The Japanese government has given Malawi a 2 billion Japanese Yen (17.7 million USD) grant for training teachers in the country.
Writing on its official Facebook page, the Japanese embassy in the country says Japan has approved a grant amounting to 2 billion Japanese Yen for the project of expanding and upgrading Domasi College of Education.
According to the Japanese embassy in the country, the project will complement Malawi Government’s efforts in addressing the challenges of shortage of teachers in secondary schools.
On Wednesday, Mr Hirotsugu Ikeda, charge’ d’Affairs ad Interim of Japan to Malawi exchanged notes with Malawi Finance Minister Goodall Gondwe.
The country still faces shortage of teachers in both public secondary and primary schools.
The situation makes teachers to have a big role in making sure that the learners or students are learning effectively since the teacher-pupil ratio is high.
The money will end up in the pockets of our delightfully and infested corrupt govt leaders and all involved. Go ahead guys share them
Just a donation ?zilibe mapangano??
Is it a donation or loan?
Mukudyaso bwino. Mugula ena magalimo ku dubai
Kulandira kwabwino koma magwilisidwe a ntchito ndi wovuta zonse zilowa m’matumba awo basi m’malo mopanga sogolo la ana anthu boma la anthu akuba ngati ili sizaliwonaso
Boma. Ndigaileniko ka 1 million kwacha ndidyere
Nde Mupangeso za maize gate
Nde Mupangeso za maize gate
Thank’s Japanese 4 our helping
DPP’s campaign money….
heeee adye bwinotu anthu andalewa
In exchange with what?coz these people dnt give for mahala
To train the teachers, hold on, the teacher’s government’s failing to pay them??
MUBENSO
kkkkkkkkk
It should read…Japan gives DPP $17.7million because we know already someone is gonna chew it all.
To steal or for what?
Nanuso ma Japanes kupusa eti
They will only train them in large numbers then fail to employ them later
azigawana kale zikafka zlowa nchithumba chawo.# poor malawi
We don’t need more teachers. We need Engineers and Archtecturers.
Mwasuta eti?
ndye ma engineers’ & ma architecture’wo azimawaphuzitsa ndi ndani kuti afike pamenepo? azangobadwa ataphunzira kale kapena? kkkkkkkkkk
You are all bright and brave enough. You know what am saying is true.
Adya zimenezo.. Kumangira ma mansion awo.. Ali chetee..
Kugoyambira chaponda ndi azizake angawana ndalama zimenezo .
30% zisololedwa.
99 per cent actually
Ndichifukwa chake timati dziko lamalawi ndilosaukisisa mukuona apa likulephela kupanga budget yoti ikhoza kulipila aziphunzisi amadalila kuthandizidwa ndiye iwe umanyoza boma umangolakwapo
For training teachers?nde azikaphunzitsa kuti? Osaonjezera kaye ma school bwanji kuti mitichi ikungokhalayi ipeze chochita,zibedwe basi zimenezo mnxxxxx!
Harf ndi za abwana.
MBAVA YATAYI IKUNYADILA ITSOLORE
Tamva nao
Kukharatu kuziba manyumba aja tamangaso Ku 43,area12,25
Amangire stadium sizimenezo ayi
momwe zateremu mbava ziyamba kukhala mmaofesi tsopano ndicholinga chot abe ndalamazo kenako asowe.
Adye zimenizo ife ayi mesa anadya akubawo
Musatiputsitse ndinu amodzi mukudziwana. Dzionjolani chipande chikusemedwa mwamnanu.
Mukatelo muba agalu inu gawanani mudye muzingolemera pathako panu
Za ziiiiiii
That is gud development but kusolora, kuba panopa mwagawana kale
Correction mzere wachiwiri mukufuna ndalama.
Mubeso
Apatseni nzeru anthu kuti mukudyna mealsma zimenezi zigwire bwanji ntchito nanga ife ngati nzika za ku Malawi tikuyembekezera kuona chiyani pa ndalama zimenezi. Baby’s pali aphunzitsi ena omwe akungokhala kodi mungalilangize boma chani pa aphunzitsi omwe apanga kale training koma akusowa chochita panopa kodi mwina umenewu sukanakhala mwayi wowalemba ntchito tsopano. Tidandaule pano ngakhale Baibulo linanena kuti zakalezo zapita choncho Boma likuyenera apa kuvala zilimbe kuti tsopano tione kusintha pamene chithandizo chikupezeka. Tithokoze Boma poyendetsa dziko ndi ndalama zotolera momwemuno, uwu ndi ukadaulo wa pamwamba ndithu. Nthawi yafika tsopano kuti mwina amalawi tisiya kubangula kapena mavuto achepa ngati chithandizo cha ku maiko ena chayamba kubwera tsopano. So ndikuona kuti apa mpata tsopano wapezeka tsopano oti zinthu zomwe sizimayenda ziyende .
Mudzidyenso a Dpp mumange maden anu ndi ndalama zokuba amphawife tikulila.
Nawoso aku japan atani? Aganiza bwanji? Ibani.
Iiiiiii Japan kudzivuta atenga zonse kuka bisa ku America Apm ndi mzake ndi mnzake …….maliza ndiwe
Miti yanu njoooooh ngati zenizeni ife amphawi tikuvutika ndikaganiza m’mene ndinayimira pa zele kukuvoterani
APA NDE MUKULANKHULA NGATI MWAPATSIDWA MPHATSO, NDE MTSOGOLO MUNO TISAZAMVE KUTI INALI LOAN
Mudye bwino ndalamazo
Ndye mubeso ndikudulani machende a DPP nose.
Kkkkkkk bg up man
Kkkkkkk bg up man muwachotsadi nthangala akaba.
Koma ndiye ndalama boma likulandiratu eeee, bola zisathere m matumba a anthu
ku bed ndiye bank paja2
khani ijayi yakhuza ayi achita zabwino
ndalama. ya ulele kapena ndi ngongole
Not Malawi, say “JAPAN GIVES MUTHARIKA $17.7 MILLION.”
Hahahaha! Anthu andale inu…..
Kkkkk
DPP yagawana kale nchahala umenewo
Training teachers who will fight tooth & nail in order to get employed.This is still Nyasaland & not Malawi.
It’s even funny that Dpp intends to construct more TTCs.
Chaponda watapapo kale zake pano
zachaponda zimenezo life zisatikhumze mutuwake sumawonaka
Good news but take care for salary gate
Prepere to give somemore to emproy them afterwards.
chichewa chake nde kuti chani?
lyk thats even enough
Good news
Dzibani
Good news