Sulom rebuffs Wanderers over Blantyre derby venue

239

Super League of Malawi (Sulom) has rebuffed Be Forward Wanderers’ request to have the Blantyre derby against Nyasa Big Bullets played at Balaka Stadium, which is their home ground.

Wanderers were adamant of using the stadium for the crucial encounter as stipulated in Sulom’s article 16 which gives mandate to the home team to use its venue.

Mike Butao

Mike Butao: Balaka Stadium is our venue.

Earlier last week, Nomads General Secretary Mike Butao told Sulom that their anticipated clash with Bullets will be played at Balaka because it’s their venue.

“Balaka Stadium is our venue and we will play Nyasa Big Bullets right there as stipulated in Sulom’s rules and regulations. In the first round, Bullets used Bingu National Stadium as their home venue and with us being the home team now, we have decided to take the match to Balaka Stadium,” he told the local media.

However, the decision has been turned down by Sulom.

According to the fixtures released by Sulom on Sunday evening, the Blantyre derby will be played at the magnificent Bingu National Stadium on 28th October, months after the Nomads lost to their opponents twice in Carlsberg Cup and TNM Super League encounters at the same stadium.

Apart from Sulom, Bullets were also ready to protest against Wanderers’ choice of the venue saying Balaka Stadium is too small to host two Malawian giants as far as football is concerned in Malawi.

“As Bullets, we will react once their office stand is known. In any case, we will not partake of any nasty eventualities at Balaka Stadium as a result of overwhelming crowds. This insensitivity by Wanderers is bad for the game if they refuse to give in to voices of reason,” said Bullets General Secretary Albert Chigoga.

In 2013, a football fan died at Balaka Stadium during a Super League tie between Wanderers and Silver Strikers when fans from the two teams clashed

Share.

239 Comments

 1. osamakonda kukana ma ground neighbour Karonga stadium yoipa,lero Bingu N Stadiumnso yoipa zikhulupiliro kapena chiyani?

 2. kwakula mkukhomerera pachilungamo. why kukuchotsa kunyumba kwako kukakuikwa kwina mkumati uku ndiye kwanu. home ground yathu ndibalaka

 3. koma I remember kuti ma guys a noma akafuna kuti tizimeyera ku lilongwe pa poti zavuta basi tiyeni ku balaka hahahahaha ma noma ur not serious

 4. Ma team akulu akulu kusowa ground losewelapo mpira yet thier supporters are all over making boring noise. Mesa nd Blantyre derby, akasewere ku Blantyre konko osat Lilongwe olo Balaka

 5. A Sulom Ndi Afam Ngati Simusamala Tikhala Opanda League Kumalawi Chifukwa Chachibwana Chanu Coz Munangokhala M’maudindowo Kma Kuyendetsa M’pira Simutha Mukupanga Apazi Zomakakamiza Team Kt Ikamenyere Paground Pamene Sihomeground Yawozi Ndichiwawa Mukuchiputacho Asiyeni A Noma Munavomerezeranji Kt Noma Homeground Yake Ndi Bk Stadium Simunkadziwa Kt Mu Tnm Muli Nbb? Ndipo Ss Kmaso Chitipa Munawalora Bwanji Kumenyera Pa Home Pawo

 6. Game pa BNS basi ngati inu a Noma simukufunapo khalani misapite sizokakamiza tikuziwa kuti mukuopa chifukwa za ulendo uno zikadutsa pa 1-0 paja

 7. Nkhani ndi chipongwe chomwe anapanga a Sulomu kwa Noma mmesa amati ngati sikufuna kumenyera pa karonga ikanene ku sulomu kamanso silver inakana pa Bingu anaimvera Noma kuiona kupusa? Pa Balaka pompo basi

 8. mukutathauza kuti wandalazi ndiyo imasokola mpamba wa solom ? kodi mabanker ndi noma sioyenela kumenyela pa nbs ? ndiuchitsiru wanji udagona kumalawi posasata malamulo ? nde mkumanamiza amalawi opusa kuti mulindimalamulo ? paja munthu akamakalamba zeru zimabwelera et ? mwakhwimakhwima mukufunika ritaya nose afam & solom mwapenganacho chamba chokondela mateam . tisadzaveso kuti wandarazi ikumenya pabalaka ngati pahome . manoma ndimwana wamasiye okulira pamtengo.

