Abwelako ku Joni opanda kanthu. Angobwela ndi zovala zapathupi pawo ndi kaselula basi. Kaya ayambila pati kumudzi kuno?
A Malawi okwana zana limodzi ndi theka kudza mphambu imodzi (151) afika m’dziko muno atathamangitsidwa ku South Africa komwe amakhala opanda chilolezo.
A Malawi awa afika Lolemba pa 29 kudzela pa bwalo la ndege la Kamuzu International mu mzinda wa Lilongwe.
Malinga ndi mneneri wa bwalo la ndege la Kamuzu International, a Martin Gondolo, abambo okwana 149 ndi amayi awiri ndiwo anafika m’dziko muno atatopa ndi kukhala pa malo a Lindera podikila kubwela kumudzi.
Umboni umene tapeza a Malawi24 waonetsa kuti pa a Malawi omwe afika m’dziko muno, ochuluka akuchokela mu boma la Mangochi ndipo kenako Mzimba.
Pa a Malawi 151, 62 ndi ochokela mu boma la Mangochi, 41 ndi a ku Mzimba, 5 ndi a mu Blantyre, 11 a ku Machinga, 7 kuchoka ku Nkhatabay, 4 ku Dedza, 7 ku Mulanje, 5 ku Chiradzulu, 8 ku Zomba and mmodzi wa ku Nsanje.
Chaka chatha mu mwezi wa December a Malawi ena 72 anafika mu dziko muno atathamangitsidwa mu dziko la Zimbabwe kamba kokhala opanda chilolezo.
Is time
Tivomereze Kut Ndife Osauka
Tibwelerakoso ku South Africa without passport and pay forward alright…ndikwathu kumene kuja, mwana mamuna ndi Kabudula athera moyenda.
Kkkkkk akuyesa anthu angasiye kupita ku joni kamba ka deport
Kma walembawe umaganiza??? aaaaaaa sionse olemba nkhani ali oganiza bwino oyamba ndi mbuzi Iweyo. Zoona mkumafusadi kuti ayambira pati? Iweyo unayambira pati kuti ufike pomwe ulipo?? Kayimbi Iwe xweeeeeee
Deportation siinayambe lero, timagwidwa nkupitanso ndipo sitidzasiya kupita. Kusiya kwake Joniyo ikafika poti yanyenyeka ngat Malawi ino mpamene tizasiyire, ndipo ndikuuzeni ife monga Ayao Dera or Dziko lomwe lituluse fungo la Ulemelero/Chumalo tilikomko. Mwamuna azikhala olimba mtima. Zokhoma mwaife zinatilowa mmagazi. Ndipo kugwidwa munthu sikutanthauza kuti alibe chilichonse anthu amagwidwa akupita kuntcito or ku shop, zomwe amakhala nazo panthawiyo zovala za pathupi ndi fon mmanja katundu amakhala alikunyumba ndiye (DEPORT) imeneyo. Kusayenda nkumene kukuyankhulitsani mbwelera baba
Palibepo nkhani apa kodi izi ndi zachilendo?
iiii zovala zapathupi ?
Zovala za pathupi kkkkkk
The first thing is that all the pensioners should vacate the office and give room to fresh young bloods, second we should stop employing old people as presidents as we have seen that they dont have the welfare of young people at heart.
Anthu onse ali Mboma ndi mbuzi za anthu saziwa chomwe amachita.Ngakhale mutawafunsa lero mwachitako chiyani chothandidza anthu dziko muno? Yakho 2019
Palibepo khani apa mungobwelezabe bwanji khaniyi
Yaphapha wena
Sikuputsa koma mavuto akanatani dziko la eni?
Kkkkkk akunama bwerani kachikena ngat tiraspot ikufuta # yanga iyi osadanda guys
Katundu wawo ndi Dora tawasungila kuno.Timangodikira kuti tomve zoti afika kuti tiwatumizire.Iwe udera Nazi nkhawa ndiabale ako,kukamwa kobwafukako selk
Zosakhala bwino ndithu
Inu a Malawi 24 tamalembani nkhani zeni zeni ndithu, kodi inu mukadalibe ndi bodza polemba nkhani zanu m’pakana lero lino?? Chomwe mungadziwe inu nachi :anthu mukuwanenawo adamangatu nyumba zawo m’makhomo kwawo ndiponso enawo ali ndi ndalama kumudzi kwawo tero ilo sivuto ndipo chifukwa choti adadzolowera kugwira ndalama mawali abwereranso ku South Africa ko.Iwo sianrhu wamba ai ndipo inu a Malawi 24 ndiomwe inuyo mukuwaona ngati ndi amphawi koma sichocho ai ndithu ndipo atsatireni kwawo mudzachita manyazi nokha ndi bodza lanulo ndithu.
