Inu amene muli pafupi ndi Mtsogoleri otsutsa a Lazarus Chakwera, ati muchite machawi kuwamanga zingwe ndi kumapita nawo ku chipatala cha anthu a misala ku Zomba.
Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika anena kuti a Bambo Chakwera amene amatsogoleranso chipani chotsutsa cha Malawi Congress akufunika akaunikidwe mmutu ndi madotolo odziwa za matenda a misala.
A Mutharika amanena izi poyankha Bambo Chakwera amene anawanyogodola iwo kuti ndi kathyali psipsiti, mkulu wamabodza mwina ngati dyabulosi amene.
“Ati ine ndi wamabodza,” anatelo a Mutharika pa mwambo wa Ijitima wa asilamu. “Dikilani ndikuuzeni munthu wamabodza. Munthu wamabodza amanama za maphunziro ake.”
A Mutharika ndiye anafotokoza kuti a Chakwera sakamba za chilungamo pa maphunziro awo.
Iwo kenako adaonjezelapo kuti a Chakwera atha kukhala kuti ayamba matenda olondola dzuwa ndipo akufunika kukapimidwa ubongo.
“Ndipo akuyankhula a Chakwera zingokhala ngati zoduka mutu, amenewatu mwina ali ndi misala, atengeleni ku chipatala cha anthu amisala akawapime,” anatelo a Mutharika.
A Mutharika ndi a Chakwera ayambapo kuthilana nkhoko pamene zikuoneka kuti zokonzekela chisankho cha 2019 chayandika.
A Malawi ena adzudzula atsogoleri awiriwa pa makhalidwe awo achibwana olimbana ndi kusinthana mawu ngati ana pamchenga.
ZA KWANU KWA CHONDE ZIMENEZI
Politics in malawi still immature.
Muntharika 2019 paulendo akamere kaye mano,2019 yanga sadzayiona,
Munthu wa nzelu akazuzulidwa ndi anthu atatu amayenela kukhala pansi nkuona vuto lake apo ayi amazimangilila basi nkhutukunve
Kkkkkkk followimg
Iweyo Peter ndamene ukufunika ku mental mkamwa mopanda manomo
Zaziii opanda manu nkamwa
Ofunika kumento ndi amemeyu
Kusowa chonena ,pogwira zinthu zikamavuta umaona ngati anthu akudana nawe kenako kumaona aliyese openga ngati pali munthu mtsogolere opengetsetsa pa onse atilamulira muno ndithu ndi ameneyu akupengetsa azakeyu achibale ake kumangoyang anila mwina akudikila ayambe kutola zitsipe ndi pamene apange kanthu,dzana timalangizidwa kuti nkhondo ya mau sitithandiza pano ndi uyu akupengetsa anthu
Apengatu Apresident,kapena Ndikutenthaku?..(it Iz Not Over Auntil It Isover).
Iweyo ndiamene ukufunika Ku mento nanga mdala wabwino bwino angamamete nchoncho
The opposite is true
Kodi Ku Malawi Kuno Mutsogoleri Kkkkkkk,
Andale onse ndia mpwesa amadyera limodzi asamatipusitse
Walitata
Za Dziko Zisiyeni.
zopanda ntchto bola kumangodya mgaiwawu
Dziko liri pa #moto
Zingokuvuta mapuya kkkkkkkkkkkkkkkk
Koma chawuta wamphavu atisogolele munyengo zino kopanda ambuye anthufe tivutika abale
oh!
This don’t make you any better Mr President!! You both childish and immature ! You both practising politics of dark ages
kkkk Kwa ineyo ndimaona kuti onse Peter,Chakwel,ndi anzawo wonse ndiwopenga misala,chonde anzathu inu muli kufupi nawo mupite nawo ku mentol.Chisankho tisanayambe.
Mbolo yako Peter Mutharika munthu wakuzibabwe iwe udazolowera dziko lovutika
Well said bigyy ndi a mpwesadi usawi chichi
kkkkkkkkkk
zowona
malawi walero azitsogoleri nthito kumangonyozana bola voti munawavotera iwo zikulowa ovotanu mufundo zachitukuko zija pano akukupangilani ntchito zonyozana .ndale sizinthu anthuwo ntchito zawo ndizimodzi
Kkkkk komatu ndi chomwe wavala iye kumutuchi akuyenera kuyamba ndi iye…hisaaa!! Mbwiyeee!!
