Zimene analankhula mtsogoleri wa chipani cha Kongeresi, a Lazarus Chakwera, pa msonkhano ku Dedza kutha kwa sabata latha zawapezetsa mavuto pamene mtsogoleri wa dziko lino amene naye ali mtsogoleri wa chipani cha DPP, a Peter Mutharika, anaganiza zowayankha lachisanu.
A Mutharika amene amalankhula kwa atolankhani dzulo, anapezelapo mpata oyankha a Chakwera.
“Wina amati nditule pansi udindo wanga, osakonza kaye mavuto ali mchipani chako bwanji usanandiuze ine zimenezo?” anatelo a Mutharika.
A Chakwera anati a Mutharika atule pansi udindo wawo ati kamba dziko lino limakumana ndi mavuto a mnanu kunkhani ya umoyo wa anthu komanso ya zachuma.
Mmene a Chakwera amanena izi ndi kuti a Mutharika asanafike mu dziko muno, ali ku Amereka komwe anthu anatchukitsa kuti akufuna thandizo la mankhwala koma eni ake atsutsa izi dzulo ati ponena kuti iwo samafuna thandizo la mankhwala koma anali pakalikiliki osaka mwayi wa a Malawi.
A Mutharika dzulo anachiona choyenela kuyankha mkulu mzawo a Chakwera.
Chakwera ndi bakha
Nachi
Nachi anthu
Opempherawa amakhala oipa kwambiri bravo APM
Amwene tyeni tisiye kulozana zala palibe amene angayendese ziko 100% never olo chakwerayo atakhalapo lero sizingatheke amene ujaso ndye nyanyi,andalewa amangofuna azitipusisa. Komaso muzen chakwerayo kut mulungu anamunyanyala sangaiphule pa malawi pano mcp athu inakwana
Chifukwa chova zayekha dziko silikuyenda bwino koma bola wava zomwe achakwela anena asawa opseze walephela yekha.
Chifukwa chova zayekha dziko silikuyenda bwino koma bola wava zomwe achakwela anena asawa opseze walephela yekha.
i hop iwowaso mutu sukugwira koma…..zilizose kumangolankhulapo aaaaaaa KOMA APM…………..aaaaaaaaaaaaaaaaassshhhh
chakwera ndi kape
Peter mutu wasokonekera Malawi siwa pita muntharika aliyese ali ndi ufulu oyankhulapo za mavuto omwe dziko lathu likukumana nawo not athene kaye ndi mavuto am MCP ,MCP is not malawi
Ithink that’s the duty of opposition leaders to criticize the luring government pamene palakwikwa nde gwape ukukana chan coz this is not abt parties its about the development of our nation.
#Mtundu_wangaukuonongeka_kaambakakusadziwa!
Mmmm
Zamanyazi munthu amati wafa uja akutilamulirabe hehehedeeee shame!!!!!!!
mkhululukileni wodwala uyu Makhwala akumwao ndi amphavu moti mutu sukugwila
Do we have the President in Malawi? Go to Tanzania and see what the President Magufuli is doing
nanga bwana mutharika akakonze xa kongeresi zitheka? bwana chakwera abakonza kaye za kongeresi kenako mavuto akathako atithandidze kukonza dzikoli ife aDpp
DPP online.Amaona ngat mukuzangothesa chitozo bwana kuiwala kut mulungu simunthu asambwazeni ngakhale zitete ndi mbewa adzidya koma inu mulibe polobulemu mudwale musadwale ine nganganga pambuyo panu monga chokolo chanu hiyaaaaa dpp imandiwaza kkkkk wazaaaaa
Paja ukamayandikira kufa umayamba makani umangoyakhula zopanda mchere awa akalamba let Chakwera atirhandize 2019 chitukuko misewu basi Fotseke
Daniel 2:44
Kodi paja president wadziko kkkkk koma inu mavuto onsewa aaaa!
Kodi iwe kamatenda ukuona ngati Mulungu wakufulatira??? Sunati,God was just trying to show you that you beling to Him
kkkkl wina aliese wa dpp masiku akatha kuchiluka zochitika amafuna akakhale best 1 kujahena agalu amenewa kaya
The difference between great thinkers and shallow thinkers, Chakwera criticised Mutharika policies and Mutharika criticised Chakwera on individual basis, who is a great thinker in between the too?
chakwera is not talking about Dpp he is talking about government business he is expressing our worries to u as the head of state malawi needs someone who has a vision and the will of the pipo at heart not bunch of crooks ..
Mukumuyamba ayenera kukusambwazani kkkkkkkkkk
enanu mukuyakhula mwaumbuli apa
Machende a Peter ndendani
Hahahaha let chakwela talk ngat dzukukanikani asakulangizeni hohohoho dzakudyelani
KKKKKK!!
Mumafuna boma zakuvutani mwayambanso kulira?
mbuzi iwe eti?
USALIMBANE NDI MUNTHU MAVUTO ONSEWA NKUMALIMBANA NDI ANTHU? DZANA WANYOZA ZODIAK!
SUNAYAMBE CHIWEWE KOMA?
TULA PANSI ZAKUKANIKA UZIKAMWA MANKHWALA UNATENGA KU AMERICA WAMVA?
USAMATIOPSEZE NAFENSO MALAWI NDI WATHU!
KKKKKK!!
Mumafuna boma zakuvutani mwayambanso kulira?
mbuzi iwe eti?
USALIMBANE NDI MUNTHU MAVUTO ONSEWA NKUMALIMBANA NDI ANTHU? DZANA WANYOZA ZODIAK!
SUNAYAMBE CHIWEWE KOMA?
TULA PANSI ZAKUKANIKA UZIKAMWA MANKHWALA UNATENGA KU AMERICA WAMVA?
USAMATIOPSEZE NAFENSO MALAWI NDI WATHU!
