Nyasa Big Bullets have confirmed head coach Nswazirimo Ramadhan has been suspended due to what has been dubbed as the team’s poor performance.
Bullets General Secretary Albert Chigoga is quoted as having said this is in a bid to allow the Burundian who was weeks ago warned by the Football Association of Malawi (FAM) to desist from attacking match officials do more soul searching.
”He (Ramadhan) has been asked to step aside just for now looking at the team’s performance”said Chigoga.
At the moment the Peoples team has opted for Ramadhan’s assistant Elia Kananji to be in charge of the team temporarily.
The Blantyre based side continue their poor start to this campaign.
In the league, from the seven matches played, Bullets have gathered 11 points which put them in 3rd position. They are followed by Wizards FC who also have same number of points with a game in hand.
Bullets are a point behind League leaders, Red Lions, who also have a game in hand having fulfilled six fixtures. Their bitter rivals, Be Forward Wanderers, are second on the table with 12 points amassed in their four fixtures.
Amulakwila Coach Samamenya Mpira.Afufuze Vuto Lina.
Koma dziwani kuti kusuta kumaononga moyo osalakwa
Neba mabvuto ndi nthawi!
from the coach,technical panel and all the players need an overhaul….its not a one man crime
Kananj Ali ndi vuto
Abale ine ndimadabwatu game ya masters one substute and yet we wanted a goal mpaka draw ndiye kuti amafuna draw basi?munthu watisowesa mtendere uyu yenda bwino kodi paja anakochapo nyerere eti?
Abulesi ndimakape,akuonangati pemenepo nde auona ntaji kkkkkkkkk neba ukunva kuwaw!!!!!!!!
chiphwisi united smoking club
Kodi paja team ya fungo eti?
Kodi mesa mumati amatha kukocha?
Ayende basi 4 games 2 points shupit
kkkkkk,mwayambatu!
chingambwe fc mukuchosa coach wabwino chingambwe chakuzunguzani mitu ok ndikuthandizeni motere – vuto lanu ndikugolesa tapitani ku FAM mukapemphe mapenate
Kodi Vuto Ndi Coach?Munalephera Kugula Osewera Abwino Ndikukatola Sakasi Ku Ma Team Ena Ndalama Ndikuika Mmatumba Mwanu Lero Muziti Vuto Ndi Coach?Pangani Manyazi Kod Mukufuna Coach Azitigoletsera?Mudzandifunse Ngati Amene Mutalembeyo Angasinthe Ma Results.
Issues of NBB should be left to them. By suspending the coach is may be one way of solving the problem the team is encountering. Such things happen in many clubs . That is why Malawi has engaged a foreign coach.
Kuno ndiye absa ikuchedwa kuyamba tamaonelani minyaka iyonso bullets sikuchita bwino…akakhala manoma amanjenjemera ndi pa 1 monga ngat ine tsilikali ogaukira kamudzu balacks naoni ana awone majombo
I do not believe that the suspension of Head Coach Nswazurimo Ramadhan will solve matters here. Learn from Manchester United. They did not fire their Team Manager Jose Mourihno due to poor showing in English Premier League. They well knew that that they employed someone who has a callibre to change things in the team. He inherited a poor team and went on with that. His true results will be seen in the coming season. Ramadhan too has the credentials and callibre to change matters at Bullets. The crop of players we have cannot change things overnight unless Bullets in skilled strikers. The problem is money and we have to accept that. It is my humble request to bring the head coach back . This team will soon build up and come up to the form.
Nilibe polobulemu NeBa uSoVeNgE!
Coach yomweyu wayimwetsapo team wamkaka kangapo…something fishy mmm malawi football, someone is fighting NBB silently
Ndilibe Chonena Ngati Akuona Kuti Vuto Ndi Coach Asiyeni Apange Zomwezo Koma Ngati Vuto Si Coach Zidziwika Zokha.
sizili bho guys ku peeps team
several times i’ve been talking that the problem is not a coarch and a coarch doesn’t enter in the ground and i dont think if there is a coarch who talk to his prayer that whenever u reach in 18 yard box mukaphonye the problem is prayers i think there is something happen which is happening inside
Ishiiiiiii uku ndye kungwaonje zela mavuto tu uku,, kom ndichan kwenikwen my team??kom ngt ali satana ayinditu wamangako maziko.
Yaa! Zampira ,komatu neba Vuto si kochi koma ma official ena aja chibadwire mpira amaonera Ku mastand, pano angofikira chiudindo olo kugula player angathe? Koch uja ndiwabwino koma sanamugulire zida zyenera(maplyer) I don’t think abig team kukagula player wa kunsanama kusata Ku tchipa zosathandiza maplyer amene aja azipita Kaye Ku reserve kwa nthawi, Ramadan akufera za eni!!! Muli nkhondo mkati mwa neba, ndithu ndipo siinathe . achoke kaye awo!!?? Kkkkkk kkkkkk
nde mukuona ngat zinthu zisintha? The best solution is to change the sponser., Immagine, b4 traininng, every player is given 12 cigarates to smoke …Nanga izi ndi zampira? Muziona ma Hule!!!!!!
Kkkkkk
Tipindulanji?
This team needs to be reformed basi,i love the team
i aiready told u ramadan kuti kumene wapitako akuthamangisanso ndi chikwanje ndi chiteam cha chamba munyela simunati
Akangowinitsa ma game onse kannanji mumva coach kma amenei kkkkkkkkkk kma malawi
That is stupidity of we #MALAWIANS ngati team ikuchitabwino we don’t talk good about coach koma yikamuluza chonchi eeeh
More-zorse
Neba, This Is Too Early To Suspend A Coach! Matsoka Mwaputawo And U Will Regret Shortly! Ndima Game Angat Waluza? Pansika Ndichan Chamzeru Munapanga? Kodi Ma Rejected Player Mukutolawa Ndiwothandiza? Obviously This Year Ku Bb Mugwiritsa Ma Coach Osachepera Atatu Coz Kananji Mwamuikayi Alibeso Ma Paper Abwino. Thats Your Own Arithmatic, Musova!!