Kkkkkk koma Malawi kodi mnthu sungasinthe kukhala wakunja am tired of Malawi shaaa
Asilamu anzanga za ijitima si ndale ndi zamulungu bwanj mukumuitana satana ngat ameneyu satawasa,alibe twahara uyu aaaaa dziko kod likupita kut
I think the president himself is mentaly ill. Why is he talking foolish things lyk this? Is he regarding himself superior?
https://free.facebook.com/l.php?u=https%3A%2F%2Fwww.malusomusic.com%2Fsongs%2F3101&h=ATMlJD4u3dsPDVaUWFbMmgFhkdCA9i6lB9djUaNbw8gd1w2IJhYR-C2MzHQFoHlEPYwfd76Bf_t81MnmXkJxDb0pxRGHw1-d4DpCTPl5vn7lsSOiFjlvwu9SHp5p5s7HaIkdQZ1f8ia0YNKa&enc=AZOksxyjKzr3LH4Gc5NXbTfalrLufM2aaFmlWepywJ9f-S27JxRURQrqXMKQJAThkORjn0kxvtJ5tMmK712NXPgycSYfo2_7hFRDBC_LJxWTWzVh-eaDpGlQLecf71caSVbg06aopKHP27Enn7jbdPkjwn8a3eGBMjz0jGf3hZxUfWg1EAsfB4vhQLpqyM8x7D9MaD94iHXf2HJCTOxgQyw6qtCslZd4nLS3NlS4ltyri4YVNECC6-Wb8lrQ0rEfqUvco9q14QJVqOCmDl1Ya20jfBC0vqlIlWvpqAaBqrdMbEhll0ZftiU1I8GVzyqGxh8fNEzPrLx7ttICDuxvMuDUIjnCNUfq_4W51R530oPxCjL40FYMwVIJ8mkRuxC-FRM&s=1
Mmmmmhuu ndale ndi uchisuru
NGATI CHAKWERA AKUFUNIKA KU MENTAL NDEKUTI IYE AKUFUNIKA ZIMA INJECTION ASIYE KUTIBWEBWETERA IFE…..TATOPA NDIKUMVA MAWU OTI TIYAMBA/TICHITA POMPANO…MPAKA LITI?? ZINTHU ZIKUONONGEKAZI NDIFUMBI……TIZIWONA MAGETSI 4HRS M’BANDA KUCHA,TATOPA
Do you consider those wwho can’t read your language on your page? hw do we read now? even the world wats 2 learn and appreciate what goes on in your country,
You come from where?
A Mbc Nu Mumalemb Zamkutu
basi kalowen kumentoko. ine zisandikhuze.after a Chakwera then a Peter nao akalowe salibwino ndithu. enafe tizikupezan komko m’mbuyomo kkkkkkkkkkkkkkk
A president ayiwala kuti aluza ma by elections because of kulankhula kwamwano chonchi, tikuwona zonse and our time is coming in 2019
Mantha madara uyu yamukulira game APA nanga ndizolankhula zimenezi
That’s how you can know the person without mfundo. We don’t attack person koma mfundo yomwe wanena. DPP has failed and it’s a fact. You can’t fool us.
Boma la DPP lawononga ziko.Sindikuziwa kuti pa za pezeka boma lonyasa ngati la DPP.Ndiulemu chabe anthu amuziko kunena kuti ndiwe musogolere.
Munthuu akufuna atwinanso ndpo iyi ndi nkhndo akumenya.ndpo sangalore kt aluze ich nchfukwa chake iye akuipisa anthu ena
Ulenje umasimba wako
GALU IWE NAWESO UPITE KU REHAB
Let us wait for 2o19 to see who is wapwesa
mulibe utsogoleli mwachakwela DPP izalamula boma mpaka yesu kubwela
Rose Fologonya
Umayamba kugotha nkhutu, imfa ikamabwera
Adzavotele chakwela ndianyawu
Was misala ndiyeyo APM
Che petulo chikond alibe munthu ukamuna mzako akudwala umamutengela kuxhpatala kma iye angolengeza amatero
ndiinu a chitsilu a president mmalo molimbana ndi mavuto mukuyambitsawa mu kuyankhula zopusa zopanda phindu Ku dziko
If Peter can win again 2019 then 2024 we are going to see k20,000 or even K50,000 Note and peter is the worst Leader forever
Qq
anthuamenewa alakwachani? kapena akudwala chani?
Adzavotele dpp ndi mbuli zolima Nandolo, people who dnt know even to write the word, blind loyalty and its meaning. Tonse timadziwa kumene kumakhala mbuli zimenezi and there remote areas.
