It is only a few hours since Rumphi East legislator Kamlepo Kalua was found this morning in Malawi’s commercial city, Blantyre.
However, the legislator had already become a subject of hilarious memes in which some Malawians are taking photos of themselves tied and comfortably sat as the legislator was found this morning.
*Since the death of Malawi’s celebrated drama actor John Nyanga aka IZEKI in May last year, Malawi has been searching for one to fit his shoes koma ndaona kuti Mulungu si james watipatsa Kamlepo Kalua kuti azitisangalatsa malo mwa malemu Izeki*
COMERAPE CARLUWER
Good joker!
shaaaaaaaaaaaaaaaaaaaa’ kamlepo should not take malawians as fools. afufuzidwe basi.
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk koma gys,,,, flames sidzathekadi ndithu
Anthu ogulitsa chamba mitu yawo siigwira ntchito. Nchifukwa chake dziko lonse anachiletsa. Chamba sipano. Mufunseni Kamlepo akuuzani ntchito za chamba
Those that are tying and taking pictures of themselves, are DPP cadets who wants to move pipos attention from the real issue here, so that pipo should take this whole issue for granted, as if the victim has gone insane or is crazy, but let me assure u, that time will tell, soon or latter, the truth shall be known.
The world is but a theater, its Hon. Kamulepo’s turn. Let him be heard.
what we are concluding is exactly what his abductors want us to think. That he staged his abduction. DPP woyeeee. Yagwila. Lets hope he has not been injected with something bad. like something that would kill him slowly. Amalawi open up your eyes.
How can a man be unable to untie himself after being left alone while tied both hands in front with a rope, #DRAMA,,, stop the crap, this is not hollywood or Bollywood…
Kkkkkkk!! abduction ya pa banja
kkkkkk! wagwira kumoyo
Komatu kamulepoyu mutu wake ukuoneka kuti watupa akuonekaso nga wamwa midori kkkkkkkkkkkkk!
Kkkkkkk analibe zingwe za black kapena red ….anali ndi za blue basi
For sure atalowa mtchire watulukila mu nseu…….thank god,after taking IZEKI watipatsa uyu KK!
Koma zoti galimoto zakezo zinabedwa ku Joni ndipo eni ake akuzifuna akuzidziwa?
Vuuuuuu!!
Lost but found kkkkk
No comment, let’s wait and see.
Iwe kamulepo ukupangitsa manyazi anthu uphunzira asaa
I believe Kamlepo was abducted by highly planned and calculated people. They know exactly what they were doing. I see most people commenting here they are playing in the mind of abductors to way people will put it.
How best do we define yourself,,Kamlepo should be given a chance to defend himself. I really sympathise with him and I wish he is well supported to determine the truth.
God still loves Malawi!
Kkkkkk……is this mocking him or in solidarity with him?…..kkkkk aMalawi be serious mwanva
Lost but found.kkkkkkk! Thats a political propaganda! Triying to increase turnishing goverment’s image. Ndale za m,ma 1960s. We r in new era Mr Kammulepo.
Who can tight him like that if it was a serious matter?, zopusa
Kamlepo kufuna podyera!?? Hahahamwakura musiyire ana zimenezo
He is stupid bcoz he was busy watching TNM on the stoep of grand mother their by Zolozolo shopping center in Rumphi.
I know a celebrity, personally lols Nyajere Wa Kwa Mzukuzuku
Hahaha inDe
you make my days kkkkkk
Haha koma ndaseka
Mwalowesa chibwana inu olamula
Mmmm amwene ine sindiyikonda DPP koma njomba awa akana akita filimu yina mwina tikana mumva
Nde akutinso memory card yake kaya yatani kaya… Mawa fredokiss akamugurire INA mu sky electronics kkk
Ine zo kundimvetsa chisoni bwanji amalawi tisamaopa chimo, ngati mkulu mu kunama kufuna kuti muipise mbili ya dziko lino Mulungu akukhululukileni chifukwa ndimamvetsera mwa chidwi anthu ena amapephela kuthokoza mulungu kuti mwapezeka. Komanso ngati muli enanu munawaba akuluwa tasiyani chitidwe otelewo ambuye yesu akubwera posachedwa asakupezeni mukupanga zimenezo.
Kukhala m’malawi ………eeeeeee!!
Kkkkkk
Museweroli Chindime anali…..
Kkkkkkkkkkkkkk kamlepo kaluwa ????
Kamlepo style hahhahahaahh
Hahahaahahahahahah
Don’t play with someone’s problems….
Dont listen to hm too much canibas
Tingoti pepeni koma maziyamba dala zinazi kaya
Kkkkkk,where this world is taking us.
Kamlepo,umangofuna kutchuka basi,shame on you!!!!!!!!!
Mkwachamba kAmlepo ayeseso plan c
Let’s not judge for anything is true until proven not….
FACT: We are living in a world where people and truth are strangers.Guess what becomes of your sentence.