That is not a solution.Kodi mkazi akangophika nsima yosapsa tsiku limodzi basi banja limathera pomwepo?Khalani pansi mukambirane palibe chosatheka.Mumafuna basi mudzingowina nokha ndiye simpiratu.Afunseni amzanu odzisata zampira ‘zimayendera nyengo izi chikati gogogo chiri kwa uyu’mwaiwala kapena?kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Fisher Must Retire Also, Old Gogo In Football
Dats a welcome development & iwil happy if he is fired
Team yathuyi tisanamizilepo coach APA iyaa
take kananji too
Kodi mwaiwala kuti kochi wanuyo anaonongaposo timu yathu ya ife aNyelere??? inu lero kukamwa mbeee muli kochi koma ameneyi kkkkkkkkk muisova
Firing Ramadhan is not a solution…………
Muchotche ma strikers onse problem solved
hmmmmmmmmm uku ndiye kungomulakwira chabe coach. team ilibe ma strikers abwino iyi. vuto ndi Lipipa ndiyemwe akuonongas team coz anakanika kugula ma players abwino. zoona team yaikulu ngati imeneyi ingamakadalire ma players otaidwa kwa neba.
Vuto ndiloti bb imasewela mpira wake chimodzimozi. imakonda mpira wa overlaping kenako kumamenya ma cross kusogolo nde mateam onse anakudziwani ndi ana omwe pano ma cross avuta , mapenote avutanso kkkkkkk mpira ndi pakati nde simunati mukhaulabe.
Dzikanganani ife AMoyale titenga chiko chaka chino
kaya kwanga ndikuvetsera kuti NEBA sinthu zinasintha
kkkkkk penapake zinthu zimangovuta koma ku malawi ndi kwa bwino ndawonela mkuluyi! akubwera kumene ku malawi kuno anali wokuda heavy,muja tiziwila ma brundi koma pano ayi! Akutha kumawonekako patali ndinthu!.
Is he responsible for that performance? Eeeesh that’s not the way to go.
Team yathu ndiyabwinibwino koma zitipotopo enanunso mukusangala chifukwa mukudziwa tikati tiponde nthaka mumalila Ana inu pamalawi nyelele ndi maule atakhala pansi ndiye kuti mpila watha panyasa kkkkkkk
Kkkkk sobody deeped his hook in the team kkkk
This suspension has no logic
He is a spent force
Nde amati anga coche national team choncho
I know that once someone get Suspended, the result is a disaster! Ask Leo Mpulura.
A bullets muki ndi vuto .koma Ramadhan wakuthandizani koopsa
it happens everywhere, when the big team is not performing well the job of the coach is always at risk
We Still dont know the solution to our poor perfomance , It is not the suspension of Ramadhan no , its not the solution . we have lazy bones on the pitch .
RAMADAN nde Simumumenya ngat mmene munamumenyera CHIMANGO KAILA kut sakuchita bwino?
Misala ya bullets iyi
Why not suspend the whole team not forgetting the Straikers
Si zachilendo izi akupanga phokosowa team yawo inasintha technical panel kanayi season yathayi.
Ok
No bulets fc no news
Mavuto sazatha kwa a neba… koma neba? Why my neighbour? Hahaha
Bullets Fans Just Give Up
Bb needs the services of coach Mabvuto Lungu back
Kkkkkkkk Maule sadzamva
Kkkkk the chamba team sopano,after oversmoking chamba now they are coming with different decisions kkkk chamba sichabwino
Kkkkkki
Patapatayo siwa bata ameneyo,chipongwe bwanji!
uku ndiye kuononga zinthu…. wabwino mukantenga kut vuto si coach
kodi paja kulidi bullets eti
ndie kumukhumbatu only two games kugonja out of 7 a Wenger asasungidwa zaka 20 koma team imagonjanso koma pali team yosagonja?
Suspending a coach is not a solution ndipo apano ndipomwe mutapitilire kufano muziona a Chingambwe simunati chaka chake nchino
Coach Odana Ndi Juju Sangalimbe Ku Bullets.
Zavuta kumpanda pepa neba
Bullets Sizamva
Shame on you,this coach knows more than Amene mukumufunayo vuto ndiloti mwazilowetsa ndale
amupanga suspend not sack ,which means any time he will resume his job
amuyika mu sack
chingambwe United madzi achita katondo
Have u ever thought of suspending some of our strikers?
They thought history can repeat itself…..
kkkkkkkkk! Why suspension is going to Ramadan why not to Players? The problem of dis team is busy buying REJECT PLAYER and Chipest koma CHINGAMBWE FC mavutotu awa
Tewesa abise magoro angazaone ngati moyo ndi ophweka
Mmafuna mumve kaye kwa anzanu kenako mulembe kkkk atola nkhani ofoila inu bwanji!!
Anva kwandni?
Inu mumafuna alembe zoti sanamve??
Kkkkkkk no problem nanga mumati alembe za bodza?Chamba team aliyense ngwa chamba basi kkkk
Sizngasinthe zinthu izi, paground pakufunika kungolimbkra ma players paokha, team nd yabwno, coach wabwno pakungofunika umodz basi
Manyaka team
Shame
kkkkkkkk musova