Respect Ur Friend To Receive Respect Too.Some Words Used By De President R Somehow Showing Rude.
Bwanji osasutsa mfundo zomwe Chakwera wa nena ndikungoyamba kutukwana Chakwera.Sadziwa Debate ena ndiitane ana a std.5 yakale awauze kuti timkatani:its better to be a nurse than a teacher because a nurse wears a white uniform
Its not good to be a nurse because nurses touch corpses which is a healthy risk as one can easily contract diseases.Thank you the chief proposer and the chief Opposer……..
Imeneyo_Ndiyontchito,yaLEAFDER.OF,Opposition
KKKKK guys look at that madala,sindikuziwa ngati Ali ndi Mano mkamwa,ena alowe pls
Sunati ukodza magazi
Mbuzi iweee mxiiuw
ALIYENSE NDIWAMISALA ZIMANGOSIYA % YAMISALAYO MUZIYANG’ANE KAYE MUWONA PAMENE PAKUYAMBIRA MISALA YANU. KODI ZAYAMBIKA ZOMAIMA PACHULU KUMANGO LALATA. UDZA APOLICE KUTI AMUGWIRE OSATI IFE AMENE TISALI AMISALA
kkkkkkk ndale ndye kaya.
kma zimakhalapo!!!!!
KKKKKK ULI BOO! NYAMATA WA PA MULOMBA,
Guys MCP singadzalamulirenso Malawi and tazivotani ndipakamwapo tidzaonana 2019 ineyo ndi wa DPP
Chakwera akuynerad kupita ku metal akufuna atiuze kut inchocho ndichomwe chili ndizeru kuposa peter kungoti ndiwe osusa panga zot magesi asamazime kuchoka pa udolo wako utatero mages osazima kusithj zithu man mavote ose azakhala ako koma man yesesan chitapon kanthu musamangosusa zinthu zopanda pake aise wayeneradi kupita ku metal akakupime mwina uzisusa za mzeru ndale wayamba liti iwe sungawine yesu sakondwa nawe posiya kutumikira wangobakoso ku mpingoko kape iwe obera nkhosa za ambuye
Wamisala…anaona..nkhondo…chenjera…ndi…nzuli…wakowo
Useless Proffessor
I bad man mthalikayu nde akufunka ku meto
kkkkk iweyo wakutumayo nonse mukufunika ku misalako.
Andale onse angopita ku chipatala basi muja anapitira Vincent Wandale. Kkkkkkkkk
Apiteko nd nyani wanuyo aka munthalika
Dziko la Malawi limeneri osangogulitsa tikhale a Mozambique
This page is so funny
Boza yake imeneyo nayeso akufunika komweko wayamba kunyengerera anthu sopano galu uyu ndiwakuti
Bola usagweso pitala ndi Biphiiiiiii
pitar ni wakuba pompano amatulutsa 2000 ndiye pano akuti 5000 wakuba meneyu wamisala ndiye akamapanga ndalama nipamene amabela
pitar ni wakuba pompano amatulutsa 2000 ndiye pano akuti 5000 wakuba meneyu wamisala ndiye akamapanga ndalama nipamene amabela
Day’s passed, day after desolate day and she was utterly alone.Hatred and Resentment built up inside her and she could hardly go near her mother.She had been standing in the rain for more than five decades,hoping she could see a light at the end of a tunnel but to no avail. Malawi is one of the privileged countries in Sub-saharan African and perhaps the best and most affordable recreational centre in Southern Africa. Its amusing nature and stunningly amazing geographical position, rich in cultural norms and friendly people ultimately makes the warm heart of Africa an attractive place for tourists.Though its political,economic and social landscape is marred by greedy,malicious and desperados politicians.Many argue that economically, politically and socially Malawi has the most comprehensive, well thought out and cohensive plans on how to run the affairs of the country.But what leaves many in suspence is why up-to-date the economy of Malawi is still in shambles despite its well thought out plans? I mean, why Malawi as a nation has tremendously failed to boost up its economy? Why are we wasting our time formulating and reformulating various sophisticated stragies and putting forward new useless measures instead of just implementing the already existing strategic plans that are gathering dust? I never got it! Let me backtrack alittle bit. Long long time ago, Harnghzou G20 summit made a number of recommendations in which it featured some significantly incredible tips on how to make Africa Great.I read the article written and shared by Li Yang with great interest. During this summit Harngzhou emphasized the need for support for Agriculture and Agribusiness development, and the importance of broadening ,deepening and updating local knowledge base.The summit also went on outlining the significance of concentrating on green technology and investing in energy and mining industry; and focusing on new industrial revolution. And this made me think deeply about home. Now ,after reading the recommendations made by Harngzhou G20 with soberness, one can easily get it, that it does not require Sherphard Bushiri to challenge the government that he can deal with these problems in 48 hours.We already have capacity an
Eeeee!! Amwene,,,,, comment yanu yatalika! Don’t do it again!!
hahah. .where did you find time to write all this?