Kulemba zopusa bas utola kham muna phunzira kuti
Apitaso posachedwapa
Ineyo ndinava kuwawa zitandichitikila zimenezi ndiye iwe ukuyakhula mopusa mboleyako ndipo ukanandiyandikila ndikanakupha phwalalako iiiiiii iweeee oky
Sikoyamba kugwidwa anthu deportee zidayamba agogo a agogo ako asadabadwe sizachilendo izi..and it’s not only malawians wh r being deported from RSA and its not only in RSA wher they are deporting illegal immigrants
..and its not a strange situation kuti munthu akagwidwa deportee amapita opanda kanthu kumudzi..and this doesnt mean kuti pamene agwidwa awadula miyendo ndi manja kuti asadzabwerenso ayi..
Try to bring something tangible here rather than bringing parasites of stories
Mbuzi
Some people enjoying looking other Malawians suffering
afika nthawi yovuta, kulinjala kuno. anyway welcome back,
very bad mmmh
My Jesus Malawi its a long way from South Africa its so painful to return home without even a capital to start even a small project.lm a Zimbabwean but l once felt shame when l was in Brandfort near Bloemfontein l saw a Malawian man he was mad,l even ask myself,WHO IS GOING TELL HIS RELATIVES THAT HE IS HERE AND HE IS MAD.even to ask anything nothing was able to come out.l wish if they deported that one not these ones.
mukamalemba zinthu mumalemba mopusa ngat inu nde muli ndi kanthu bwanji lembani zot tikawerenga tizimva bwino not manyi anu mumalembawa
Kkkkkkkkkkkk koma iwe ndiwe wa phuzo yeti athandize kaya ndimayesa ndi azibale ako amenewa apase chochita mawa azathandizaso iwe
Home boys pa mangochi sipamavutakubwelela ku joni mayazi ndipo sikuyamba kubwelela chotelo come back guyz dnt worry things happen worry nt
Ife siaulesi and I agree with you Elias M. Pemba. Ngati pali mtundu wa anthu amene saopa kupita kwina kulikonse ndife a Yao. We always get what we wants and that’s how it works. By the way, ife timayamika Mulungu chifukwa tayenda ndipo tadziwa mabvuto mmene amakhalira unlike ena mwainu munabadwila ku CheMusa and grew up in Likoma. Koma ife kuno ku Joni takumana ndi mazangazime but that’s how it is. Ambirife simbuli so you should know. Tili ndizinthu zazikulu zikulu zomwe tapanga because of the you call it; sasafulika in your version.
What a stupid question akafikila pa khomo pako uzaziona ukazayenda you don’t know what comes tomorrow shame on you
Adapitila ndalama zawo abwela they know how to source money iwe phee umaona ngat they hv nothing in store.empty tins shame kwa mlembi wa nkhaniyi udzafa osauka
Amzawo ena tasala tiaganizila ka transport abwelelaso usalakhule monyoza futseki
Mwaonatu bro.nyaupe uja mnatuma admin kuti adzigulisa wayamba kusuta yekha.chifukwa chake akuleba zoduka mutuzi
kkkkk wazungulira mutu admin
Ndipo ngati afika awuzeni kuti adzibwebwera olo pay forward sibvuto akwele kunyasalande ndi dziko lokhalo lozuza anthu inuyo ngati mukukhalako mumangokhalira bola moyo emweyu masiku mkumatha mpaka kukalamba
Mudyadila…koma zoona amnzanu amapeza zofuna zamoyo wao kumeneko
abweleranso komweko si nzika za Malawi nzika zimakhala ndi ma national Ide ndiye akaponyedwe ku dzaleka ndi ma refugee amenewo
Walemba nkhaniyi ndi bakha weniwen omwa pa chithaphwiiii……ndipo Ku utolankhaniko u never fully qualified unangogula ….
