Samalani oyendetsa minibus chifukwa ngakhale nduna tsopano zalowelela pa nkhani yolanga anthu onse ochita chibwana ndi malamulo a pamseu.
Nduna yoona za m’dziko a Grace Obama Chiumia anadabwitsa anthu mu mzinda wa Mzuzu pamene analanda makiyi a minibus chifukwa inanyamula anthu moonjeza.
A Chiumia ati anakwera nawo minibus imeneyo imene inali pa ulendo wolowela ku Karonga. Iyo inaika anthu anayi – anayi pa mpando m’malo mwa anthu atatu – atatu.
Minibus itaima mu Mzuzu kuti imwetse mafuta, a Chiumia anatsika ndi kupita kukatenga makiyi kumudziwitsa oyendetsa kuti ulendo wathela pompo kamba waswa malamulo a pamseu.
Iwo kenako anayitana Apolisi kuti azawanyamule oyendetsawo kukawatsekela.
Patachitika ngozi zoopsa mu miyezi yapitayi, Apolisi akhwimitsa chitetezo cha pamseu ndipo ambiri opezeka akuswa malamulo akulangidwa mopanda chisoni
Osayi.walaso kulanda.ndalama zomwe zaba zinduna zizanu.zomwe.zawonjezaso umphawi.kwa anthuosauka
Tchito imeneyi asayisiyile pomwepa agwilero magalimoto apamdipiti chifukwa amaphwanyaso lamulo lapamseu amathamanga kwambilri komaso amayenda mbaliyosayenela kodi lamulo likamapangidwa mumafuna kwangokhaulitso osowa tonse ndife anthu palibe moyo woposa uzake!
Ndakumvani munthu wankulu
From legislator to law enforcer. Kkkkkk
Her, me, you its our responsibility too.. Bravo Obama grace
Azakumana ndi ma driver a chamba azasiya asiyiileni a police nthito yawo,tizimvaso kuti nduna ya gwira wa kuba ndalama za boma a cashgate tingasangalale kwambiri,akugwila min bus ngati was police,ma driver ena amapeleka ziphupu nde sazalandila,tisatengele lamulo mmanja.ndintchito ya police iyi abale.
50+50
Apa palizifukwa zina osatizimenezo ayi,ndunayo ndiyakuba
Stupt mind azapange Ku blantyre azaone kuno Ku bt ulibe makape or police timayasa ….ithnk azilanda ma kape a eraz kuchimake kwa zisilu
Ikhale nduna ya nzelu osakalanda ndalama za chimanga kwa galu wakubayo bwa
Nosense ndimavuto angati omwe boma likulephera kuwathesa katangale thoo kukalimbana ndiwaminbus mmalo mofufuza ndalama zankhaninkhani zamphawi zomwe anthu akuba kubomako mkumazigwiritsa ntchito zapersonal shame u minster
wautsiru ameneyo
Osaphwanya bwanji? Alanda minibus ndiyake
Am reading some of the comments here….
Mbola zenizeni …..
NTchito yabwino
Mboli yake ameneyo
Nduna yabwino yofunira a malawi zabwino weldone minister keeo it up
akhoza ngausiru oendesa ma min bus
LETS BE REALISTIC. Ngozi zikamachitika its the govt being blamed. To my side I see nothing wrong for the Minister of Home Affairs intervening with the aim of trying to minimize the road accident
Kaya alibe ma powers olandila minibus koma anachita bwino kwabasi…. Bravo
On the part of the minister this is commendable. However, it speaks volumes of the inefficiency of traffic police and RTD
M not a DPP fan nor keen in politics but this driver spoke rudely to the honourable minister and his vehicle was way too much overloaded. Mind u I was there ndipo mayiwa amipita kumaliro ku Nkhatabay.
Keep it up anduna! Am in total support of this!