@MadalaMadala,, hahahaha after magetsi kumazimazima ndangoti ndilembeletu, za Week yonse lol……
Mza week yonsed kkkkk well said though.
There ‘ll Be No Presdent Other Than Ngwazi H Kamuzu & Bingu
bambo noel katete zisiyeni zangwazi ziwirizo palibe wabwino pamene paja kumbali ya nkhanza ngwazi yachiwiriyo imkafuna kupha amalawi onse pakamodzi atasunga ndalama kunyumba kwake mankhwala kusowelatu nthawi yomweyo mafuta agalimoto kusowa zakudya kukwera mtengo inali imfa imene ija bambo katete kkkkkk
Chimwemwe ndiwe wabodza panopa zimene wakambazo zupezeka nanga athu 20 tsiku limdzi ndi kamuzu angovomelezani zani agogowa zithu zawavuta
not Bingu bola kamuzu
Chakwera moto kuti buuuuuuuuuuuuuuuuuuuuu…………..am with u
wamisala ndi pitalayo, tatopa ndi mbava zimenezi, tionana, 2019.
hahaha
hahahaha
Kma aixe ndeee wamumasulatu, kkkkmkmmmm
MR IBU wapengadi iwe
kkkk owooo ok
Wamisala anaona nkhondo, koma ndie tonse tikhala amisalatu mdziko muno, chakwela wamisala, Wandale wamisala, ndiye wabwino m’ndani? Kapena iwo amene?
Kkkkkkkk.Naneso2 Ndimaganiza Kut Iyi Simisala Muthu Wadzelu Sangathawe Tchito Yamulungu Kuthamangila Za Ziko Lapansi.Bac Mupelekele Akayambe Kumwa Raaaa!!!
Chakwela vote yanga ikudikila iwe Basi enawa andilephela…chomwe akuziwa ndikupange ndalama moti apange magetsi akuti ayi koma tipange ndalama..zazziii
Peter timutengere Ku chipatala. Ndiopenga
Kodi awa ndi Sheikh mutharika ?
kkkk
Tingowazolowera awa nthawi zonse zokamba zao mbwelera zokhazokha
Haha …… Misala ngati imakhala ya Chakwera bola nane ndikhalenso wamisala….
Ndipo ngatidi, watero big man akunena zoona m’busa m’utu mwake simukuyenda bwino ma vesi athawa
Kkk Bwampini Ameneyi Wapenga Ndi Magazi Wapopawa
Mukadzangowona wamisala akunena anthu amene ali mentally fine kuti ndi wopenga (if s/he is lacking some sense of reality tht s/he z not mentally stable), mudzangodziwiratu kuti misala ya munthu ameneyo ili in incurable state ndipo sasowekeranso kupititsidwa ku Bwaila(when in central region) or ST John of God(wen in North) but straight ku Zomba mental Hospa and prognosis z most of the times poor in tht state, endless kakakakaka
Kape uyu wasowa zolakhula eti?
kkkkkkkkk koma mbudzi ya munthu imeneyi
pamene mukunyoza otsutsa mpamene mukuwapatsa zkm a pzdnt mutmenyera kapn 2019 mcp boma!!!
Wofunika Ku mento ndiinuyo A Dpp ndi ma 5pin anuwo
munthu wamisala,saziwa kuti iye ndiwamisala, koma amawona misala ya nzake! ulendoooo 0019
Wamisala ndi amend akukanika kuchotsa mbabva zake ziri m’bomazo. Ubwinowake wamisalayo anaona nkhondo ndipo anthu anathawa angakale iyeyo
Koma kumentoko nde kukupta anthu ofunika zed…wandale naye alikonko
Ndiye zopusa apite iyeyo mithalikayo
Sindikudabwa kwenikweni bcz munthu ukamamuloza mzako zalazina umaziloza wekha ndiye apa a Munthalika muyiwara kuti zala zina mukuziloza nokha openga ndinuyo mwachidure
zoonadi wamisala amaona anthu ngati a misala Kulibe dziko ndinamvapo akunena zoti chiphaso cha unzika chitha mphamvu expire date boma malawi simisala imeneyi chimene mkuyenera kudziwa a malawi si openga
Haaaaa apa wamisala nde ndani.