Rubbish reporting…
Anyapapi akuti anthu omwe amachoka dziko lawo kupita maiko aweni ndi alesi. mukamva umbuli ndi umenewo kuyambila iwe amene walemba nkhaniyi ndiwe kape. amene mukuti alesiwo kukhala kumeneko simungawathandize munjila iliyonse ngati likulephela kukuthanduzani boma.ANYAPAPI ndalama yomwe anthu akulandila patsiku Ku SA inu ambili mukuthoka shit pamwezi simumayifika pan…..yo…..pa…..nu
Kkkkkk nanuso amalawi24 ndinu amwano kwambili pakachocho
Atha kugwira ntchito kwa 2hrs without it a car koma yemwe akumunenayo KT wabwerera alibe kalikose atha kupanga return back,, popano ndi kuphura,,,
I like these guys I call them the dreamers wosamadandala kuti zinthu pa Malawi sizikuyenda kumachangamuka kumapita malo wopezeka zomwe tikufunazo basi
achita bwino kuwagwira ena anayiwala zot anasiya ana kuno. Malawi ndiyovuta chan! enafe tikhula bwanj
Mbuzi ndinuyo munthu wabwera kwawo basi. Asanapite ku Joni amachita chiyani?
Iweyo umati ayambire pati kulankhula ngati ulibe mutu
kak
East west home is best
Musaiwale kuti amadyesa akhwangwala osalima what more munthu wanyonga zake? May almighty God be with you guys.
Tiwarandire tiwarandire tiwarandiree
arendo athuu tiwarandireee abwera lero tiwarandireee!
pano siyinuso Makwerekwere mwava?
Ulbe kanthu ndiwe wa mw 24 pantumbopo olo pa Zambia pompa sikupaziwa Galu osauka iwe
Ubwino wake timadya thukuta lathu sitipempha or kudyetsedwa ndi boma, kadzichedwani
No problem kusaka ndipalipose kuno ku malawi kuchita kusowa ntchito or yosambisa galu musanyoze joz ndi dilu
angel chilwa
Only God knows, simathelo atsogolo lanu,yesaniso njila zina.
Welcome back to Malawi.East west home is best and thank God that your still alive guys.Don’t try to go back again to SA but seeing way forward for saviour. Our God we save is in control of everything.Your past gonna be a history and this challenge for reading survive gonna mek u grow
Kmaaa
Gamba kulimbichila ngani syangamanyika ? ? ? akusaka atujendekasyeje mwaoga kk
Welcome back to the paradise but full of parasites…………… Nkhuku zotchipisisa zija mudzisowaso, ma baby otchipa aja kuno sapedzeka, mowa osamba uja kuno mudzijiba kwinako muona kuti mutani…….. kunoso kuli K2000 yapepala
Koma na amalawi, mwenzi wose uno tidzingomvatu yokha yokhai, basi. muliuze boma kuti afikapo amapatsidwe ntchito kuti asabweleleso. chifukwa afikapo ena afikakale kutheba ena akukonza zobwelelaso.
Too bad
You are malawians,we are too ,welcome back home
Wa ku holiday umenewo after 2weeks abwelelanso
Kkkkkkkkkkk
TO FRIENDS AND FAMILY I JUST WANT TO ASSURE YOU THAT I’M STILL LINGERING AROUND IN SOUTHAFRICA GOD IS IN CONTROL!!!.WHEN TIME COME I WILL LET YOU KNOW BUT AS OF NOW I’M SOUND AND SAFE!!.
Iweyo ungopita akakugulitse phone yakeyo, chifukwa iwe ndi amene ulindi anthu oti uziwayimbira. Iyeyo m’mene anali ku southafrica, unamva kuti anathetsa ubale ndi anzake? Kulankhula mopusa, iweyonso ndimodzi mwa anthu ogula katundu mwakuba.
Hahaha muuzeni zenizeni amwene ndimbava imeneyo amagula katundu mwakuba asaa, komanso za deportee ndi nkhani ngati.
Chonde potipatsira nkhani mukuonjezatu pena kumamvako chisoni vuto ndi ulova,,, nanga sikuti boma lathu likulephera ku walemba ntchito achinyamatawa…ngakhale paonkha angathenso kuzilemba ntchito…Tamva
Ena chinakakha chodziwa bwezi ndalama ya passport atayambila business
WELLCOME GUYS .
Deal imeneyi ndikunziwa amene waipanga push siwina koma AKA hash tag Pitalaaaa.Cholinga fans ipangitse ma ID opanga expire anga ndi bread.The more I know Madolo omwe apangidwa deportee-wa abwelera ASAP deal imeneyo ikanika.
