Mkangano mu chipani cha Kongelesi wafika pamponda chimera.
Mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha Kongelesi, a Lazarus Chakwera atenga chiletso chokaniza kuti kusakhale msonkhano waukulu wa chipanichi umene ayitanitsa a Gustave Kaliwo.
A Kaliwo ndi mlembi wamkulu wa chipanichi ndipo analengeza kuti mwezi wa mawa kukhala msonkhano waukulu wa chipanichi.
Iwo anati msonkhano umenewu uyitanitsidwa pofuna kulongosola mavuto amene ali mu chipanichi komanso kusankha adindo atsopano a chipanichi.
Kwakhala kukumveka mphekesela yoti a Kaliwo amema anthu ndipo ali ndi kuthekela kochotsa pa udindo wa mtsogoleri wa chipani a Lazarus Chakwera.
Koma a Chakwera tsopano athamangila ku Khoti kukapempha kuti a Khoti aletse Bambo Kaliwo kuitanitsa msonkhanowo.
Padakali pano, a Khoti apeleka chiletso kwa Bambo Chakwera kulepheletsa msonkhanowu.
Ngati malamulo aMCP akunena kuti convention should b held 1 yr b4 G.election nanga a Kaliwo izi sadziwa ngati Kaliwo akuphwanya malamulo achipani nde angazakwaniritse malamulo adziko?aaaaa pali akumtuma ameneyo bwanji osafunsa nzeru kwa a veteran aTEMBO?
God have mercy on us
palibeso wabwino angatsolele Malawi ayi koma Mulungu yekha ndamene watsala.
Zatha. Shame to all devils.
aaa odala mkayesa ngat ochakwera atithandza koma a betaso otembo dala odali omuna zed….indee ka……
zimayamba choncho mu MCP we need not any other sign! shame on U !…….advice to Chakwera…..open yo eyes and see things r fallen apart!
consitution of MCP says a convetion should b held a year before general election @ Pangan Junior enawa akufuna kukwanilitsa zolinga
That is a clear sign of weakeness. I dont know about their constitution but Mr Lazarous could have humbled himself and prove things wrong.
Achimwene dzizimvetsani zinthuzi sangapange zinthu chifukwa choti ena afuna kukwaniritsa zofuna zawo. Nthawi ikwana convention yovomerezeka ipangika. Iyi inali yotumidwa ndiena omwe sagona tulo ndi mighty MCP cause they really know oneday its mcp.Ndie mukamafoira kuti mcp akukangana amafuna anthu ngati inu muziona choncho momwe muoneramu ndi mitu yanu yosankhwimayo.koma ife timazimanya kuti mmm awa asewera yoduka. dere nchifukwa chake anzawoo awatembenuzira mbali ina.
i dont think a GS can call up a meating without a knowledge of a chairman,a kaliwo akusewera phadaa ndibwino apite kapena ayambe chipan chake
There is no PC at MCP since amangolumana
Who is kaliwo after all?
Abusa bwelelani Ku ntchito ya amuye
Excellent And Next Achotsedwe Mchipani Whoever Is Advancing For A Conuention. We Know Someone Is Behind Ith Nonsense. Agalu Ena Amasekerera Convention Kufuna Kuti Chakwera Agwe Mzayende Moyera Mwauponda. Chakwera Is Man Of The Moment Mwamva Kale Za A Afro. Munya.
Zovuta Zimenezi Amalawi.
Ife tili duu
Kaliwo ayitanitsa bwanj I convention ngati iwo ndimtsogoleri wachipani cha Congress? He is only being used by the dpp to confuse Mcp followers
Amene aziwa za constitution ya mcp andiuze imati chani za convention? then ndiziwa who is crocodile btwn these two madolo
Ngati mukuopana nokhanokha mpaka ku court nde 2019 mudzadzikozeratu hahaha Mcp chipani cha magazi
aaah akuopa chan
A DPP musathe mau ai!Inunso kwanuko mukusunga bomba and pompano tikuonerani.Musamale posankha running mate!mwamva agalu inu!
AMALAWI: ATATE NDI AMAI!! Ndithu ndikakhala chetee, kusuzumila dziko,boma ndi zipani za ndyale m’dziko lathu zikusonyezelatu kuti AMALAWI safuna chitukuko koma kunyozana! NYIMBO YATHU YA PFUKO LA MALAWI IKUMUPEMPHA MULUNGU KUTI AGONJETSE ADANI ATHU ATATU: (a) NJALA (b) NTHENDA (d) NSANJE!! Komatu ndi m’mene zilili pano m’dziko lathu n’theladi talephela kuchotsa nsanje,nkhwizi, kaduka pakati pathu, ndi chifukwa chake dziko silikutukuka! Zifukwa zili mu MCP zingathe bwino pokambilana pachiweni-weni m’nyumba yomata! Koma taonani tsono zikuchitikazi, anthu atsatila yani? Anthuni monga ndidanena kuti,” NYUMBA YA NG’ALU SIILIMBA!! Chonde chotsani mtima wa NSANJE, ndipo mukhale amodzi n’cholinga chotukula dziko lathu. Ndikati chetee kuisuzumila DPP, siinabise mau, inanenelatu kuti ku MPOTO kaya kungapezeke wa nzelu, akumwela sangamuvotele, KODI TIKATELO CHITUKUKO CHILIPO? TICHOTSE MTIMA WA NSANJE UWU, N’CHOLINGA TITUKULE DZIKO LATHU: INE NDIKUMVA CHISONI PAZONSEZI ZIKUCHITIKA M’DZIKO LATHU CHIFUKWA CHA NSANJE!!!