Ndiye Azt 2019 Boma Akunama Amewo Anthu Akuvutika Zikolawolomwe Panopa Makalipentala Akuvutikakumwelaku Akulandidwamipandoyopangapanga Akutikutetezachilengedwe Mmalomopitakukhalangokomweko Poti Akuyendandi amdf
Well done MAM pitilizani akutiwonjeza ama MINBUS
Ndipo amayankhula chipongwe ukamawauza kapena kuwapempha zokhala pa mpando anthu atatu
Chisanzo chabwino amayi moti uthenga uwu upite kwa zitsitsiru zonse zimene ziona ngati iwo ndi ofunika kuposa onse …. Sinthawi ino yoti chifukwa ndine pasenjala ndiye ndingamulekelere driver amene akundiyendesa kuti adziledzera kapena kuphwanya malamulo kuti apedze phindu lochuluka at my expence
kod nchifukwa ninji malamulo akulunjika kwa minbus driver ekha osati ma bus driver?????cholinga chanu mkutolela ndalama kwa wa minbus kut mubenso sichoncho?????
Iwo amalolelanji kukhala 4-4 ??
Mmalo mothana nd vuto lamadxi atudxi mwayamba yapamsewu kulanda maphapha aweni??mulungu akuyenderen
Hi Am Tman From Ramotshinyadi Ilik Afreand Any More
Akukwezabe asamva mkunkhuwa sinanga akumanyemabe
We love you mama and teach us more for Malawi need more people like you. God bless your family in Jesus name
Salute,sizokhazo ambirinso mwa iwo sakumasamba nde ukakwela minibus ti mabongo taoto pepani fungo lakelo.otelewanso ofunika chilango chokhwima musaiwalenso kudzalandako kwathu ku Lilongwe akumationjeza pakhani yotikweza mopilira atatu pa mpando.kmanso inuyo zomaba ndalama za Boma kapena kut anthu osaulafe chonde tasiyan tagwila miyendo yanu anthu inu ndalama simudzapita nazo kumanda ndizotsala pa dziko and musamaiwale ndi zomwe zinaphetsanso yesu,timveleni chisoni
uchitsilu basi kumaopa ngozi koma ma plain osawaopa uhule
chilungamo chimamasula anthu amene akunena zoipawa maso awo sawona zeru zagwera pa ndalama keep it up
mukulimbana ndi wamin bus kusiya wa cashgatte minbus driver ndi wosauka kodi akabe za pa zimenezo OK osamangoba ndalamazo bwaji one ndekha tidzaferana ana anga adzali akeso adzalire
Amene Zanyasa Ayambe Ndale Kt Akhale Nduna Asamagwire Maminbus, Tidzifabe Akapolofe.
Vuto limodzi la a Malawi limenelo lamulo ndilamulo we have adhere it anthu mukufuna kunyamula ma 4.4 koma tomato mumati angaphwanyike well done minister
Koma Mashovelife Eeeee Tiziona
Koma Mashovelife Eeeee Tiziona
Palibe chovuta pamenepo, aliyense akudziwa kuti ndilamulo ndiye kulemekeza lamulo ndi bwino.
Anthu okuba awa na pali nkhani za ndale palibe wabwino mbava ma criminal killers
awatu angofuna kupangirapo mbiri
It is the work of each and every Malawian to see to it that drivers are not breaching with road trafic laws and regulations.I prefer to applaud her,she has love for those on the journeys
Anthu opusa mukulimbana ndimanibus koma dziko silikuyenda bwino ayi cashgate bwanji kusowa kwamagetsi madzi abwino kulilongwe anthu kumwa suwegi malipiro ochepa 2019 musawelengele chonde ndiinu anthu oipa opanda pokomela kulanda Minbus ukutathauza kuti iweyo ndiozindikila uzalande yanga uzaone ngati suzathawa Malawi muno
That’s what we are looking for nice work madam grace
Mvuto lamakhwalawa ndilimenelo ukawamwa thawi yayitali mutu sugwira ndaonela pa uyu
We Malawians forget that we are poor nation. Malamulo ngokomela Mayiko olemela. think of this
Bola akanawaimbira apolisi kut aigwire pa Dunduzu. Ngakhale mchitidwe okweza 4 4 ndiobowa ma minibus alimbwee basi mzisanja anthu ngat matumba achimanga Zoon a zimenezo?? Ngat ili profit kaya mwapedzapo 40% ndiyambiri koma kakakaaa 100%
Nduna siyinalakwise kulanda ma key chifukwa awo mukuti ali pa Dunduzu ndi a chinyengo chifukwa zimandusa popo pa Dunduzu komaso sikuti iwo anayendesa ayi koma analanda ma key nikuyitana apolisi kuti angwire ntchito yawo
Good job !proud of her!
