Malawi Defence Force (MDF) soldiers have been advised to set an example to all Malawians in respecting the country’s laws.
Speaking during the 2016 Year End Ball at Kamuzu Barracks, MDF Commander General Griffin Supuni Phiri said there is need for all soldiers to behave well in all areas.
Supuni Phiri said soldiers should not be the ones breaking the law but they must always abide by the law so that people should follow their good examples.
“We as soldiers we need to lead by example, we must not be the first ones to break the law but we should be obedient to the laws of the country,” said Supuni Phiri.
He added that soldiers must not feel superior but should always observe discipline and order in the country.
“As we claim that we are disciplined and professionals we must always be open even when a police officer asks us to show our driving licences, we must always show it as we have nothing to hide,” he said.
The army commander also urged soldiers to always be fit, to work hard, and to protect the country from its enemies.
Ndi Mbuli
Umphawi ndi asirikali omwe. Uniform zina zidasuluka kalekale. Shame to the Malawi government.
iwe uniform yako tikusitana ndinzanzako ango kutola patchila
Amalawi amzanga ulemu mkupatsana ifenso tiyeni tiwalemekeze asilikali athu.
Don’t tell soldier’s that, but the Malawi police and dppp which do not respect and follow that.
Agalu athu awa, kuphunzra ntchto yabwno ng@ imenei mkumakadikira nkhalango,,? Jezeyo ng@ yobwereka, nkhope zdaphwanyika kalekale,,kuchnda mahule 2much, azkaz abwno alinawo mmanyumbamu,,angochnddwaso nd akabaza, akamenya mkaz kungokagwadwa kwabwana ulangdwa, ntchto yanj yolembetsa mkaz,,?
Indeed akuti akavala uniform yao ija ya u soldier it’s like the owned the whole Malawi but they forget that tonse ndife a Malawi
Alibe mwambo amayendela mphamvu ngaliba manganya avinile unamwali wa jando asiye mwano kwa malawi anzao
Bwana Supuni Mukuwoneka Kuti Tanzania Muthana Nayo Ndizantopola Olanda Mbali Ina Ya nyanja Yathu.
Katetezeni nyanja
Awuzenidi amenewo apo ayi azingowonesedwa mafight ndi mafana aku mulanje
this December here in south africa almost every one was wearing Camouflage , but sindinamvepo kuti msilikali wamenya munthu kamba ka zovala za Camouflage. inavuta ndi sukulu pakati pa asilikali aku Malawi
Akakhala kumalawiko amamenyeranji anthu opanda mfuti?Kusunga mwambo kudziyambira pakhomo
Not when some1 tempers with our forest
Is the responsibility of every citizens to respect each other as Malawians, sometimes we pple!,we are so arrogant when we drunked, trying to test our energye to the wrong pple like Soldiers, do you think that you wanna stand? So we must look on both sides.
That’s not true. Its only in Malawi soldiers think they are above the law. I have served as a soldier. U can lie to others.
zoona Michael
usilikali pomenya amakala !!!malawi at 51.
Matupi akachilombo look at them
Alingizeni awonjeza kuzudza anthu osalakwa
Zima uniform zosiyana siyana bwanji chonchi??? Zaumve basi aasaaaa!!
Zimasoja zosauka zapa Malawi,zpewa znatuwa kalekale ndi dzuwa kkkk-93 brigade
Kkkkkkkk zosauka koma kutimenya basi
Man davie ndi man joe mwandisekesa zoti sizinawoneke !!
Kkkkkkk
Bwanji Tose Titasiya Ntchito Zathu Nkukayamba Ntchito Ku Mdf Kuti Tipeze Ufulu Mukuona Bwanji Anzanga?
Bwanji Tose Titasiya Ntchito Zathu Nkukayamba Ntchito Ku Mdf Kuti Tipeze Ufulu Mukuona Bwanji Anzanga?
MDF akapita ku Peace keeping mayiko omwe kuli nkhondo amayamikira kt ndiosunga mwambo but akakhala ku masewero ampira amamenya zodesa nkhawa zija, pamenepa mpamene ndimadziwa kt ku Peace keep kuja amachita mantha osati ndiosunga mwambo even kukupeza utavala chipewa chapakaunjika km ofanana uniform yawo amakumenya moipa
kkk ku peace keeping amachita mantha ndi nkhondo,,koma alibe mwambo
Kkkkkkk ngati unama csta
Hahaa mukunamatu inu koma aunt Kate mwasowa zed
These niggaz are useless
People been wearing camouflage across the globe but not once someone was beaten down by soldiers but here in MW…smh
Koma zoti inu asirikali muzimenya anthu chifukwa cha zovala za kamofulajoi sizowona.Ine ndilinazo zambiri kuno ku SA wina aliyense amavala ndipo zilipaliponse kugulisidwa masitolo komanso misika.Ine ndiye ndikuzavala basi muzandiphe tikuvala ngati chovala basi.Nanunso aboma mukanayenera kuwawuza azilonda anuwo aziziwa zimenezi.Amazitengera muchigulugulu koma utati wapezana naye modzi kwa modzi sangakuvulise amaopa.Inu asirikali timakupasani ulemu koma mukawonjeza ndithu mutha modzi modzi kulowa usirikali sikuti mumatha kumenya kapena basi kuwatenga ma Civilian ngati makape musiye zimenezo
Chipongwe chake chimenecho ndiye ungasiyidwe osamenyedwa.iwe ndiye ofunika kukukhazika pamanyi ka.bwanji ku jon mukukasambisa mitembo n suchosa manyi nkhalamba koma simukudandaula kuti akukuphwanyirani ufulu
Kkkkkkkk josaya wona wekhakumaprofile kwangako ine mwai okha okha ndikupanga pannel n paint specialists ndikukoka mafana anga azibwera nawo azaphunzire ntchito kuno.Kuno ndakhazikika ine kwacha ndi Rand kutalitali zedi.Ndipo ndakayika ngati ndingazagwirenso ntchito Mdziko mwanumo kubwera nkumabwereratu basi
Tilibe ufulu ndi asirikali amenewa kuno kudzalanyama,,,, akuzuza wina aliyese amene wakwera njinga yakapalasa
http://Cashni.com/?refcode=75553
Alibe ulemu amenewo amamenya anthu chifukwa chovala kamofoleji wa fonkong’o emweyu
I think its time for all citizens to exercise their rights without any soldiers ,police, politician to abuse poor Malawians . young women are abused if they refuse an affair with these pple. Young boys are been abused if they are dating a girl these pple wish to date with. In taverns pple don’t get peace if these pple get paid. And this will lead to violent revenge that will bring disorder. This is only show how arrongent these pple are. They are suppose to take order s from the government not them to make order
ife tilembedwa liti ntchito yo imba ma choir ndi kumenya mpira , komanso ndikumenya ma civilian
Unafusa bwino koma waipisa kumapetoko
Komano when ia an intake
Kkkk bambo mumaifunaso kod? Koma ndipompano bro koma osamawanyoza anzathuwa siwonse ali ndi khalidwe loipa
i love and respect M.D.F …..amatha…
Bwana alangizeni anyamata anuwo aphunziledi kukhala ndi discipline. Asamangozipopa ngati iwowo ndi a Army a mulungu ayi ndizosala izi, aphunzile kukhala wodekha