Nkasa comes to the defense of Chaponda: Chaponda is ‘Yosefe wa lero’

Joseph Nkasa

Mose wa Lero hit maker Joseph Nkasa has come to the defense of Minister of Agriculture George Chaponda who is being accused of corruption.

In his latest release, Nkasa has accused Malawians of being jealous of the Minister and thereby framing him as a thief.

Mwandisandutsa wakuba, nkhani ya chimanga. Mwaimitsa mboni zonama. Chimene ndaona ndi mtima wa nsanje wakula m’Malawi,” sings Nkasa.

Nkasa likens Chaponda to Biblical Joseph claiming that he is being disliked by other people for his close association with the President as Joseph was disliked for being a favourite of his father.

Joseph Nkasa
Nkasa. Backs Chaponda.

“Nkhani ya George Chaponda ikundikumbutsa mamuna wa mu Baibulo uja kalekale,” sings Nkasa claiming that the accusations against Chaponda are a resemblance of the plot that the relatives of Biblical Joseph made.

Nkasa however warns all the people fighting against Chaponda that they will soon be begging from Chaponda for a place to rent as he will be the landlord. A reference that some people think means Chaponda will replace Mutharika as it has been rumoured.

 

Advertisement

599 Comments

 1. ankasa mudadyapo zingati?kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkndakomoka ndiphwete ine kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk ziiiii

 2. Mutu ngati mkasa, wamva nyau zidakupanda zija sizinakuphunzitse, galu iwe eti, wasowa zoimba kapena misala, uzimvera nyimbo za abzako

 3. Inde ndalama nzoofunika koma Nkasa wanyanya. A Chaponda momwe asokonezela ndalama za anthu (taxpayers) komaso kutentha ma office a boma built by late Kamuzu (ause mumtendele) burning like his own farmer mkumati Chaponda ali bhooo Mkasa go 2 hello

 4. a mkasa kale timkagula nyimbo zako koma utalowa ndale tidasiya ndipo sindifuna mtavera nyimbo yako olo utulutse 20 sindingaononge ndalama zanga ,azako omwe saimba zandale mpaka lero akutchuka akupindula .sungabakire mkango otha nyama nkhalango ,kunali saku amkaimba zomwezo adatha

 5. a mkasa apano nde mukufun kumenyedwaso. muthu ovesa chisoni kale ndi kale mukufuna kupitilizika kuvesa chisonibe… kod muzazindikila lit ankasa.. kapena muligulumo? tiyeni nazo mupeza posiyila…

 6. Mkasa is useless, amafuna atalowa ndale koma vuto geri sakutenga, olo certificate ya STD six yakale IJA alibe, mbodzole munthu ochititsa manyazi

 7. Amkasa ngati lilidyera usamale udzafera zayeni chilichonse uyamikire koma ndiye ndiwe munthu ochititsa manyazitu xul ndiyofunikadi ndaona Matumbi sanalakwe pokunena kuti unayithawa tsiku loyamba WK yoyamba term yoyamba

 8. Anthu mwamulalatira Josephy Nkasa.Mwalankhula zakukhosi kwanuko.Komatu ulenje umasimba wako.Ine mwaochepa omukonda Nkasa pa nyengo imeneyi ndine mmodzi wake.

 9. Apamkomela mvula ya chilimwe,zitsiru ndiwomwe amamuchemelerawo.Mchitidwe umenewo ndiwomwe ukuzendewela dziko lathu la Malawi kuti lisatukuke,kumangosekelera zopusa.CHIKUNTHIDWENSO CHIBOLIBOLI CHIMENECHI!

 10. Iwe mkasa mâchende agreen wo and very stupid You have a villagetic problem get out useless munthu

 11. Mkasa amuyika mkasaka. Kosaka Mkasa ayamba kumusaka iyeyo. Mkasake mkasake mkasa anakasaka kasaka kandalama kwa Chaponda, Chaponda atayitulukira adamuponda Mkasa poona kuti amafuna amiponde Chapondayo ndalama za mkasaka komwe Mkasa akukafana.