Othawa ntchito yamulungu,amakumana mmavuto adzaoneni ukafuse yona chakwera siunati zazikulu zikubwera nkholokolo umati ukuthana nazo zija sizabwerera ndiye udxionana nazo bwanji kkkkkkkkk usova,kunrna kwandithendithe nanthambwe anazitengera,phokoso litayamba tinane musabwebwete zambiri monga inu busa onani pakhota mukonze kma simunave,kma kuliuza dziko kt mukuthana ndinkholokolo mu mcp,pano zabwerera dziko muliuza chiyani?tinakuuzani mukuphumzira ndale dekhani achina jumbe ndimikhang’a pandale pano ndiizi kaya ine ndingoti dpp woyeeee apm woyeee
all ov u you are just waisting ur tym,what i know is that there is no politics here in malawi,this is just a game of cash…..
Sorry,its Mr Edward Chirwa.I Totally Agree With You Sir.They Shared Our Tractors Among Them Selves.The 3 billion at mera,hw much was spent at UNGA?.its our tax
Auze MCP kumalawi ayi sitingapange zimenezo mitu yathu imagwira bwino ntchito
Auze MCP kumalawi ayi sitingapange zimenezo mitu yathu imagwira bwino ntchito
Brother Edward Banda,you Have Said It All.The 577 billion remains un solved etc,the country is on the standstill
Asamatero
Amene anganene zabwino za boma ili ndi omwe akudyerawo.Mlakho!
Hahahaha koma muphana,mmmmm ndibamwa kaye wa mbatata ndibweranso kudzawerenga.kkkkkk………..lol
Kodi ngati munthu akulephera kutsogolera chipani bwino nanga dziko angalitsogolere bwanji? Think twice.chakwera go back to church…
Aaa guys chakwela mulungu anamukwila coz analithawa baible nkukayamba ndale ndee aa tisayembekezele zabwino from chakwela
chakwera alibe ntchito!
Athane kaye ndi chisoso chomwe chili m’maso mwake
Munthu akamadwala mutu wake sugwila tingoti sorry
Let the President without pulling him down.Remember that he too is a human being who happens to be at painly especially when empty tins seem to provoke him.This Homo sapien who fell away from God’s hands should have apologised for what he said after the president’s press conference.He was happy upon hearing the rumour of the President’s health.Let’s be like God fearing pple-wishing each other well.
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk APM 4eva
Chakwera akukanika kuyang’anira kapena kusamalira miyoyo ya anthu 91 nde angakwanitse anthu 17 million… pita nawoni uko Chasika chanucho
Vuto loramulidwa ndi matchona ndrimeneli
Peter is piece of manyi
Chakwela go to hell, rubbish
Peter will not fill shire river with water to reduce blackouts of rain will not come next month believe me expect worse things to happen
Guys sitima imakoma akamayendesa wina, wina aliyense mulungu anampasa mbali monga bwana chakwela, kma lero ayiwala mbali yawo alingat yona kunenevi Nb afune asafune chakwela sangalamulile dziko lamalawi abwelele kuntchito yake
Pa forum yi amene akuikira gvt kumbuyo sakupereka mfundo zogwira mtima zobakira mtsogoleri pomwe a oposition akulemba mfundo ndkuipanga support zomwe zikungosonyezeratu kuti makanni ena ndi opanda nzeru. Osangovomera nkupepesa bwanji kuti sanachitedi bwino….Mxiiiiiiiii!!!!!!
Kodi A Chakwera akulotabe maloto aja koma nde wakomedwatu koma adzazuka pamene akugonapo kkkkk
Winawe Sungawine ndinane kale ine bcoz Sungasiye nkhosa za Mbuye ndikuyamba kumatukwana a2 Mulungu ali wokwiya nawe…….pipo Mzandkhukupilira
Zithu zangokuvutani musanamizile achakera Inumumat azingosekelera zilizose achakwera zilalakhulani ndithu osaopa akanyimbiwa utsogoleri wabwino amasakha ndichauta osat kuta kulimbira lero zukunyelekanani mukade muthuwana amuthalika amafuna kungotchuka chabe muziona musanat ife ndia malawi sungatipufitse
A Robert Mbozizagona mukukanika ndikulemba zolongosoka kuthamangila ndale mumalo mokalowa kaye ya kwacha bwanji
pajatu muthu akamwa makhwala ambili mutuso sumagwila ndiye achakwera ndi azodiaki amujhululukire nkuluyu ndiwodwala mutuwake sukugwira bwino ndichifukwa chake sonkhano watolakhani anapangitsaso mochedwa
Hahaha you are the man
Kikikikikikiki
Mavuto amukongolesi si aboma
WHY BACKING THE PERSON WHO IS ALWAYS MILKING THE ARLEADY THIN COW…….. If your House is Lit by Escom and Water Supplied Daily Then Say This ….. Tobacco Farmers are Crying,Taxes are Going Up and Being Imposed on Basic Needs,Cashgate Suspects Names Just Sitting On … NDIIYENO NDIKUMASAPOTERA JUST BECAUSE NDI MLOMWE MZANU…… ZA DZIKO NDI ZA DZIKO ….. INSTEAD THE LEADER TO CHANGE HE CANT BECAUSE PALI ZITSIRU ZIMENE ZIMANGOTI INDEEEE BWANA
Ka chakwela mkachaniso apa ka m’busa kaziwanda aka
Ndale ku malawi zafikapo…
uyambe wachosa chisoso chimene chili mu mcp
Mulungu chonde chonde mtengeni mwachangu musogoleli wa Malawiyu kuti mwina nkuwona zina ,mbuye imvani pemphelo langa
Dpp woyeeeee!
Kkkkkk pa malawi
Kunod ndkumalaw kungovomeleza tyen tizpangana saport osa kupezelanapo patanyozelapo musamapange ngat mungakwanise bawotu amawona nd amenealikunja.amalawi vuto mchiyani.
Loko mtatukwana paribe cmwe mtapindure nzukwa akukulamuliranibe its a tym for all de deciples of chakwera to repnt b4
Kunod ndkumalaw kungovomeleza tyen tizpangana saport osa kupezelanapo patanyozelapo musamapange ngat mungakwanise bawotu amawona nd amenealikunja.amalawi vuto mchiyani.
kma ndiye
Kukhala Mmalawi ndi kulimba mtima.