 9. Zisamakomele mbuzi kugunda galu ndimayesa zana noma mwaikakamiza kuti ikasewere Ku karonga munaiwala kuti kucha ngati bullets inalola kupita Ku Bingu ndiuchinsiru wawo paja ndi anjala ndi ndalama

 10. Abale sizowona kumenyera maground ang’ono ngati balaka zinazi kumapewa matimuwa ndakuluakulu akuyenera pa Bingu bas

 11. Koma malawi tili kumbuyo ndizinthu zonse, ,,,
  Uniform ngati ya Ku primary Zoona, ,,
  Stadium chonchi?
  Pakamwa ndi kutukwana phwiii.
  Kulibe chabwino kumalawi, ,,

 12. walter choyambilira thako lako pamozi ndi fam yako yonse #2 sulomu mapwala anu osalira kumbuyo ngati ankhumba, mafuta mwale tiyenazoni bg tiri pambuyo panu bwana nyamilanduyo akutenga fam ngati yamake foolish

 13. Neba wayamba kale kunjenjemera…Game ngati imeneyi zoona ingamenyedwe pa Balaka ? Mmesa padzana pompa umakana pa silver kufuna pa Bingu..lero ukutinso ayi pa Bingu paja..mutu sukugwira iwe Neba.

 14. Kubulets kukanakhala anthu ozindikila akanamvesa,zanazanali sulomu yakana pempho lanoma kuti game yachitipa asewerele pa mzuzu stadium, sulom inanenesa kut sizingatheke mpila ukhale pa karonga stadium yomwe ili home ground ya chitipa Nde rero iwe sulom ndimisala yakoyo ukati pahome panoma pachepa? Mmene mumkapanga approve club license simumkaona kuti ndilaling’ono? Madeila you a man keep telling them kut akatikakamiza komwe akufuna Iwo all the expenses zikhala zasulom that’s the fact

 15. Kutanthauza Kuti Mateam Alibe Ufulu Omenyera Mpira Pa Home Yawo? Penapake Asulom Asamawaike Dala Mateam Chala Mkamwa Kuti Akawaluma Aziwalipilitsa, Nawoxo Mateam Ali Ndiufulu Wao Osati Nthawi Zose Kumawapangira Zochita,

 16. Nkhani ndi ndalama kumene inu mumati? Palibe za balaka apa bns go konko. Zomadalira nyanga muziona. NBB fc pa easy neba asiya zotokotazi pompano. And ndikuuze neba uchita ngozi coz ukuyendesa kutsogoloko disk liri kumbuyo basop samala. Bullets inanyamuka and sikulankhula lankhula koma ikumangodusa iri phee mmmmmm so sweet and creamy

 17. I ve seen that there is a secret behind sulom and nbb, this is not acup game and why to treat noma like that?. Team iliyonse ili ndi home ground, ndiye zakhala bwanji kukakamiza matimuwa kukamenyera pa bns?. Nthawi zonse noma ikapereka madandu ku sulom samawathandiza, aaasssssa chikomere mbuzi kugunda galu?. Taonapo ma team angapo adakana kuwasinthila ma group awo, monga silver strikers, chitipa just mention afew kma sadawaphwanyile khumbo lawo. Noma ndi team imene yazunguluka kwambiri season ino, kuposa ena onse ndiye bwanji osawemvera pempho lawo?. Ngati asulom akonzekera zonse zoyenelera pa ulendowu, awauze anoma kti ndalama adzawalipilira komwe akupitako. Zilibe ntchito kti game imeneyi ndi derby,kmabe taonapo ma team ambiri amatsata ndondomeko yawo yokamenyera pa home ground. Asulomu musalowetse ndale ndiku mpila komwe, cfkwa pothera pake muononga zinthu. Tsatani njila ina yopangilapo ndalama ngati zili choncho, zisiyeni nyerere nazonso zidzamve kukoma pakwawo. Mwamuna mzako mpachulu nkulinga utakwerapo, ndiye winawe wachingambwe samala manu ako mkamwamo.

 18. Akuoneka kuti amalilira kwambiri a Noma, chonde osakalilira zigoli Big bullets yakonzeka kutenga unomber one posachedwapa.

 19. Kuti game ikhale pa Balaka patha kuchitika ngozi due 2 overcrwdng mwina ena kufa kumene ,ndife tomwe tidzati aSulom analekelera.Popewa zambiri tiyeni tingosamutsa ziweto zathuzo 2 LL.Gud decision SULOM

 20. Nthawi zonse a noma amakhala akuchitidwa nkhanza ndi sulom chifukwa chani. This law of home ground ithe. Tisamvenso za home ground

 21. Wandrels Itachinya Bullets Mu Bus Ipite Return Match Inayankhura Motumbwa Kuti Bingu National Stadium Boma Linamangira Iwo.Mpaka Anayi pasa Dzina Loti Chande Stadium Nde Lero Mwasinthaso Kkkkkkkk Imfa Sithawika.