Zoziyamba dala, sindingawamvere chisoni ine..kulowa dziko la eni popanda ma documents or kuphedwa zimathekanso coz u threaten the security of the country.. Ife tikadalima kuno, mvula kuvuta koma kangachepe tikolola ndithudi nkumadya masiku nkumavaya basi.thank God u r back alive..paja ma guys APA South Africa amaotcha akafuna….phee in Malawi ife
komwe samaotcha ndikuti,komwe amampha anthu osalakwa kumati ndi anamupopa magazi ndikuti,?aliyese ali podalila inu zilimani,akupemphani ndalama yama documents mukufunawo?komaso sizinayambe lelo zimenezo.tazingoyamikani satana wanu kapena mulungu wanu kuti mukolola.sanakupemphe chisoni chako ali kale ndabale koma mabwezi awo owamvela chisoni osati sayenda iwe.umbuli osaona malo ndimayiko ndichocho.
Kulankhula kopusa,sitisiya kupitabe,next wk tili komko,iwe uli chikhalire kumalawi ukuganiza ungafanane ndi amene akuyendawo
Ada inunso NDE kayatu….
Udziyenda udzaona ndi kudzikindikira cifukwa chimene anthu amachokera ku MW kupita Ku SA….ndipo udzamvetsa kuti sikungofuna kusiyana ndi abale awo okondedwa kumudziko ayi koma kamba ka mavuto …anthu amakasaka kuti mwina nkukhala odzidalira atalephera kuyesa yesa kumudziko zinthu osayenda….
Komanso udzamvetsa kuti Ku Joni obwera si a Malawi okha a Ku Mzimba kapena MH…kulinso Nigerians; Congolese; Somalians; Ma Taifa; Zimbabweans nde kwao ….
Osamafulumira kulalata poti ndi pagulu anthu akuchemeleleni chosecho mukulankhura zoti simunadzionepo ndi kudzipanga experience.
Sindingapite ku joni nkumakayenda mozemba mudzina losaka ndalama…zaziii…kangachepe ndimapeza kuno kamakwana wamva Andre? So don’t think ndidzasirirako mapitidwe ake amenewo, NO..xenophobia mwaiwala kale alunji? Sanapemphe chisoni changa yes, ngat mmenenso ine sindinalemphere timaganizo tako pa comment yanga..ukagwere kutali mwana waulesi iwe… Aaaa hasan opusa kwambiri ndinu, mmalo mongolemba comment yanu explaining your feeling and altitude muli busy kupanga za comment yanga, nde kupusako kumeneko..ngati ndikuganiza mopepera osangosiya inuyo nkulemba zanu zanzeru zopotokazo bwanji…i can’t support za ku SA or mutandilozetsa mfuti mmutu..dzipitani mudzikabwerakonso opanda kanthu, tikaone kuti udolo wake ndi uti……ndikudikira chitsitu china chopanda nzeru chiyankhenso mwaugalu mmalo mongolemba maganizo ake pa comment box…mxiewwww
Mboleyanu akulu
Yako yobudukayo, mbuli, mbuzi
Kod fans mumakonda kulimbana ndi fan’s ya jon bwanj…. Sindinganyoze joni ndinali yani ndikukhala ku nyasalandi koma mulungu anandichitila chifundo mpaka ndili joni moti pano ndinaphudzitsa geri aziphwanga ndi sisters ngakhale ger sinapitilize koma pano 2019 ndikukapitiliza ger nde winawe yomwe ukuiziwa spoon feeding kwamakolo ako nde plz uziyakhula bwino uwu ndimoyo…
Achita bwino nthawi yolima ino
Sionse amene alibe kathu some of them they build good house they have properties that u don’t have they have money in their homes, don’t write your news like ur from Mozambique stupid
Interest & Fact
Thanks
I support Your point boss
Thx brozi
Uyowoyenge makola iwe nawoso mbanthu akwaa
Muwawonanso akubwelera komweko week ikuzayi anthu aketu ndi awulesi ndikulima anazolowela ganyu yoyitanila kawunjika Ku john ko.