That’s commedable from the Honourable Minister, she just had to do that considering that some traffic officers are corrupt who allow some minibus drivers to go scot free
Ummm bro
As the name say
Kulowelera ntchito yaeni kumeneko
How?
Thus what we call the responsible government aliyese ayenera kutenga gawo pokhwimisa malamulo athu osayang’anira kut unduna wake ndichan even Ife mapassanger titha kuthandiza boma kukhwimisa malamulo athu …..well done Madam Obama…..hope other ministers will do the same
Achitabwino kwabasi mwina azitsata malamulo apamusewu
Good job madam minister Grace Obama
Mukulephela ngati mukuganiza mukuchita kapeni ya 2019 mukuluza basi
Tilibe ufulu kuziko lathu lomwe
Mufuna ufulu ophwanya malamulo?
Mmmmm analibe bus nde angoganiza zolanda basi
nduna ya bho iyi apolice umbava
a 24 ndizisirunsotu cholakwika mchani lamulo limeñelo ĺa wina aliyense including ma passengers bcz mtengo olipira ndi omweo or apaniķizane
pamenepa ndkuona ngat ndunai yaganiza mopambana ngt mphongo… chfukw tafika pano aliyense malamulo okhunza 4-4 akuwadzwa kut ndmulandu koma akondera mbali imodz, kugwidwa akumang drv nd conderctor…nanga okwerawo.. nawoso akanat aziwathira nawo zingwe.. kuwalipilisa ma two pin..chotero zkanabweresa mantha kw ma passengers kukwezedw ma 4-4
Pali ena to this effect sakudziwa kuti kuli lamulo ku malawi kuno langati limeneli komanso nkhani yaikulu ndi yoti anthu ena tisanakwele timayamba tanenelera minibus ndiye simungayembekedzere kuti munthu wachoseledwa ntengo ayankhule ngati zinthu zina zikulakwika.
thats gd move
Blessed, 3, 3 bas
kkkkkk mpaka nduna imene eeeeeee
kodi inu a malawi24 muzapangako publicify zabwino za Boma la dpp? mundiyankhe coz since I liked this page the political stories are full of against the goverment osangovomereza bwanj kut we are under them no matter what
Mixson Officer
K.ME R. K.kimiy.mom.MNM mku
Anthu mini bus akutibera. Anakweza mitengo ndi cholinga choti tidzikwera 3 pa mpando koma mitengo yokwerayo akupitirizabe kutenga Anthu 4 pampando.
Let me guess…its Grace Trump chiumia…this lady is an actress
apatseni ziphaso zogulitsira mbeu kunja osati zomwe mukuchitanzo chimanga 40 kwacha pa kg
Simply To Confess That Players Have Failed To Deliver So The Coach Itself Decides To Get In And Play Fo Them. Kkkkkk
show malaw madam,koma czot mupatse atcito anu minbus yo
Dull people with dull minds as if Malawi is rich
I appreciate her action
MMMMMM
That can happen again and again
Ndipo apitilize,ama minbus amajaira kwambiri
I like that go on
kenako timva kuti mr big man nao alandanso minbus nanga iwo asalire kkkkkkkkkkkkkk
Kkkkk yah neh
alisense pano ndi presdent
Wrong.
asaaa, zafika pamenepo, ndiye ma minbus angothesedwa anthu akhale mwai omakwera nao magalimoto ooopuma kuthandauza kuti a police sakutha ntchito yao, koma inuyo anduna mukupanga zimenezo
inu mukhale oyela mzanu akapeze mabvuto mumaleka. kungomuzuzula ndiye mongati inu nduna mulibe .upangili ongomulangiza munthu kuti izi sizabwino? koma kuonesa kuti inu ndinu NDUNA komanso wa traffic eti. mwana wa anzanu mwamuika m’abvuto ngati angamangidwe muzikhala ndi nthawi yomakamuona. komanso 4 4 ndiufulu waokwera kuti akafike, kodi zinaonesa kuti bus imenei siikafiikaaaa?