Nyamakadzi ikagwira ubongo zinthu zimasokonekera
THE APMS AKUPENGA DON’T MIND HIM. KUMAWAVESA MATENDAWA
Kkkkkkkk yaaa
U President sichida choopsezera komanso ulingati mvula imatha chilimwe chikabwera.Chonde tisamale poyankhula.Analiko anzanu ankadzitcha amuyaya anagwa chagada.
Malawians
Its very pathetic kumaomba mmanja kwa munthu Amene akuona anthu Ku mudzi ngati khasu lake.
Mulungu simunthu dyererani Kaye ,imwani,kondwani ,nyozani koma kumudzi anthu akulira ndi mavuto.
Fodya 5 cents pa kg mkumati zikuyenda
Chakwera chatsika kkkkkkkkkk
So many dpp followers are blind visionless people, poverty has ruined their thinking, they have turned inhuman. Blackout, water scarcity, corruption, cashgate are good things to dpp followers? Surely the devil is guieding them but let them know you can only delay justice and truth but a day comes pangavute bwanji when they will be answerable to true Malawians. WHY THESE BLIND FOLLOWERS NOT LEARNT ANYTHING ON CHITSULO CHANJANJES DEATH? They exalted him in 2008 as if he was the one who brought rain for the bummper harvest. They praised him with lots of self exalted names, mose walero, chitsulo cha njanje, mpulumutsi etc. What followed was meant to teach these blind followers a lesson but opss, they turned more blind and started praising this other their leader the same. Believe me and mark my words God will very soon punish you severely unless if you realise no one is super even your so called ndidzakunyenyaninyenyani. GOD IS ALWAYS IN CONTROL
Ndimaona ngati andale ndi anthu eshhhhhh ndiye bola kumasapota mpiratu
Palibe choyang´ana kwa APM or atabwera OBAMA sangakwanitse mavuto omwe tirinawowa, even BINGU ananena kuti satana anatikhalira pansana panopa ndikuziwona pomwe pastor akusiya kutumikira anthu ake kuyamba kupanga za ndale eishhh zosezi chifukwa chakusitha kwa nyengo u can go to kamuzi damu pano kunawumiratu…… amalawi azanga tiyeni tipephere mosalekeza
Big up Mr president these people are talking nosense things,chakwera this is the right time of stepping down for politics bz god is waiting for u to proceed where u left
Chakwera ndi gwape mulungu anakwiya nawe wamva kusiya za Mulungu kufuna kutukwana kkkkkkkkk abusa olenga
Abusa kulimbana ndinzawo kkkkkkkkk akatengela masewelatu tiwachosa mumpingo
Zimatiwawa Ife mbuzi zina zitamadana ndi chilungamo ndi dziko lanji longofuna umvera munthu mmodzi iweyo ndi agogo akowo ndinu mbuzi … Pano dziko lifunika anyamata ….Chakwera akufuna chilungamo chioneke .mchifukwa chiyani anthu madana ndi chulungamo ? Mmandinyasa zedi fotseke agalu
Ine sindingavotere Chakwera. Munthuyu ngwachinyengo. Zoona munthu siya kulalikira nkuyamba kumanyoza anzake? M’busa wachinyengo.
kungobweleza.1,chakwera sanalakwise chfukwa nd mkulu wa otsutsa boma.2,mavuto a mcp siokhuza dzko lose koma chpan cha mcp koma mavuto a pitala nd boma lake nd okhuza dzko lose,a malawi ose akwakhuza ndpo akuva kuwawa zedi.
Zawo ndizimodzi asatiphimbe maso
Kkkkkkk zingavute maka mcp ndi UDF sizalamulaso
PEPANI ACHAKWELA MUNGOWAKHULULUKILA MALEMUWA ANGOSOWA POFELA AKUFUNA AZITI ADAYAMBANA NDI ACHAKWELA PRIVETION IS BETTER THAN CURE ASIYENI ADZIFELE,
Wi o malawians.if u wish him bad he wil wish u worse
Sambwaza? Ndiye kuti chani? Lip service yo? Achite implement zija amanena zija. Tere apa magetsi kulibe, madzi akutuluka okuda
A visionless leader do not accept advisor, they look at advice as castigation let alone blind political and selfish desire are promoted at the expence of poor Malawians. Poverty has turned many blind and to be educated savages. Learn to run civilized politics. Be a father of everyone not the selected few. We all belong to Malawi
auze auze braz kuona ma comments alembaedwa APA mmmmm it really show kuti umbuli kwathu ngwambiri Ku Malawi.
KODI MUKUWONA NGATI MULUNGU AMAKUWONELAN UKONDWA NDI GOGO WANUYO INU A DPP MWAYESA MPANDO WAWU PRESSIDENT UFUMU OTIMUZILOWA PACHIBALE AZANUSO AMAWUFU MPANDO UMENEWU ALA,
Asatinyase Demon Cane wa Ku Malawiyo chabwera Ku manda leave abusa athu alone,mmalo mothokoza Mulungu kuti upumabe muli busy kunyoza anthu,khala phee and c wht God is planining.
Kodi mmaona ngati mulungu wakumwambayu ndiwa Chakwela ekha eti?koma mmadzivuta cos ochakwelao nde mmawaikamotu koma ukanadziwa
Wht
Ufuna ukhuluma njani wena
abusa my foot!
Razaroyoso ,sazaununkha Nkomwe Mpandowu Coz Ndotembeleredwa Munthu Sangasiye Kutumikila Mulungu Mkumat Alowe Ndale,nkhan Siyot Akonze Zinthu Koma Dyela Bas Naye Apezu Phindu Eish God Lamuliran Nokha Zikoli.
