Malawian killed by South African wife

439

A Malawian man has been stabbed to death by his South African wife after he went home drunk on Saturday in Cape Town, Malawi24 has learnt.

The deceased has been identified as John Kawonga who married a South African woman and lived with her in Dunnoon area in Cape Town.

knife-bloodChristopher Nkhoma, a Malawian who is Kawonga’s neighbour told Malawi24 that during the night of Saturday Kawonga went home drunk and that did not go well with the wife such that a quarrel broke out between the two.

During the fight, the South African woman took a knife and stabbed Kawonga before running away with the couple’s child.

“Late Kawonga was my neighbour and I witnessed his death. I failed to go and rescue him since here in South Africa doing that is like putting your own life at risk,” Nkhoma said.

According to Nkhoma, the body of Kawonga is currently in mortuary at a hospital in Cape Town for postmortem.

He further said that the remains of Kawonga are expected to be brought in Malawi after all arrangements are completed.

Late Kawonga hailed from Nkhatabay district in Malawi.

 

Share.

439 Comments

 1. Akazi ajoni ndi choncho.amakudikira uwapangire chuma kenako amakupha iye azitsala kumanjoya.atengeni akazi achimalawi womwewo.akachuluka. nzeru kudzangomutula kwawo.

 2. RIp brother kwakee kwatha ndithuu tanvomelaa komasoo mwina infai yabwela ndi cholinga mwina ndi mwai kuti azimbamboo ena amene muli kuno Ku SA muphudzilepo kanthuu. Munyanya azibamboo kutengekaa sindikuziwaa kutii chimakhala chanii plz a mw NDE iiii nchochoo bee okumnva APA wanvaa osanvayoo akhale . nzimu wake uusee muntendelee .tinamukondaa koma mulungu wamukondesesaa akapumee kuzolemesazii zikomo

 3. He is dead, finish n klaar. Wat he was doing wth his lyf is none of ur concern. Learn 2 mind ur own biznes. U r buzy talking nonsense over his death, hw r u goin 2 die? Stop taking painkillers over somebody’ malalia.

 4. Inde guys tiyeni tipewe kumangotenga azikazi akunu mapeto aka timazibwelezesa mavuto ena anasiya mukazi kumuzi ,Ana and makolo akufuna chithandizo kwa ife koma tikamabwela kuno zonse taiwala ayi si bwino sikuti ndi amuna wokha ayi Including women’s also ladies

 5. Regardless of all the comments you people are making here, one important thing you need to know is that as a family this side we have lost one of our members through such a brutal death and that we feel pained…… God knows everything!!!!

 6. These are the last days we have to trust in Jesus our only gud father everything will be moving forward and we shall have great victory in all and in any works

 7. wats so special with this story? ???? news 24 pliz, if you can’t fynd something to write,then muzingolemba za njala ili kumuziyo basi,or else tell pple the proper reason why the prices of commodity are increasing daily,kkkkkkkkkk ,surely this would sound better on your pages

 8. Sorry just want to clear you guyz, not a wife but girlfriend. Only that a guy didn’t like a lady then he decided to drop her. We can say that’s why a lady got cross grap a knife en killed a guy. I know a guy but not a lady.

 9. Zalakwika poti nzathu wamwalila koma kunena zowona amalawi timanyanya,kuno ku south africa kuliwobwela kuchoka mayiko ambili wonsewo amanyenga akazi,koma ife amalawi tapyola myeso plse tiyeni tiyese kusintha khalidwe.

 10. Ndatha kuona timacoment tanuti apa ndadziwa kut ambili nzeru mulibe…..kufa sizachilendo koma nzowawa kwaotsala coz ambili amamudalila m’baleyu…..kukhala ndi nkaz sizokanizidwa komano nzochitika kulikonse mamuna kuphedwa ndi nkaz wake…..kumalaw munganene kut amuna samafa ndi azimai ao……best way is to say RIP ndicholinga kut osalawo athontholeko……dont play with death gyz nzowawa

 11. Mulungu analemba imfa kwamunthu aliyese iye nthawi yake yinakwana I can’t blame you bro zayimfayako mulungu analemba kale Rip

 12. Kuno tithelako mbambadi tikapanda kusamala .
  Kunoso ku cosmol city a malawi awili aphedwa vhifukwa cha akazi .
  Anthuwa ndi a kulumphi

