Charcoal lands three in jail

Advertisement
Charcoal Malawi

The Machinga Second Grade Magistrate Court has sentenced three men to nine months in jail for being found with five bags of charcoal.

The three convicts are Friday Matchani aged 50, Kenneth Saveya, 35, and Kaunda Wailesi aged 42. They were convicted for being found in possession of forest produce without a permit which is contrary to section 68 of Forest Act.

Charcoal MalawiWhen presenting facts in court, Prosecutor Rodrick Kamuona told the court that on 20th October 2016, the Department of Forest conducted a joint operation with police officers in protected areas within Machinga.

Whilst on duty they managed to arrest three suspects who were trafficking charcoal without a permit.

The prosecutor said Matchaya and Saveya were found with two bags each while Wailesi was found with one bag.

Kamuona asked the court to impose stiffer punishment to the convicts for they are contributing to climate change due to wanton cutting down of trees for charcoal making.

During mitigation all the convicts prayed for a light punishment such as community service punishment or fine for they are all bread winners.

When passing judgement, Second Grade Magistrate Maxwell Boazi concurred with the prosecutor that being found in possession of forest produce is a serious offence and that the three are contributing to climate change therefore he slapped them to nine months imprisonment with hard labor (IHL) without option of a fine.

Friday Matchani hails from Mpamanda village T/A Malemia Zomba, Keneth Saveya is from Makina Village T/A Kaduya Phalombe while Kaunda Wailesi hails from Matupa village Traditional Authority Chamba Machinga

Advertisement

166 Comments

 1. dem really take poor people fi fool,mbali yaza khalango mumaika ndalama zochepa zina mmatumba mwanu,,koma akati kuzamidulidwe nde eeeee;!!!!

 2. Ku Malawi oba nkhuku amamangidwa kupita ku ndende pomwe oba ma billion aboma ndi mfulu. Lero wa makala akalowe ndende chifukwa chosowa omulankhulira . Ambuye kumwambako imvani kulira kwa ana anu , chitani chimodzimodzi monga mudachitira Paulo ndi Sila. Dziko lomwe mudatipatsali enatu akukhala ngati ndi obwera , ena nzika zenizeni. Ndi ndani adalirandira ndi manja ake kuchokera kwa inu ? Kundende kwadzaza a mphawi pomwe olemera ndi a mfulu amenewo ndiye malamulo a boma la Malawi .

 3. Zikukanika bwanji kukhululuka bwana azanu akupangira mavuto simanyado awa! Think like human being! Paja sukulu simachotsa uchitsilu eti!!

 4. Can justice not prevail please.if not chacoal,what else.inenso ndimagwilisa ntchito chacoal.zanditengeni.

 5. you judge , you must very stupidy, savange, barbalic judge, which penal code are you using, foolish,. I am aprison monger and i dnt care about thy nosense

 6. aaaaaa uwu ndi uchisilutu mwamva mmene akuvutila maganyumu nde mmati azitan? magez kupanda kuyaka anthu sakuona zachilendo.this is stupid

 7. Frozy mwaletsa, makala mukutimanganawoso, magetsi ndi awa akuyaka 4 hrs patsiku, sugar ndi uja akudula ngati apangidwa ku England, chimanga chakweraso mtengo, tikadye kapena ku hospa kulibeso chirichose even mankhwala njee .TITHAWIRE KUTI PART 9. Muionere nyimbo imeneyi

 8. Kumangoweruzira mabuku basi! Shupit. Akifuna anene kuti magwtsi mmene akichitiramu kunyumba kwake samaphikira chochokera Ku mtengo? Kufuna kilanga osauka basi?anthu azigona ndi njala?

 9. koma mene akuzimila magetsimu ndiye tiziphikilachani kusaganizabwanji khozan koma sitonse tingakwanise kuphikila magetsi ndiye mukatiponyakoditu tonse nanga tiphika bwanji

 10. Apezereni chochita china kapena resign kuti achichepele nawo apeze nawo mwai wa nchito , munthu mpakana zaka 70 ali pantchitobe kumati enafe tikagwira ntchito kutiko?

 11. Its not fare, why not arresting the users aswell, instead you arrest sellers only why.. Mesa chamba (marijuana) akamati cholesedwa amamanga onse ogulisa ndi ochigwilisa ntchito… Boma litangopeza njira zina zosamalira mitengo, anthu amaotcha makala chifukwa amaona kuti kuli msika wake…

 12. there iz no power 4rm escom, hw r we gonna be cooking, in this black out tym it is wrong arrestng them may wen electricity wl be there o day then u may do the arresting thing.