Amapitaso through human trafficking
Amalawi bodza!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Njira mukuidziwa,zikayenda kubwelanso basi,
ayambila pomwe analekezeta
Inu pangani zanu! Mwatani kodi? unava kuti ali ku joeniko amangokhala osasungako ndalama ku Bank? Sibwino kutha malovu pa zomwe zachitikila wina pamawa ndiwe
komaso mwayi wa munthu uli pena pali ponse kaya ndi mtown kaya ndi kunkhalango kapena ku joeni
ndiye kumaupeza mtima please
Awathamangitsa nyengo zolakwika,adziwona Chaka chake nchino,first in history sheikh agulitsa bayabaya wa nkhumba,let me enjoy my Kachasu ndangoweluka kumene kudimba ine
angofikira kulembetsa sim card basi
Abwere ndikufuna anthu wondithandiza kulima Fodya
Mlimi wafodya angalembe ntchito munthu wakuti anali pa joeni kkkkk mudzienda osamangokhala pamodzimodzi ngati Bowa
Eya apeze poyambira
Ena aiwo amakhala kuti ali ndi ndalama zochuluka zomwe ankasunga ku account yawo ali ku joeniko ndiye enanu simudziwa izi
Kkkkk Ine ndikunena enawo alibewo
Mukhalila chocho azanu zikuwayendela mwandikwiisa hvy@ine nde mukazandiona dziko laumphawilo muzandithile madzi otentha
Deportee bambo sakutengera katundu kumalemba ngati munapitapo Ku xool ngakhale munaphuzira ya multiple choice. Amenewo mukuwaona ngati alibe poyambila koma pakutha masiku ochepa akuimbilani atabwerera mtima wa chikolopa bwanji Iwe uli ndi chani munthu oti umalandila R780. Mwezi onse Ku golosale uli ndi book la ngongole umakalembetsa mpaka kope kutha ndikusithitsanso
abwelako ndi chiyankhulo osati abwela opanda kanthu. adziwako mfwethu khuluma wena kkkkkkk
Axova!! Amathawa Xul Ameneo Lero Ndizimenezo
Mazoba a news 24 nthawi zonse kulemba mbwelela pasanathe mwezi akhala atabwelela kuno
Tawalandila.
Ndiye mwati ambiri ndiaku mangochi?lingokhala dziko basi
Please be professional in ur headlines presentation..dont twist to make it alito bit sounds bias. page of morons!!
Dou you say opusa??Opusa ndiweyo!
mukanangoti aMalawi apangidwa depoti osati mpaka abwera opanda kanthu chipongwetu icho
Ayambila pati limenelo kukhula funso poyamba amatani mesa kuno ndikwawo ukuyakhula ngati ulibe mutu bwanji
mwatipeza2 kwanu mkwanu
Kodi munthu akapita kwaeni zimasonyeza kuti sadzabweleraso?
eya ena sabwelako?
chachitika ndi chiyani kut awathamangitse?
Kkkk fuso limeneri? Iwe usadavepo kuti dziko la malawi lagwila anthu ochokela ku Ethiopia? Anthu amene aja amakhala kuti atani kuti awagwile?
No explanation yake sili bobo achiti depotee its okay koma angot athamangitsidwa u see mpake ndimafusa
Abwereranso within a week!! Malawi is the same as a helo who would like to stay there?…………..
‘Malawi is the same as a helo’.
??
Ena amathawa sukulu nde ayambe magobo akuno ku mpanje
Mukunamatu anthu ozolowera mavuto inu.Fans imene ikunziwa Jonzi boooo boooo singakhale Mpanje chifukwa cha deporteee abwelera pompano uwaonanso.
Abwelere kwanu nkwanu adha akhala jonz mpaka lit? apeze chochita kuno ku Malawi mavuto sazolowereka
Majaketi asaizi iimeneyo kulibe kuno siakomweko kwanuko akupita kokalembetsa ma SIM card kkkk
Tawawuze mazoba a news 24 azikhalila kulemba mbwelela kulila ndi umphawi wapamalawi
Kkkkk akhalira zomwezo zathu zikuyenda
Mulungu akadalikutikonderabe
Amene akuwayankhulawo anafikaso kale kale kuno moti ma Rand a mwezi uno alandila nawo
Legister simcard koma malawi wandionjeza kungot pot adati zizindikilo zamasiku omaliza zzachitika zosiyasinasiyana nde adat zizachitika kumalawi konkha? Eish
anthu aulesi, chase them plizzzzzzzzzzzzzzzzzz
Ukamati anthu awulesi ukutanthauza chani?
Bola inu Aphanvu bigy
Mulungu akupatseni zoochuluka
ulesi/?? what are u trying to.say
Ulesi wake uti kape iwe??