Wasalaiwe kkkkk akugwilanso
Umbuli uwu. 4 4 siufulu waokwera, ndimalamulo adziko
osangocimenya bwanji cimeneco
We want an iron hearted woman like her.
Nthawi zambiri zopanga komanso zoyankhula za nduna iyi ine sindimagwilidzana nazo koma apa pokha mayi Chiumia achita chinthu chanzeru kwambiri ndipo apitilidze tili kumbuyo kwawo. Anthu a ma bus wa amawonjedza kwambiri kudelera. Mwayitha kwambiri anduna. Ngakhale muli munthu wamayi komabe tinena kuti inu ndi abig man.
that’s good
Zachisoni eve mitengo a maminibusiwa amangokweza mmene akufunira.Just imaging kuchoka mtauni-Lilongwe to Area 25 mpaka MK500.00 or amatha kufika MK600.00 pa munthu.Ku Lilongwe kunoku mitengo ya maminibus is not justified.Boma likanalowererapo zamitengo yamaminibusiwa.Nanga minibus fare pamwezi ipose minimum wage yamunthu imeneyi akulandira pa mwezi.Zomvensa chisoni Malawi is like moving without malamulo.
Its too much indeed…..I stay in BT kma last month was in Lilongwe…..ndakwela minibus frm ntaun kupita Ku 25 pa simso paja kma mpakana 500 ine eeeeeee kunoso ndye sindingakhalekotu kkkkk ife timakwela frm limbe to lunzu ma 300 kma ndipatali ndithu sungafanizile from ntaun ya Lilongwe to 25….its just too much in Lilongwe indeed eish……..
popeza chosaziwa kuli kuiphwanyisa min bus yo ku nayeso afele pompo
M’malo momafufuza ndalama zikwizikwi zinasowa zija plus maizegate mukulimbana ndi ama minbus kupusa
Well done Minister
Kkkkkk that’s Great Obama the performer minister
Nduna imeneyo sikulkwa no matter enanu muli ndi phapha, kod myo wa anthu nd phapha lanlo chofnka nchani? Akangokhalanso muvekele ngozi! boma silikchta how do can do? musatinyase agalu inu mwava? ife sitingamayendere lamulo lanu amagalimo chosecho mitengo mwakeza .
Is that the work of home affairs? Kulowelela kumeneko. Ndiye minister of transport apite pa boarder azikaona ma passport kkkkkk
Ngakhale iweyo you can do that to save people’s life what’s wrong with you?
Sorry sindicheza ndi prostitute pa fb plz be away from me
Petro ndi mmodzi wa anthu osafunira anthu zabwino
Kuonetselatu kuti ulibe chonena shame on you
Try kumphumzila something good from good people its not too late my dear sorry I was trying to help forgive me
it’s not her work but thus her responsibility…..komanso let me warn you sibwino kumutchula mkazi woti sunagone naye olo kumuonera kut hule……apa zaoneseratu kut ndiwe moyamoya
Aliyese ali ndi mphavu malamulo akutero, chofunika ndi uboni
Poor country…..
Kuchepetsa ngozi zapansewu ndi udindo wa aliyense
That’s absolutely good move, God bless you mom, I believe even our traffic officers have learned from this too.