 12. Ankasa kungomva zoti yuda anagulitsa yesu, inuso mufuna mugulitse luso lanu ndi achaponda.kkkkkkk koma kumalawi olemera akutigwiritsa nthito

 13. amene zikukupwetekani kagwereni uko kasa ndie wen,wen zisiru inu mumangozolowera kulalata enanu muzintchito mwanumo mwabaibam musamuweruzezanu chaponda sanabe ai koma maboza basi munya muona koma ndie mukakhuta chimanga cha chapondda mwayamba matama munali ndani inu kupanda DPP kukupulumusani munali ndani inu zeru zochoka kwamulungu anapatsa aDPP lero iyoo ikudutsa ndithu

 14. Amkasa Ndi Opusa Iwowa Amanama Kuti Ndi Phungu Waanthu Osauka Koma Iyeyu Akukokezera Kut Nduna Ziziwononga Katundu Wofuna Kuthandiza Ovutika

 15. Its year which we wait.why Malawi?l saw sme opportunities ,as Malawi struggled to come out of its worst economic crisis .oh father i prayer to u to stocked this people fathers for this issue father to this corporate father .aman

 16. Kkkkk kkkkk ngakhale kuti nda comenter mochedwa komabe ndangoenela kutero maka pongofuna kugwilizana ndinonse ndinonse amene mukudziwa kuti akuluwa ngozelezeka. ukamati Yosefe walero ukutanthauza chani iwe munthu osokonekela mtundu? Mabala anakugwila gwila ku Dowa aja wachila ukufuna wina atengenawe tsoka? Wekha unayimba ndale nkanyama koipa wekhatu osatinso munthu kukuuza, iwe nkumakasapota ndalezo ndinu opusa bambo mwamva? ukapitiliza tingowauzanso Anyamata aja azakugwire gwilenso mmene Chaponda wakowo wawongela dziko lino ungamaamikile za uchitsiluzo? munatha akulu vomelezani mwamva? nthawi yanu inapanga Expire palibenso zokokela, kodi pano nde ukubisala kuti chikumenyeleni ku Dowatu unasowatu, koma samala aise Malawi wa Lero wakwiya samene ukumudziwa wakale uja anthu atha ku kupanga zosapanga. ingomupempha chaponda wakoyo akupatseko ndalama zakubazo.

 17. Bustard mkasa, kodi mwasowa zoimba eti? Akulu inu ndi opepera kwambiri. Anthu ambiri akulira ndi #maize_gate inu busy kuyamika mbava. Inu ndichifukwa achair anakunamizani galimoto. …muli ndi phuma pandalama zandale

 18. Eeeeh kkkkkkkk….going thru the comments here- che Nkasa komwe muliko bisalani..ngati inali ganyu ndalamayo ndie ingothela timabody guard tu kkkkkkkk

 19. Shupit za mako akazi ako ndi malemu ambuyako kuphatikiza malinyero wakoyo chaponda uziona mkasa iwetu ulibe ma board guard tikunyenya nyenya

 20. Nkasa ndiochenjera amapita pamene pali ndrama inu odandaulanu palibe chimene mupindulepo muzanu wadyapo ndiye kuziwa dale bt I see some of u guy simuzalemera u r stll blind open ur eyes and c what’s going on

 21. mphuno salota animbila mfiti manja chosadziwa tini ninin nini nini ehh ndangodutsa ine pano.ko,a Mr Mkasa ngati mulibe ndqlama ingoyambani kukumba ma toilet kapena kuwomba zidhina zofanana ndi mutu wanuwo kapena mutha kupita kumakasenza matumba a chimanga ku admarc osati kuimba nsete ya nyimbo yomuyamikila George ChapondaNchimbaWagalu

 22. The “wakwathu syndrome”. chitsiru chili ndi mwini.

  dont insult before praying for them. Malawi needs God’s intervetion. zafika ponyatsisa.

 23. KOMA CHOSANGALATSA MCHAKT NKASA BAIBLE AMAKHALA NALO PAFUPI KOMA ZIMASOWA NDI NJIRA ZOFALITSILA UTHENGA WABWINO ,MUWONGA AYIMBASO INA YOTCHEDWA FARAO WALERO

 24. Zkuonetsa Chaponda Ndi Peter Zawo Mzimodz.Peter Bwanj Sakumuchotsabe Chapnda Pa Unduna???,akuwopa Akamuchotsa Azamuulura.Chapondayo Akukaniranj Kutula Pans Udindo??, Akudziwa Ali Ndi Omubakira(peter).Mbuziz Znachta Kupangana.Nawenso Chitsiru Ndi Munthu Ovetsa Chison Mkasa,sunalapebe Muja Anakusasantha Chmutu Changat Chidinacho??.Wait Uwona Zazkuru Tsopano.

