Days after some human rights groups called for the arrest of musician Mwiza Chavura over his rape song, Malawi Police are yet to arrest the artist.
Chavura recently released a song titled Ndizakupanga Rape whose contents sparked a heightened social media storm.
Police said last week they will arrest the musician and question him.
However, National police spokesperson James Kadadzera has told one of Malawi’s media houses that Chavura “is not in the hands of the police yet” and the law enforcers do not know his whereabouts.
In the controversial song, the musician warns a girl that he will rape her.
Following the release of the song, Family Rights, Elderly and Child Protection (FRECHIP) called on the police to arrest the musician.
FRECHIP said one form of sexual harassment is through rude jokes and suggestive stories hence the call for Chavura’s arrest.
A police akumalawi kusowa zochita mbuzi za ana
This police are very hilarious for sure kkkkkk koma Malawi sazatheka
Ku malawi nw dai apolice kulibe bt mbava, ndkumadabwa akumamang athu oti ndwoxalakwa afix nd mikang ali iwo,, kd ena xi athu apa akuxia a chaponda, omwe ali ndi ndalama xathu xomwe tithakuthandxikira kwa xaka xingapo,,,i dnt n kt achpatala akumeneto akulephelelanj kuwatenga apolice amenewa,
Ku malawi nw dai apolice kulibe bt mbava, ndkumadabwa akumamang athu oti ndwoxalakwa afix nd mikang ali iwo,, kd ena xi athu apa akuxia a chaponda, omwe ali ndi ndalama xathu xomwe tithakuthandxikira kwa xaka xingapo,,,i dnt n kt achpatala akumeneto akulephelelanj kuwatenga apolice amenewa,
Where there is a technical operation surely there must be a technical error.to my opinion it was a composition error.pali wina wayimba…umugwire chakuti, umugwirenso chakuti,koma simmene amabvinira azimai ace amenewa…Amachula za ulemu za zimai zoti sungazitchule pagulu.Why Chavura?
Police yaku Malawi z getting mad
Sure,there are other important issues in the country which needs such great attention by the police such as unethical conducts by these so called politicians,,,its just trivial to dwell on chavula on his song.
Futsek..kuxowa zochita eti..pali khani yommangir pamenepa..osamanga Gwaladi bwanji..yemwe amayimba nyimbo zotukwana ol de tym
For hw long dey wil b looking 4 dis man?is he in Malawi or abroad?
Kd bwanji mwasowa choti mupange post eti? Chavura sapangitsa kt chitukuko chikwere ndiye bwanji umaposta ma development issue coz mwatikonda nazo musiyen Munthu@ ma rubbish
Abale, Mwiza musiyeni. Mukufuna kuonetsa umbuli wanu bwanji? Mmmmmmh.
Forsake apolice plus Peter Muthalika i dont mind him full of nosense president
Ndikaimba nyimbo yolowa kumwamba !
Ndekut ndalowa kumwamba ? …nde pot nyimboi achinyamata ayikonda monga muziwa mayho !
Mumange ovelaso ndie
I saw him on Monday morning, he was chatting with George Chaponda, go and check there
He too is looking for policemen
Oimba ni igwililira muyenera kumanga uti stupid pipo serious
Are u telling me that the police can’t find him,I doubt. I just think that they are nt sure if they should arrest him or not,they are confused.
Analephera kumanga a police womwe anapha anthu ku mzuzu nde mukufuna kuti amange munthu woti wangoyimba nyimbo
Ndikanakhala ndilindimphanvu ndikanangobwela kuzango sintha anthu onsense omwe Ali muboma lathu chifukwa Malone moyangana pasogolo mulibusy kutsekelana madaliso ,Chicco that’s true baba I got ur point and ithink atsogoleliwa alindinthawi yosewela ndi anthu awoke mmalo motukula dziko lathu tikulimbana mkumawaika anthu kundende
Musiyeni chavula zongofuna kutaya nthawi boma mmalo molimbana mkumatithandiza ife anthu omwe tikusowachochita zaziiiii
Osauka alibe mawu
Alibeee ooh
Alibe mawu
Alibe eee
#Billy #Kaunda
Apatu a police bwinotu musaoange visaversa mutampanga tinting kuti asowe nkumanama kuti tikufuna timugwire kkkkkkkkkkkkk Apolice mukuteteza chani pamenepa za ziiiiiiiiiiii.