Akuopa chani ,kugwetsedwa?
A. CHIMBANOOOOOOO KKKKKK kuinyumwa convention kumeneko
Kkk eeh wainyumwadi
Kkkkkk Akuopa Chani Chakwera, Wazieza Pasikelo Waziona Kuti Sakukwanila, Akaliwo Musabwelele Mmbuyo Msonkhano Uchitike Akachosedwe Pampando Mtsogoleli Wopeleka Mimbayu Kkkkkk
Chipanichi chimalakalaka chitawina koma mmm anthu ake akutsogolo amangodziwa kulongolola ndale sazidziwa. aliese wotsutsana nawo amat achoke mchipani. ndale za zotelez zidapta nd kamuzu muja ankachotsa ma founders a mcp. chakwera too much ma temper, chot adziwe izi nd ndale zimafuna anthu kut chipan chiwine. mtsogoleri wa andale amakhala pa chiopsezo nd achipan chomwecho komaso zpani zina but learn to be accommodative and follow open door policy.
oky
Obaba oChakwera okongwa zedi
bola zisabweletse ma heart attack
Nonse pitani mukachite umodzi titenge boma pogwilizana ifenso kulamulira timakufuna
Zinalinso choncho muthawi ya aTembo ndi aChakuwamba chipani chake chomwechi tsokatu iri
Ochakweratu Oli Kuopa Kuti Zawo Ziwadera
Inu adpp mwakhaula mumaona ngati zofuna zanu zikwaniritsidwa. ngati muvutika ndi ana aprimary mungathane ndi MCP, mwachepa ana inu. Mukhalira kupha anthu chonhi.
Kk tsono wakulu tafotokonzan bwino pakati pa kutenga chirenso kwa a Chakwera ndi Dpp dzikukhunzana motani?
kkkkkkk #Harrison funso labwino kwambiri ayankhe ameneyi
kkkkk abroh,osamasokonyeza zithu
KALIWO AMAMUTUMA ndi a DPP
Mcp idachuluka zinyalala ife ndi achigawo cha kuyambira makolo athu koma mmm chipanichi chikufunika formating too much viruses. president wa ma virus ndieso nd wa ma temper
harrison sombea timitu tanu nditosankhwima pandale.Zoti anthu ena amatumidwa kuti azisokoneza zipani za anzawo.Ndie khalani choncho.
Kodi akuiopera convention?
O chakwera ulikuopa zedi,aa?? Mpaka court injunction.
Kkkkkkkkk koma ana amenewa akumuzuza munthu wamkulu kwabasi
naweso iwe was Malawi 24 paliso kunjenjemera APA akutuma eti mxuuuu usamale
Akhalebe olo atadzaitanitsa third term pali kupusa kwa otsutsa zomwe zikupeleka mwai kwa mbuzi
Koma ndiye convention ndiyiwoopsya zedi eeeee mpaka khoti pulumutseni…. kkkkkkk
HEHEEEEEEEE MUZINGOTERO IFEYO NKUMANGOKUPENYANI NDITHU kkkkkkkk musova
Nkhani yachitika liti coz ine ndaiwelenga 4 days ago
Ndiye ife zitikhuze?
Mumadikira ena akalemba inuyo mukope hmmmm makape
Koma azipani ngati simusintha atsogoleri kuzipani kwanu osusa inu!,UYU SIMUMUTHA 2019.DPP IKHALABE MPAKA 2024.
Hahahahah apa nde ayambad kale njenje njee kunjenjemela
2019 Talamulilaso bas weather you like it or not DPP nd moree
Chakwera Ndi Galu Mai Kabwila Ndi Gulu Lanu Kachotseni Msanga Chiletso Chimenechi.
You call him galu, who are you? Idiot
guys ngat kuli chipan chovesa chisoni ndi mcp. dpp kuendetsa chuma poor koma ndale akadaulo ndietu satenga ndi chuma koma ndale. chenjeran a mcp anthu akapatsa mpata inu, koma zochitika zanu agologolo, agalu enieni kulimbana.2019 muzikat atibela pamene mphavu ya ndale mudaikana. vuto mukusiya zomwe mulungu adakupatsan kupta ku ndale muyaluka muona.
Kkkkkk….koma F.Jumbeeeee
Iwe Frank Jumbe Iwe Ndiwe Ndan?Ngat Ine Ndi Idiot Iwenso Mapwala Ako Ndi Chatsika Wakoyo Mtsogoleri Opanda Masomphenya!
Iwenso ndie weniweni galu wake.
iwenso ndie fisi wen wen ndi pitala/petulo nyapapi wamathanyula.pachilungamo petulo ndi galu utsogoleri wamuvuta
Chokani Ana Lazaro Chakwera!Ine Sindine Wa Mutharika Koma Uyu Mukut Chatsika Uyu Mpaka Ku Court Kukatenga Chiletso Nayeni Kape Ameneyi!
kangat
ANA ACHEPA DPP SAYIKWANISA 2019 BOMA
Ngati alephera kuthetsa vuto la ku primary mudzakwanitsa chiyani? do no dream to defend the govt 2019
kkkkk ka leave grant kachaniso
Wainyumwa