 25. ..kungomva kuti grab every opportunity in life basi,wati udye nawo za maze gate

 26. ehhh koma mkulu uyu.from kuimba mapwepwete mentioning names like tam tam,darious mtambo, bingu, joyce banda, bakili muluzi pano george chaponda….zangosomyeza kuti mkuluyi amanyambita kuphazi kwa aliyense wamakobili olo kuphaziko kutaponda manyi

 27. hahaha,, he want to take advantage of desperate chaponda for personal gain. that is his opinions and we cannot follow his demands. nkasa must also recognise that he is out of fassion now and not popular but rather common

 28. Munthu Womvetsa Chisoni. Anabwera A Bingu Anaimba Akuti Mose Wa Lero. Anabwera Amai Akuti Mai Wachifundo. Lero Ndi Izi Akuti Walakwanji. Taking Malawians For Granted.

 29. ZANDALE IZI MUKALIMBANA NAZO MUCHEDWA AKULU AKULU. ASIYENI ANDALE APANGE ZANDALE NDIMMENE AMADYELA. INU PANGANI ZANU. NONSENU KULIMBANA NDI NKASA BASI. NONSE NDATITU NONSE MWANYOZA NKASA NDINU MBULI. NDINU OPHUZILA KOMA NDINU MBULI. ALIYESE AMENE AKAKHALE PAMPANDO AMAPANGA ZAKUNYUMBA KWAKE MUSADIKILE KUTI KUNYUMBA KWANU KUSINTHA AKAYAMBA KULAMULA AKUTI AKUTI MUNGOCHEDWA PANGANI ZANU NGATI ULI ULESI MUKHAULAAAAA

 30. Hahahahaha koma amkasa moti inu simukudziwa kuti mukuyimbila fiti mmanja ndimkakuwonani ngati ndinu a nzelu koma ndawona kuti ndinu bwampini

  1. Aaaaaa koma ine abale power imazanditela pena nkaona zomwe news zaku malawi amalemba ,after all who is Nkhasa kumalemba on news this a national issue if he was wina wake wa politics oky fine but this noansess ting akafunda mbalame yeni yeni ,ine mafuna APM ayankhulepo ndi mlomo wake anzao amapanga bwanji alibe mphamvu nkomwe no voice za ziii zenizeni Nkhasa watumidwa anthu muiwala Chaponda your attention malawians will fall on Joseph pls ,lets match basi whole malawi , the government has to step down we call for emergency state , pls malawi aaaaa why inunso amalawi24

  2. Ur on point bra! Nkasa chisilu chamunthu ichi chimapita komwe kuli dollar! Aliyese olo mwana akuziwa kut chaponda ndiokuba

 31. Nkasa akufunika sukulu yakwacha kuti mwina azitha kuzindikira kuipa ndi ubwino wa chinthu. Nanga wilt thou compare a thief and the Biblical Joseph?

 32. Amkasa musatiwonongere dzina loyerayi chonde. Osampatsa mavuto walero bwanji?? Kwaamene anakumenyawo anaku khululukira, uzayetsere kubwera kukaronga kuno, tizakugulura mafupa uziwire2 zimenezi. Nyani wachabe chabe iwe.

 33. ngati pali munthu omvesa chisoni ndiwe nkasa pa malawi pano sumaziwa kapena? uzimvere chisoni ngati pali mbuli pazoimba pamalawi pano ndiwenso fool and stupid

 34. Sindinamvepo oyimba kapena otsatira chipani akuyamikira nduna koma amayimba nyimbo zoyamikira pulezidemti tsono nkasa akuyamikira achaponda zikukhala bwanji mmalo moyimba nyimbo yoyamikira apitala

 35. A Mkasa umphawi uwapwetekesa awa. Wayiwala paja achewa olusa ku Dowa anampumuntha nkhani yoyamikila Joyce Banda mkunyoza Chakwela. Mu ulamulilo wa Bingu anakwela ya Bingu (Mose wa lelo)
  Mu ulamulilo wa Joyce Banda anakwela ya Joyce (got beaten up)
  Mu ulamulilo wa APM wabwelelanso ku DPP ndi uyu akutsutsana ndi maumboni onse ngati ndi iye lawyer.
  Zoona mbava akuiyelekeza ndi munthu wolungama wosankhidwa wa Mulungu si misala iyi? Zoonadi mitu yina imangokula, umphawi si zinthu ndithu, umamusandusa munthu chitsiru.