If you think head chef doesn’t know how to cook think again, she is the head officer of traffic officers, do you think she can’t do what the traffic officers can do? Then Think again, I truly like what she did, it’s very good example, God bless you mama
ndilekeni ndiyankhule ngati wazamalamulo… kodi pamenepa mwini minibus atamang’ala kubwalo lamlandu ndunayo ikakhala mbali itiyo?? kodi ndekuti wapolice aliyense ali ndi ufulu oimitsa galimoto panseu nkuyamba kuiunika ngati ili ndi zinthu zoyenera? kodi ndunai idakachitapo malamulo a zapanseu? kodi ndekuti nduna yaza umoyo ili ndi ufulu ophulisa chithupsa cha munthu kapena kuchotsa mano? mmm kodi ndekuti aliyense okonda dzikoli atha kupanga chomwe akufuna ngati akutetedza miyoyo ya wanthu? kodi nchifukwa chani galimoto za boma zimathanga kwambiri chonsecho mdziko muli a speed trap? kodi galimoto za boma zimasechedwa mma roadblock athuwa? ndekuti mwini minibus yolandidwayo akadalipulumusa khofi akadakhala kuti wamenya ndani? mmm zovuta zedi… pa chifukwa ichi tikuwapemphe Hon minister of health azatithandize ka procedure kenakake ku lilongwe Central hospital main theatre
am following u with interest, akangomugunda basi, wat kind of ppo ongofuna zabwino zonse zikhale zao :angovomereza kuti dziko lawa kanika kuendesa with ve numerous problems in our country koma kuli ziii eg The Malawi ‘s back bon is farming ndiemuone mmene mbeu amwenye akugulira zautsilu ndikumalakhura mopanda manyazi kuti admark igura mbeu at. gud price, this is August funso mugura liti poti tasara ndimiyezi yocepa kuti mvura igwe tizarenso sins?
baseless comment ikachita ngozi ena lifa nde uzidandaila aaaaaaa you are all wiseless
iwe utapeza munthu akuba ungomusiya chifukwa si iwe wa police?Inunso muli ndi udindo wogwira munthu ngati walakwtsa ndi,kumupeleka ku police.
Nchifukwa dziko lathu ndi losauka kwambiri chonchi chifukwa ndikuona kuti anthu ambiri amaganiza ngati inuyo bwana #antonio.moti kusukulu munapita koma sukulu yanu ndi mapepala siyinakupindulireni kalikonse chifukwa simukutha kuwugwirisa nchito mutu wanuwo . …
Moyo wamuthu kuchipatala ndi kulanda minbus nzithu ziwiri zisiana. Wachita bwino kulanda
ACHITA BWINO KULANDA KUPELEKA CHITSANZO CHABWINO. Ngozi zikamachitika mumatukwana boma, ndiye boma layamba kuonetsa ukali kwaophwanya malamulo mwatinso lalakwa?
bwana amenewadi nzeru zafupika apa…nchifukwa facebook ikufunika dislike button
Vuto ndise okwera, nanga min bus yazaza kale , then ifeyo tikukwerabe. Olakwa ndi ma passengers.
Osakagwira mbava bwanji?
Kodi iyeyo ndiwa traffic? tiyeni tiwasiyile eni ake antchito.
Komatu mulungu azachita nanu musaone ngati mukuchenjela
oky
Ngozi zimachitika chifukwa choipa kwa misewu yathu. Kozani misewu kuti ngozi zichepe.
Kkkk ndale gentlemen ndi mphavu,,ihi! Ngati ukufuna kupanga business momasuka,,lowa ndale m’bale
Nanu inu pali ndale pamenepa?
i support the minister well done Madame minister
aidziwa BOK HALAM
Nduna imeneyi ndaunyadila kobasi, mitengo anakweza nkumanyamulanso anayi anayi. A bakha a traffic awachotsemo mmiseu mu. Sakupindira a malawi
Good show
I truely support the minister
Chabwino tamva…
That is malawi walero
Good move
She did well as resposible citizen,,but this is not her duty,she was only supposed to call nearest traffic officer to handle this,otherwise its unprofetional
Akanapanga monga mukuganizilamo zikanalowa corruption…sizikanafika poti ife kuma commenta…uku ndikutopa ndi chinyengo amalawife mmmm ayi ndithu
CHIMWEMWE MUUZE ZOONA SOLMON PHIRI TIMAMATOPA NAZO ZOPANIKIZANA TIKAKWELA MINBUS AKUTI KUZISAKA ANAKAONA ZILI KUNO KU RSA
Kkkkkk yaa ndikukuvanitu ndipo maganizowo siolakwika,komaso musayiwale kudi dongosolo ndilofunika,chifukwa chisawawa chimakolezela kuononga zinthu nthawi zina chifukwa ena amangolowelelapo ndikuyamba kudyela anthu
What’s the basis for saying that its not her duty?
