People in Mulanje have been engulfed with disbelief after a girl who died 20 years ago reappeared in the district on Wednesday.
Mulanje Police Spokesperson Gresham Ngwira has confirmed the development with Malawi24.
According to Ngwira, the lady only identified as Mercy Chibwana who is alleged to have died in 1997 while she was in Form 2 is said to have resurrected at Namulenga in Mulanje.
“Yesterday the girl reappeared and started following another woman who asked her where she was going only to tell her that she would narrate everything to police,” Ngwira said.
“When she arrived at Namulenga police unit she failed to say anything compelling officers to refer her to the nearby health centre.”
According to Ngwira, while there she started mentioning some names of her relatives which made the people to call the mentioned relations who identified her through some marks on her body.
Currently she is at Mulanje district hospital for further treatment.
Ndkufuna mkaz omanga naye banja kkkkk adali asadafe ameneyo ufit fanz
Plz any one who know VG and TA send me.
koma amfiti anakakhala ngati ascience. bwezi ali pa no one amalephera ntchito zawo kuzionesera poyera
Mmmmmm
Malawian girl or phantom?
But she still looks 20
Ndizosatheks zimenezo
Iyi si resurrection chifukwa resurrected munthu sakhala ndi mafupa fufuzani liu loti mugwilitse ntchito Resurrected Munthu amakhala Ghost iyo ndiyo Resurrection
All Who Are Saying This Cannot Happen Definately You Have Never Visited And Stayed In Mulanje. That Is A Magical System Called Ndondocha,they Use These People In Farms.
people confused on the word “ressurrection” may be you should not use this word, coz if you can go to her grave you will find may be no way out, why Jesus’ tomb a heavy rock opened, so this one was just somewhere magically.
Mmmm
ximachitika
Ndiye PA Malawi Pamenepo
welcame back
sure mac
Ndizoona zimenezi?
In mulanje we trust in magic no one can say no
boza ili,apo ndye mwasusana ndi plan ya mulungu
This is all nonsense! Why do Malawians believe in such crazy stories? Truth is that once dead and buried then a human being ca never come back to life. This is more fiction than fiction!!!!!!!!
There’s nothing like that,true lies !
it’s not a new story,resurrection? if you believe there is no God,evil deeds and superstition at work
Kaya Zako Izo Kayawazukira Kuti Upeze Mwamuna Omanga Naye Banja Wauponda Panopa Anthu Akukwatirana Amuna Okhaokha Komanso Akaz Okhaokha Ndye Usova
Izi zikhoza kukhala zoona ndithu kunoso ku ntheu zachitika mwezi wathawu amakhala kuti munthuyo sanamwalile ayi koma anangosowesedwa mmatsenga khulupililani ndithu zikuchitika izi
What a zombie!
Girl usaone ngat yelusalemu wasopano uja nduyuyu ai.izi ndi chito zasatana mmene zikugwilila tchito, ndiganiza utamwalila amalume ako anazalemba kalta kuziwisa zamalilo ako ku tauni selfon inali yosow, ground fon inali ku boma, meshi zophoda ndi zonyezmila ndi zo sekemela zalelo usazilondole ndiye chionongeko cha moyo uno, ungoyang’ana panta wa yesu kut ukapulumusidwe mu chilango chili nkuza.
Could this be news?
Alomwe musatinamizepo apa
She did not die after all She went miss ,If she was dead her body was supposed to decompose. Maybe witchcraft take place mufutse bwino ameneyo
Izi ziliso nkhata_bay west,mnyamata anamwalira 6 years ago,koma pano akumaonekera kwa makolo ake.
ndkunena pano akumabwera ndkumapita and as for now akumamu siira nsima yamazulo ndikuiika pa( chitanthali in my Tonga language) poyanika mbale.
usiku amabwera ndkuzadya nsima yemwe amamsiirayo.
Anaulura komwe akumamusunga ndi omwe anamuzembesa magically, ndipo atafusidwa afitiwo anafomelezs,analonjezaso kut azamupeleka chifukwa akuwavutisa,komano atafa tinamu kwirira
Anapha eti ndkumu tumiza Ku jowen kuti mwana wawo azika landira kawiri pamwezi,komano man yaku joweniyo inamkana eti coz anali friend wake
Tikudira tsiku lomwe afitiwo analonjeza kuzamupeleka ndipo ndikaona nawu
Its raining here in Mchinji kaya amzanga kumeneko nyengo ili bwanji?