 36. Komanso a Nkasa umbuli wao ndiwautchisi bwanji, zikugwirizana bwanji za mbava yoba chimanga ndi Joseph munthu wanzeru? Kkkkkk ngati mwasowa choimba amfumu siyani zopusa ife timakana!!!!

 37. He doesn’t know even to sing mbewa imeneyi , what he knows kupempha thru manganje ake amaimbawa, nthawi ya Muluzi adaimba yopempha, as well as Bingu’s regime, now ndi izi, searching 4 green pasture

 38. Our government need young leaders. I said this just because we can see how these elders leading us. Akutipotoza and they very good pochita katangale. Malawi tikhulupirire ndani kodi? Ophunzira amene ndamene akuba! yo! Fuko langa!

 39. Ankasa inu muli ndi ubongo,munthu omvetsa cisoni aphunzitsi ako ali amene anakuphunzitsa primary,atamva izi aaa angangoti nthawi yao anapatsa pusi onyera muufa,hiiii,wapusa pandalama,mwalandilazi nzamatembererotu ,kazibwezeni,kapena mukagulire manda alendo kwanu,udzimvera cisoni abale ako amene akuvutika wamva iwe,

 40. Ankasa inu muli ndi ubongo,munthu omvetsa cisoni aphunzitsi ako ali amene anakuphunzitsa primary,atamva izi aaa angangoti nthawi yao anapatsa pusi onyera muufa,hiiii,wapusa pandalama,mwalandilazi nzamatembererotu ,kazibwezeni,kapena mukagulire manda alendo kwanu,udzimvera cisoni abale ako amene akuvutika wamva iwe,

 41. According to the holy bible Josephy’s character was like Jesus Christ. So the question is do we find Jesus in the maize gate, Was Josephy involved in corruption and telling pple lies. I think Mr Mkasa has mised a point and h is confused coz h want to become famous with evil. Stop preaching evil mr mkasa and take Jesus as ur personal saviour and you will understand who was Josephy in the bible.

 42. He is just another disgrace who is always listening to his own outdated music. Ask him who did the torching of Kamuzu offices.

 43. Kodi choir ya Nkasa idakalipobe??????? Ndimaona ngati inathatu. Mpake kumaimba za Chiphazi chopondacho poti pano anyimbo za choir imeneyi zimanvera ndi nkhalambazo.

 44. Nawe jonse ukuika nambara yakoapa kuti katsa ayitege fundo zakuchepera ukadwara utsati titsokhe ine ndeayi mikhakhana yaufiti kuipatsa nambara nawe katsa ukutipagitsa manyazi kuvina sitha koma uhure ndatsegura school yovina kwa chendausiku pa kware koma ukabwera ndiufiti ukathera koko kuriadara umaziwakare chutu

 45. atan munthu vuto he is ineed for money ,mkadakhala inu mukadatan kma in real sense chaponda and his govt si anthu oeunka kwapanga support

 46. Mkasa guys sanalakwitse ineso ndipez njira ndidya nawo ndalama zimenezi kkkkkkk 9.9billion???? Asaaa Chaponda ndimunyengelera kuti ndizichulutse mmatsenga ikwane 50billion……..Honestly the mistake is of our President here he wud have shown the public that the said minister is a culprit already,,,,,,,,why is he keeping him in cabinet?thats why anthu opanda xool yokwanira adyera ngati mbuzi imeneyi akulondola ndalamazo,,,,,,,,,,,,Timuveka matayala ameneyu akachita chibwana ife ndi anthu okwiya kwambiri had they used the money for drugs,kumanga ma xool block,kungogawana iyeyo ndi anyapala anzake aku Admarc achina Mulumbe….

 47. Kkkk ndakumvan guyZ mwatokota hvy..kkk vuto limodzi mkasa samamva chizungu..mwina angafune kuwelenga nao ma comment ..chonde favour him…kkkk

 48. Maluz Angomupha Bas Wangoganiza Kut Adye Za Chaponda Eeee! Walemba Madzi Amalawi Adachenjera Pano Zolamulidwa Ndi Mbamva Tithetsa

 49. Zikavuta ku town muliko ankasa zingobwerani kwamoreni tizapitilize kugulisa matumba oika chimanga malume anuso che bauleni anamwalira kuno kwamayaka