Kkkkkkkkkkkkk apitedi
bachedwani mkumaona misalyaanzanu muzindikira kutacha.
kkkk komaku dpp kuli azilangizidi kapena atailila akungomwa frozy?
You should also go to mental hospital because you are taking the country down to the drain bwampini.
munati a wandale apite ku mental in within two weeks time mukutinso a chakwela apitenso ku mental. mainly who is mentally disturbed among you three? izi zi kuchitika chifukwa chosavetsetsana.
muthalika yikumuwawa 5-1 dziwa izi 2019 mcp boma kulibe kubela mavoti dyelatu ndalama zabomazo ndiwe mbuzi
ayambe iyeyu kupita Ku mental
Sukugona naye tulo Chakwera usadati
Wamisala adaona nkhondo. Nyumba ya chitsiru siikupsa. Blanket la chitsiru sakuba
Miromoyo bwanji man! !!!!!!!!madam akumenyani? ??????? Kkkkkk kkkkkk
nkhanii amuthaliwa ndi dausi mwachangu masankho asanayandikile apitiletu kumento akawachape timitutaoto.
nkhanii amuthaliwa ndi dausi mwachangu masankho asanayandikile apitiletu kumento akawachape timitutaoto.
We are waiting to see who the real mad man is…
Wamisala namene afuna kupanga 5000 imodzi
Peter ndi amene tikufuna apite ku chipatala cha anthu amisala, chifukwa mutu wake suwukugwira kupa k5,000?
hahahahah if chakwela is mentally in mind why akanena zithu dziko lose limagwedezeka ngat chivomelez wake up malawi let’s have change
inu nde kayansotu mpaka K5000 zoona?zakukanikani zinthu ine ndiye ofunika kumental ko
kaya ndweyo kapena uyoyo ari nd misar kma iwey vot yanga su iyiona
koma ndie odwala Ku mudziko akuchulukatu hahaha
kkkkkk mental izaza
kodi 5-1 uja sakukwana
Dpp woyeee!!!!
Mutharika mumuona akubwerera kwao 2019 ndipo amene amuuzawo amuuzenso kuti iyeyo ndiye ofunika ku mental
Tivotera a mental omwewo
MCP ikuyenda bwino kwambili pansi pa Chakwera. Mwezi watha womwewu tawina ma MP 3 a nyuwani achinyamata okhaokha. Ma khansala 2 achinyamata. MCP 5 – DPP 1. 2019 kuli ku sesa.
Ipose yakoyo? mlakho
Amuthalika ali ndi ziwanda zosaneneka ,zoona anganyozemunthu pa zochitika za chipembedzo,pakufunika kuwapempherela ndithu mkuwachotsa ziwanda ndithu,,
Mu ulamulilo wa peter from 2014 apanga k2000 pano akupanga k5000 three years zokha nanga atati alamulile ten years adzapanga one milliom, zikuwavuta akuluwa sadziwa kuyendetsa dziko
My vote will go to MCP
Are those words really coming from a state president? Keep calm and be smart my president. Don’t lose temper as somebody who wants to go to mental hospital
APM ndiwaukape!
Why ku Mental?Otsutsa akati apite patsogolo ndi ntchito yawo podzudzula zaphada zanuzo m’malo mwa ife omwe tilibe”good platform”basi alakwanso?Why can’t u jst check where u actualy went wrong & make abit ‘f collections or else accept that u’v failed to lead us?Muziona zaulendo wuno,kkkkkkkkkkkkk
Wamisala ndi amene waona misala yamnzake Chakwera akamapita ku Zomba pItaLa akhala akupangidwa surgery yamkamwa
onani kukamwa ngati chule
Misala Ya Pitala Akufa Nayo Posachedwapa Coz Ndichiwewe,imagine Wandale Wamisala Chakwera Wamisala iiiiiiiiii Kungodziwiratu Kuti Wamkulu Mimbayu Ndiye Wamisala{aka Pathological Lier)
Uyuyu yekha nde sakumunamidzira
Why ku Mental?Otsutsa akati apite patsogolo ndi ntchito yawo podzudzula zaphada zanuzo m’malo mwa ife omwe tilibe”good platform”basi alakwanso?Why can’t u jst check where u actualy went wrong & make abit ‘f collections or else accept that u’v failed to lead us?Muziona zaulendo wuno,kkkkkkkkkkkkk
Bwino nazo muyamba kugwa nazo chifufu Biggie
Hahahaha mpaka pitala agwe chifufu
Kkkkk #Nyasaland iwe ungopengesa anthu #misala
Nthawi zina tiziyesesa zochita zathu zizitha kumasiyana ndimmene tionekela,sibwino kuipa maonekedwe ndizochitazathu zimene.Palibe mzeru kutukwana Pulesidenti.apatu ndikochekera kumene mumasowa khalidwe.Yes tikuziwa kuti zolakwika,tiyeni tikambe zimenezo,osati kutukwana.
