Police in Machinga have arrested a 31 year-old man for killing an elephant at Liwonde National Park in the district.
Machinga police spokesperson Davie Sulumba identified the suspect as Elifa Makhwele from Liwonde village.
“It is true that we are keeping in custody Elifa Makhwele aged 31 for killing a male elephant at Liwonde National Park” he said.
According to Sulumba, Makhwele together with his two friends who are at large went to the protected area and killed the elephant.
Park workers did not manage to catch the poachers but they recognised the suspect and reported the matter to police.
The law enforcers then raided Makhwele’s home at 3am on Friday and they arrested him. The police however are still hunting for Makhwele’s friends.
Elifa Makhwele who comes from Imani village in the area of Traditional Authority Liwonde in Machinga will appear in court to answer charges of poaching and illegally entering a protected area.
Aaaaaaaaaaaaaaa Malawi wa lelo
Anthu oyipa osafunila zabwino dziko lathu .
Munthu ndi nyama chofunika kwambiri ndi chani? Kodi mukuziwa kuti mulungu anaika ulamuliro mwa munthu kulamulira nyama osati nyama kulamulira munthu?
apolicewa nawonso ndi agalu achabechabe .tell me how meny peaple the dea about elephart and how meny elephat do you rest ?? zapha ndi kuwononga zinthu zaanthu kumachinga so what u do kupusa basi shoopeat give him a barow
A Police amangodziwa kumanga koma sangaphe njovu iwowo! traning yawo ndi yam’chichewa.
ngati ukunama aise traning yawodi ndiyaukape sangayelekeze kuipha timphamvu tawo tokokerati
why arresting him mumafuna akanaphedwa iyeyo
Apolice amzanu,Khotekhote mazengera, Namisisi adaba matumba achamba 50 kusalima uko osawamanga bwanj? Pano angochinda mahule alipheee… Uja wabetsa mfuti kamba koledzera uja omsamanga bwanj? Mumaoneka anzeru zkakhala nkhan zaanthu ena, zambanja mwanu nde kukhalira, Njovuyo ikadamupha Elifayo mukadatan? Mdatopa nanu agalu inuuu…
Y not shoot him ? Useless man
If the elephant killed him, what could have happened?
We would have clapped and cheered
Very sad#$ Malawi my nation##
Njovu nzambili inu. Kukakamula ngat wapha munthu
eti!!
try to achieve something great by killing bwampini…
Mukanabetsa gologodera
Muma Suleni Munthu Mwasowa , Zoci ta eti
apolice ndinu zisiru ndiposo agalu anthu mukumanga munthu opha njovu koma okupha munthu ndiawa ari free
opha njovu wagwidwa nanga opha abusa uja osagwidwa.kuteteza nyama patsogolo munthu pambuyo zamanyanzi agaluwa
Boma la #Malawi_silizatheka_bcoz latanganidwa kumanga anthu pa milandu yopanda pake ndicholinga chongofuna kupexelapo ndalama.
Osango muombela n.manja kuti ndi dolo waphayo bwanji koma njovu ikapha munthu nde ziiii sizimamangidwa bwanji ndindiwo imeneyo ndemuka mumanga idzuka njovu yo ndinthawi yoka longo sola iwola nthawi muku musungayi amati gulitsa motchipa akapha nyama ameneyo zimasiyana ndiyoti takagula ku msika
INU NDE BASI APHILIP ZANU NDI MBWERERA BASI
Arrested for killing an elephant?koma opha albinos alibe mulandu?nanga njovu ikapha munthu mumaitani ?
Shoot him not arrest
Stupid!!
Stupid indeed
Dirlu imeneyo ,tikupangani bello man
Opha nzake nayeso death penalty
Komatu ulemu wake mdala ameneyu kupha njomvu.?..anaipha ndi chani? is greatest man leave him f**k police
Really? So the elephant is in mortuary right now?