 50. one roman legend had this to say “….wen yu find yoself in the postive [email protected] of the majority u hv to pause md reflect”……koz something might b in yo thinking capacity…… in this case mkasa wuld hv paused nd reflected that @time wen the country is turning against chaponda over corruption allegations …..sb chooses to b inndefence…….guys its high time we have used awa music to bck nosense…….mkasa grow up

 51. Kkkkkk waziwala nyawu zaku dowa dikila ndimuuze raster dema kuti wayambilanso zako zija ndiye uzinamiza anthu kuti una borne kape iwe

 52. Munthu okhwefuka diso angawaone bwanji mavuto a anthu; ankasa ndi agogo akowo nonsenu ndi agalu odya matewela; nkhope ngati kumbuyo; anthu osusuka inu; mpaka kukazinga chimanga mu office; kodi nsogoleli wathu wakale alikuti?; IWISH YOU CAN CONTINUE TO BE PRESIDENT;DR BAKILI MULUZI;(!

 53. Mkasa is currently living under a tremendous poverty level. Chaponda has helped this piece of shit financially to step into the studio n record. Mkasa thinks we are still in those days we used to blind.

 54. ndimafuna kuti andigaireko zomwe chaponda waponda kuchimangako ndinamva kuti ndi ma billion

 55. Aaaaa! Mbuyace, amoya, akwen, azinaa! ndie pamenepa mwapanga chan ati? zomwe mwapangazitu mchimodz~modz kunyela muufa nkukukwilira, Azina inetu ndkamakhalaa!, ndkamagonaa! ndkatoesa ngat ndwe munthu ozindikila kma nalero ndatokudzwa kt ndiwe mbuli, achamatowo, tombolombo, muleme wachabe~chabe. Kma iwe kwanu kunatsala anthu kpn uliko wekha? Nanga ana uli nao? Azinaa mesa paja mukati ndinu phungu waamphawi? Mukatotinamiza eti? nanga tawonan lero mbiri yanu yayipa ndzinthu zaziii, Ngakhale chapondayo ndie wakupatsa zngat munthu oipa wakhama ngat ameneuja ndan samudzwa? Chenkasaeeeee! pomaliza ndngot apot wambwambwana wakhalira zako zomwe.

 56. a Nkasa umphawi mukufuna kufika nao pati, zoona kufuna kupempha ndalama amatero? ai ndithu chitani manyazi, uyu ndi Chaponda akupondani, ngati mwatopa ndikuyimba ingopezani zochita zina, pitani ku ma community colleages mukaphunzire kusoka masaka achimanga

 57. Sukulu ndiyofunika kwabasi. Osati chifukwa choti uzagwire ntchito yokha koma even kaganizilidwe ka munthu. Apa zawoneselatu kuti nkasa ndi mbuli yeni yeni sikudziwa kalikonse what malawi is going through chifukwa cha munthu yomwe akumupanga praise. Umbuli unakupweteka khala chete nkasa

 58. Kuzolowera kurandira zakuba,kapolo iweo pokwatira akazi 15umati udziwadyetsa cha????? Galu opembedza mafano iwe ,fool

 59. Nkasa analowa uchitsiru ndipo anatha basi. Iye akungofuna kuti Chapondayo akamumva amupatse ndalama paja anadzolowera za ulere. Panopa Nkasa sadzayimbanso nyimbo zabwino ngati kale anafoila basi, kupusa.

 60. Amkasa Ngati Ali Maluzi Mukufuna Kupempha Tangopemphani Osati Munamepo Apa,dyela Muzamufwira Vyawene Chizeleza Iwe Huuu,,,,,wiiii!!!

 61. He was poor before!! Poor people made him rich!! NOW HE FORGET WHERE HE CAME FROM!! HYPOCRITE !! You’re the person who pretend to love the poor whilst to eradicate your poverty!! Mind you!!
  GOD IS JUST WATCHING!!

 62. Ngati pali mbuli ya oyimba pa Malawi ndi mkasa. wangokula mutu opanda mzelu akugula ambuyako nyimbo zimenezo.ndiwe galu kwabasi anthu akuvutika iweyo ukuwombelaso mmanja pansana wambuyako

 63. NKASA Nde Kaya. Dyera Ma TEPI Sagudwa, Ma CD Ake Sagudwa, Ma DVD nawoso sayenda. nde abale mumati akanatani mwana mwamuna? akananyoza sakanapeza phindu 😀 😀 😀 😀 😀 Koma apa amugulila galimoto .