Ukawauze amako zimenezo
Misala Ya Pitala Akufa Nayo Posachedwapa Coz Ndichiwewe,imagine Wandale Wamisala Chakwera Wamisala iiiiiiiiii Kungodziwiratu Kuti Wamkulu Mimbayu Ndiye Wamisala{aka Pathological Lier)
Uchindere
Ananuso Anzanga Achisilamu mukumpasa kuvala chipewacho sanadulidwe ameneyo ndi haramu imene mukupangayo
Za utsilu opusa inu ndi president wanu ine ndilibe president or mp
Ndili mkati mogura zidza zanga zankhondo zatsala pang’ono kukwanira mwatizolowera kwambiri
Mr Muthalika pantumbo panu mwamva, misala yanuyo yotulutsa 5000 mwati mumpake wina, nyapanu mwamva
K
Chakwera must fall
Chakwera is rising while mutharika is falling taonera zisankho zadutsazi
KAOMBE NDALETU IZI… Kkk.. Oho….
Ife timavotera zimenezo….Mpwesa womwewo…5-0 ikuwawadi zoona,I can see the side effects.
CHAKWERA IS FAILING TO BRING UNITY IN HIS PARTY. WHAT MORE A COUNTRY, CAN HE MANAGE TO CONTROL OUR BELOVED COUNTRY MALAWI? I DOUGHT
What more unity do u want chipani chawina ma byelections pompano bcoz pple worked tirelessly together as one. Which party is disunited btwn dpp and mcp here.
Mr Mpeketula tamachangamukani moti nonkha simungawona ,ngati anthu onkhala ku state house anavotera MCP who are you?
jack up my friend. This is by election not national elections. Its just some parts of malawi where mcp is settled. Come on 2019 elections you will agree that dpp is a powerful party in malawi
zoona zimenezo ampeketula chakwera sangalamulire dziko ndiponso sangawine dziko ndilalikulu ili angafunenso tambala wakuda ndi ndani
I have seen thy comments, koma adzavotele dpp ndi mbuli za athu . People who dont know even how to write the word, blind loyalty, and its meaning. Mbuli zolima Nandolo. Mbuli mdziko muno tonse timazidziwa komwe zimachokera.
kodi inu mco yo yawina mipando yonse musatinyansepo apa kwagweleni uko come 2019 muzaimbanso nyimbo yanuixa yoti atibela atibela kuchokela 1994 mpaka pano muzakhumudwa muona
mbuli ndiwe Assah chabwela mulesi wachabechabe ovina nyau umafuna tonse tizisapota mcp yakoyo ndiye upondatu my bro
NKulira uko a Davis Mpeketula….limban mtima ndithu coz 2019 mudzalira chikhakhali…..dpp siidzawinanso basi,zavuta kuchipani akulu…a Malawi anazindikila nowadayz…ndale zopereka ndalama zinatha kalekale..olo atadzapereka dzigayo zaulele monga anachitila masiku apitawa,ai ndithu. Zavuta basi,..limbani mtima ndithu bwana Mpeketula
MCP woyee
Koma chikuchitika ndichani atsogoleri kumangolozana chala m’malo mugwirizana zachitukuko mukupanga 5pin mukut chimecho ndie chitukuko?
Ndimakhulupirira Day Inayake be4 2019, Ma Guys Amenewa Azachapana..
Zomba zomba.
Iwe Peter wodwala pakati pa iwe ndi Lazorous ndani?
POMPANO IFE A DPP TIYATSA MAGETSI 24/7 TIONE ANYAPAPI INU CAMPAIGN MUNENA CHANI POTI IFE CHITUKUKO MUKUCHIONA IPSANI MTIMA NDIPO MUPSADI MTIMA IFE TIUDYA UKAPSA MPAKA 2024 TIKULAMURABE
Nde wati Profet Yoswa mpaka 2024?? Afikako amene uja? Akumayenda atavala chi thewela yu. Khazikhazi nyamakazi admit ku USA. Hhehehe….ife Nsanje yonse ndi Chikwawa vote ndiya MCP ndi Dr. Laz Chakwera. Nkhalambazi zakanika.