Ndakaika ngati anthu adzabwerere Ku votera MCP mwina zipani zina osati MCP
Peter alibe chonena kambani zamavuto muthanawo bwanji koma basi nkumalimbana ndi ma Radio kenaka achakwela hahahaha ulamulilo wavuta yapa
Kummwera Kuli Maboma 14 Kuli Anthu Ambiri,pakati Maboma 9 kokanganilana ndi dpp chifukwa alomwe ali paliponse,ku mpoto 6 Koma Amakwera Yolamula.Achakwera Dpp Imawinira Kummwera Chifukwa Simuingawine,ndipo Mpovuta Kugwetsa Boma Lolamula,taona Anthu Onse A Mcp Akuukilan,mwasala Nokha,munalowa Field Yolakwika Is Better Baibulo Lomwe Lija.
anthu mumatha kuyankhula eish ine mantha
Afuna oti apite naye
Aaaaaah zovuta kwabasi
Bwana Munakatumiza Anyamata Achipani Amthibuleko Pang’ono,.
Dpp ikuziwa kuti chakwera 2019 ndi boma akuyesa kuxema ziyau.
Mmalo moti awuwudze mtundu wa MALAWI zomwe amachedwera kuti apinduranji osanena zimenezo ayi Koma kulimbana ndi Achakwera zadziiiiii .Bwanji osamangomwa mtera atenga Ku UNGA!!!!!!!!!
Awaa dats why Kwa America amakatengako matenda.
Munthu wanzeru sangasiye kutsogolera nkhosa za ambuye ndikuyamba za ndale Mulungu wakwiya ndinkona zao zisakuyenda
Being people of God u want Satan to rule u why osaona mafumu a kale sanali anthu a Mulungu?
kumusakaniza ambuye amakana. bweleran mukakbweze nkhosa mukhola lake zikusochela chifukwa mb’usa kulibe ali buzy kuchipani .
Ndiye kuti peter ali bzy kukhoza mavuto aku chipani cha achimwene awocho kenako za dziko mmmh ndiye liti ?.Misonkho ya anthu osauka ngati malawi kukazikhalira kunja mpana mwezi ,awononga zingati?Esh my Malawi.Apeter chisoni mulibe mukapita kumidzi ndikukawona anthu omwe mukwaberawo kuonda kwake anthu odya chauya ,therere Kkkk
Work hard u lazy idiot ..stupid
Nzeru ulibe iwe Dalitso, kuyankhula mopusa ngati uli nkanthu bwanji? Ua more than idiot!
nayenso uyo athane ndi vuto la Magetsi
Koma chimene ndimadziwa ine chipani chikakhala ku Opposition ndi ku ma nyozedwa pafupipafupi chipanicho chimawina eg PP vs DPP! kkkk!
Mcp inateamba kunyozedwa kalekalq simawina bwanj hahaha mbuzi za anthu
Man mukunama nthawi yakwana yoti MCP itenge boma man! KWACHAA!!
zoonadi Big ana achepa…magulu achina tereza
Kkkkkkk wapengadi pitalayo
sabweza matenda amavuta abale inu
Alangiza chani nayenso mpando akuufuna.
Chaxwera sanga2e xanthu axungoyankhula
Muziona nonse osaganizira anzanu zabwino inu
sibwino kuti amalawi mukwanyanya waumphawi chifukwa chakuti anthu odziwa akuba,abodza akukanika kufufuza anthu aja adaba ndarama za amalawi osawuka aja ndiye umkumayima apa umkumayikirana kumbuyo muwasi amarawi arankhure mwawufuru wawo
Achakwelaonso ndi ndani kodi? Pya ziiiiii
Mr p simunalakwise uziyamba wachitsa chitsotso chomwe chili diso lako ndipo ukhoza kuona chili diso lako nanga bwanji nanga:D:D:D
Mtundu ndi mtundu uzaukirana bible say
Wanena zomwe wawona osati kusambwadza musamabweletse zigawano kuzipan ndinu makape mw 24 mulungu aliko zonyozeka zalelo mawa zimapatsidwa ulemu ilindidziko peter munthalika chakwela amalankhulila ifeamalawi telo sadaziyikem’mavuto komaso ku MCP kulibe mavuto m’tsinje umalimba m’ziyangoyango bless chakwela our god
yamba wacosa cili diso lako, kenako untha kuwona ca mzako.
Ok
Yes first chosa kaya chamu diso lako b4 chamu diso lamuzako or if u fail to drive dumper nanga heavy goods wt trailer?kk
Chakwe meee
Yofatsa imalumira kumchira. Wamtokosera dara!!!!!!
Big up Chakwela uyu mmmmm wasala mazi amozi
koma mwati a chakwerawa ndi abusa?abusa ake a satana kapena a mulungu.Koma baibulo alinawo?nanga ndale amadzidziwa?kodi iwo atatenga dziko lero palibe chomwe anthu angadandaule?ndi dzikotu ili.Mulungu sakondwera ndi makhalidwe otere.Adikire 2019 ndiye azayambe campaign.
Koma ndiye munthu odwala odwala. kumvetsa chisoni kwambili munthu ameneyu kungowononga wononga dziko lathu?? kkkkk koma abale akuti prophessor, uprophessor wake wa using’angatu. kadziko kakang’ono kukakanika kukalamulila.
Nde ndiwe mbuli yothelatu ngati mukanika kulemba nde mungalamule dziko
IWE PAMTUMBO, KUKANIKA KULEMBA NDANI NGATI UKUKOMENTA SIKUSONYEZA ZOTI WAMVA GALU IWE WACHABE CHABE. IWE IFE TINAVUTIKA NTHAWI YA KAMUNZU PALISO CHIYANI APA TINGACHITE NJENJENJE ZA ZIII. LELO MALAWI ALI PA NUMBER ONE UMPHAWI PADZIKO LOSE LA PASI NDIKUMATI NDINE PROPHESSOR.