 13. mulowelelepo #ambuye tayamba kunyozana pa zolenga zanu munatilengelaz eishiiiii chonde #Ayesu_mngobwelasanga #chasatana chayamba #man_to_man defeating Ashiiii charcoal yomweiii ena agwilanawo galavula ena alandilanawo ma#checky

 14. Izi ndi zitsiru zapereka chilango chotero ,akulephera kugamula mlandu wa cashgate koma wa makala canzeru ndi ciani pamenepa?kufuna kuzunzitsa mabanja a anthuwa.

 15. Kumalawi kuno tonse ndi mbuli zokha zokha ndithu kkk bwanji osangowauza kuti aliyense apereka 500kwacha nanga umeneo ndi mulandu oti mpaka munthu akakhalire ku ndende kkkk

 16. That judge iz so in human…u know he even gat to go to jail as well coz his wife iz using charcol to cook him fud n charcol aint a criminal offence..shame if at all this iz true..

 17. The nation is experiencing 23 hours of blackouts a day n what exactly does he expect people to use for their cooking n whatever else

 18. We are tired of mediocre you need to understand there is nothing to smile about here you fools called magistrate, mumafuna afe ndinjala?y not arresting those killing albino’s, those people involved in corruption but you rather fight against the poor above all innocent!!! Fooooooolllllllsssss

 19. Very stupit , mukulimbana ndi anthu oti akusokola chifukwa akusowa pogwira mukumasula anthu akuba ndalama zaboma, and mmalo momanga olephera ntchito yamages koma mukulimbana akuthandiza mages akavuta osawathokoza bwanj, mbuli za amalaw

 20. Boma liphunzitse anthu kuphikila malasha,mmalo mwa makala,koma akhale thumba la 50kg,mntengo wake k30,kwacha basi,amasuleni anthuwo chonde,

 21. Akumanga amakalayo Anke nayasa magetsi mmakomomu kuti anthu azigwiritsa ntchito osamangopanga tiziganizo topusa uchitsiru etiiiiiiii

 22. Yes onse a makala amangidwe coz tonse tikudziwa bwino za kusintha kwa nyengo,so government likuyesetsa kuuza anthu kuti siyani kudula mitengo but nkhutu kumve sizikusiya tsopano izi zidzatiyika pamavuto mpaka moyo wathu onse chifukwa cha njala, and we can see that nyengo inasintha kamba kudula mitengo mpsasamala, so ine ndi okondwa coz wina atengelepo chitsamzo

 23. Kkkkkkk za ziiiii Anthuwo muwamasule nsanga.munali kuti pamene nkhalango zimatha.Ichi ndiye timati chibwana chanchombo lende.

 24. Even omwe angwita & kumanga athuwa kuti tipite kumanyumba awo tikapeza kuli makala ndiye nawoso amangidwe tiphikira chani magesi kulibe ?

 25. Judge manyi ako ambwiyakoso mimbayako mutuwaukuluwo kwanu kosauka ulibe minda ndipo ndiwe mphawi ukufuna kulemela uwatuluse anthuwo en wth bell ayi free bell uwatuluse

  1. TON SAY THE TRUE,A MALAWIFE WE ARE BEING PLAYED AROUND JUST LIKE FOOTBALL. KODI MUNTHU WABAMBO ADYESA BWANJI BANJA LAKE CHONSECHO NTCHITONSO KU NYASALAND KUNO KULIJE? KODI POPANDA MAKALA KOMANSO MAGESI A MALAWI TIZIPHIKIRA CHANI? AKUTIZUNZAWATU USE GENERATORS & HAVE A LOT OF MONEY, ZOBERANSO A MALAWI TOMWEFE? APADI TIKUNGOYENERA KUTTHAWILA KWA YESU ASI POZINNDIKIRA KUTI NKHONDO TIKUMENYANA NAYOYI SIYANUTHUPI KOMA YA KU UDZIMU.

 26. Zimenezo ndizautsiru mitengoyo ndiyachilengedwe sanabeyi chowamangira nchaninso yapa?? Nanga akuba ndalama m’boma mukuwatulutsiranji? Mufuna anthu akakudyeleni kuti? Ntchito kusowanso

 27. Magets kulibe what you think peiple will use as source of energy instead the government could bring the thing that will replace fire wood rather it could help,even if we can go to the judge who passes that judgment he is also using chalco as source of energy.This world is unfair …….This judge is in human how could you punish poor people in such a manner and yet you are keeping chalcos in your home,you shall be judged soon kunali anzanu iwe watsala pang’ono !!!!

 28. Nawo agadge chikhalile mu court mo, ndikulamula inu mukakhale kundende miyenzi 9 chifukwa takupezani ndi makala. ulibe ndimzelu zomwe kunyumba kwako tikapeza ukuphikilaso makala mbuzi ya munthu.

 29. Lets all pray for Malawi. It is poor in almost everythi
  ng:electricity, water,security,job creation,domestic fuel etc. Oh God help Malawi.

 30. Lets all pray for Malawi. It is poor in almost everythi
  ng:electricity, water,security,job creation,domestic fuel etc. Oh God help Malawi.

 31. Ndichifukwa mayiko anznthu amati xool ku Malawi kulibe zowona munthu akhale mundende chifukwa chamakala ma judge apamalawi sindikuntha kuziwa kuti xool yake amaphunzila chiyani kkkk

 32. That’s where we miss, what has the government done so far to give us an alternative sources of energy? otherwise electricity is so expensive and not even reliable at all

 33. why judging these poor innocence people like this?nine months for what?may God judge you mukusiya milandu ikuluikulu mkumaweluza anthu osauka motelemu free them pliz ino ndinthawi yolima azikalima osakalimbana ndi anthu achuma akutha chikangawa bwanji.is true that the world is coming to an end whereby munthu avulaza mzake pomulamulila.

 34. koma nde mwafika pena zoona y u peps u think 4 ur self zimakusangalasi tikamavutika tikayesala mutigwila malawi pano siwathu zukomela inu akumipando nde muzikapeleka zakudya kumanyamba anthuwo ali ndi ana ndi family nde adya chani pamwyezi yoseyo kupusa inu mudya bwino kanuko check yhis out iyaaaaaaaa kumbwambwana eti

 35. Pomwe a cashgate oba ma million akuwatulitsa akuti aonetsa khalidwe labwino kumaula,,,, kodi mdzikoli tikhale bwanji poti osauka akuzifunira kuopa mwambo omvekedwa matayala

 36. Uchitsiru wa ma judge, how can he does that and yet he uses the same charcoal at his daily basis. It only shows lack of humanity leaders we have.

 37. Umenewo ndi utchisiru ndie mukuganiza kti ife tiziphikira chani poti magetsi ndi 2 weeks pano asakuyaka kma zoona kumanga munthu bcz of madala aaaah that’s bullshirt malo moti mumange anthu anaba ndalama zambiri mbiri Ku capital hill uko

 38. Akulu akulu a dziko la malawi mukuganiza bwanji? Ma judge athu kumalawi nanga ndi chani kod? 1 kumalawi magetsi avuta nde athu kupeza makala kapena kugulitsa makala akulakwa? 2 kumalawi pano kulinjala, chimanganso chikumdula nde atha kupanga makala kuti agulitse apeze ndalama yogulila chimanga kuti akadye msima ndi ana akulakwanso? Pakana kuwatengela kundende kuti akagwire ukayidi wakalavula gaga kwa miyezi 9 zomwenso? Nde mukuganiza kuti ana awo ndi anzikazi awo,ma family awo atanino? Atawasamalila ndani? Chakudya awafunila ndanino? Kapena inu amene? Mukungopeza sambi chambe ndizachilengedwe zimenezo,ndizamulungu ogamula ndimwini mulungu iiiii my malawi iiii shame on u

 39. do these judge realy went to school? see whats is cullentry happening in our country,black out through out.so wat if people stop selling Charcoal do you think people will survive? think twice b 4 u pass the judgement

 40. Amphawife sitizapezapo chabwino. Nanpa munthu apange biznes kuti athandize banja lake inu achumanu nkumlandaso,banja lake nkumavutibe pamene inuyo nkumadya ndibanja lanulo! Ndie fuso nali: makala omwe mwalandawo inuyo mpaka nawo chani? Mkathira ku bin kapena? Anthu oipa inu!!!

 41. Ayaayaaa malawi police ur very stupid osaiwala ma judge munthu akupezera ka soap pompo kukana kuba mukumangaso…we suffering every day…tell us weh we ago do?

 42. Atulutsidwe pasanathe masiku awiri kulephera kutero judge amene anagamura mulanduwu adzasowa akadzadya zakudya zophikidwa ndimakala.