Amadya chani mmandamo ameneyo mmmm koma alipeza banja nde azafenso kachiwili?
i think anamusandusa ndondocha not dead ndiye angomutulusako atopanaye
This is not strange but The Malawi 24 you need to come up real evidence rather spreading news without proof!!
Makosana chiukililo sichinafike ndithu,iyeyu akufunika apimidwe,mwina ngati nkhaniyi ikukhudza ziwanda nditha kumva
A Malawi 20 yrs akuyenela kukhala atakalamba
uyambeso kudya nsima ye wlcm
Enze ana soba chabe uyo….she just got lost.
Run out of stories ? Then shut up.
Anamwarira Ali ndi dzaka dzingati? Nanga pano Ali ndi zingati? Mmene ndikumuoneramu, zikuoneka ngati Ali ndi dzaka 20 zimene.
apite naye kwa aja amati ufiti kulibe aja akawafuse kt nanga mumnthuyo anali kuti?
BBC NEWS
She was not dead she was somewhere else
Wagonjesa imfa
kunoso Ku ntcheu zachitika .mzimayi anamwalira mchaka cha 2001 wabwera Ali wamoyo .pano ndinena ali kwawo kugwira ntchito zapakhomo.akuti anamwalira pa ntcheu district hospital as she was derivering her baby.
from 2001 anawuka chaka chitcho???
chomwechino last month.she says that she was at tsangano .and was sold by her uncle BT the uncle passed way
#Inno you are aliar , which bible do you use ? Jesus raised the dead and not him never heard of Prophet’s bones which raised a dead person ?
Kkkkk kkkkkkkkk sikweni kweni ndakhala ndikuzionapo izi ndi kwathu zimatero paja kuli anthu okwima
Kodi nkhani ngati zimenezi zimangochitika ku malawi konkha abale?
ABENA MALAWI MUKALEKE JUJU FIMBUYA FYANDI UBUFONTINI
I guess she has breasts now if she died with no breasts
The same case happened in Tcheu, Mlanda where a woman died in 1986 came back to life in 2006 & she explained clearly that she was alive by the time her
i second u.
The case with this woman same story
Why she didn’t talk then? How can she watch her own mother in agony?
Ebrahim Jamal , its normal not to speak until she is ta
Its normal not to talk in this normal world unless she consult man of God or traditional doctor
I wonder how some people pretend ngati sadziwa
koma amalawi timachitilanji izi? Mumapitanawo kut ndipo mumakawatan? ZOKHUMUDWITSA.
That’s wonderful
Welcome back
Anamusunga abaleake uyo paja mulanje nyanga kwambili wauka?iyeyo kutani olo kalelo anthu amauka atatha zaka zambili choncho
Kutereko simunamveko zangati zimenezi zitachitika???
Zakhala zuchitika mobwereza bwereza izi
Usually it’s connected with black magic,the person could have been put to death by the powers of charms or rituals I may say it that way then after the rituals expire its when the dead can resurrect SIMPLE AND STRAOGHT FORWARD
Why urging like you ain’t sons and daughters of mother Malawi where magic still in practice
with wichcraft this is possible.the real body is that resurrected one,that which was burried was just a her shadow.we have experienced similar cases like this. to hell satan
with wichcraft this is possible.the real body is that resurrected one,that which was burried was just a her shadow.we have experienced similar cases like this. to hell satan
Koma sugar nde alipa k1001 mulimba kumwa tea kapena mudzngoyipota ya mmawa poti tangokolora kumene.
Kkkkkkkkk waganiza bwanji?
These are last seconds
nothing is imposible to God but it is deficalt to belief
Tell us more!
what evidence do they have that its realy the girl that died.did they go to the graveyard and check whether bones are missing or not? or did they do DNA testing to realy make sure they are related with the family.A malawi tisamango khulupilila zinthu ngati ndi make dzana kulibe science. wake up
I don’t think she died,hop anasowa kupita kosaziwa munthu aliyese…lyk abduction
Zosatheka Zimenez!!
Waku amaukatu kuthupi bola chikhulupiro nanga lazalo anauka bwanji? Nanga mtsikana wambaibulo ujaso? Ndiye uyu simunthu?
That will nevver happen .She is just resembling the one who died.Nobody will resurrect apart from Jesus who resurrected bibilically.But scientically no one can. She should be examined mentally.
Hahahaha Tell them bro. I told them but seem to stand their ground. Jesus and only Jesus.
muzimva anthu inu sikut anamwalira ai, koma anamupha mmatsenga , now wapezeka is just ukulu wa Mulungu
is she not supposed to look old counting the 20 years that has passed
Welcome back!! wapeza dziko litssintha, kuli fb, watsap etc. zakumwa zozizira zatsopano eg fronzy. Team ya Bullets umasapota ija pano ikungoluza, uiwonera wekha sunday likubwerali ku mulanje konko. tinalamulidwako ndi mzimayi mdziko muno. a president anafako ali paudindo. zina ukuuza ena
Kkkkkkkk
kkkk iwe uzizimisila chambacho ukafuna kudya wamva
Haha koma nawe
Eeeee koma athu ena basi kkkkkkkk
kkkkkk
kkkkkk
kkkkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkkkkkkk muuze
Pansana pako iwe kkkk
Kkkkkkkkkkk Kunalinso Cashgate Ndi Maizegate Olimbenazo Aise
IWEE BWANJI KODI KKKKKK
Kkkkkkkk koma guyz
Azinzako pano ali ndi ana anzawo komanso zizukulu, komanso nanja ija lake malawi pano siyathu.kkkkk
Zambiri zasintha ku Malawi.We have got so many prophets komanso kuli Miracle Money.
kkkkkkkkk guys sambi
walandilidwa ameneyo basi alowenso mpingo waine
komanso cash gates,maizegates,watergates
kkkk
Ukanabwela mofulumila ukanapezaso ozimanga zingwe za blue
Guyz angodziwiratu zot kwacha inagwa …ndezinthu aaaaa kaya awona apangabwanj!!!
Akanadziwa sakanadzuka, pano malawi ndi number 1 pa dziko lonse lapansi kusauka
Kkkkk Malawi anthu anasiya kulambira Mulungu akulambira ma prophet
Kkkkkkkk koma ndaseka anthu mumaitha kkkkkkk iiiiiii kodi kumulandira?
And across th border kuli Mugabe amene zinthu zotchedwa azungu zaona polekera, so logger tht too plz hahahaha
Koma munthu walandiridwa uyu… Kkkkkk
Bullets yokhayo musamuuze angabwerere komwe anali.
Koma komwe ukusutilako chamba chakocho mpaka ndikufufuza Mpaka ndikupeze,Tidzabande limodzi
Kkkkkkk anthu inu mzathu yi mwamulandiladi ndaona chomcho. Ayi ndikofunikadi kumuuza zina ndi zina zomwe zachika iye kulibe.
Kkkkkkkkk eeee kma ndye wapeza zambiri zitasintha kkkkk
simuli serious kkkkkkkkkkkkkkkk
Ganja at its best
Pano Kuli Amuna Or Akazi Ogonana Okhaokha.
u pipo,we had a similar story here in zambia,but it ended without proof.they went to exhume the grave and found a skeleton of their dead.it ended up as mistaken identity
zamasiku omaliza
Iiii Lee
eee ufiti suzatha
Welcome back!!
guyz nd zoonad koma?muxakhale mwakoka nazi nde nkumanamza anthu y.ngat nzoona pelekan nambala ya doctor,polce or amfumu a mmudz wawo
Ngati ndizona ine ndinafunitsitsa atazafotokoza ekha pa programme ya zilipati,chifukwa anthu enanu aaaaaa idont trust them.BOLA NGATI AKUYANKHULA.
Zoopsyatu izi asisi…
Ineso ndikadzafa ndidzaukaso
ndukuuzani mwava kufa mkudzuka eti nde luso Lanji limenero
1979 mukut mwanabe mpaka relo zitheka bwanji, samakura kunali iyeko, muthui ndi ZOMBIE uyu,
Sanafe ameneyo,bcuz whn o livin tinz e.g anthu,dies,decomposes&bcomez manure,how possible iz it tht she must come out bwinobwino,is her graveyard still intact?..anatulukila pati,kapena ngati anatuluka yekha how dd she manage to kick de soil&coffin out?..zaboza izi,i will only bliv if sum1 dies,ressurect&bcome azombie.
I Agree Wit U Wanena Zowona Ndi Zombie Ameneyo Lol
Eee man ! to resurect its nt a simple story to tell. Cant happen. bru
Look at now, it is been proved to be no relationship with those claiming she is their daughter.
Dont worry akwatiwaso magaye ake adyela inu
Now afraid to visit Malawi again
uwu ndi umboni woti,satan ndi olephera. soka kwaochita nchito za satan chifukwa mulungu mwini mulengi aza ulula zonse zobitsika.
Kumapemphela- anzathu omwe adamwalira madzana azaka zapitazo, mpaka lero adakali m’manda. Thupi lawo lidakhudzidwa ndichilakho cha matenda, moyo unagonja ,
Paja kwanu Ku mulanje ndi kwa anthu okhwima hetiiiiii
Eish koma dzikoli abale zoopsa kwabasi….chikuchitika ndi chani mdziko lathu lino
Akuoneka ngati akukana kumwa fantayo, mwina amuyiwalatu.
Nane anandipangako ndinathawako kuli mavuto
shaaaa
Talapani abale,kupha- mukupha anzanuku tsiku lina mudzakhala inu mudzamuuza chiani MULUNGU?
Is she still in the same old age or she is a Mama now?
Stop twisting people with lies
Holy ghost… fire…kkkkkkk
koma tatiuzeni mutsikanayo pa 20yrs ndikanthawi, akuwoneka bwanji akukalamba kapena momuja
tsikanayo Anamusowetsa Mumasenga Ngati Kuti Wamwalira Koma Anali Atamutenga Ndikumakamugwilitsa Ntchito Zolemetsa Mumasenga Mwaomo. Bambo Yemwe Anapanga Zamasengazo Anamwali Ndipo Zinthu Zonse Anasiyira Mkazi Wawo, Ndiye Tsikanayo Wapeza Mwayi Wothawako Pamene Anzake 5 Adakali Konko… Kwavuta Kunamulenga Eti Afukule Manda Ake Kuti Apeze Umboni Weniweni
After 20yrs she can stl trace her home?
After 20yrs she can stl trace her home?
unbelievable
Mmmmm
Eeee 20yrs its too long bt …
Alengezad pazodiak kolma alikuhosptal
Bible limati wakufa sadziwa kanthu bii.komanso limati kufa kamodzi kenako chiweluziro
komatu munthuyu anakaikidwadi kumanda and she’s back.Only God knows
Eeeh ine nditamuthawatu..mmmm
Someone is trying to scare man of the Moment ,,Hon Kalua
20years its too much dnt fool people here
Ask Mr Thindwa ufiti kulibe
God’s glory is being manifested
Mulungu adzalanga
Amawazembetsa m’matsenga, samakhala kut amwalira. Zinachitikako kumudzi kwathu
kumudzi kwanu nkuti?
Ku Lilongwe TA Kalumbu
So how old is she?
Eeeeee masiku otsilizadi eti mmm!
Not ressurection She was used as ndondocha,bathwa. ndie muziti kulibe ufiti
Kkkkkk African stories
welcome back, ine nde ndigwira basi ameneo
Nde ena akakhuta akumati ufiti kulibe heeeee muzaziwona sindikunenatu ndrama
Wafikira kumwa fanta
No such thing. Religion has brought more harm than good,,
No such thing. Religion has brought more harm than good,,
Zaboza izo
Byb ndizoonadi
mmmh mwinadi but I’m not sure……..100%
tsono. oukayo. wangofikira. pa fanta. analidi. kudzuwa mutchini osati. kumanda. ziziimba zangosuluka
abwere kuno ndikumufuna banja
Pls tell us what really happened?atiwuze kuti anali kuti?cz guys ufiti mst be a true thing,but im glad shz bk wt her family at last image th trauma sh mst hav gone thru
Mmmmmmm kma ku malawi
May be she was kidnapped by mfiti oops paja mfiti analetsa a President
ndi mzukwa umenewo
Let someone from Mulanje tell the exact thing.
Ndizoona aseh. I have relative komkuno ndi nurse pa mulanje hospital.. Wacheza naye.. Of course tym imeneyo ati samalankhula bohbo. Coz amakhala ngt wasokonekera.. Kma abale ake anali konko
Kkkkkkkkkkk
Masiku omaliza satana akulamuliradi yooooo
It’s possible.with God all things are possible.
Anali chingayo uyu
Malawi51, have you followed the story to the core? Could it be resurrection? Really?
I’m quite sceptical. Only Christ Jesus resurrected, the rest of us are doomed, thanks to Eve’s sinning against God. Death was given to us as a punishment, we must die and never wake up again someday.
Are you really sure sir?Don’t you know the scriptures about the resurrection of the saints during the rapture??
He doesn’t know,school him,may be he doesnt believe in resurrection like the saducees
Whaaaat…!
Zoopsya guyz hv sn wif my nakd eyes its true kma nzaufit
Eeeeee aise ndye wafkira mmavuto2 ingobwelelan man dziko linaipa ili, : amuna akukwatana okhaokha, anthu kuphana, achuma akungozilemeretsa, milandu ikukomela achuma, just few! Anyway uziona wakula watha
kodi ndi tsikanabe kapena wakula ndi amayi
Just thank God my dear for what has done to u.
“Glad to know that She has been alive all the past 20 years”.She will die for real one day,just like all of us will.
Eeee Alibo Ndipo Ndikwatira ine Bas
Mmmmmmm nde wina azisokosa kuti ufiti kulibe? Fokolo zake
Koma Brashyo yobaya iyo ili mmutu mwakeyo ndi momwe adametela mu 1997 yo kapena mwamumeta waukamo? Nkhaniyi ndiikhulupilira ngakhale zaka zikuchuluka koma poti mwaika maina a mapolisi officers, ma health center komaso polisi unit , ok amulandile koma abale ake akawadziwa eti?
Kukhwima a malawi kukonda kudya za magazi ndizimenezotu ndiye pamenepo tiziti zichani zimenezi
Za CHAMBA eti! mwasowa chokamba eti?
Not true
That means she wasn’t dead! Really u people can’t think?
Harf Kumwamba analiko, sopano walowa mlig yaulendo wathu wautali ndiso osabwera.
ndie achibale akumati naye bwanji ?
Km lero tidya kapena tixingomva xomwez aaaaaaa
I can’t bliv this
Mulanje eish
Zosamveseseka
This cant be true. She wasnt dead…she just went mising
Mozambique jives.
Wangobwera kt adzaonere game ya Bullets ndi Silver pa MJ park
kkkkkkk apa ndiye wayithatu mwina tipume poti ndabva kuti wawabweletsela magolo aja anasowa ku bullets aja lipipa umayitha kkkkk
Abwelere ku school akamalizitse pliz
Watopa ndikulira mu chigayo
atada ngati ntumbuka kkkkkk khope ngati ndolo ma hope a jo gwaladi
Kkkk kma big mwaganiza bwanji?
u r very stupid,mulungu akukhulukire
Kulankhula kolakwika uku pedzani ena malo ochedzera
Yes ndizoona ndipo dzina lake ndi Mercy Chibwana,anabadwa muchaka cha 1979 ndpo anamwalira muchaka cha 1997….Padakali pano akumupima pa chipatala cha boma ku Mulanje
serious?
Was buried?
Kmano anazindikira bwanji mudzi wakwawo iyeyo n atamufunsa walongosola kut zakhar bwanji kuti apezekenso akuyenda pa dziko pano
akuti sakulakhula kalikose.ndikuona ngati anangomusunga masenga ameneyu
Malawi stories
Yes anaikidwadi mmanda koma chodabwitsa ndichakuti wapezeka ku Nkando ndpo anapita ku police ya Namulenga..atafunsidwa walongosola kuti zaka zonsezi anali mushop ina mu Limbe mumzinda wa Blantyre…Komanso anakwanitsa kutchula maina aabale komanso achibale atayitanidwa abvomera kuti ndi m’bale waodi
Za chigao chino izi
Axe Tiuzeni Zoona.
Tiziwitsen zambiri adolo
ameneyo amamugwiritsa ntchito ngati ndondocha, ndizamatsenga izi,
ine ma photos ake ndawaona
Wina akuti sakulankhula. Wina akuti akulankhula. Timve ziti ziti? So far amene anauka kwa akufa anatero mu nthawi ya Yesu basi (Yesu mwini, Lazaro ndi kamwana kakakazi kaja).
kkkkkkk koma abale zina kambu zinaleku
Kkkkkkkkkkkk
Musanamizidwe kuti sakulankhula…anakakakhala kuti sakulankhula apolice akanadziwa bwanji abale ake,kwao komanso komwe anali nthawi yonseyi….Kumeneko ndikwathu thats y ndakwanitsa mpaka kutchula dzina lake komanso mudzi wake
#ANN_MSOKERA… mwati sakulankhula kalikonse..
#PAT,,naye akufotokoza monveka bwino kt kupolisi mun2yi wazifotokoza bwino lomwe…
#TITSATE_ZITI???
nanga wa shop ku limbe yu,akumufotokozanso??
Mesaa ati sakulankhula ndiye walongosola bwanji?
pano ali ku chipatalabe?
Nde iyeyo wafotokoza kuti analikuti nthawi yonseyi?
Kom Andrew iwe moti sunawelenge bwino comment walemba Pat yo?
Pat wutiuze zosatira za ku chipatala.
Mwana amene anabadwa 1979, panopa ndi amayi azaka 38, ndie muthui wabwera ali mwanabe analiko samakura, izi ndi zaboza muthu akakwililidwa samazukaso ayi, ameneyo amachedwa kut, (zombie)
Ndikubwela ndizamufusile,mwina nane ndizauke,wanna ask detailz inbox
ZOMBIE
Inde,Lucy tandifotokozere mnene wamvera.
Tell us more mmene ziti ziziyendera
Zikachitika tivela kwa iwe Pat utiwuza momwe zikuyendela ku Mulanje ko ngat mtolankhan wathu kwalero lokha
Musaiwale Kamlepo
Ndizodabwitsa kwambr Kma Is This Real
Masku omaliza dyabu ayaluka ndithudi
Ife zoterezi tinaziona ndi maso , koma anadzaoneka one year later ndikunena pano alipo mpakana anakwatiwa
Apite akafukule pa manda omwe anaikidwa akakapeza mulibe mafupa ndiye kuti ndiiyeyo
Mulanje wake wa kt popedza ine kwathu ndi komweko osamawanamiza anthu mukakhuta tsabola mwa amwenyemu ayi,
Ndizoona ndipo ndi Mercy Chibwana wa kwa Bulaimu vg,T/A Juma
if u r in Mulanje does nt mean u can know everything happening in the whole district, mwaona ena akuwuzan za mudzi kwachtikira zinthuzi inu simukudziwanso pamenepa wakhuta tsabola waa mwenye ndani?
Anthu enawa, kumangotsutsa zilizonse?
ndizoona Mr inu nde kuti mumakhala kuphiri ndi anyani
Mumvelen chson mun2yu nd THOMAS DIDIMU
kkkkkkll ndaseka
Iwe usawachititse manyazi alomwe amzako!!! kumangotsutsa zopandapake basi..
Argument yako yofoila heavy….
mxiew!!!! ndaBoweka nawe
iwe osangonkhala chete bwanji iwe ngati kulikwanu ifenso ndikkwathu koma tikudziwa kuti mulanje ndiwamkulu dzedi ndipo sitingadziwe madera onse ayi nanga iwe kwanu ndimulanje yense? chitsanzo ine kwathu ndi mulanje border koma sikuti midzi yonse yaku border ndimaidziwa ayi nanga iwe munthu odziwa mulanje yense ndiwakuti dela lakwanu mwinanso ine mulanje ndikudziwa madela ambiri kuposa iwe from mkando ulendo mzizila uyo mpaka kwachinyama mbowela msika wanjala chisitu kwansona kwagawani and many more kuzungulila mulanje koma or half mulanje sidamdziwe ayi
and munthu ameneyi kwao ndikuphiridi onyamula nanazi kutsika nawo phiri kudzagulitsa ku minimini ndiye ukadziwe zakwajuma mwina iwe umauluka usiku boma lonse kuti udziwe zamulanje yense
Hahahaha mpaka amakhala Ku phiri ndi anyani kkkkkkk
Zoopsya kwabasi kkkkkkkk
Her grave exist? Zamasenga zimenezo
What????? Hw old is she now??
Idont Bliv This Crap
Zoopsa
What?????
Pano nde sanakalambe? Kumene analiko samakula?
Kkkkkkkkkkk aaaaaaa mbwiyache inu
zowopsa kwambiri kugonjetsa imfa for 20yrs
Jeepers creepers; Reloaded
Is she the second Jesus? Dziko lili pa moto ili.
muntu yo nd wamkaz??
malawian girl resurrect after 20 years …… inu mukumva ngati ati ndi munthu wa mkazi kapena wammuna?
Kkkk wathamangila kuwona mutu bwanji………..enawa awona ngat mutu wankhanitu
kkkk iwe amaenela kuikaposo muntu wamkaz kkkk kapena muona ngt sitidave haha malawi!!@indoda
Is this real?
Nde zakumulanje zimenezo
You can’t die twice, what happened to her please?
zaulendo uno
It means she dd not die, ok fyn how old is she panopa??
Eit eit….sanafedi,anangosowa
Kkkkkkk How old is she now? Ngati ali ndi usinkhu ngati wakale akhoza kukhala yemweyo.
Ufiti kumulanje.anamusowesa eti eiish.You better thanking God girl