He might have thought that the industrial hemp that has met positive reception in the corridors of power refers to the common hemp and that misunderstanding has landed a Blantyre man in trouble.
Police in Blantyre city have arrested a 20 year-old man for cultivating Indian hemp locally known as ‘Chamba’
The suspect, Chifundo Kaliati is reported to have grown the hemp behind his house in Ndirande township in the city.
Confirming to Malawi24, Blantyre Police assistant spokesperson Andrew Mayawo said well wishers reported the farmer to the law enforcers.
“Actually we got a tip from residents around Ndirande that Kaliati has grown cannabis sativa behind his house and we went there and found twelve trees,” said Mayawo.
Meanwhile, the crop has been sent to Bvumbwe Research station as part of investigation before Kaliati appears before Blantyre Magistrate court for growing the illegal herb.
The suspect hails from Gomani village,Traditional Authority (TA) Kunthebwe in Blantyre.
Apolice ndinu makape bwanji muku gwila anthu kukhani ya chamba amati ku chiphweketsa chakudya chanzako ndi nchimo ndimango kuonani anthu amagwila okha ntchito ndiku peza ndalama ndiku kagula chamba okha osatuma munthu chikanati chamba chima yambitsa kuba ndibwezi tikuti kazi agwilani koma cholimila manja awo kugulitsa so okha inu mumalimbana ndizanzi bwanji abingu ama tiuza kuti ndalama zili muulimi inde amati kusuta kuntha kuononga moyo nde bwanji sumakawamanga anthu amagulitsa fodya kuka nengo aja nde ziku siyana pati bola so chamba chi fukwa chimango pengetsa makolo ako nkumaku ona koma tobako nde amapha
Kodi Mukuti Chamba Or Chambe?
nkhani izi zichepe!! omanga wachamba amangidweso!!
mukumanga mlimi koma muli osuta chambacho :-> zitsiruuuuuuu
Kumadya zomela police have problem
iwe Musiye msanga ukalimbane ndi mbava uko zimenezo tiloleza kale kodi ukugwiritsa ntchito malamulo ati ?
:p
Sheeeeeeeeeeeeeeeeeee
Chamba is my food pls don’t play with it
Apolice kamuzu ananena kuti chuma chili nthaka ndiye mukumumangilanji
Mukwalesa kulima chamba ndiye zipanga chani
Game over, Noma 1-0 prison wakwiya ndimfiti!
apolici na
Apolis ndi anthu amodzi mwa obwezeretsa chitukuko kumalawi, kaya amawalipila zingat kaya? Mbuz za wanthu
Helb is the weed not a drug.
Mesa anavomereza kuti tizilima????
REGALISE
Asowa chochita eti .
Boma linavomereza kulima Chamba nanga apanso bwanji
12 mitengo basi? but remember malawi chuma chili mthaka
Kod chamba analemba ndi Mulungu inu mugwilinja anthu ongolima???osakagwila amene anachilengayo bwaa??
Sinthawi yomazuguzana thako ino iwe wapolice panga zako
Iwe wa police mesa analoleza nde ukupanga chan apo biii Kamugwilen Jah Jah pogwetsa mvula kut chamba chimele
leave the farmer alone remember malawi z agro based
Achitanji mwana wamwamuna kwacha yavuta iyi.
Amusiye ameneyo akuyesako mwayi chuma chavuta pa malawi
until when?