A police officer has died after taking dangerous herbs in Nkhatabay district.
Reports that Malawi24 has gathered indicate that the deceased identified as Friday Kalonjere of Nkhatabay Police Station visited a herbalist together with his friend.
The two went to a herbalist known as Rabson Milanzi of Mongola village, Traditional Authority Nkanda in Mulanje district.
At the herbalist’s, they were given herbs but as soon as they took them the two began feeling unwell and when they left the herbalist’s premises the police officer began vomiting and collapsed instantly.
The two were rushed to the hospital where the police officer was pronounced dead before getting any treatment.
The other victim is still unconscious at the hospital.
wapolisi wake ndani guys but it’s sad RIP
Mmm guyz aliyense ndi mtembo basi koma zimasiyana ndi nthawi,nde kumalankhula bwino msakhale ngati ndinu ambeu…..palibe angathawe imfa nde msachenjere pa imfa ya mnzanu chifukwa nanunso idzakuchenjererani,,,,,cmnts?al da best continue…
May his soul rest in peace
Guyz musayakhule choch mwakula mwatha mawa ndnu mukanafusa kt makhwalawo anali achan osamangopang cmt zopusazo munazolowela kwanuko kukhwima zopusa nd mukuganizila izo azanut muzaziwona
Achita Bho Apolice Oipa Amenewa
Kukhwima?
Osamalemba zanzelu bwanji? Mukuona ngati inu ndi ambeu?
Munangomva kuti koma kumulanje ndie anthu amakakhwimako mapeto ake ndiizi akupatsani poision
RIP, uyenda ndi lupanga azaphedwa ndi lupanga
Ndiye Ali nawo ntchito maliro a zobayi ndendani
Apa sitinganeneretu. RIP MR. May God be with the decezd family pa nthawi yolemetsayi.
zomvetsa chisoni nanga tikayamba maDEMO akateteze ma shop ndani?
Njaratu imeneyi abale inuyo kuba ndalama za chimanga kuchikweza kuti mupange profit amatero,
Wachita bwino wachepesa chiwelengero shuputi zake
OK
RIP
apita bwanji kuchimbudz osadya? Aboma apasen chakudya anthu anu.
Akafike
baaaaaad rip
Byebye
Uzeleza Pera
Say halalala to everyone you gonna meet there to the new world
Next is u
Anayibanda hvy Ganja kkkkkk
Mmmmmmm zovuta kwambiri
Zavutatu apa
ndi nthawi basi,akakumane ndi ambuye yesu
akuti munthuyu analedzera ndiye atafika pena pake anadzera kwa asing’anga komwe anakamupeza zake Akutenga mankhwala oti azithandizire mumimba koz iyeyo akapita kutoilet pamakhala povuta kut azitandize nde anangoganiza naye zomuuza sing’anga uja kut nane ndiliso ndi vuto ngati limenero mimba mwanga mungozaza nde mundithandizeko nane mwina kutheka zitha kukandithandiza , nde sing’anga uja sanachitile mwina ai koma kupereka mankhwalawo onse limodz ndi zake , koma atamwa mankhwala aja kuzayenda kamtunda pang’o wapoliceyu anayamba kusaza , zake ataona kut zavuta anamutengera kuchipatala koma asanafike kuchipatala wapoliceyu moyo wake unathera panjira koma mene amafika adotolo anawauza kut munthuyu wamwalira kale , koma xakeyo nayeso wagonekedwa ku chipatala konko
ndi nthawi basi,akakumane ndi ambuye yesu
Nooo sizinakhale bwino but mzimu uwuse muntendere ngati anachita bwino kudziko lapasi ameeeen!!
ause nd mtendele
ause nd mtendele
9ce story enafe tipeze ntchito abale
It happens,RIP.
Yah
It happens,RIP.
wachita bhoooo nawoso amatimanga akakumane ndi apolisi mmandamo nyerere,mphutsi komaso kufa grave arrest
oh
what type of herbs kkkkkk
chimanga aponda abwna onani mpaka @ police ayamba kudya zosadya apa#Yesu akupezani pompano kkkk
Kkkkkkk dangerous what?
iiiiii zinazi nthawi
whish herb? Gondolosi kkkkkk