As a minister it simply means there are other ppl who are perfoming duties under her orders,not herserf overtaking them,that is not protocal
Even the law itserf has protocal,u don’t just jump into conclusion,is it??? A police officer incharge can not just go arrest a boy stealing mango himserf,while there are several police men on the ground working under his order,kkkk i don’t think so
Read the law bwana Solomon Phiri, it will enlighten a lot of issues. There’s no protocol in the enforcement of the law
May b there in Malawi,but here down south no police officer who is not in traffic,depertment can arrest any one on traffic offence without traffic officer approval,and hear there is mush worse on the road interms of driving than there,but i have never seen such thing like that,every happenes in order,but my b there things can b done any how
Undunawo utha pa may 2019 sipatali ai mzatipeza kunja kuno
Alibe mphamvu zogwilira minbus mai ameneyo amuchotse undunawo.
ndiye mpaka amuchotse? comeon guys..
You don’t know what you’re talking about it doesn’t matter kaya ndi nchito yako or not bola kupulumutsa anthu ku ngozi kumakhala ndi umunthu sometimes please
Akanawauza a police # ya minbus not dat dpp lad 2 react bcz her duty z 2 make sure dat de police performs beta. i tic u understand dat guys
Willy Koy, have you read the Road Traffic Act? Zoti sintchito yake mukuzitenga kuti?
Alande kumene dzikutiwawatu okeerafe
Chitsanzo chabwino anthu otere ndiofunika m,dziko chifukwa chothandiza nawo kuteteza miyoyo ya amalawi ulemu wanu anduna mukanamumangitsaso wokweza 4,4 yo ku polisi
Akweza mitengo koma akupakira ngati matumba
Big up our minister
Vuto lili pa Malawi khaya ndi umbuli sindikuziwa,Inu minibus iyenera kutenga anthu 16 kupatikizapo driver,ndiye nawo okwera akumalolera kukwera 4-4 osasika bwanji?.Apatu okwera,madriver onse akupwanyadala malamulo.Ine ndikanakonda akagwidwa otenga 4-4 wa okwerawonso azisisidwa ndipo osawalolanso kugwilitsa ntchito minibus yogwidwayo,aziyenda pansi kuti mwina okwelawo asamalole kutengedwa 4-4. Komanso otenga 4-4 wa akagwidwa alipilitsidwe ndalama,apite kundende miyezi 6 komanso akatulusidwa asayendetse galimoto kwa zaka 5,chifukwa akumapanga dala malamulo akuwaziwa. Amalawi ziwani kuti ndalama akupeleka anthu amenewa ngati chindaputsa choyamula 4-4 sichingafanane ndi MOYO WAMUNTHU.
Ngati palinduna yofunila anthu ake zabwino izitelo amamin bus kuzolowera mwano anthu kumawatenga ngati zitsilu akuwonetseni zeni zeni
Thats very commendable. Anthu awa ndi mbamva zoba masanasana eni ake tikuona.
Anakweza mitengo ya minibus pazifukwa zoti anauzidwa kuti azinyamula anthu atatuatatu koma akumanyamulabe 4-4 pa mpando nkumalipilitsabe mitengo yokwerayi.
Ulemu wanu mai obama.
Landani Kaye Magalimoto A Chaponda
We need pipo like u Madam kutsogolo kwa Team ya Flames it seems like u can manage to score more goals than CR7
We need pipo like u Madam kutsogolo kwa Team ya Flames it seems like u can manage to score more goals than CR7
zachitika kuti ?