Kamangeni banja lamtsogolo likutha mtundu wa amalawi
looking for him where,on Facebook or WhatsApp? lazy police !!!
Sono mapic akuchokera kuti amene akumujambulawo ndekuti munthu sakupedzeka aaaaa ingonenani kuti alibe mlandu basi
Chavura tili Naye ku cape town Kuno….anathawa kalekale kumeneko
Muyambe kaye mwamanga akutumanio
Mwiza Chavura wali ku kaya ku bolero mu boma la rumphi kkk
kumumanga munthuyu sikwabwino, koma nkhawa yanga ili pa mwana amene akubadwa lero kodi adzachitanji akadzakayimvela nyimbo imeneyi?
and there is no freedom to reply shirt then i will deal with u too
can we see women commenting against police or the law on this issue…ma comment angobwera kuchokera kwa ndevu zokhazokha.
komanso inu a media mukukolezera nkhaniyi pliz shut up
mlekeni mwama pliz
Chavura iwe,chimutu chako!!!
Ukakhala pa wanted ndi police tulo sitibwela man kkkkk
But there is no freedom for talking shit, otherwise we will whip your ass.
Ndewina ndikumat malawi azasitha hahaha kulimbana ndi munthu oti sanalakwe ndi nyimbo chabe pamene ena akuba ndalama za anthu osauka mukungowasiya aaaah malawi ukupita kut
Myimbo ya chigawenga chimenechi ikumandikumbutsa malemba awa #mateyu 24ves 12 komanso yohane 8 ves 44
A police ndizakupangani rape mukapitiliza
Koma police kumalawi mmmm kkkkk koma amene amakutumaniwo akuzelekesani ndithu, mwalandil zingati kodi? Ineyo sindikumuikila kumbuyo chavula ayi, koma mau anga kwa inu a police munthuyu anakupepesani ndipo anapepesanso ntundu Wa Amalawi kusonyeza kugonja, mwina tikuuzeni anthu amene mukuenela kuwasaka zikuoneka kuti simukudziwa oyenela kumangidwa, zimatiwawa tikamaona mizimu ya anthu osakwala ikupita kumanda chifukwa chakuzindikila ndikubisa ziphuphu kwa anthu ankhaza ngati amene tikuwaonawa
Like seriously????
Kuli nyimbo amati ganja time and ikamayimbidwa ganjanso imadyedwa, sindinaonepo munthu atamangidwa double standard…azimayi adavulidwa kulilongwe palibe adamangidwa….wina akungofuna kutchukilapo apa…
nonsense
Looking for him on what grounds? Thats insane and bullshit trash for the Police. We respect our police very much that they cant be busy with that very minute issue!
Mmuuzeso peter mnthalika kt chibwezi pakati paine ndi Gertrude wakeyo sichinathe moti pano tikuphana sizinaoneke
GAYZ OSAIWALA THAT OUR POLCE THEIY WORKE UNDER DPP SOWHAT EVER THAT DPP WANT, OUR POLCE THEY GO TO DO IT NANGA CHAVULA WATUKWANA NDAN? TAKAGWILENI NDUNA 7 KU DPP, NGATI NDINU APOLISIDI ) NDICHIFUKWACHAKE MUNAMANGA MUNTHUWAMOWA YEMWE MUKUT AMAFUNAKULANDA 30,000 KWA PETER ZOWONA PRESDENT AKAMANGE MUNTHU KAMBA KANDALAMA YAUNISIYI KKKKK, BWANJI OSAMANGA OPELEKA CHITETEZOYO ? KENAKA MUKAMANGE MAHURE ONSE DZIKOLINO THEN OITANILA MAMIN,BUS SIMUNAWALEPHELA?
MWIZA CHAVULA ANAVAYA UK
Mayaz,chimutu chake sichingakwane mu ndege.