Patient uyu mutu sukugwira abwelere ku chipatala
Chakwera sanalakwise iwe bwapini pitala mavuto amene alimuziko muno sungayelekeze ndimavuto a MCP popeza iwe bwapini wanyamura anthu 17 milion muziko muno frishiiiiii Mr ibu kuyakhula kopanda zeru mcp mavuto Ali muchipani chawo nanga iwe mavuto muziko muno uthesa liti bwapini kupusa basi chiwone kukula muto ngati bakayawo zeru chilibe magesi akuvuta mazi akuvutaso muno mziko njala anthu ndiposo kwacha akupitilira kugwa phavu ndimavuto womwe umawalonjeza anthu pathawi yakapeni kuti uzathesa malata unasisa komso cement komso ndunazako Aruba ndalama chaponda khope ngati tmbo hule kaliati wose awa alinimavuto muwulamuro wako bwapini frishiiiiii
Kmtu kunyoza kumeneku olo mutamutukwana chotani mpando umeneu simuzaukhalila pamoyo wanu onse bwezi mukumangokhoza mtima wanuwo kt yesu akazabwera ndiza khalila mpando wake uti?izi nzadziko lapasi zosala tizingolipepherera dziko lathuli kt mulungu aziliyendesa bwino basi
Umafuna mavuto a kunyumba kwanu athe president,u savage bwanji
Kupepela kwenikweni uzilimbikila
Ine ndine wolimbikira agalu inu simungalimbene ndi ine mbewa inu or ine sindimavota chifukwa agalu andele angonamiza chabe anthu ndawonera bwapini woyamba ndi wose agalu a Dpp ndi lhomwe people frishiiiiii nose agalu inu
Koma ndiye kkkkkkkk
Peter Wanyamula Anthu 17+million Pamene Achakwela Anyamula Anthu 2thousand Dolo Ndani Pamenepa.,,,,tamangogwilani Ntchito Chabe,, Mbuzi,,,,,.
Mbuzi ndi bwapini akulephera kukwanisa malonjezo pitala
KKKKKK ndafenta bro
Mwati frishi munthu
Frishiiiii pitala wakulu wangokula mutu ngati bakayawo palibe zeru munthu wakugwa khunyu bwapini
Mavuto Ali ndi pitala waononga dziko LA Malawi wanyutuka pitala
,@ muwamba point of correction ….sikuti athese mavuto akunyumba kwa munthu ayii koma mavuto omwe wabweresa iye u can’t see if ur naked maso
I mean with ur naked maso kkkkk
Madalitso amen
Sakuziwa agalu awa Dyness Thawe umbuli ndiwawukulu agalu awa akuyiwara kt bwapini analonjeza zithu zambili zamukanika apo mr ibu
Onse ndi mbuzi za anthu za muchombo konyera. Dziko laonongeka basi nyo nyo nyoo pa msata basi amupase bushiri mpando kkkkkk
Eti anafa ziwalo pitala KKKKK
Pano chayamba kukana chi pitala kuti chinafa chiwalo
We r not kids kkkkkk
Mbuli ndiwe thuswy unathawila kujoni
Anthu enanu ndinu omvetsa chisoni ndithu, muzitha kutsiyanitsa zinthuzi, mabvuto achipani ndiwokhuza anthu ochepa koma apapa achakwera akuimira kulangiza pazamavuto omwe akukhuza dziko lonse la malawi koma winawe ndi agogo akowo nkumati asakulangize popeza iyenso ali ndi mavuto. Nonsense!….ndisiye ndiziononga poti iwenso ukuononga…is that how malawi of today gonna be? Tingatukuke koma? Pali democracy apa? Kaya ine dziko ili silizatheka ndi atsogoleri otere
Komadi ndizoona mavuto amuchipani amakhuza anthu ochepa ndipo monga akhuzila anthu ochepa mposavutanso kuwatjesa, koma chakwela akukanika kuthananao ndiye tingoelekeza kuti amupasa usogoleli wamalawi tonse ndiye angakwanise? wanzelu opanda mamina mutu mwake atha kuvomeleza kuti sangakwanise kusogolela dziko ndipo akuyenela asove kaye mavuto ake
mwandsangalatsa man, 1,chakwela nd tchto yake ngat mkulu wa otsutsa.2, mavuto a mcp si a dzko lose kma achpan kma mavuto a peter nd boma lake nd adzko lose.
Kkkk Odi Uko Dpp 2019 BOMAAA! WINA AFUNE ASAFUNE
Adalephera kuyendetsa mpingo ndiye angwanitse dziko? Akulephera kuyendetsa chipani ndiye angakwanitse boma? Munthuyu adazolowera kungolandira satha kugwira ntchito. Munthu wamanja lende. Kuyendetsa boma ndi serious business.
Kutula pansi ndi kulangiza?ndinu achitsilunso eti..anathawa mpingo uko..
Kkkkkkkkkkk koma nkhaniyi ndiyosekesa coz omwe anavotera Dpp ndiambiri koma omwe sanaivotere ndiochepa example Mcp, ndiye mukamati Chakwera akuyankhulira aMalawi onse ili ndi bodza coz anthu ena amumvesa kale president inu a Mcp zisusani mpaka yesu kubwera bolanso John Tembo
ngati akulephera kukonza Maputo a want hi ochepawo nite adzatha kukonza mavuto a dziko lonse. tamaganizani anzanga
Ndakunyadilani amalawi anzanga nonse, maka amene mukutsutsana nane, chinthu chimodzi chomwe tingakumbutsane mwina enanu simukukumbukira, mpovuta kutsutsa mtsogoleri wadziko than wachipani chabe, pulezident amalemekezeka kwambiri kusiyani ndimsogoleri wotsutsa…izi zilichoncho kamba koti chilichonse pulezident timampangira ndife tomwe monga ma citizen…ndalama zathu zomwe ‘ misonkho yathuyi’ ndizomwe akunjoya nazo, pomwe iweyo mnzangawe ndi ine ndemwe…lero tikunena pano, wagula candle koma mnyumbamo magetsi angochita kuzima, madzi amene ukumatunga utsiku nkusunga popeza mawa kulibe, bizness kulibe umapanga zometa magetsi kulibe ana ako akuvutika, kuchipatala akuti mankhwala mukagule ku pharmacy koma iwe ndalama uyitenga kuti sunatsegule shop kamba kamagetsi, njala yilinso mkati Mmm tikamawombela mmanja tizidziwa zoti mwina si ife… Zathu zilibwino koma azakhale ako, azichimwene, ankolo, azichemwali kumudziko zawakhuzatu,… Iwe wandale wongowombera mmanja zilizonsewe…lingalira bwinotu, k1000 ungafupidwe lero siyingakwanetu kugula zosamalira banja lako, koma nkumatsekelera …asaaah nyasiii!