Watch ur mouth, my men!
ife trikomkuno tikupanga ma hustle . koma makapewa mbuli zawanthu
Wattie, Mfiti yosaukitsitsa iwe padziko lonse udzilankhula zamzelu
Ngati muli olemera pewani kuyankhula mozimva,mungayambe kutenga matembelero a Mulungu masiku ochepa ndikukhala mphawi kuposa ife.Ife amene timabwera ku Joni si anthu aulesi komanso tinaphunzira bwinobwino. Koma aliyense amene mutu wake ukugwira ntchito amadziwa mmene ku Malawi kukuvutira.Infact si anthu aku Malawi okha amene ali ku South Africa kufunafuna mwayi,kuli anthu kuno ochokera almost dziko lirilonse mu Africa,Asia,ndi mbali zonse.Ngati Mulungu wakudalitsani musamazimve kuchenjera.
ndakumvan, but atleast suggest y they r being dhased if they r @ the rightful place. stop commenting just becoz ur uncle z among the victims but attach logical reasoning, I HAVE SUGGESTED LAZINESS & I CANT WITHDRAW THAT, wamva mwana wa mmbwenu nd mdyomba?
kaya zanu izo ife tizivutika komkuno
the way mukulimbikila ntchito ku Joni,WHY don’t do same Kino ku Malawi.
Ukalemera udzilankhulira kuchipinda
komaso ndibwino kuopa munthu osauka chifukwa sukudziwa kuchuluka kwa zinthu zomwe chauta adzamudalitse nazo mtsogolo
which Bible verse said that when ur poor u shall go to S. Africa? tiyeni tizilima komkuno we can still do better
#Wattie sakunama nonse mumathawira Jonz ndinu alesi, mbuli zachabechabe mumathawa kumudzi kuno kunatani, enafe sitigwira ntchito tikupanga survive bwanji? Azikuthamangisani choncho ndiye poti simumva mubwereranso
Yes they nid 2 be smoked out they belong here ku Malawi enawo anathawa atapeleka zimimba kumamidzi kwawo alesi, manyaka awanthu
ATonie tayankhulani mogwiritsa ntchito ma phunziro ndi mzerutu zomwe mulungu anakudalitsani nozozo,
Inu tu ndi bigy ophunzira koma dziwanikuti anthu ena amapitaku Joni Ku ambiri ndikokasaka poyambira kuti azichita Tina busnes tao kumuziko mmadziwa kwathuko maganyu kusowa
Tilindixifukwa zambiri zomwe sitinakhalile ma professor ngati inu NDA amzanuo
Zoti mwina muthanso kutinvetsa
Enafe mukanatipasa maganyu kulima mmunda mwanu kuti tipeze mpamba sibwezi tilikunoko
Koma polimbikirapo palibe kumuziko,ulimi ukufuna fetereza mjomba
So try to feel kuti mutakhala simunadalitsike munganve bwanji
Tilipo ambiri mayiko osiyanasiyana ndipo timalimbikira ntchito zopweteka
Kugwidwa koteloku ndivuto ndithu bwana
Awattie
Like my page Sparks Electrical and see what we are doing here
We came her deported and rise up again pano tili ndi mapepala running our business and studying as well, very soon we will be oparating there !life is all taking risk
Muziyankhulabwino
Udakadziwa mmene anzako akutolela chikwama kuthebako sibwezi apa ukutokota zawusilu zakozi nyapapi wamunthu iwe
Osangoyamika bwanji kuti naa ngati malawi akuwoneka bwino ndi anthu ovepha kuthebako mesa kugwidwako ndinthawi yawo nawo
ena mwa inu mulibe ndrama zopitira ku John ena mulibe koka fikira ena zangokhala sanje basi
Ukunama iwe!
kwa amene akuti amene akupita ku joz ndi alesi mukunama chifukwa fanz ili kumeneko ndiimene Ikupangisa malawi kuti asinthe enanu pali inupo passport simukuiziwa ntengo wake guyz mukamalankhula muzizuyang’ana
leave them Mr Joe mtima wa nsanje umenewo anthu akudya ma KFC kamba ka joni president Dr h kamuzu banda anayambira ku kugwira ntchito iye ndindani uyu sanavareso ndi tayi yemwe wochemerera ma min bus awa
Mulungu ndiwadongosolo sangawataye nawonso ndi zolengedwa za za mfumu yamafumuyo