Plz let me know
Ha ha ha ha ha ha ha ha!!! Koma ziliko ku malawi!
ua masters took him thy wanted to do wat they did to Chasowa
Hahahahahaaaaaa en kkkkkkk Kanlepo is diruu…..mmmmmm the same like “Gwanda Chakuwamba….ine kunva kukoma amafuna kupha km #Mulungu wakana man heheheheheeee Malawi shame!….
kamlepo made my weekend kkkkkkkk
Whiskey nyama yootcha zanga pheee
ku abduction kumakwanisa kusamba konko kupesa mumatha man
Kamlepo wapezedwa apa hahahahhahaha amati Amalawi ndiogona amva dilu yakeyo, koma wadabwa ndi m’mene A Malawi akuyankhila
Attention seeker idiot
Am tired of seeing this shit of Kamlepo ..are you telling me that theres no other thing to post hee ??? f *ck this page..
Zinazi ayi ndithu
Koma abale….
Hahahahh cant stop laughing! This has now become a laughing matter
ndi kape
pezani plan ina kamlepo mwagwa nayo imeneyo
Bwanji a William Kamlepo akukuchititsani manyazi eti?
Found
Kkkkkkkkkkkkkkkk ayese plan b mwina igwira.haha
hand off we are tired of Kamulepo news find other news so that we see strange things
You can say that again
Kamulepo ndibulutu
Iwe ndie munthu?
linali plan,cholinga chogwetsa boma
Boma lake liti? lokugwa kalero, Yenseesss
dpp
aaaaaa munthu sakuyankhula muzitinso ndi plan ubulututu uwu mukamba apau moti nokha simukuchita manyazi?
am not bulutu,km ndi plan lake wamva.ndale za ku mw
Siolakwa kamlepo
Tizigwe timeneti osadula bwanji kkkkkkkk koma chambachiiiiii kkkkkkkk
Kkkkkk mkuluyi utambwali suzamuthera
Bt what if it is true?
The possibility is very high considering that the police refused to be involved and then the man reappeared
They want us not to take the guy seriously
Don’t bother yourself brother it was not true he’s an idiot
The family did not report the matter to police
Uyu alandire makofi basi mbuzi ya MP
same storeee??
Hahahaaaaa akitaa saafa amangopezekaa wo njatwaa kkkkkkkkkkk
kkkkk kamlepo ndidoro zamatikitiki chweee mwana chiwee kkkkkk
*Since the death of Malawi’s celebrated drama actor John Nyanga aka IZEKI in May last year, Malawi has been searching for one to fit his shoes koma ndaona kuti Mulungu si james watipatsa Kamlepo Kalua kuti azitisangalatsa malo mwa malemu Izeki*
COMERAPE CARLUWER
Good joker!
shaaaaaaaaaaaaaaaaaaaa’ kamlepo should not take malawians as fools. afufuzidwe basi.
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk koma gys,,,, flames sidzathekadi ndithu
Hahahahhhhaaaa mmalo mompatsa ndalama alandire makofi
Kkkkkkkk CHAMBA CHOSUTA AKULUAKULU KKKKKKKK MISALA YAYAMBA BASI APA Kkkkkkkk ULENDO UNO SUPATSIDWA OLO 1 kwacha kkkkkkkk. Walemba mmadzi
Kkkkkkkkkkkkkk paja kukhala mmalawi ndikulimba mtima aati
Anthu ogulitsa chamba mitu yawo siigwira ntchito. Nchifukwa chake dziko lonse anachiletsa. Chamba sipano. Mufunseni Kamlepo akuuzani ntchito za chamba
Those that are tying and taking pictures of themselves, are DPP cadets who wants to move pipos attention from the real issue here, so that pipo should take this whole issue for granted, as if the victim has gone insane or is crazy, but let me assure u, that time will tell, soon or latter, the truth shall be known.
The world is but a theater, its Hon. Kamulepo’s turn. Let him be heard.
Just wait azitolele alakhula ameneyo
Tiyeni amalawi tizipanga zina ngati anthu akuluakulu, zinazi olo mwana atha kuletsa.
what we are concluding is exactly what his abductors want us to think. That he staged his abduction. DPP woyeeee. Yagwila. Lets hope he has not been injected with something bad. like something that would kill him slowly. Amalawi open up your eyes.
How can a man be unable to untie himself after being left alone while tied both hands in front with a rope, #DRAMA,,, stop the crap, this is not hollywood or Bollywood…
Kkkkkkk!! abduction ya pa banja
kkkkkk! wagwira kumoyo
Komatu kamulepoyu mutu wake ukuoneka kuti watupa akuonekaso nga wamwa midori kkkkkkkkkkkkk!
Kkkkkkk analibe zingwe za black kapena red ….anali ndi za blue basi
For sure atalowa mtchire watulukila mu nseu…….thank god,after taking IZEKI watipatsa uyu KK!
Koma zoti galimoto zakezo zinabedwa ku Joni ndipo eni ake akuzifuna akuzidziwa?
Vuuuuuu!!
Lost but found kkkkk
No comment, let’s wait and see.