Koma akadapha albino ndiye mukadamusiya,kunena kwake mumati ziribe umboni koma lero mpaka pano mwana sakuwoneka anthuwo ali free.Wapha njodvu lero lino akugwira ukayidi mmmmmm shame malawi wamoto machinga eeeee
ukapita kuchipatala ukalandira mankhwala angokupatsa panado ati enawa ndiodula kaguleni kuprivate,kodi ogulitsawo amawatenga kuti?amawapatsa ndani?bwanji osawamanga iwowo?koma mulibzy kumanga anthu oti mfutizo mudawapatsa nokha lero mukudabwa mukuti atiphera nyama!nkhani ndiyoti dealyo simudagwirizane mwina sadakunyemereni,kuthamangira kumanga oba nkhuku koma acashigate aliphe kudya misokho ya amalawi,kumvetsa chisoni kumalawi
Koma elephant njovu ikapha man munthu simamangidwa under arest.YEHOVAs Watching you.
Apolici unu mulibe mzelu bwanji osamanga iba ndalamawa akapolo awanthu inu apolici aku mw opusa mukungofuna kutchukila bas mbuzi zapolici
Nanga njobvuyo ikadapha munthuyo..???
#StopKillingAnimals ,leave Nature as is it is .#FeelsGood for that man to be arrEsted
wow You kill a person they arrest you and now you kill an elephant they arrest you again, this world is unfair
Are they game rangers or policemen who made that arrest?
Let’s try to reserve our natural
Oba ndalama za bomawa nde mukuwakanika koma awa nde akuphwekerani Police ya Malawi yolimbana ndi aphawi
Nkhani yabwino wachita bwino mumafuna kuti Njovuyo imuphe.Mukanayimangakuti ikasewenze jeri komanso ndi ndiwo imeneyo athu achape nkamwa.Mumumasule alibe mulandu ameneyo
Nyama zikutha ndi anthu oipa ngati awa, give him a stiff punishment
I totally agree with you dude these thugs deserve a stiffer punishment
why don’t u arrest an elephant ikapha munthu? zokondera bac!
Mngoni ameneyo amafuna akakhwasule zankhuli ndipo ukakhwasula nyemba ku Maula
Why arresting him for Killing an elephant? He must be very energetic and courageous, in the bible Samson killed a Lion who arrested him? This other boy called David also killed Goliath who arrested him? Instead all these guys were given a hand of applause and given special titles, so our man in Machinga must be given a gun and employed as a Game Ranger.
Aaaaaaa
I’m just joking anthuwa ngofunika shaliya law akagwidwa chonchi
Kkkkk
Good English koma aaa wandikaikixa ndye coz ukungocheza
Kkkkkkkk
dada munthali mwaghanaghana uli kkkk
linali deal la boo apolice nsanje sunawagaileko pang’ono.
Igt Surprised with this gvt they r’bzy arrest Innocent Pple,he kill an Elephant he want 2sell Ivory is money,wy dnt Ugo arrest those Cashgaters out there’Muva Apolisi Kwa a Vumbwe amanga anthu 40 nyengo ino ya X-mass kamba koyenda Usiku,zaziiiii.
is he innocent???
It seems that you have no idea how wildlife is important to you
Umbuli
Njobvu ikapha munthu palibe mulandu munthu akapha njobvu amangidwe
Aaaaaa just kill him also! case closed!!!
Stupid minded
yes! coz he has already made huge damage & keeping him will be very cost in our malawian jails!
Kodi njobvu zikapha anthu mimazimanga?
kunziwa kumanga opha nyama koma oba misokho ayi pot nawonso akupangitsa kut makhwala azisowa nzipatala za ziko muno kupangitsa abale ndi anasi athu kufa ndai matenda oti akadatha kuchila apolisi inu mukhale serious mwanva
Zats Nc
Aaa, Shitiiii
Bad news, lets conserve our natural resources plz
Zaziiii ikapha munthu amayimanga?
Njovuyo anaipha kumalo otetezedwa ku park siinali mmuziyi kut iphe munthu mukanawerenga kaye nkhaniyi man…
.
Mukut zanziii simuziwa maiko aanzathu ngati South Africa amapeza chuma chambiri kaamba ka njovu ?? Muziwerenga kaye nkhani musamangopanga reply nkhani musanaiziwe…