A 28 year-old man has died at Manase township in the commercial city of Blantyre after drinking beer without taking a meal, Malawi24 can report.
The deceased, Petro Mapanga, was drinking local beer on Wednesday but he later went missing.
Confirming to Malawi24, Blantyre Police assistant spokesperson Sergeant Andrew Mayawo said the man was later found under a tree lying on the ground.
“His brother came to report that the man was missing but later some people found him under a tree lying on the ground and he was taken to the hospital where he was pronounced died,” said Mayawo.
He added that Police suspect that the man has died due to too much alcohol consumption without eating as postmortem from Queen Elizabeth Central Hospital (QECH) is yet to establish the cause of death.
Mayawo has since advised residents in the city to resist from drinking beer before taking a meal.
Mapanga was from Kadzuwa village, Traditional Authority (TA) Bvumbwe in Blantyre.
Mwina anamwa mowa wa power kwambili, monga bibida. Anthuni tidzimwako Chibuku, mowa woti ukamwa basitu imeneyo ndi nsima
Musaweluze poti simukudziwa kuti chenicheni nchiti tiyen tidikire oweruza weni weni the most highly G0D adzaweluza mosakayika 4 he watches everything lets not judge…….!
Aliyense anamulengera imfa yakeyake
R.I.p
moto umapita kwasala tchile
shooter or win
So he died of hunger not beer ……
Considering the population boom.
Mostly the wise are overwhelmed with the too much of these stupids.
Its like in every 10 we have 8or9 of fools leaving the remainder the wise.
If one dies of beer, we will need some few unclassed and neutral people to tell us where does this dead body belong “the wise (1or2%) or the stupids (8or9%)?
Definitely this drunkard belongs to the fools.
And to me, the population has decreased in a natural method.
Humbly I will ask;
Fools
To
Bury
fellow
Fool…………………
Aefeso 6vs18
Mwaitha Ccta..!
Good news
Wafa akumva kukoma
Thank u Mr beer for killing the idiot who always makes noise in the street
I am so sorry for that because i drink beer to
Zovu zedi m’meenzi odala atii! mulupenya mmeepapa oti mpaka kutsamii nkono chifu cha mowaa!
beer kills man n govt bans frozzy….. govt likes doin thndlgs upside down
Wanyanya Kumwa Osadya amayesa size yagogo ake? wakula watha.
dying in the very act of sin. azakunenera mulandu wako ndani.?
Rip
Waphedea ndipoison osati mowa Eish koma Malawi 24 ndiyabodza 90%yankhani zake zimakhala zabodza bolaso Nyasatimes izi ndinkhani zina kkkkkkkk.
Mowa uli ndi malamulo ake so ngati mwaphonyetsa malamulo amenewo results yake ndi mistake yayikulu ngati mwaonazi.
What kind of animal is beer?like seriously this animal is killing too many people nowdays.why not consulting the rangers to deal with it before it finishes us
Wafa ndinjala,,bwanj ine sindikufa mowa ndimamwa dairy & panoxo ndayaka,zaunsiru eti
Plz government think about your citizens how can allow people to sell beers which is killing the future of Malawi such as kalaubongo & shooter…
Osamatero zili kwazanu
Wina ndi nzeru zina amvekere anthu akufa chifukwa chanjala
Chisakho chake
wafa imfa yosawawa kusiyana ndi kugendedwa miyala
ntchito za manja ake zamuikira umboni anyway RIP
Kkkkkkk alomwe kumwa mowa musanadye kanthu mapeto ake ndamenewo ife angoni tidzaziyamba kalekale koma munthu sadafepo ndi mowa kuphunzira kumwa kumeneko tamangodyani njokazo inu alomwe mowa mutitsiire
Pasadi Katole# usamale pakamwa pobookapo alomwe akulakwila cha
Kkkkkkkkkkkkkkk
Sanafe ndi mowa koma wafa ndi njala ameneo
Malaw24and AllMalawian don’t worry about him when u walk with knife that knife will kill u .thanks God to take him that way thanks again RIP
Wachitha bwino mmen ikusowera ntchito dziko muno chifukwa chochuluka anthu ndiye tizichepako njira yakke imeneyo ndipabwino zikomo mulungu RIP to him
Zovuta
Wafa wafa bas
Ndindan tiuzen dzina lake am away?
It should be ( Man dies after drinking beer without eating ) not Beer kills man in Blantyre why write as if beer is a human beiing ?
Hahaha muziwavetsetsa,, xul mmm yapang’ono
MANASE ndi dera lomwe anthu amamwa mowa mwa uchidakwa kuerekeza ndi madera ena onse ku BLANTYRE, watch out
KANTUMBIZI
KUMASOFA
KWA NAMBE
Be specific…. beer yanj?,,,,,,long live chibuku..
Wapona Wamnyane Iwe Walekana Navyo Vyamchalo! Eish Umoyo Uwu N’ngwakusuzga!!
Mowa Supha Munthu Bodza
mowa sumapha mu2 amwene..wafa ndi njala
kodi mowa wake ndi umenewu kapena ndiwomwe umamwa iwe#admin?
Mwakumana ama bodza ena mukuti wamwalila ndinsima ena mukuti ndimowa chosecho nose mukuti ndiakwa MANASE koko nanga ife timve ziti
Wafa ndi njala osati mowa ayi.RIP bro
Wafera zakezomwe
Mowa poison, kumuthililaso poison zosayenda ngakhale pang’ono. mowa ndiyedi munzu wa machimo ndithu koma zidakwa kakaka mma bar.
tidikire postmortem.
baaaaaaaaaaaaad
Izo ndi ntchito za manja ake
Komabe mowa siwabwino no matter how he dead,
baaaaaaaàaaaaaaaaaaaaad
Sanafe ndi mowa ameneyo..wafa ndi njala
Mwayambadi bodza. He died after taking nsima which is believed to have been poisoned. Mubwere kwa manase mudzafufuze. Mukulemba zonama
achta kumuikila poison mufufuze bhobho ife ñdakwamanase konkuno
achta kumuikila poison mufufuze bhobho ife ñdakwamanase konkuno
Ndi ndani amwene?ndipo manase wake wuti?
manase wake wakunsika
koma anthu amakagumula bar yaachabadwa akut zikuwakhuza paimfa yamunthu yo
omwalirayo nd petulo mphwake wa nyelamboni
Zofuna
Pamowa masiku ano alowetsapono zidani kumangophana
Haha iwe sanafe ndi mowa i stay kwa manase konko achita kumupha anamuthirira poison mu mowamo do your research well