 13. Mnzanuyo waziona ma guy aku Malawi mwatsala inuyo kutengeka kuyiwala umphawi wanu mmalo moti mugwire timaganyuto mupungule mavuto a nu ndi umphawi wa azimanu mukulimbana ndi Ku kwatira zigawenga muphedwadi simunati ndamva chisoni makolo ake amadalira iyeyo kaya enanu akuonetsani yotani imfa yake asanakuzingeni kumuuza Kaye kuti udikire Kaye nditumize ya sugar sikuti ife tizagule sugar womwela tea pa maliro anuwo mufa yozingidwa May his soul R I p

 14. Please Malawian guys be careful with women for South Africa ngakhale akazi aku Malawi nawoso they are very dangers take care yourself guys

 15. The problem is that a lot ov us Malawians who are here in RSA kaya ndi chimidzi kaya ndi chani timafuna kuti tizioneka ngati ma VIP ..kunoko nkwaeni tiyeni tisamale makhalidwe anthu kunoko..ambili a Malawi omwe amaphedwa kunoko nkhani zake zomwe amaphedwela zimakhala zimozi akazi or mowa..I hav been here for two years now sidamvepo mmalawi oti amakhala simple life kumapanga zomwe anabwelera kuno ataphedwa….most of us tikachoka ku mudzi town yoyamba kuiona kumakhala kunoko nde timaona ngati tikuluza that’s y we get involved in such stories…moyo ndi wekha know where u r cmng from …..pano si izi wamwalira mowa uli mu mutu that’s bad nde makolo aziti chani pamenepo kungopwetekesa mitima ya anthu ku mudzi..

 16. Shame i heared the news yesterday hey its so sad they said he was staying at Danoon cape town koma zakumwazi eeeeehhhhh anyway kwa watsala life Gomez on

 17. Vuto anthufe timayiwala Komwe tikuchokela tikabwela kunoko n anthu akusouthafrica kuno mumawaziwa ndithu Kuti Kupha ndikwawo ndipamene mukawashosha dala kuyiwala mavuto akwanu

 18. The lady has just done a good job most of these men are leaving their wives and kids to suffer they hv to pay for their sins

 19. Zoziyamba dala kumalawi kuli akazi okongola komaso a ulemu ndinso not after money but kumkonda okondedwa basi a lesson to fellow malawians may his soul RIP

 20. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk ngati amakanyenga kwina malipilo ake ndamenewo samalora zulu zimenezo wadya balalika

 21. Wazipha yekha kuno tinabwerera mavuto osat kunyenga akaz akuno alibe love iwo amafuna ndalamazo bac nde mmmmmmm kaya R.I.P

 22. Aliyense amalandila malipiliro kutengela ndimmene wagwilira ntchito Amuna akumalawi ndiochitisa manyazi amuna osamanga malisani akaona akadzi Mulungu anakudalitsan ndi mkadzi waulemu koma mumamusiya akulira mkumakanyenga mahure God have mercy

 23. When it comes to luv,Palibe chabwino kwa munthu wa joni,usiye mkadzi ku malawi,ena azikunyengera/amukwatila,umutenge amachuluka dzeru mpaka kusiyana,ukwatile wa joni ndi aids,chilema kapena imfa,rest in peace bro ur not to blame

 24. amalawi akabwele kutheba kuno amafa mitu akungoendela mwambi oti kumene kwaphya tong`onala suziwa ntima wa moto ngat ulinako kanthu dyelatu chile pofela samalambula….. nkhani yaikulu kupewa chiwelewele RIP

 25. R.I.P….Tonse tinabwela kuno kudzachepesa umphawi,ku malawi ambiri mwa ife tinavutikila kukapangitsa passport,kugubilanso pokayitenga,4 days traveling to here..pano tayamba kugwira ka Rand kochepachepa,tayamba kuyiwala dzomwe tinabwelela and m’mene tinavutikila kutenga mapassport.

 26. He died while drunk? oh my, may God save us all from that kind of death dying in that state.lesson learnt to all living persons

 27. kusiya akaz ku malawi abwino bwino kumalimbana ndi mahulewa ? Remember the late hon Ishumael Chafukira anadyetsedwa poision ndi Zulu woman ku hotel , these are prostitutes please,.

 28. Pepani kwambiri makolo (anamfedwa) amunyamata wamwalirayu! anyamata nonse mau akulu-akale adati,”phukusi la moyo sakusungila wina koma wekha,” madzi akataika saoleka!!!! MWAMVA!!!!