 22. To me idont see any problem 4 that derby to be played at balaka stadium,why taking any game between bullets and noma to BNS? Asulom nkhali ndi ndalama basi kufuna kukatamukila pa ma player athu shame on u

 23. Kodu ndiye kuti a sulom Ali ndi anthu awo imwe amawavera madandaulo owo chifukwa ndayamba kudabwa Nazi a silver katakana oa bingu abawavera ndipo zinatheka a chitipa katakana kupita ku mzuzu kufuna ku karonga anawaveraso tsopabo noma ikufuna nayoso home ground yawo ndiye kuwakanira???? Aaaa zikutathauza chiani zimenezi !!! A sulom alibe chilungamo ndithu

 24. Kuti zofuna zako ukwanilitse kudalila nyanga poyamba mumkati pa BNS nde pabwino mwaonakuti mikodzo ikakuvutani mxm kapado fc

 25. ine I don’t see any problem having that game at balaka stadium. That’s their home ground why forcing them to Bingu National stadium?

 26. Wampila ndi wampila sathawa ground olo atanena kuti magolo mukasiye mu nyanja mpila asewelere m’madzi akaphurabe basi

  BB fan

 27. Chelsea hosted barca at their small bridge why didnt they go to wembley? Sulom ipange ma ticket ogwirizana ndi Balaka stadium akatha enafe tizamvera pa radio or mbctv

 28. Noma is good at mind game. Kutengera za Noma, mupusa nazo. Amati ku Karonga sapita akudikira a FAM awayankhe. By thursday they were already in Karonga. Zimakhala bwino coz anthu amayamba mofulumira kukamba za game yomwe yilimkudza. Bravo Noma the wise pples team.

 29. Komabe kupatula zonse mukunenazo, Noma ndi imodzi mwa matimu omwe ayenda kwambiri mchaka ichi. ,, osat zomwe ena akuganiza. Mwachitsanzo ku Nzuzu & Lilongwe , Noma yapitako kangati? Tikakumana konkooo!!

 30. Nkhani Yomwe Mwakanila Ku Balaka Siya Security Koma Mukufuna Kukaba Ndalama Za Pa Gate Ngati Mukuti Home Team Imasankha Bwalo Ndiye Mwakanilanji? Chitipa Inasankha Kalonga Noma Inapita Ngakhale Game Imayenera Kukhala Pa MzuzuMukabe

 31. Ine ndilibe team koma tnm super league ndimaisatila bwino, Noma ikunena zoona pazifukwa izi. Noma inauza asulom kuti game ya Silver bwanji tikamenyere pa BNS sulom inakana komanso silver inakananso, mu FSD Chllge cup Noma inapempha sulom pamodzi ndi moyale sulom inakananso ponena kuti aliyense ali ndi ground yake zanazanali Noma inauzanso a sulom za game ya chitipa kuti akakumane pa mzuzu stdm sulom ndi chitipa adakana ananena kuti aliyense ali ndi ground. Lero noma nayonso yakana ikuti nayonso ili ndi ground yawo komanso ndamumvela bwino ine Stev Madeila wati ngati FAM or SULOM ingawapangile chilichonse ku nkhani ya transport, ndalama ya anyamata awo or malo ogona ipita ngati FAM OR SULOM yagwilizana nazo ipange zomwe Noma yanena.

  • Noma iribe ground Balaka anamanga si Anoma . Mbuyo monsemu Noma vs BB game imakhala pa Kamuzu stadium. Noma ikamanga stadium zizakhala zomveka. Komanso Noma imakana pa silver chifukwa amati tikufuna ndalama za pa gate zichuluke. Guys be serious Noma vs Bb game singakhale pa Balaka omwe amapita kumpira akuziwa zimenezi koma omwe amamvera mpira pa radio sakuziwa kuti pa Balaka pakakhala ziwawa coz masapota akasakanikirana. Chisekeleni cha Kamuzu stadium palibenso stadium kumwera yomwe ingakwanise kuchitisa masewero a Noma ndi Bullets.

  • #Rowland_Navicha ukulankhula ngati oduka mutu, nkhani ili apa siyomanga ma ground ai. Nbb ikugwilitsa ntchito mdc yomwe silawonso, kma bvuto lakula ndi dyera asulom or afam. Noma ikudandaula pankhani yakaendedwe kmanso ma expenses ,omwe angaononge ngati game itamenyedwere pa bns. Sulom ikufuna kukapanga ndalama zochuluka, asiyeni anoma apange zofuna zawo. Bk stadium ngakhale itakhala yaing’ono, kmabe ndi home ground yawo ndiye winawe usalowererepo.

