeni ayamba kulambula misewu poti awona kuti akungoluza zisankha zazing’ono zikachitika Dpp kwawo kwatha awa yanga ndi mcp basi
Yah ziwuzeni mbavazi iyaaaah
ine ndimakonda MCP koma singachite Ku votera Mia or chakwera , better Peter yemweyu. the demon u know is better than the angel u don’t know
nice
mbuzi yopanda mano kusi
Utesipela
mbuzi mia ndi chakwera
Usavutike iwe arthur ife tivotera mcp
Muzitukwanitsa khalani tchende, ooops chete
Peter musarika yemweyo
lets waiting for 2019 ,,,,u ll c
pitala sangawine
Hahaha chipani chilichonse anachikhalapo …..kufuna ndiwo zabwino demet zako akuvotera a gonthi omwewo ine ndakukanira zopepera zakozo
Mia si mlendo mundale. He is a failed politician, nde lero angatiuze chani cha nzeru?
vuto lonyoza achinyamata ndilimenelo mr ibu lelo akuti mupakile. kumawapaka penti achinyata mwati ndi tsogolo lawo lelo alusa ati mupakile pepa mr.
Cadet vs crocodile
Kodi mwenye ameneyu bwanji?nawe upakire uzipita kwanu ku lndia
Linda madzi aduse nde udziti wandala………
Mia Ndi Mbuya Wa Thu Ku Nsanje
Ndi mwenye wa ku India
Mr Mia chenjerani ndi mayankhulidwe anuwo tsiku lina muzachita manyazi kwambiri, ndipo chomwe mungadziwe inu nachi ;zandalezi ziri ngati gemu ya mpira ndipo zidzimaziwika bwino lomwe ai m’mangoona zitatha basi. Choncho wopakira kapena wolowa sadziwikanso ai tiyeni tiyang’ane za kutsogolo kwathu kuti chingatipatse mulungu m’chiani DDP kapena MCP.
MCP
MCP yomweyo
ku ndata heeti
Kkkkkkk koma!!
Mia akunena zoona komaso azawo atula pansi maudindo tsopano ameneyu vuto lache ndi chani?
political hule….. mia
Usaiwaletu kuti ku Dpp ambili adali aMcp Dausi Mntaba kungotchulako ochepa
@kaliba. Koma akunama akuyankhulazo?
the story is not about ntaba. and sinanene kut kwinako ndiabwino….am not either talking mcp or dpp. iam talking abot mia
Tsono ndi nthawi ya congress kusolola, Mia walonjeza izi from his statement shaaah!!!
Kkkkkkkkkkkkkkk
Zoona mbuya
Kkkkkk ntima suvala nsanza lekani kulota mulimmaso inu.
Udzakhumudwa ndipo sudzadya nsima azakoso ku zambia ankatelo koma mmene adagonjela Lupia Bwezani Banda wachipani cholamula mmmm zovetsa chisoni kunoso zichitika zimenezo
Since 1994 munayambira kunena kuti sitidzadya sima pamene simayo simumadya ndinu kkkkk
Tatopa nawo akanganyawa
Zowona azipita atikwana agwape amenewa
F.. MCP
mmmmmmmm Mia z a mad person…….. kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
mmmmm Mia wadyera angatiuzenso chani wasintha zipani zingat? wangozetsa mpungwepungwe ku MCP
Auze mwana wamu lowershire
Never again