Ndiye nkhani umayankhiranji,Mutu wako sumagwira eti,uzilimbana Ndi mavuto nako osati peter,stupid
Zomwe ukunenazo zikusonyeza momwe iwe ulili, it means ur head is so empty…umangokankhidwa like an empty vessel kkk mwinanso kuchipaniko ndiwe woimba ngoma…ha ha ha
Chipeta , chikhala Malawi ali ndi anthu oganiza ngati inu bwezi zinthu zikuyenda bwino koma vuto kunuachuluka mbuli zosakmganiza bwino zoti akazipasa K1000 nkuiwala mavuto awo ose. Monga anzathu akumwera kkkkk eish nimavuto kwambiri.
If you remember very well the opposition leader said the president must resign.Imagine the president resigned today is this going to address all the challenges malawi is facing?To my opinion i thought the opposition would hv come with the solution to proove they are capable of solving the challenges.Through your own means you would hv contributed in reducing the scarecity of medicine in our hospitals,how many opposition parties here in malawi did this,not even one.I therefore think that be opposition is not to make others failures ..be part of the contributor to the nation.if you realy love your nation and part of the citizens of mw learn to take part in developing the nation.You find that some pple might be part of tax invassion people for example with an intention of making someone fail and yet the ones who need medicines in hospitals are our nephews and aunts.lets be patriotic
2019 boma asafuna azikande pansana…..
sungapenye pamene maso ako muli chisoso. ukuyenera chisoso chako uchotse kaye ndiye ukatero ukwanitsa kuona cha nxako
Mukamuze peter wanuyo patumbo pake
Mukulimbana nd ufumu otsala, wadziko lapansi,zandkhudza
Kkkk
Kodi Mwati Chakwela Hahahahaha Chipani Chamagazi Ichi!
Chopanda magazi ndichiti?
Chopanda Magazi Ndi Cha Brown Mpinganjira NDA!!!
Amaenda mm’bali chakwela ….. Apapa Big yamuthila faya…. Mumuona athawanxo ku MCP
kodi muthu akasala pang’Ono kufa amapenga osamutengera achakwera malemu ameneyu
kwa amene zukuyenderani ndimwai wanu koma ngat ena sizikuyenda simungawaletse kulankhula mogwrizana ndimavuto awo chakwera status yake is improving koma sangakhale chete ena zkuwavuta chifukwa cha leadership yope iripo
Sanamusambwaze koma kumuuza chilungamo zake zikumukanika
577bn dpp cashgate,MSB illegally sold by dpp,Tractors stolen by dpp,15bn cashgate at agriculture under peters watch, 3bn at MERA under peters watch, News of corruption ,Frauds is the order of the day in Dpp regime.How much was spent on UNGA trip ? How many did he take to UNGA ? Last year it was the whole village .This is Tax payers money malawians deserve to know.577 bn dpp cashgate would have bought power from mozambique,and buy drugs.Thieves at work.
Uxucita xuchula ntchito za ndalamazo….nxumat cash gate
Moto (Mchinji market now);(
Tell dem koma vuto umbuli amalawi school amapita koma mitu yawo inadzadza madzi
Alekeni adzikundikire dzindalama dza anthu osaukawo koma vuto,mwatsala madzi amodzi.Chauta akukanthani odzikonda inu.
we wouldn’t have even borrowed money from the chinise government for the stadium n BICC we could have used our own resources to build these facilities komaa dyera enao mpaka ma tractor kushopetsa iiih
Ts abt problems of de nation nt a party baba,blackouts,hunger,poor hospital condition…kubwezera zonyozana nga si anthu aphunzira koma kumalawi
nde achakwera wo mavutowa azawatha? azachita kupanga matsenga? ngati akuti madzi aphwera, magesi achepa iwo azakumba ma dam?
Etieti mwina azakumba kkkk
mayazi sizoti achakwera mwakut kwakutizo apa,to me sanalakwitse coz ndi mtchto yake ngt otsutsa amayenera kulankhulapo pazomwe nawo ngt otsutsatu ndati aona kut akhoza kuyankha,that’s the power of democracy,,,big up ochakwera msafooke angatambalale anthuwa ndi misonkho yathu imeneyo
Kkkkkkk kumangosusa mpaka Yesu kubwera hahahaaaaaaaaa ndakomoka
yesu wakupezani kale amzathu mukhalira yomweo ka 36% mukulamulira nakoka muziziwa kuti kakutsikaa
kkkkkkkkjkkkkkk
Olo lero Peter atangoti watula pansi udindo a Lazarus Chakwera simungaunukhe udindo umenewu you are too far chifukwa a Tembo anakusiyirani ndale anadziwa palibe chabwino chatsala Ku MCP,Tembo sangangosiya zithu paulere anaionera meter patali.
Muuzeni mbuyanuyo akonzemavuto tili nawowa rather than kumalimbana ndi Chakwera. Stupid comment. Muuzeni tatopa naye. Nyamakazi mpaka one month ali ku USA. Ngati ali wanzeru alikonze dzikoli osati za zii tikuonazi
Frank apa ndizoti mufune musafune Bwamphini akulamulirabe ndipo 2019 akutengaxo boma
Inuyo likonzeni man ngati mungathe ndi Chakwera wanuyo komanso ndikaonanso ndi olephera kale zithu pa Malawi zinaipa kale kale mbuyomu.
Sangaunukhe Ata Olo Pang’ono Aferamo Ndithu Kakakakaka
alomwe ndiamenewo mbuli zawathu. Okuti chimanga tizigula mk250 profesala ameneyo walomwe heede mubeso 2019 mwayi mchilima wanuyo muyaluka
Kkk 100% sure sangaunukhe udindo,ndani angavotere mcp ndye kuxungulira mutu
Nyamakazi ma complications ake nkubwebwetuka zopanda phindu
Palibe chanzeru kumuyankha Chakwera ndikuwawidwa ntima chabe koma mavuto ku dpp ndiye alibwee ngati simukudziwa dziwani mmayesa ine konko akudilira mpando wakewo akuti ndi achinyamata bola kukongelesi anthu akudziwa kuti ndizotumidwa koma simuitha kongelesi chitha ndi chipani chanucho Udf inkatani lero sifwaa basi nanga .tsogoleri wake alikuti?
“Njovu zikamamenyana umavutika ndi udzu”
the boss on the move,,,_____atsala awa a Malawi24 akusambwadzeninso…..Dont take peters quietness as a weakness…..//mumva kuwawa
Amayetsa ngati, ali m’tchalichi kuti anthu anena Amen. Chakwera mbuzi yamunthu kwabasi, sunafike polangiza president iwe ubwere kwa azibusa anzako akakumvera. Uku wayambaku, ngakhale utamufunsa John Zenus Ungapake (JZU) Tembo akuuza bwino zampando umenewo sikwamasewera ayi.
watsoka???????????
Koma iwe ukuti uliphee pa Thebawe, akakusendani zikopa ndiye paja mumafuna boma likudzakutengeni kumeneko. Bakhalani adzingokusendani zikopa ngati anyani.
Man boma silimazatitenga ife mwamva,,,,,ndipo ndalama zomwe zimathandiza kutenga anthu ku Joz si za Mr IbU,,,,ndalama zija ndizathu Anamuika pa Mupando ndanie?si ife tomweee,,,, simunati mukhaula ndima black out.
Malawi ndi kundende yoyendera koma eni amalawi saziwa. Mavuto onse ali mmalawiwa pali chosapotwra apa?. Taziyendani maiko anzanu nkumaona osati zoola zili mmalawizi.Inu nkumaonda koma yes bwana osasiya. Ena or aphunzire bwino koma mmitu mwao ndi thonje basi. Umati osusa boma azitani ndipo ndi udindo wawo kutero osati zambwererazo. Simungazimvere chisoni magesi, madzi, katangale ,njala ndi zina pomwe mukusapotayo zonsezi sizikunkuza. Ukauzolowera umphawi sibwino kulowerera kupanga kommenti zinthu zokhuza dziko. Pali za chipani ife we dont care ndiye pali za dziko ndipo ndi ndalama yathu imene akumatizuzirayo.palibe zonamixana apa or RAS Zuma amamuuza poyera chifukwa anthu safuna kuswa msabwe dziko lokhala lawo. Joice Banda anali wamkazi koma no black out. Why Malawi ??!!!
Yona chakwera sadzalamulira dziko mpaka kutha kwadziko azingolamulira zinyau zinzake
Munthu Ovetsa Chisoni Iwe Busy Kunyoza Azako Iweyo Ndi Pitala Wakoyo Pamaso Kuphwanthika Ngati Vampire. Nyawu Ndi Ndani Basi Kuzolowela Kutenga Madzi A Mkapu Kukathila Kunyanja Mbuzi!
Galu Iwe Ndi Mlomwe Wakoyo Chitsiru Chogonela Nandolo Ndi Chinagwa Mtundu Wopanda Chikhalidwe Ndi Mafumu
mukumvabe kuwawa peter anakalamulirabe mpaka 2019 mumaona ngati afa akakhala chakwera wanuyo wothawa mpingowo akalambira ku opposition konko akafunse tembo
kkkkkkk he is Judas Iscariot, he will never rule Malawi
kkkkkkkkkkkkkk!
Never never chakwera kudzalamula mtundu wa a malawi
Mwayamba kale kunjenjera inu nyau+ng’ona party DPP 2019 ikulowaso m’boma
Hehehehe neba akunva kuwawa wasegulaso kale mimba uyooooo Dpp oyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee
nyau ndi iweyo kaa moti sukuona anthu opanda tsogolo mdziko lanu peter ndekuti chani mbuli yophuzila aaaaakoma zinazi
Olo abwele chakwelao nde azatani azagotiuza kut ambuye ndiwabwino
Usaiwale kut ur not God bro & u don’t know what comes next, Ndan amkadziwa kut Malawi ingalamulidwe ndi mzimay?
Nose okongelesi mulutaya thawi nunyoza pitala ichakwela oyona tsanu okumana nimafunde panyanja nameo muluwaona mavuto yosatha mchipani
Machende anu nose kunali DPP inachokela kuti kupanda kupandukila mfolena wanuyo akanalamulilapo mbuzi simukudziwa chomwe mukunena nyamanu
Pali chifukwa chotukwanila apa?muzikhala ndimanyazi ndinu akulu AROBERT ching’ombo
Dpp boma
Panyapanu makape a dpp,Kungosangalatsidwa ndi chipani koma dziko likukukanikani. Ndiye mukunyadilapo zichani.
Tikunyadila APM wathu mpaka 2024 woooo
zikuwavuta kuyendesa cipani ndipo liu la loti achoke liri mkamwa mwa achipani nanga dziko angalikwanise?auzeni achose chimtengo mdiso lawo kenaka aone chaamzao zikawakanika akapepese ku chihema
Munthu osamva uyu,ndimayesa chakwera amafuna kumnthandiza koma kusayamika madara awa.Ndiye blackout,kwacha kugwa mphamvu,madzi ,kukwera kwazinthu ukudikira chakwera athane ndi mavuto amchipani chake ndipo uzakhoza mavuto alipo awa.Wake up mr A.p.m
Pamenepo wanena zoona chotsa chitsotso chomwe chili mudiso mwako then ukachotse chamzako , chikwara amaonjeza
zoona LC achotse kaye chitsotso mmaso mwake then amchotse APM chake
CHAKWELA wa sempha lemba
Please chonde tazingomwa ma tablet otsalimbana ndi anyamata paja yangosala matsiku wowerengeka eti,,,,Chakwera otsamtengera munthu wodwalayu ndi matenda akufuna azibale ake azikanena iweyo ndi amene wamupha.
ukatero walemba pamenepa
Ndipo tamufunsani ameneo
Iwe ukuona ngati ink palibe apa
Kodi Iwe Wakufa Sadziwika,.Chakwera Wakoyo Nayeso Ndimunthu Chinachilichose Chikhoza Kumuchitikira,.Mind You,,
Kkkkkk…u cnt even write Chichewa???kkkkk u too hv to remove yo speck brah Lol
This guy is indeed full of shit.. Your Chakwera wil never rule Malawi for your own information, akafunse John Tembo.