  • Ndipo lyton Gondwe walemba momveka bwino. Sulom ikufuna noma isatenge league. Mchifukw noma akuipanga zimenezi. Kwa amene simukudziwa balakanstadium ndi home ground ya noma. silver inakana pa bingu noma sinawiringule kodi lero zaipa pot noma ikukana ku Lilongwe? Mukanena ziwawa zachitika kulikonse. ku bingu kunafa kale anthu komanso bis yawanderers imagendedwa komweko ndi bb. nde apa nkhani palibe apo bii sulom ndi fam pangani select mukamenye mdi bb pa bns. ife pa 28 waku balaka a

  • kodi afisi inu game yoyamba ija bwanji panalibe zokuwakuwa? tiyeni pa Bingu wina asazaname. zifukwa (1)palibe mpata okozera pagolo (2) palibe kuthirana mafuta (3) zonangila mu mchunu zikathotholedwa (4) palibe zokauluka pa ground ngati mu funa AYAYAWO mukawalipilira osati zamanyi zanuzo

  • Usati Afisi Ngati Ndiwe Munthu Nthawi Imene Ija Munasankha Ndinu Kt Tikamenyerepo Coz Timayenera Kumenya Pa Homeground Yanu Inu A Zigafa Fc Ndichifukwa Tinalora A Sulom Ndi Fam Mukachita Chibwana Tikhala Opanda Tnm Mudziko Muno Akwiya Ndizimene Tipange Asiya Kupanga Sponser

  • Bullets fans are so blind. SULOM ikufuna pa Bingu because akufuna ndalama not security. A Sylom amagwiritsa ntchito ma team athuwa ngati makasu iwowa nkumakolola. now Noma home ground yawo ndi Balaka. they are at Liberty to play at their home ground. payback nayo SULOM ikasume ku FIFA. #Shaapaaa_Bankers_4_Life

 32. Ndale za mumpila izi ngati enanu simukudziwa ndaona kuti ambilinu ndi ana ndale za mumpira simukudziziwa noma ikudziwa kuti pa bk sangamenyerepo ndi neba

  • ukakhala munthu wanzeru poyenda umayang’ana mmbuyo chifukwa chobwera kumbuyo chimaopsa kupotsa chobwera kutsogolo.Muli ndi mapoints angapo komano ife timatha kukulandani nyoma yofikafika pakamwa pako neba usaiwale #Carsuburg zinalinso dele dala.Iwe tangodekha kaye mtima pansi matako mmwamba uone zomwe zikakuchitikile pa @ Bingu National Stedium u wll never forgate untill Jesus come ok!!!!!!!!!!!!!!! #Maule moto buuuu!!!!!!!!!!

 33. But pachilungomo game imaenera kumenyera pa bingu stadium anoma alibe ulemu kwa mtundu wa Malawi even kunoko derby amamenyera stadium yaikulu kulemekedza dziko Lao that is derby you have to play to our big stadium because some country a gonna watch also so you can’t playing in balaka stadium that is nonsense for noma

 34. kkkkkkkk NEBA iwe Bullets ili ngati imfa coz siithawika! Kaya kuBalaka kaya kuBNS kulikonseko tikakupeza ndipo tikakupasa 3-0 yako komweko

 35. Hahahaaaaaa wa Noma iwe umayesera kuzemba chikwanje ndi wakomana ndi mpinitu SULOM yangolozera pa manda.
  Listen Neba you have to construct your own stadium then you can choose where to play but as of now you have no choice Zatenge sasakha ndiwooooooooo.
  BULLETS go go go BULLETS!

 36. hello everyone am happy sharing this with you, am not suppose to be doing this but i can’t hold back my joy so i have to share with you, you too can be help just as i was helped by Dr Odudu who cured me the HIV virus after suffering from it for some years and CD4 count was very low i was depressed, i was desperately in need of getting rid of it, but the ARVs were not helping so i was eager to contact Dr Odudu who gave me his herbal medicine, today as am posting this i am HIV negative, don’t hide your sickness or else your sickness will hide you, contact Dr Odudu today so that you see a reason to back through the years of your depression and smile to yourself, you can call or whatsap him with his number (+2349067902914)or email [email protected] , pardon me i offend you with this post, but i must share this good news

 37. Vuto lokula modalila ndilimeneli,kalikonse kukadandaula kukula mopusa eti?Tiye pa BNS weekend ino usatichedwetse nthawi sili mbali yathu.

%d bloggers like this: