![FAM](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/06/Fleetwood-Haiya-235x176.webp)
Fleetwood Haiya ndi masomphenya ake, FAM ikusintha
Bungwe loyendetsa mpira wa miyendo la Football Association of Malawi (FAM), motsogozedwa ndi mtsogoleri wake a Fleetwood Haiya, lavomeleza chigawo cha ku m'mawa kukhala imodzi mwa zigawo zake. Izi zikutanthauza kuti zigawozi zawonjezereka kufika pa… ...