Good and patriotic people should defend the Minister. She is the minister of Home Affairs. The Traffic Police are under her ministry. Their duty is to ensure that laws on the roads are enforced including on capacity and roadworthness.
If those minibuses kill people, you blame the government kuti ndi ya satanic, the responsible minister and the traffic police.
Obama did well. Minibuses are supposed to carry 3 passengers pa mpando. Well done madam minister. That is being proactive and practical
Yes sir
Gud Mr.
Gud Mr.
Azayelekeze kulanda yaine ndkadya pakhomn pakd tsiku limenelo, komanso asanatenge glimotyo ndtamuonesa kae kiyama, uyekeze kulanda ya 25 LL
apo mpakamwa mungonena.lamulo liposa mphamvu
Ena ndaonesapo kale
Ndiuze number plate ya minbus yakoyo, nzakulanda mkukumabga kumene ngat walakwisa malamulo.
Iwe ine nd mwana mulomwe 4rm BLK, wina azaese {BLK 223}.
good
Minister / road traffic officer… Overlapping defender…kkkk
Haha
The law allows them
Ngati a traffic akulekelera malamulo akuphwanyidwa,ndiye nduna itani?? tili pa mbuyo panu mayi tiye nazoni
loading….
Good one!
Nkhani yabwino kwabasi
dpp yaukape ikungofun podyela
Akanangoyang’ana mukanatokota,a police sachitapo kanthu mumaminibus mzawo akamachita za cashgate NDI ma driver
Uyu nde Fodya tu
Grace Obamayi Wakonzeka,akwanisa? Asamapange Zibwana Ngt Chmenecho.Asiyire Road Trafic Police Not Her,bneat Where Ever U R.
I second the move
Alipo wins akugona
Kkkkkkkk no tadzuka to welcome the move big up madam minister
Walowelera Ntchito Yaeni
How?
Serious business, akanati azitelo kwa onse okhuzidwa ndi cashgate aja bwenzi corruption ndikusakaza ndalama za amphawi bwenzi zitatha anduna limbikirani one mundipase nambala yanu ndizikutumizirani registration number ya minibus yomwe yatenga 4 -4
Offside……
GRACE OBAMA CHIUMIA
Azimayi matama! ! Akungofuna kutchuka……….kulimbana ndi anthu osauka pamene iwo ntchito kuba ndalama zamisonkho basi
pitani uko inu!
Kodi ndiwe wa minibus eti, malamulo suwadziwa?
Malamulo ake ati inu mulibe kanthu……..nduna zonse zizilanda makey dziko likhala bwino????? Vuto la amalawi wen ship is sinking u smile mukamazati timatani mwavulala kale…..this is dictatorship time in Malawi
Sudziwa malamulo,munthu oyipa iwe ,mukhaula kumene mulandidwa ma mini bus kumene
Nde zithandiza chani popeza ngozizo akuchititsa ndi zomwezo ndunazo si nanga zikupembedza pansi panyanja
iwe sudziwa kt amin bus amatibela tkuona
Kukubera ukuona nde kupusako nanga nduna sizikuberani mukuona? Mwaona kuba kwa osauka anzanu. ….
Zoona….
Amange miseu yabwino osati miseu yake imeneyi
Ngozizo mesa ndi devil yemwe akupembezayo akuona ngt sitikudziwa
Tikanakakhala kuti tonse a Malawi tagwirana manja ngati mmene yapangiira nduna iyi zinthu zikanasintha.Tikuzunzika m’minbus ngati sitinalipire.Abale anthu akufa everyday pa nseu chifukwa cha overloading komanso overspeeding.Thanks anduna keep it up.Inu a Kanjanga ndinu achitsiru kapena mutu wanu sugwira.