 29. Amalawi kuno sakumva akhala ngati atopepetulidwa, zimene akuchita kuno kulanda akazi ayini ake kunyenga akazi ayini ake kumwa mowa mwauchidakwa ndizimene akuluza miyoyo yawo kuno

 30. ….. taste his own medicine, he left a wife and 2 children behind so that he can find a greener pasture, afika ku capetown uyo mnyasaland wakumana ndi matako achixhosa mu Du nooon area, kuiwala mkazi ndi ana…. now let it be a lesson to all of us……..

 31. That’s family matters. None of our business , I advise my fellow malawians over marrying in foreign country. It’s good but let’s b very careful. Anyway R.I.P ☺

  • Eish ndakhumudwa nawe
   Ine im a south african married to a malawian.mmmm ngati imfa yake inali yampeni by a woman even a malawian could have stabbed him.

  • Mpume Banda u haven’t understood my concept, marriage is good but it depend on whom u r marrying to . Ihv said it’s good but we should b very careful. Ihv many friends of mine who r married to foreign woman n have happy family.

 32. Zimakhala zomvesa chisoni kwambir maka mwina Makolo ,azibale ako onse amadalira iwe…nde kumachitikaso zinthu ngat izi essh..Tiyeni enafe titengelepo phunziro…AWUSE MUMTENDERE pot stidziwa zomwe analakwaa!!!

 33. Zimakhala zomvesa chisoni kwambir maka mwina Makolo ,azibale ako onse amadalira iwe…nde kumachitikaso zinthu ngat izi essh..Tiyeni enafe titengelepo phunziro…AWUSE MUMTENDERE pot stidziwa zomwe analakwaa!!!

 34. Guyz tinene mosapsyatila anyamata akumalawi mukuwonjeza muri no one kunyenga nkazi wabwino simuopa nzanu ayitanise wake mumamunyegerela mpaka mugone naye muzimuyalusa azikuteloni mwina mukumbuka amayi ndi Ana munawasiya aja ndinyozeni chilungamo kupweteka

 35. that is why i dont date any south african lady,i know most of them have got rotten mind,normally i go for zimbabwean ladies.they are very understanding ladies,of course they some few rotten apples.

 36. I’ve seen a Malawian woman killing a Malawian hubby in houtbay capetown stop judging all south africans for one person’s mistake God of all nations will judge us all

 37. Very unfortunate and these things do happen all the time even though being drunk cant be the cause of his death in his marriage. The story is not much detailed and Capetonian women coloreds and Northern Cape women stab with knivesor screw driver, Zulu women just shoot with a gun, Sotho and Tswana women just leave all the belongings from the house, the Xhosa women just bring another man in front of her husband and you fight and whoever wins takes the woman, the Limpopo and Mpumalanga women just bewitch a man. South Africa what a country. Indeed going to South Africa by road and coming back home as cargo. This is very upsetting indeed.

 38. Myself Am Not In South Africa But To Say The Fact My Friends Over There Especlally U Guys Please Avoid South African Women Remember What Brought U There, Lastly May His Soul Rest In Peace He Is Our Fellow Malawian.

 39. Chilungamo chake kungopewa kupanga zibwezi ukamufuna m’kazi pompopompo basi nanga mwam’va zimene zam’chitikila M’malawi mzatuyo

 40. Honestly speaking …I hav just stayed here in (SA) for a year now but mmmmm kumvetsa chisoni on how some of us foreigners behave…..Am not saying this because of the deceased guy koma there’re so many incidences occurring each everyday involving foreigners. ……Of corz zigawenga/ Robbers if they want to attack pena saona nkhope kut uyu ndi nzika / obwera they just grab what they want from you….Let’s watch over our deeds and at least some incidences can be avoidable and God protects in such a conduct….This issue has got nothing to do with the MW Govt……Living in a foreign land, guys it’s at our own risk…and it is by the grace of the Lord….As to the deceased. ..may His Soul R.I.P…we can’t say much of whatever caused the incident and we don’t hav evidence for that matter.

 41. R I P angakhale ena mukuganiza kuti he made poor decision koma mtima wanza ndi sidya lina komanso sizitengela kuti mkaziyo ndi wadziko lanji love them all trust no 1

 42. Amalawi Ambili Amakha Ndi Chiganizo Chosamala M Mabanja Akakhala Kuti Ganyu Kpn Ntchito Sadapeze Angopeza Asitha Zochi Ndi Mikwiyo Yamabanja Awo Amene Alikuno Kumalawi.