 43. so give us onother source of cooking energ coz electrity is not relaible tiziphikila chani? Khuniso mumalanda oooh God have mercy for malawi .Zikanakhalako zoveka if magetsi athu ndiokhulupilika so i think malawi needs to pray hard coz we can´t solve these own our own penapake ziganizilaniko osauka popanga malamulo anuo

 44. magstrate wopenga uyu!! mbuli zophunzira.Akuba 52billion mukakanika kma kulimbana nd amphawife. iweyo mkumaphikira makalaw… does it mak any sens.

 45. Mmmm nanutso amalawi 24 nthawi dzina muziona ndi nkhani dzake dzopangano post, imeneyi ndi nkhani yoti inu kumapangano post???? mulu ndi dzeru koma?? nthawi munaononga apa popotsita nkhani imeneyitu bola mukanapitano kokanya kaye mwina mukanankhalano ndi dzeru.makalawo adzipedzekano kuno ku RSA ndiye anene kukachilumba ka dziko ngat kameneko. MXM pa nthako panupo nonse amalawi 24

  1. Ase nkhaniyi uimvese bwino bwino usanatukwane coz anthu akuzula judge pomanga anthuwa miyezi yochuluka chonchi pazinthu zomwe ngakhale judge yonso amagwilisa ntchito tizimvesesa nkhani ikatuluka kumanso kumazipasa ulemu kukhala Ku south Africa sindiye kuti ndiwe dolo ayi khalidwe ndilofuni polankhula

 46. Noo good! Let us have pity on dose people. For someone to reach the extent of doing that business, it means he/she has absolutely nothing for his/her survival.So jailing him/her is as good as killing them and their famillies too! Lets jst find a better solution to this problem.You’ll find that those who are jailing them will take that same charcol to their homes or even selling it! So what difference does it make? Lets pity dose poor peopleeee! They are very less previleged.If we want them to stop the act, let us find a better way of telling them.

 47. Malawi contributes less than 0.01 percent to global warming,
  Putting these people in jail accomplishes nothing, but educating people to plant trees would have been a better sentence.

  Arrest the users of charcoal that will stop the practice of manufacturering faster,

  Government is so stuipd, if not cooking with charcoal it us with wood, as escom is not producing enough electric nor are they providing electric to people’s homes,

  These people were not convicted of selling or producing charcoal But because they cut trees in a protected area

 48. hahahaha uwu ndiye uchitsiru uwu..vindere vakufikapo…mukulimbana ndi ogulitsa makala kusiya omwe anaba ndalama zankhaninkhani zathu m’boma….koma muli ndi nzeru inu???iweyo magistrate kodi azibale ako amaphikila chani m’makukamu..mesa amaphikila makala omweo????…osawamanga nanga bwa?????…..ku malawi sitizathekanso in case of passing judgement……

  1. Akumipandowa chilungamo akuchizemvetsa,opha albino amatuluka,woba ndalama osawazenga mulandu koma munthu osauka yemwe akuvutikira banja lake kuti lidye kuopa kuba mwati akalowe zoona? Mitengo anadzala ndi iye?

 49. Even the magistrate himself from his chamber he will eat charcoal heated food. Why punishing someone while we don’t have any alternative? Where are we going to find power? Blackouts everyday what else do we need to use? Hey my malawi!!!!!!

 50. Thats not gud as most of malawians they dpend on charcoal for cooking so if those who selling charcoal can stop it are the ones staying in town will survive? electricity is too expensive beside that its bkackout everytime the court must think when they come to judge !!!!!!!!

 51. Hello friends my name is Zeida Mohammad I was one of those millions of people around the world suffering from HIV/AIDS and and i was healed through the help of DR Abumen I was diagnosed with HIV/AIDS in 2006, I had no hope and felt useless. All these negative feelings quickly suppressed my body immune system and my body started to deteriorate quickly with physical signs of rapid weight loss, my story began to change for good when i met DR Abumen through a woman’s testimony, he sent me an herbal medicine which i took for some days, after taking the medicine according to doctor’s instruction I went to the hospital to get my blood tested for HIV/AIDS. The doctors were amazed when my first blood test result came back negative. They asked me to go back again for another test, which I did and the result came back negative. The doctors could not believe still,To cut the story short, “DR ABUMEN HERBAL MEDICINE HEALED ME COMPLETELY WITHOUT A TRACE OF THE DEADLY HIV/AIDS VIRUS IN MY BLOOD” am so happy, am sharing this to the world to save some lives, believe me there is a cure, you can contact DR Abumen on his email address [email protected] and you can also call or whatsapp his number which is via +2347085071418.

Comments are closed.