Futurewise Kanjangah komano iweyo mpaka lero sunazindikilebe kut ngoz zambiri amayambisa ndi ama minbus??.…ziwani kut ngoz zina ndizopeweka
Kodi a minibus amawuluka mesa amayenda pansi nanga amadusa pati popeza every single kilometre mupeza pali traffic? Ndunayo ikakambe ndi a police wo not direct approach like this mawa ikamenyedwa muziti anthu oipa
Si nduna zonse. Nduna iyi ndi ya Home Affairs. Si choncho?
Man sizingatheke inu kumenya nduna, isaaa!!!
A Traffic oti mumawapatsa ndalamawo?
Is it her responsibility to check driving license on road? If the ans is no then kulanda makey ndi udindo wake?
#Profigo udakali mwana ase mwaiwala PS ku Bingu stadium was manhandled with bullets supporter zimenezo zolowelera ntchito za a police zo…..who is minister inu munthu akakwiya sawerenga izi
Ngoz ku Malawi zafika poyipa, wina aliyense akuyenela kukhuzidwa ndikuteteza zinthu ngat izi or mosayang’ani udindo wamuthu…ngakhalenso iwe amene monga mzika ya Malawi ukuyenela kutengapo mbali pa chitetezo…osamangot zilizonse devil kumachita kumtokosola dala ayi ndithu
Zoona #Chimzy ngozi zavutadi I guess minibus zikayamba kutenga anthu atatu ngozi zitha! ! Nanga bwanji miseu yathuyi inside the cities,big towns miseu no lights. Mukati maintenance nde kumata phula kuikapo chi bump how will curb accidents?
Kumbali yamiseu ndagwilizana nawe maganizo…ku Malawi miseu silibwino ndimbali imozi yomwe ikuyambisanso ngoz
Ochita makani ayenera kufufuzidwa like iwe #Kanjangah lero lomwe upezeke utauvala unyolo/nsimbi ngozi zikuchuluka chifukwa cha iweyo
Kkkkkkkkk nde #Achimzy taganizani inuyo kuti kodi kulanda makey kwa minibus drivers ndi kukonza miseu komanso kuchepesa katangale ku a police apa msewu chinthu chomwe chingabweretse ubwino kwambri Kmanso mwachangu ndichiti?
#Omex mwina if u will involve Interpol police yes mungandipezedi…………..am not an ordinary person as u think
kkkkkkk dziko lokondera kwabasi kuti muione gamato yaandunao ilibenso misonkho
Amalawi nzomwe amafuna zimenezo nde kuombera mmanja
Shut up you morron are you happy with the situation we are in now? malawi everyday is about road accident
U r such scumbag young man looks old with big empty head…………don’t take it personal…..u will kiss ur black a*s
kodi a Futurewise Kanjangah mukut chani
dziko laMalawi lizachita bwino ngat muthu oyipa ngat iwe utazamwalire sukuyenera kukhala moyo you deserve hell
Lack of work
#Harlord_Phiri nchifukwa mukumwa madzi a manyi zimenezo zongoombera mmanja zirizonse just bcoz they r rulers..
…..iweyo nde to hell with ur minister
Ufiti
Idont see any problem line minister kulanda makiyi a min bus ngati woyendesa walakwira malamulo chifukwa amati at the end of it all amapedzeka akuyankha mafunso kuchokera kwa anthu amene akuoneka ochenjera mmayankhulidwe panopo its high time tinayenera kumakhala anthu ochita osati ongolamula chifukwa kulamula kaya mmati shouting orders has proven to be a problem ku malawi chifukwa cha anthu okonda ziphuphu ndi katangale.
Amandibowa bwanji
I bet you people have never read the Road Traffic Act, and you don’t know that it is within the powers of a line minister to execute duties within the purview of his ministry.
Not in such way hey what w can expect to hear from u…….she is ur homemate
Walakwa pati nduna? Akukhomelera mu njira yanji guys mmmmmmm ngati mumayendetsa minbus ingotsatani malamulo bro otherwise mukumana naye Grace lol
Nduna imeneyi ndindani
Chiumia
Kkkkkk koma zavuta eti
Ndaninso nduna yache
Akut Chiumia wa home affairs
Kkkkkk