A Malawi alibenso chikhulupiliro mwa a Mutharika, ati bola a Chakwera
Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika akuyenela kukhala ndi mantha. Malinga ndi kafukufuku wa Bungwe la Centre for Media Development (CMD) ati anthu ambiri mu dziko muno ataya chikhulupiliro chawo mwa a Mutharika. Kafukufuku… ...