Mukangoasiira ma music association of malawi, cosoma ndi malawi music. Osati a police
first chaponda plz not jst a song to dance you plz poor police men
maluz avuta pa mw
malawi police pezani zochita zina plz,iyi sinkhani yomumangila munthu,
Zankutu
Ali ndi phulusa ndani apa ndikufuna kudya bwemba
Kodi sanamangidwebe mpakana pano?
Mwiza Chavula adathawa.
Wasting Time And Money.Am Sure The Purpose Of Those China Donated Cars Is Not To Ease Mobility In Arresting Musicians.
So many such songs why only one person? People are cashgating K500m and left free
A
Just ban his song and let him flee,FULL STOP
koma flames sizamvadi yoooo
Mesa Zinatha Akumufunanso Kachingat Tizit Sadamumange Mwina Sindikudziwa Ndine Tandiuzekon Maguyz
Kod mukungobera zomwe yanena zodiak bwanj?
CHAVULA MUST FACE MUSIC 4 HIS MUSIC!
Lucius anaymba life .adamangidwa? Now he dnt hv mony chvula thats y? Chapinda .mkhitho anatan nd chasowa? Nowdays justice fading out
Do you desire Wealth, Riches, Fame, Sport light, Powers to perform SIGNS and WONDERS, you have business ideas but no finance, Unlock your destiny by joining the Illuminati occult today, you have full access to eradicate poverty away from your life now, don`t miss this opportunity. Add us on Whatsapp +2348077436656
NDE kuti a police anthu owagwira ayamba kusowa eti?ine ndiyimba yogwilira amuna tiwone mulandu wake kkkkkkk
Ndakaika ngati dziko lathu la Malawi tingadzachangamuke apa kuteroko ndiye mwati mulandu wa mwiza ndiogwilila?
Yes. ..anahwililila mu lyric kkkk
A police wo alibe zochita zina?
who has bn raped ? How many pple implicated in state capture , stealing the the state money bn arrested? Chaponda’s case and his colleagues are still there , pple who have got millions of kwachas robed from the state, walking tall , what is so special of mwiza’s song to awaken you pple senseless so called law enforcers ? Please leave that boy alone , deal with those crucial cases of millions of kwacha and later come to arrest Mr chabvula. This country is really run by mafias , they leave those they deserve to be handcuffed and go for the civic educator like Mwiza. I rest my case
Mwiza Chavura Mwiza Chavura
Kkkkk kumalawi abale mulipa pamavuto ndithu apa mwamumanga muthu analanda ndalama manja sogoleli waziko malo molimbana omwe amamugatila sogoleliyo
Ikanakhala kut nyimbo imasintha munthu. .malinga ndiuthenga omwe ukuveka munyimbomo um sure ndibwez amalawi titasintha ndi national athem (nyimbo yafuko lathu) koma nyimbo ija chiimbirenicho amalawi nsanje yokha yokha. Kutanthauza kut nyimbo singasinthe munthu. .leave chavura alone
hahahahaha
amangidwe
Iyaaa palibe khani yomumagira
Malawi mene wachepelamo sanamugwirebe nanga atathawila kunja nde zingathe zakazingati
why not chaponda
Chaponda tinamponda kale.
Seems a police a ku Mw saziwa tcito yao ndpo albe chocita
arresting him aint a solution this guy z getting mad..akufunika kumental uyu!
Fokolo go and arrest real criminals out there..leave him alone.
kkkkkkkk malawian police amakhala bzy nkhani zopusa
nkoyamba kumuona chavula,ngat ndiamene Ali pa chithunziyo….NTHAWI ZONSE NDIMA USE FREE.FACEBOOK.COM
A chaponda anaba chimanga aliku chichiri Kod???
Anaba zindalama zaboma aja anamangidwapo ndan?
Koma chifukwa cha nyimbo chabr imene sinapase umphawi muthu aliyense ndye amangidwe??? Zimenezo ndye zopusa muwuzane nonse amabungwe nd a police anuwo kumeneko ndiko kupanda mzeru mituyo mumangoseza et mxie
okae
The police must go to hell
kkkkkkkkkkkkkkkkkkk