Iwe kamulepo ukupangitsa manyazi anthu uphunzira asaa
I believe Kamlepo was abducted by highly planned and calculated people. They know exactly what they were doing. I see most people commenting here they are playing in the mind of abductors to way people will put it.
How best do we define yourself,,Kamlepo should be given a chance to defend himself. I really sympathise with him and I wish he is well supported to determine the truth.
God still loves Malawi!
Kkkkkk……is this mocking him or in solidarity with him?…..kkkkk aMalawi be serious mwanva
Lost but found.kkkkkkk! Thats a political propaganda! Triying to increase turnishing goverment’s image. Ndale za m,ma 1960s. We r in new era Mr Kammulepo.
Who can tight him like that if it was a serious matter?, zopusa
Kamlepo kufuna podyera!?? Hahahamwakura musiyire ana zimenezo
He is stupid bcoz he was busy watching TNM on the stoep of grand mother their by Zolozolo shopping center in Rumphi.
I know a celebrity, personally lols Nyajere Wa Kwa Mzukuzuku
Hahaha inDe
you make my days kkkkkk
Haha koma ndaseka
Mwalowesa chibwana inu olamula
Mmmm amwene ine sindiyikonda DPP koma njomba awa akana akita filimu yina mwina tikana mumva
Nde akutinso memory card yake kaya yatani kaya… Mawa fredokiss akamugurire INA mu sky electronics kkk
Ine zo kundimvetsa chisoni bwanji amalawi tisamaopa chimo, ngati mkulu mu kunama kufuna kuti muipise mbili ya dziko lino Mulungu akukhululukileni chifukwa ndimamvetsera mwa chidwi anthu ena amapephela kuthokoza mulungu kuti mwapezeka. Komanso ngati muli enanu munawaba akuluwa tasiyani chitidwe otelewo ambuye yesu akubwera posachedwa asakupezeni mukupanga zimenezo.
Kukhala m’malawi ………eeeeeee!!
Kkkkkk
Museweroli Chindime anali…..
Kkkkkkkkkkkkkk kamlepo kaluwa ????
Kamlepo style hahhahahaahh
Hahahaahahahahahah
Don’t play with someone’s problems….
Dont listen to hm too much canibas
Tingoti pepeni koma maziyamba dala zinazi kaya
Kkkkkk,where this world is taking us.
Kamlepo,umangofuna kutchuka basi,shame on you!!!!!!!!!
Mkwachamba kAmlepo ayeseso plan c
Let’s not judge for anything is true until proven not….
FACT: We are living in a world where people and truth are strangers.Guess what becomes of your sentence.
Plz let me know
Ha ha ha ha ha ha ha ha!!! Koma ziliko ku malawi!
ua masters took him thy wanted to do wat they did to Chasowa
Hahahahahaaaaaa en kkkkkkk Kanlepo is diruu…..mmmmmm the same like “Gwanda Chakuwamba….ine kunva kukoma amafuna kupha km #Mulungu wakana man heheheheheeee Malawi shame!….
kamlepo made my weekend kkkkkkkk
Whiskey nyama yootcha zanga pheee
ku abduction kumakwanisa kusamba konko kupesa mumatha man
Kamlepo wapezedwa apa hahahahhahaha amati Amalawi ndiogona amva dilu yakeyo, koma wadabwa ndi m’mene A Malawi akuyankhila
Attention seeker idiot
Am tired of seeing this shit of Kamlepo ..are you telling me that theres no other thing to post hee ??? f *ck this page..
Zinazi ayi ndithu
Koma abale….
Hahahahh cant stop laughing! This has now become a laughing matter
ndi kape
pezani plan ina kamlepo mwagwa nayo imeneyo
Bwanji a William Kamlepo akukuchititsani manyazi eti?
Found
Kkkkkkkkkkkkkkkk ayese plan b mwina igwira.haha
hand off we are tired of Kamulepo news find other news so that we see strange things
You can say that again
Kamulepo ndibulutu
Iwe ndie munthu?
linali plan,cholinga chogwetsa boma
Boma lake liti? lokugwa kalero, Yenseesss
dpp
aaaaaa munthu sakuyankhula muzitinso ndi plan ubulututu uwu mukamba apau moti nokha simukuchita manyazi?
am not bulutu,km ndi plan lake wamva.ndale za ku mw
Siolakwa kamlepo
Tizigwe timeneti osadula bwanji kkkkkkkk koma chambachiiiiii kkkkkkkk
Kkkkkk mkuluyi utambwali suzamuthera
Bt what if it is true?
The possibility is very high considering that the police refused to be involved and then the man reappeared
They want us not to take the guy seriously
Don’t bother yourself brother it was not true he’s an idiot
The family did not report the matter to police
Uyu alandire makofi basi mbuzi ya MP
same storeee??
Hahahaaaaa akitaa saafa amangopezekaa wo njatwaa kkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkk
Abwana zakusekesani kikikikiki
Kkkkkkkkkk anthu atopa bro