Muzakhumudwa chipani chanu pano chili pa low. Chaluza zisankho pompano musachepetse kuluza mwaluzaku. Anthu pano tinapenya no more dpp after 2019
Pitalayo nde openga not Chakwera
kwa ineyo ndikuona ngati a munthalika ndi omwe akufunika kuchipatala cha mental Ku zomba zifukwa zake nazi: A munthalika sakubweretsa poyera umboni wa ma pepala omwe achakwera anatulutsa oonetsa umboni wa argument yawo pamene amunthalika akungoyankhula pamenepo Iwo ndamene Ali a misala. 2 chilowereni m’boma 2014 tikatenga manifesto ya DPP only 20% of it has been achieved but look here only 1 year remained to genera elections the rest is miyala ya maziko …pazifukwa zochepa ndanenazi munthu uyu akuonetsa kuperewera kwa ubongo in short wires are disconnected in his head so need a medical review especially from psychiatrist
Umakwana Aise
Zoonadi misara ili ndi a president
kkkkk
Simasala yokha komanso ndi nkhwandwe iyit
KODI CHAKWERA CHOMWE ADZAPANGE MCHANI ASANDINYANSEPO APA? MUNTHU OLEPHERA KUYENDETSA CHIPANI DZIKO NDAKAIKAA NGATI ANGADZAKWANITSE
Mcp yawina ma by elections pompano iwe nkumati chakwera akulephera kuyendetsa chipani. Mutu wako ukugwira koma. Pakati pa peter mutharika wanuyo ndi chakwera olephera ndani pamenepa.
MCP ikuyenda bwino kwambili pansi pa Chakwera. Mwezi watha womwewu tawina ma MP 3 a nyuwani achinyamata okhaokha. Ma khansala 2 achinyamata. MCP 5 – DPP 1. 2019 kuli ku sesa.
Inu Malo omwe mwawina ma by-election anuwo mufufuze ndi ma strong hold a MCP okhaokha kukakhala Ku ndirande NDE ukudziwa low turn out anakabvota a MCP okhaokha dikirani muone ndithu
Salowa Mcp
Muthalikayo Pa nyini Pa Make.Mumuuze Kuti Watitopetsa Ndipo Ikanakhara Kut Ndi Mbeu Bwenzi Titangokazinga Kut IsazamelensoOnce Again Pa Chi Nyini Cha Masten AkeChonde Mundifikizile Uthenga Wangau
Big man tangoyesano kulongosola mwabowokamo chifukwatu ngalawa iyi ndiye ikumiratu
Apitedi ku mental ameneyo,ife timadabwa kuti amangosutsa chilichonse watsala pang’ono alondola dzuwa ameneyo
He does recommend other things koma nkhalama yaniyu siifuna kuvomereza ikauzidwa chilungamo
Wamisala Ndi Pitala Akufunika Ku Mental Mwasanga Popeza Chaka Chatha Wapanga 2000 Chaka Chino Akuti 5000 Kwacha Pamenepa Wamisala Ndani Misala Ima Posa Apa
Wamisala nd Peter
A BENARD TSEGULA MASO NDI KHUTULO THEN BACK UP UR THUG
5000 sindalama ibwere tidzizayigwilitsila ntchito,mumafuna kukhale ma K50 basi?olo itatuluka K100,000 palibe vuto ndindalama bac
Maclean Chidzeka Charity Pankomera Precious Evalistus Gratia Winnie Kaziputa Pemphero Samu Bridget Chiepa Vincent Soka Soka Denis Gwaza Alfred Nsona Mkhutabasa
Maclean Chidzeka Charity Pankomera Precious Evalistus Gratia Winnie Kaziputa Pemphero Samu Bridget Chiepa Vincent Soka Soka Denis Gwaza Alfred Nsona Mkhutabasa
iyi ndi drama yakulu akulu nanu a 24 mmaziwa kukomesela nkhan cholinga anthu azingopsabe mitima.
Zathina APA.