 43. Amalawi Ambili Amakha Ndi Chiganizo Chosamala M Mabanja Akakhala Kuti Ganyu Kpn Ntchito Sadapeze Angopeza Asitha Zochi Ndi Mikwiyo Yamabanja Awo Amene Alikuno Kumalawi.

  • Yeah bro amati akapeza nkazi amafuna akhale nkazi wawo while kuno eni wake amati gal friend , nde u can’t control a gala friend pa Joz amakhala ndi ufulu wose opanga zimene akufuna once u try nizomwe aona a bro izo lucky wa ampha muzimayi Mtembo wapezeka koma akapanga hire amuna munakanamva akusowa dat means ataya uyo Ku Dumping area.

  • ndukuuza bro! anthu suzaona apolisi akukhala nazo bizzy ayi!!! its just their life…nde mmm zinaI kwathu konkuno but Jozi dnt try

 44. Zomvesa chisoni.inde enanu mukulankhula choncho.koma kwamunthu ngati ine.ndinawona chilichonse.ndizondimvesa chisoni.ndipo wafa imfa yowawa.mulungu oziwa kuweluza azaweluza.l.i.p

 45. Vuto amunanu maziyamba dala pena mmasiyilanji kuwaitanitsa azikazanu akumuzi? mamusiiya nkazi kumuzi oti mwavutika naye kuti mupeze passport mukabwela kuno zonse mmaiwala, pewani muziukonda moyowo,

 46. Eeish ife powopa ngati izi! timangodya ma take away e.g ama R50,R70 ndikumapita paden panthu koma izi zobukilatu kuti Wachibwezi eeeee!! timaluphalupha timawopa ngati izi!!.

 47. Maliro muike konko ku joniko, mngayambe kutithera zakudya kuno ku malawi…zinthu zadula udyo kunooo…!! Palibe kanthu ataikidwa konko yesu azamupeza konkooo….! Sankatumizanso ya mchere weni-weniwu nde lero asativutepo ifeee….tili buzy ndima ganyu olima misewu kunooo……muphedwe ambrii ndithuuuu…usiru wanuwoooo

 48. Moyo ndi choncho! Komaso ngati ine mamuna moyenda muli mavuto. Akazi aku Malawi akayamba kulalata kuti adabwera wokha kuno aaaaaaa sungafuneso. Tiyeni tizingo dya ugulawa basi.

 49. Zofuna,,,ambiri anasiya mabanja awo kumudzi nkumakatamika ndi aximayi akulu RSA,,,,m’malo mokasaka ganyu apezako mabanja, amuchita bwino kuti zisiru zina zitengerepo phunziro

 50. First of all RIp to the deceased, tinabwela kuno kuti tidzachepetse umphawi wathu koma lero tasintha program yomwe tinabwelera’yo tayanja mowa ndi akazi popezeza kumudzi kuja simumatha kuwanyenga ndiwovuta koma kuno ndiwosavuta chifukwa akufuna ndalama zakozo tiyene tisinthe khalidwe loipali tili ndi udindo ku makomo anthu komwe tachokera

 51. Biased news, why include nationality in this? Just report, a man killed by his wife or wife kill husband.

 52. Akamati Atengeni Akazanu Ku Muzi Amaopa chani?Sizi Nanga Mai Ku Malawi Ali Manja Nkhosi Mmalo Moti Mukanangowatenga !Koma Ayi Muli Azandilanda!Sizi Nanga?Kuno Sikokwatila Ayi Kokwatila Ndi Kumalawi Basi!R I P.

 53. nanga mumati athu atani ngati uphawi wachuluka kmanso kusowa kwatchito?kma ku south africa simalo abwino ayi muthu umachita kukakamizidwa kukwatira mkazi wakomko ukapanda kutero ndekt iweyo ndiwakumakabuli basi kapena kt imfa ndiye amalawi bwerani osazuza moyo ayi uphawi sumapha ayi mzimu wake uuze mu mtendere

 54. Mufadi mukapusa a Malawi ndithu zofunika kunyenga kutayana naye osamanga banja ndi anthu amenewa ndimakape.Inde amaonesa chikondi koma mchaboza kumachenjera.Akazi ambiri akuno ku SA kukonda mowa kwambiri komanso malamulo ambiri alimanja mwawo.Kumenya mkazi wapalamula.Koma amakondanso amuna obwera kwambiri akuno sawagwira ngati ife.Azimuna akuno ambiri zakudya zawo zoyika mankhwalazi zinawatseka shaft mchake ambiri akazi alindi azimuna obwera koma samalani

 55. ineso ndili konkuno kunenazowona amalawiena timayiwala vutolomwe tinasiya kumudzi akazi akunotu ndiakupha akangomva kuti umayakhula ndinkaziwina amapha akaziathu ndiachimalawibasi omvesabwino

 56. Sizachilendo kwa ife izi.two wks ago taikanso wina waku nsanje ku jobec komkuno ophedwanso ndi mpeni.za kuno mzotelo azisunga azapits kumudzi ndi moyo ena onjoya ndi mabebi akumatha chomchi.sizikutengera kuti uyu ndi ndani .Nice time imapha.