 64. Nkasa, speak louder cos very few with a gift of wisdom see where the winds are blowing from, how & why.

 65. That’s a song of a madman who lost sanity in music production by blowing with political wizards for search of money. We Malawian we can’t reward that stupid song.

 66. stupid man.kodi kuyimba si mbali yako kapena?.we are tried of your stupidity.mind you if you are out of your nsenses,malawians will kick you.

 67. Kkkk mkasa iwe nde ndi mbuzi. Yopanda nyanga poinyoza amat mbuzi yanjumwa ,,,,,,, chidzete iwe ndithu ,,,,,,, ukhwima kapena ,,,,waiwara ku chiromoni kut anaku phumura zakozo urekeretu komaso usadzafike. Dera ra kwathu udzayenda majamaja ,,,,,,chimutu gati mbatire

 68. Ndiri ndi chisoni Nkasa kuziononga Dzina lako kamba kamakhobili.I see now why people are joining Satanism Nkasa is the one.

 69. Only those who promote looters will support Chaponda but if real Malawians who really love Their Nation will Never Vote for Chaponda or peter 2019,Chilima is better.your party has good Manifesto but a party with thieves… No-no no its better to sleep under the bridge than in the room full of Mosquitoes.Nkasa Wait… for chichewa comment.

 70. wangokula mutu nkasa eti? zoti galu chaponda watibela ndalama zachimanga sukuziwa? amalawi pano akuvutika ndinjala. muzipatala chakudya mulibe , kundende akaidi akufa ndinjala ndimwambili momwe mwakuzika ndinjala anthu mmadela osiyanasiyana akuvutika ndinjala pomwe ndalama galuyo wangozikhalila ngat zathumba lake koma zopasidwa kut amalawi mwina vuto lanjala lingachepeko. kusowa zoimba madala inu ? mwakula pumani coz simukuziwa chimene mukuimbacho mwina mukufuna kugawilidwa ndalama anatibelazi? bolaso joe gwaladi ndi inuyo kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk musova. muzi farao walelo osat mose walele. efe amalawi tili kwafarao akutiphulisa njerwa zamotu panopa anthu andale awa. bola kufa tikapume

 71. Tym Yimene Ndinali Mwana Ndimaganiza Kuti Munthu Akakhala ndi Mutu Waukulu Amakhalaso Ndi Nzeru Zambiri Ndimasilila Chimutu Chakocho Mbuz Yamunthu Meee Mee

 72. no matter what we can do there will always be people who will see things differently from the way w do.thats the way he sees it.the good thing is that should the issue go to court,they wont take mkasa’s song as evidence so it doesnt realy matter.

  1. You are right Joseph people criticize other people’s opinions forgetting that the way we see things differs indeed even those criticizing Chaponda today had it been him Chaponda is their friend or relative they could not criticize him. They could be on his side Malawians must know that 96 % of our population lives in poverty palibe angalowe ndale kumalawi kuno napatsidwa mpando wabwino osabapo sizingatheke. Anthu akuba ndalama za a mphawi monvetsa chisoni go to Auction floors, Immigration, Road traffic, MRA etc there is total rabish happening only that ambiri are not Exposed. If one has different opinions from us let him/ her be coz somebody’s opinions can’t determine the way we live. Its what we do what we believe that determine our life style

 73. Akufuna ndalama ameneyu,anaimba mose walero,kenaka anati zonsezi ndi amayi ndiye pano chani???kkkkk pitani kumunda

 74. Does this monkey realise kuti ndalama zomwe akuba adalezi ndi thukuta la anthu osauka ngati azibale ake through misonkho ????? Am really disappointed nkuona 2mb anakuuza poyera kuti ur not a true phungu

 75. this is the nkasa i know he goes where gold is and its an open secret that the single has been funded by the big man himself

  1. English it’s a language if speak English doesn’t mean you are educated,go around lake shore people they speak fluent English but they not educated,it is just a Malawian mindset that if you speak English then you educated,nowadays ndi ana aku nursery they speak English fluently to them us just a language like chichewa

  2. English it’s a language if speak English doesn’t mean you are educated,go around lake shore people they speak fluent English but they not educated,it is just a Malawian mindset that if you speak English then you educated,nowadays ndi ana aku nursery they speak English fluently to them us just a language like chichewa

  3. English it’s a language if speak English doesn’t mean you are educated,go around lake shore people they speak fluent English but they not educated,it is just a Malawian mindset that if you speak English then you educated,nowadays ndi ana aku nursery they speak English fluently to them us just a language like chichewa

 76. DAVID ANALIRA MALIRO AMWANA WAKE ABISALOM and mr Nkasa akuziwa kuti GC ndi mwana wa nkhosa amene wafela aMalawi nthawi yanjala panopa chimanga ponseponse and GC NDIWOSALAKWA COZ KUZIKO KUNALI NJALA

 77. DAVID ANALIRA MALIRO AMWANA WAKE ABISALOM and mr Nkasa akuziwa kuti GC ndi mwana wa nkhosa amene wafela aMalawi nthawi yanjala panopa chimanga ponseponse and GC NDIWOSALAKWA COZ KUZIKO KUNALI NJALA

 78. Chimenechi ndichifukwa anachitibura kwa T/A Lundu akanachiphulisa mutuwo chinachuluka dyera chimenechi kuteloko akufuna achigayile za chimangazo umat ndiwe phungu uphungu wake umenewu bustard ndakwiya nawe

  1. Hahaha wandiseketsa kkkkkk ofunikadi kumugwiragwira ameneu wachuluka dyera , asaaa chaponda akakhala Josefe ? Waganiza bwanji nkasa kumaombera mmanja mbava.

 79. I think nseme zija, kapena titi masweswe aja mmutu muja maganizidwe akuvuta masiku ano, ngati nzeru zatha zamaimbidwe mmutu bwanji osangotsanzika

 80. ati kudziika pa map. akanadziwa koma mmene a Malawi alili ndi nkwiyo ndi nkhani zimenezi sibwezi pano akutaya nthawi yake ndi ma sample ngat amenewa

 81. nawenso mkasa umasowa zinthu zapangila umboni. ndani sakudziwa kuti chaponda ndiwakuba .ngati ukuganiza kuti iweyo umupulumusa ukunama iweyo ndi chaponda wakoyo nonse ndinu mbava

 82. Opportunist mkasa!!!you have nothing to say and offer! Men who are beyond their prime swing like a pendulum so is mkasa!he go where he thing kuli mane from mose wa lero to amayi then today ndi izi typical of men who have no direction in Life, wake up mkasa not all opportunities are to be taken some are traps.

  1. Kkkkkk what he has done thus what we call direction. Which direction r u talking about? He has taken a stand, its only zat it differs with yours.

  2. Mkasa is giving his opinion on the Chaponda issue. The fact is Chaponda is innocent until proven otherwise by a competent court of law. Noone and I mean no one is coming in the open to say he stole how much but its an issue of going beyond the portifolio barricades when dealing with suppliers he wasnt supposed to meet as a Minister as he is not in the Procurement Realms of the ministry. The question is ‘what was his intention’ thats the probe.

  3. Dont hate people with discerning views and dont force people to follow your line of thinking. We look at things differently and dont shove your ideas down Nkasa’s throat. He knows where he gets his food.

  4. Fools always will never prosper with there wicked ways of getting needs instead of getting much they always lose too much

  5. Mpasu was jailed not bkoz He stole but koz of his involvement n influence on suppliers like Chaponda -wakeup friend collings !

  6. A Kanyinji, mwalankhuladi koma akulu akale adati nthuzi sifuka popanda moto. Bwanji m’tundu sanantchule inuyo a Kanyinji. Nkhani ndi ya maize saga. Office ya a nduna kuontchedwa. Pano tava nyumba ya Judge a Mkandawire kuotchedwa, ayi boma iloooo!!

 83. msamuone ndevu ngati ndimunthu mumtu mlibe nzeru tingomkhululukila mutu sugwila ntchito chifukwa cha mankhwala omwe amamwa

 84. Ukuona ngati akugulira Galimoto? Waiwala Kuti Bakili Muluzi anakupusisa, ali ndikupase Galimoto wagwira ntchito yanji? ine ndinati Nyimbo zako nzokoma kumvera mugalimoto

 85. Nkasa do u want chaponda to share with u something from maizegate mmmmm u have to be sorry with poor malawians dont defend someone with aim of getting something from him

 86. 0 out of 10000000….. Chindere chakufikapo, kuzolowera kudyera Andale Bambowa. Mutu unangokula koma nzeru mulibe wawa…..

 87. Komaso oimba wena akumalawi kupwambwana ndichifukwa chache wena mumatibulidwa ndithu. cholinga wakubayo akuseni?? koma umphawidi sizinthu ndithu.