What is Chiyao after all #Moron Ernie Erthah Thayoh yoo you better close your eyes mfana go back to school.
Chakwera will rule this country #believeThat Brown
Aaaaaaah amalawi amisala osankhanso mcp kulowanso.prove me wrong 2019
Ngati ukufuna udzivutikabe pitiliza ndi dpp mphwanga koma otsalira
U fool why don’t u shut de fuck up ..believe u me chakwela will Neva rule this country..mgalatiya opusa iwe ..amene amwalila kunyanjawo akuuza kuti anali adwala…wina aliyese akhoza kufa . including ur chakwera who escaped God calls..stupid galatians…fool
Mayo!!!!! #Seleman usandikumbutse nkhanza za MCP nthawi imeneyo mmmm,kodi unali usanabadwe eti??
Macadet kuteteza mchere.kkkkkkk
akazakwata amako azakhala president chakwera wakoyo.
Chakwera ndi president wa Ku Kasiya wava mkhumba iwe selex
Usandikumbuse nthawi ya MCP Uncle anga ali pa Chanco anamangidwa ndiye za Chakwera zanuzo ine ayi ayi ayi ndikutitu ine ayi abale funani wina and by de way who iz Chakwera?
Paja Pitala akumachinda amako etii #Steve kkkkkkk koma ukumavala ma over size mwana wa bwampini
iwe nawe alimbane ndi mavuto anchipani chakecho asatisokose
Koma mchele ukuthatu chaka chino agalu inu fweeee ngati anakulozan bwampiniyo #moron iwe P Dalitso undisamale wamva ndikuchosa mano amene asalawo
Black or white ,chakwera is the man, my brothers
By the way who is Chakwera?
Hope you are not a Malawian,Burundi by tribe #Muluya ogulitsa nyemba
Ukuona ngati m’busa wakoyo timpasa mita kaya kwanu kuntandile komweko mcp ife ai
Kutandile ndekutinso kape iwe,,, Daud nde chani sindimayina womukana Yesu awa,
Am get tired of this stories since last month.
Please who can block me from this stories? Nkhani zandikulira izi.
yes peter is right , first chakwera must solve the problems in his party mcp ,then give advice to the president, ungachotse bwanji chitsotso cha mdiso la mzako ,chako chili mdiso lako?
shame on you lazalo!
kodi achakwera angalamulire dziko chomwe amafuna munthu nkulawa mpando umenewu osati kutsogolera bwino chili kwa nzako chigwire nyanga koma tagwira iwe nyangayo kulephera achakwera ngomvetsa chisoni osangokhala bwanji kungomva kuti ngotsutsa adzingotsutsa chilichonse
chakwera akusiya maliro akwawo kukalira aeni,sikupanda mzeru kumeneko?well done mr president
Koma ndiyetu
Awuze ngozi!!!! olo mukanatumiza anyamata acipani akatibule pang’ono…
Chifabe chimenecho
Anthu awa amadziwana poti amadyera limodzi i lyk dis song by Evance meleka,nde pagona ndalepo nde pamenepo,ps ndale palibe kunens chilungamo.
Amalawi ndiye muli pamavuto atsogoleli mbuli owatsatila mbuli nose ………. Ife pa theba pheee kuonelera ku Malawi uchitsilu wa utsogoleri
Nyamakazi petala yamgwira ku mutu ayamba misala
Nkhonya yobwezera kuwawa sanalakwitse a #President pobwezera nawoso ndimunthu amanva kuwawa akamanyozedwa
koma ndiye
pitala ulendo wakufa umeneu paja wayamba kale stroke akunamizila nyamakazi kkkkkkk
Kodi inu mukunyadila imfa ya mzanu..bambo akoso amwalira peter alipo
hahahaha oipa afe ndithu !! ine bambo anga anafa kale nanga iwe ako aliiipo ?
hahahajahahahahahaha a mutharika tisiyeni a Kongeresi fe tikhale ndi nnofu wa bakha
Ndiokuba Onseo mukakumana nao Muwauzeko Kt Nd MBUZI zenizeni
Ndiokuba Onseo mukakumana nao Muwauzeko Kt Nd MBUZI zenizeni
When Muthalika stays quite anthu amayesa ngati he is a coward. Mwachita bwino big
Zoona enanso amati wamwalira akakhala quite time nazo petulo
kkkkk koma ndiyedi
Palibenso cha mzeru. Let him show us amene amakumana nawo ku USA. We have told this several times but the only fruit is retrenchment
Koma mbuli suzatha Ku Malawi
He is just the employee , just like any civil servant , nt the President , koma Bingu he was more than a President
Koma ndietu ndi munthu wanu okanika kulankhula chichewayi muvuta kwabasi
Koma wadya admin?milomo ili mbuuuuu ngati umamwa madzi amchere
Kuyankhidwa simavuto eeish
Amalawi kodi mwatani mtundu wanga? kungo umanyozana basi?
Zoona,munthu siungalimbane ndi mavuto anzako kusiya ako.Ngati chipani cham’kanika angakwanise kuyendetsa dziko
Go depper
Tambala wakuda ndizomwe umafuna akuchitabwino
kkkkk wakhaula laza kkkkkk …kom azibusa ambuzi awa kuvuta ofunika kumawatelo
Mmavutoso ati
Kkkk koma chakwera ndimunthu omvesa chisoni ndithu,musiyeni mzanu naye adyerere iwe nthawi yako mwina mwinatu izafika
Yea adadi muuzeni amvetsetse angamaderere
Mmmmmmm Zacemako
waishi dye kumasulira kwakwe koma ndie achiyakhatu
…but Chakwela is in robust health.
LAZALO KUFUNA KUCHOTSA CHITSOSTO CHA MASO MWA MZAKO
hahahahahahahah yeeeeeeee ndiye mwati?
Mcp moto kuti buuuuuuuu chakwera 2019 boma
Kkkkkkkkkkk koma yeah thats NDALE zapa Malawi