 57. Wakumana nazo kuzolowera akazi aku Malawi mukakhuta mowa amakutsegulirani chitseko plus kummenyanso ngati walakwa koma kumangopilira ndiye wakumana nayetu dolo mzake

 58. Marrying a Zulu woman its like digging ur 6feets inadvance. Ndi agalu anthuwa no matter how u be good to them they take as a liability to them. Akaz abwino i swear before God alikomko ku Malawi

 59. MMM I was staying next to them sanali nkazi wake chinali chebwenzi and they were both drunk. May his soul rest in peace,mayi ake amadalira iyeyo

 60. Thats it..mumasiya azikazi anu kuno ndi ana pochoka zabwinobwino mukangotha mwezi muli..”zako izo” lero zatembenuka nd “zanu izo” deal with it,nde winawe uli nkhongo gwa ku immigration” uli ndikangovaya jozi sindidzabweraso ndi kakwatira konko”……mukudzinamiza!!

 61. kumene kwatsala tchire ndiko moto umapita, evn ku Malawi anthu akuphana, palibe wamuyaya, nde osamantha mawu chili pa anzanu ayi!! ihope akanakhara mbale wanu simanakayakhura zimenezi!!

  • What are you doing to the goverment of Malawi while there in South Africa? Did the government sent you there? Are you paying taxes to the government of Malawi? Some of you can’t even build a house or helping ur families in Malawi. You forgot ur relatives, just enjoying in a foreign land but when time like this, you point fingers on government…WHY?

  • zikukukhuzana bwanji ndi boma la malawi anakwatilayo linamutumizako ndi boma la malawi? samalani pakutumiza makomenti opanda phindu

  • Honestly speaking …I hav just stayed here in (SA) for a year now but mmmmm kumvetsa chisoni on how some of us foreigners behave…..Am not saying this because of the deceased guy koma there’re so many incidences occurring each everyday involving foreigners. ……Of corz zigawenga/Robbers if they want to attack pena saona nkhope kut uyu ndi nzika /obwera they just grab what they want from you….Let’s watch over our deeds and at least some incidences can be avoidable and God protects in such a conduct….This issue has got nothing to do with the MW Govt……Living in a foreign land, guys it’s at our own risk…and it is by the grace of the Lord….As to the deceased. ..may His Soul R.I.P…we can’t say much of whatever caused the incident and we don’t hav evidence for that matter.

  • What you are saying is absurd am not even where you think am i mind your business and i didn’t invite you to comment so silly just be busy being extravagant and i don have dreams of going to a .

  • What you are saying is absurd am not even where you think am i mind your business and i didn’t invite you to comment so silly just be busy being extravagant and i don have dreams of going to a. africa am already having what can make me happy.I don smile fool government deeds who are they to me silly more over tis thee relatives to you gone far country doing silly jobs not me men hot head ateeeeeeeeeeeeee! No time to see your replies do what you can gain somethin if you are government people find me here in mpoto/Northern region no fearer

  • Viwachewa inu mngandiuze chani tamangogwilani utenati kumeneko aka school mmawuziwa mtundu wa blackboard nde ndinu Kachani zopusa basi ndichifukwa mmakhala ndi viwanthu vopanda mano vokanika kulakhula nkomwe

 62. nde katundu abwera bwanji kuno kumudzi..?? tidziwe program yake kuti tigawana chani…anayesa ali ku mpanje koti akazi amangopereka ulemu nzopanda ntchito zomweee…mzipedwa chonchoooo

 63. Ndeno Ife Chikutikhudza Ndi Chani Pamenepa?
  Cape Town Sili Ku Malawi, Mukufuna Tiyike Masamba Kuno Chosecho Maliro Ndi Aku South Africa?

  • Lessons Learnt:
   1 . Never date a girl who isn’t your tribe, she may end up breaking your heart as well as your life.

   2 . When we are in foreign countries we should not forget our malawian riddles (ukayendera zengo usati asakwi afumbura)

%d bloggers like this: