A 65-year-old man died on Friday in Nkhatabay after taking Kachasu on an empty stomach.
The man has been identified as Zawo Kasambara.
According to police public relations officer for Nkhatabay Ignatius Esau, Kasambara who was living alone was a known drunkard in his village and on September 22 he was found dead in his house.
Police and medical personnel from Mpamba health centre rushed to the scene and postmortem indicated that Kasambara died due to abnormally low blood sugar.
Zawo Kasambara hailed from Nsanja Village, Traditional Authority Timbiri in Nkhatabay district.
Police in Nkhatabay have since called upon community members in the district to refrain from the tendency of taking alcohol on an empty stomach.
Fanta wa ma Ninja etiii
Hahaha ameneyo nd dolo,anali njala nkuganiza kt amenye chasu wez cholinga malaw 24 izt wafa nd chasu,,kkk
Mhsrp
Ndimakuuzani nthawi zambiri simumamva.. Onani anzanu ndi awa oho Manzy Phiri
JONN MOOSSA MUNALEMELA MOT SIMUZABWELASO KU JON KUNO
aaa boza inu, nanga ndalama zogulila kachasuzo anaztenga kt?
That won’t kill a man, its what the Kachasu was laced with that killed him…
Kuyipisa mbiri chabe ya mowatu uku
Wamwalira ndi njala
Kkk Koma
drinking without eating is dangerous thus the fact I know.
George kafodya, wamwalira ndichakudya mmimba munalibe kanthu
man ndmbali itiyo kodi?
mmmm ineso sindikudziwa kuti ndi mbali it
kma dzina ndlomwelo?
kodi ase,kafodya oimbayi!
Eya oimba yemweyi
So sad
Zoonadi Naomi zosakhala bwino ayi
mukafuna afe ndan?
Not beer kills man. But man kill himself
Wakumoto kale ,Jahannam.
He has died of Hunger…You can’t walk from Malawi to South Africa without eating….Ufaso pa Dedza pompa usanafike
Time
Zachitika bwino kut anthu ena atengelepo phuziro.kumangomwa ngati mawa kulibe
Nawoni jolopiko
Awuse mumtendele
Lets face reality guys. One day hunger can kill somebody? Haven’t we heard that taking kachasu on empty stomach is dangerous? For your thoughts???????
Wafa ndi njala ameneyo
Wafela zake
Akumana nazo ena akufuna moyo ena akugulisa ndi kachaso zopanda zelu?
I didnt know kachasu is also beer.
Wafa ndi njala osati mowa
aaaa eti? hahaha ine ndimkamwa kachaso osadyawhole day kkkkjk
Adlai I’m sorry
Koma mowa uzikhala ndi mutu umenewo ndi mowa wabwino? Anyway RIP
“Olezera sakalowa mu ufumu waku mwamba” atero Yehova. 1 Corinthians 6:9-11 (NIV) “Or do you not know that wrongdoers will not inherit the kingdom of God? Do not be deceived: Neither the sexually immoral nor idolaters nor adulterers nor men who have sex with men nor thieves nor the greedy nor drunkards nor slanderers nor swindlers will inherit the kingdom of God”.
phwando likakoma zosatila nzomwezo
wafa ndi njala uyu osayipisa mowa iyayi
Tchimo limabala nthawi zonse munthu ukapanda kusamala,chonde tiyeni tisamale pochita zinthu ndizowona kuti imfa sithawika koma osamachita kupopa dala mowa muli ndi njala kapena kupopa mopitirira muyezo kuti mutchuke ayi! kulibe shop ya moyo koma ya mowa! kkkkkkkkkk?
Smart ànd timely death…RIP
Kachasu is not beer.
ahhaha amaganiza ngati akumwa frizEs wamalambe
Eat before u drink malamulo a mowa Rest in peace
Lazy dudes….
No rest for you.
But still won’t legalize marijuana, the only cure for glacoma! Smfh
Sin kills. Go well man we will find you
I used to cry thinking I would die of the HIV virus, I never knew there was a cure to HIV until I was completely cured from the virus by Dr Ikuku herbal medicine after suffering from the virus for over 7 years. Sometimes last year a lady posted on this page of how she was cured by this Dr Ikuku. At first I doubted her but I was convinced when I saw others the doctor has cured.I tried the herb and it worked on me. I can boldly say I am now negative after series of tests conducted by different doctors. If you are positive or have any disturbing sickness you can contact the doc now on call or Whatsapp +2348079062707
Amakhala kut iwowo
The big man 65 aaaa anadyerera akapume
Shame
Kkkkkkkkk
I don’t think kachasu is a beer
So, wt is kachasu
Spirits or liquor
Ana a mahulem’mamuziwa kachasu im drinking kachasu now
Zabwino zonse
Malilowotu ndi onyamula mukudandaula chani anthuni……inunso inde simujomba ayi
Its not beer then. It’s hunger
Had it been sadamwe kachasuyo akanamwalirabe ndi njala ya one day? Kkkkkl
mwaiso kuti anaponyamo kamowa mmimbamo..kupanda apo akanafa mwansanga nddinjala
Tawonga pakutiziwiska
Hii! was he 65?and kachasu wamupha dzulotu not Friday.Atorankaninu!.
Who’s He?
That was a planned death, he didn’t wanted to die by rope, poison or any disease.
Malawi 24, the guy has died of hunger not beer
Fact z man die coz of hunger not beer
kmanso Kachasu z nt beer
No,he died from taking alcohol on an empty stomach.when people stop defending the indefensible?
Wafa ndi njala, mowa suupha
tell me why hunger coz we had bumper harvest last season
Hahahah timve ziti? Tell mi the 2truth
Anakuuzani kuti alindi njala? Kachasu is a highly potent spirit and hence the presence of high levels of alcohol in his blood stream caused death..
Mwafulirwa Juwala Mwakhuyu Samuel
Njala not mowa
Njala ndi mliri oyipa kwambiri
Kodi inu amalawi24 mowa umakhala ndi mpeni kuti mpaka kuphera munthu,wangofa ndi matenda basi osati mowa, mowa ulibe problem osawunamizira,tidzamwa mpaka kale.
Kkkkkkkk
winaso tizatengako ulendo nawo kumwamba kkkkkkk
Kikikiki ati lack of food killed him osati moba! Kennedy Mulenga Chisanga Mbolo Kumanja
Hunger killed him not beer…
Hunger kills man osati beer.
How did u know
Collect
Sure
Kmanso Kachasu z nt beer
Well Done Take Note Of This
Well Done Take Note Of This