Twenty two mattresses which were stolen by health workers at Chikhwawa District Hospital have been recovered by Police.
The mattresses were among twenty eight mattresses that went missing at Chikhwawa District Hospital earlier this week.
They were reportedly donated to the hospital through a project and were meant to be distributed to health centres but were stolen a few days ago from a storeroom by workers including senior by officers.
Reports show that maintenance supervisor at the hospital opened the storeroom at night and started distributing the mattresses to some members of staff.
Police were informed about the issue and they recovered the mattresses after raiding homes of hospital workers.
Kkkkkkkkkk
Apolisiwa so ndimakape.Akukanika kumanga Joyce Banda ndi Chiponda,kumalimbana ndi anthu otola matress kmaso akutha kale.SHURT UP CHIKWAWA OFFICERS
Kodi osakangogula anu bwanji, ndalama mumalandirazo ntchito yake ndi chani mpaka kufika poba matress akuchipatala.
Guyz you can’t be serious, kuzolowera kuba mankhwala mwati komanso zogonera za odwala. Your so stupid guyz am telling you, ndakwiya nanu kwambiri.
Ndipo boma likuyenera kukuyimbani mulandu okupha odwala amene abwera ku chipatala kuti adzalandire chitandizo
Ndindalama zingat kut ugule matress mpaka kuba matress oti pamafera anthu kalanga ine kuzipasa matsoka ndi minyama
kuba anayamba ndi President ndi nduna zake nde mmati apanga bwanji anyamatawa
Osawamanga anthu abwino zedi amenewa ovumereza mmane zithu zilili mdziko guys ngat simukuba kutchito kwanu zanu izo mudzafa amphawi akuyambitsa mtsogoleri wadziko kenako nduna zake kuba inu nde otan kt musamabe ? Kumangofunika kuchenjera osamaba moonetsala chonchi koma kumaba ndithu mungazadandaule mtsogolo nthawi ndiyomwey
Punish the thieves.
Mukadwala muzikagonera chani Anthu Ozunza inu
WHERE WERE THE GUARDS?How about their moral integrity, core duty and responsibility (ies),empathy, passionate!!!????
Hhh
Inu mumati akakudyerani kuti kuti osakamanga anthu amene akuba ma million ku capitalhillwa bwanji
Koma Malawi mpa na kumaba mattress am zipatala?
Wankachisi amadya zankachisi kkkkkkk
If they manage to steal mattresses what about drugs??
Inu mudabwa chani azikaba aku capital hill wachipatala ndindani ,,,,,,,,
Achita bwino.
Just forgive them…. Forgive them…. He who never had committed any theft must arrest them…..otherwise, just forgive them
my people my people kkkk nothing to say , zafikapa mpaka kuzembelera chovara chako chomwe chili pachingwe kut ube
Kkkkkk Oven Medson Mankhanamba onan nawo izi kkkkkk
Kkkkkkkkk
kkkkkkkkkkkkkkkkkkk matress gate
Akwidzingeni! Anjateni!
Alekeni Vuto Siioo Vuto Ndi M,nthuma
zokubadi zikasowa umaba zovala za ana. ako eti
Ndiye Ngat Ogwira Ntchito Ukuba What More Munthu Oti Xakugwira Ntchto He/she Is Not Earning Anythng,u Fools
Nsena ndi choncho zake zomwetu koma kumazibelanso mapeto ake aziti boma silikupeleka matress
Following
koma maluziwa amenewa eeeish!
Sack them so others can take a precaution
Ndiye awamanga kale ?
Fire them
Kodi dzina LA chikwawa linatha?ndikudabwa chikhwawa
People eeeish too much desperate with money everything stilling nooo we need to change
Lock them all!
Mmene akubera soya wa ana otsika scale anambwa amenewa, angalephere kuba Mattress.
Cashgate,maizegate,matressgate ……list goes on thats what put my malawi on the map seems we are known for nothing but stealing.God heal our nation
anthu akuba matress akumangwidwa koma okuba ndalama m’muboma akuyenda freel range ena a maize gate, cash gate, tractor gate, shame shame shame i mean SHAME
Arrest them fast
Thats one way of reserving our animal
ndakwiya zimenezi kwambiri
Arrest them
Shame weh,mayb they stopt getn paid.
they must be arrested and brought to justice.
Chikwawa
Chikhwawa or chikwawa?