Police in Blantyre have arrested two men suspected to have stolen a mattress at Queen Elizabeth Central Hospital (QECH) in the commercial city.
The two, John Mizere aged 40 and Samuel Austin aged 28 were arrested after an official from the hospital reported about the missing mattress in Ward 6A.
Confirming to Malawi24, Blantyre Police deputy spokesperson Andrew Mayawo said Mizere who works as a guard for Kwacha Security Company stole the mattress and sold it to Austin.
Mayawo added that police investigation led to arrest of the two suspects and the mattress has been recovered.
The suspects are yet to appear in court to answer charges of theft contrary to section 281 of Malawi’s penal code.
Mizere comes from Kunkhoma village, Tradition Authority (TA) Nthache in Mwanza district while Austin hails from Kabuthu village, TA Chigalu in Blant
Kkkkkk hajahahaa kikikikikiki koma zochitika kumalawi?!!
zachisoni
APOLICEWO NGATI ASALI A DPP AKAMANGENSO MBAVA ZOMWE ZIKUKHALA NGATI NDUNA M’BOMAZI
Okuba amanga okuba anzawo.
shame
kkk mattress
Opusa ndiwobeledwawo
Kkk koma matress akeo ukanadziwa iwe wokuba…sukanaba….
Mpofunika Kumamangadi Oba Matiresi Kusia Oba Ma Billion Kkk
Mbavazi musazisiye. Ngati uli msonkho kodi matress amenewo anagulidwa ndi misonkho ya awiriwo? Nanga misonkho ya okalamba, olumala, ndi ena ambiri omwe amadula misonkho siku ndi siku kuzera mukatundu amene amagula monga sopo, mchere, matches, sugar ndizina zambiri. Surtax zimayiziwa mbavazi?? Ku chipatala sikochitila masewera. Boma linaganiza bwino kwambiri kuti munthu wodwala amafunika kugona pawofuwofu chifukwa mumidzi odwala ena amasaukila kugona pa bwino. Mbavazo muzisunge ku nyumba ya chisoni
Bwanji osamanga Peter bwampini ndi nduna zake
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Mbava yozindikila sitchola panyumba pamunthu koma m’boma momwemo awa sanalakwe aliyese amaba chomwe akuchisowa kwao
Koma kumeneko kwabookaso
Kikikiki mphasa zatopetsa abale inu, tkagona pa matress nd ku hospital?
Kkkkkkk matress?Shame
My name is Musonda Kaluwe and this a testimony of how i became HIV NEGATIVE, i have been suffering from HIV for the past six years, i have spend a lot of money finding cure for HIV/AIDS until i found this true man who cured me completely with his powerful herbal medicine, i have tried different means to get this virus out of my body, all the possible ways i tried did not work out for me, i came across doctor olumo through some amazing testimonies concerning how Dr Olumo has cured different people from various kind of sickness like HERPES,HIV/AIDS, CANCER, with the help of his powerful Herbal Medicine, so i was encourage and i contacted Dr Olumo i told him about my Sickness, He told me not to worry that he was going to prepare some Herbal Medicine for me, after some time in communication with Dr Olumo he finally prepared for me the herbal medicine which he sent to me through courier service and he also gave me prescriptions on how to use it, after taking the Herbal medicine for some days, i went for test to confirm and the result was totally negative ,i went for test again in a different hospital still the same negative , Today i am fit and healthy to live life again, I am so happy for the good work of Dr Olumo in my life, if you are having a simillar problem kindly email HIM on { [email protected]} OR CONTACT HIM WITH HIS NUMBER OR CHAT WITH HIM ON (WHATSAPP) (+2348138956767) together we can live an HIV free life.
kkkkkkkkkkk! olo ntavutika kwa 10 yrs I cnt involves such fucken deal
kumeneko ndiye kupusa anyamata mukuba zinthu zopanda ntchito mulungu akulangeni inu mudware tiwone mukagonera pachani zitsiru zimenezo
Nanuso apolice ndiye zitsilu zedi mumaleka mbala zenizeni nkumakagwira anthu oba nkhuku.
ok
nanga mawa akazadwala azagona pati? ufiti umenewo mpaka kuchipatala kusowa zakubazo, ndie mawa mkumati kuchipatala kulibe mankhala mutamaliza kuba. zulo mwaba mafrigi lero matress nanga mawa mibeditu sichoncho nanga?
Mwasowa zakuba eti?
Yayayahyah akuba anzeru sanabe za munthu aba zaboma mukatuluka mupitilize pofuna kudya nawo ndalama zabomazi
Uku ndiye kupusa kulimbana ndi mmalawi oba mattress oti flow ya mukwana,kusiya nduna zoba ma billion. Ndi mattress angati ma billion amenewo angagule foolish….
zayambira kulikulu kkkkkkk
Koma abale inu ku malawi mavuto sazatha mpaka matress akuchipatala zoona!!?
Kkkkkk koma zinazi
Anthu anzeru kwambir amenewo, sanabe pakhomo pamu2 ay!!!!! imineyo ndimisonkho yawo!!!! ndipo apolice amewo muwamasule sanalakwe.
Really?
Yah really, sanabe pakhomo pako. kapena waba pakhomo pako?
Iwenso ndimumodzi waiwo nde usationongere kukonza zinthu!
Doreen ukadzadwala udzakagona ku mwai wathu eti….
anthu ena alibe chisoni,,,kuba kuchipatala zowona? nanga akadwala akagona pati? apasidwe chilango chokwanira kuti ena atengelepo phuziro….