Wampewesa ndiwe zaka zochepa zomwezi mpakana Kwacha ukufuna upange one million imodzi ngati kuzimbabwe ukufuna dziko lithepo chifukwa choiti iweyo wakalamba
Zawutsilu, zopandapake, zopandatsogolo, zazii , zomayalutsana ngati ana, ziwoneka 2019
wausilu iwe chakwela boma zaka zikudzazi olamula ku mental
Nayenso ndi wamisala kuposa adzizakewo kkkkkkkk amisala APA aziwana ndithu!!!!!!!!!
kodi inu a manyuzi, cholinga chanu chimakhala chani mukamalemba zowawitsa mitimi ya ena chonchi? mumasangalala ma sapotawo akayamba kunyoza mtsogoleri?
Andalewa Sakumadalisa Zolankhula Zao
Vintu vinangu ivi ziko yaynu yaonongeka zoona us waiting for developmental issues anvekere 5pin ituluka pompano kkkkkkkkkkkkk eeeeeee Rejected governance ndiyomweyi
Kkkk iye waiwala misala yake
kumeko ndi mankhwala alipo. Paja iwowa misala yao amapita kuja!
kkkkkk politika ndi game yamatopedi. uyu anene mzake lero uyunso mawa nkudzatokotanso koma osakumana kuti akambirane.
Ukamamuloza Mzako Kuti " Wamisala Uyo Mgwiren!!" , Zala Four Zimakhala Zikukuloza Wekha
Last week was Vincent Wandale who was mentally ill now this week is Dr Chakwera mentally disabled again kkkkkk who is next……..loading kkk aliyense otsutsa boma apita ku mental ndithu chaka chake ndi chino
Zoona koma akumuopa chakwela
Seriously #Lawrence kkk awawa ndi manthadi man kkk
Amuope chakwera kuti watani amalawi simuchedwa kuiwala sure, Chakwera yemweyo muzamtembenukiranso kuyendetsa boma sizamwanatu
Every strong opposer to ruling gvt will face a music, either kundende or ku mental kkkkkkk abo bii Kupha basi
Ian usatitopese ndi peter wakoyo kagwere
Chakwera asanapite tiyamba inuo kae
Is this an excuse to for having an incompetent President Ian Clarence?
#Ian u have a point and that is true, only that pali zinthu zina zake zoti utha kukwanitsa kuzilongosola ngakhale iweyo mkumayenda koma this gvt is failing.
this DDP is stupid guyz seriously I hate its leadership personally
i second ur point #Michael, thats a gud question.
Dpp total failure and disgrace .Dpp inali ya Bingu osati agogowa
Dpp total failure and disgrace .Dpp inali ya Bingu osati agogowa.kulamulira ziko zawakanika. Peterayo ndiye apite kumento coz alibe clue yoti angasinthe zinthu
Brian banda also to be sent to mental.
#Kennedy Bernard apita limodzi ndi a Kasakula kkkk
Guys mwailandila bwanji nkhani ya 5000 note akufuna kutulutsayi?
Pepani azanga ndithandizeni ufa watha magetsi kwathu kuno anazima dzana.Zavuta akuluakulu last yr K2000,this yr K5000 next yrK10000 pitara ameneyo aliphe akuti sakudwala….
Peter Ndi Mbuzi
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
kkkkk we are indeed being ruled by a mentally ill reader.. pajatu wamisala amaziona ngat iyeyo nd wabwinobwino and the rest normal people nd amisala… kkkk ndakomoka nd phwete ine ..
Ndiye mukundiuza kut 7000 tidzitenga ndalama ziwili bas 5000 and 2000 peter yo waganiza bwanj peter apite Ku mentoooo bas,,, shemu
ameneyu wandinyasa ine 2019 ndivotera ena mwina voti yanga izasintha zinthu.
kkkk ndale zafikapo…
galu kwabasi ayambe iyeyo kupita Ku mental coz mutu wake sugwira ai munthu chaka chatha wapanga 2000 kwacha lero akut 5000 kwacha chisilu kwabasi wandinyasa kwambili pitala
chaka cha mawa apanga 10000 note!! paja chaka chilichonse new note!!
Professor osathandiza uyu
Iwenso ukuthulura pitala
kkkkkkkk mpaka mpwesa
Dr Ibu Bwampini
misala yake akunena ayiwona yekha 2019 Boma
kkkkkkkk politics indeed its a dirty game
Ayambe ndi iyeyo
Chokani inu mumabakira zampwesa bwanji?
Galu chifukwa anakulemba ntchito ku MRA?
Zikugwirizana bwanji misala ndi maphinziro a Chakwera? Zopanda nzeru ndipo wamisalatu adawona nkhondo nanga ma generatorwo alikuti? Wobodza ndani pamenepa