Update: Police arrest one in gruesome attack on albino lady

232

Police have arrested a man identified as Joseph Ndimbwa in connection to the attack on Lucia Kainga, a lady with albinism who had her arm chopped off by her attackers.

The arrested man is a neighbour to Kainga’s family.

It is said he connived with the other thugs to kill the lady. Over the weekend, 51 year-old Lucia Nyakainga was attacked by four unknown men together with her husband in Chitipa district.

Her husband, Yohane Mfungwe said the four men broke into the couple’s house in the early hours of Saturday and threatened to kill them.

Lucia Kainga

Lucia Kainga in pains.

It is said that another family heard a scream outside and they opened the door to check what was transpiring with the person calling for help. The men then chopped off the woman’s arm and went away with it. They also injured the husband.

Mfungwe, was the first to be assaulted with a plank of wood on his way out to help.

It was after this that Mfungwe fell down and collapsed. The attackers then went ahead and attacked the wife with pangas, targeting her hands and the head, and leaving her with deep cuts on the neck and the left hand.

This comes hot in the heels of calls for government to consider introducing the death sentence on albino attackers.

But Peter Mutharika led government has however remained coy on this.

Share.

232 Comments

 1. Hello I’m Samuel Okizou by name, I’m giving a testimony about Dr.Sule the great Herbalist, he has the cure to all manner of diseases, he cured my HIV disease, though I went through different website I saw different testimonies about different herbalists, I was like: “Many people have the HIV cure why are people still suffering from it?” I thought of it, then I contact Dr.Sule via email, I didn’t believe him that much, I just wanted to give him a try, he replied my mail and Needed some Information about me, then I sent them to him, he prepared the CURE and sent it to me via UPS courier service, they told me that it will take 3-4 days before I’ll get the parcel, 3 days later I received the package and I started taking the medicine as prescribed by him, after 7 days of taking the medicine I went for check-up, I was tested HIV NEGATIVE… IF YOU ARE SERIOUS YOU WILL BE CURED!!! contact Dr Sule on whats-app +2348162447651

 2. anthu ngati amenewo ndiwofunika akafele ku ndende anthu aulesi kugwila ntchito ofuna kulemelela ziwalso za anthu ena ofunika kuwakhomela m’prison nkutenga ma key a sell imene alimoyo nkukawataya pakatikati pa nyanah ya Indian Ocean chifukwa mu Lake Malawi akhoza kukawapeza azizake

 3. Its only God who can rescue us from this, we need to cry to the creator. psalms 107 v 20. he sent out his word to heal. respect God,s words do not kill. late president used to say chuma chili mu mthaka. you must work hard in the field. when God created man he gave him the garden of Eden to take care of it. not killing our brothers and sisters. fear God.

 4. akuluakulu zinazi sizofunika kuchita kudikira Mulungu kuti awalange,anthu amenewa akufunika chilango kumawayambira pansi pompano,kumawadura chiwalo chimodzichimodzi kuti afe imfa yowawa,albino is a human like us.

 5. I hate when i hear someone calling my country the warm heart of Africa, We don’t deserve such name am obviously sure that we don’t fight cause we have nothing to koma kuti tionetsetse a Malawi ndi athu ankhanza kwambiri,, Imagen cutin someone’s arm for what reason?? Yet de so called Pitala iz givin dose thugs a support instead ov teaching those idiots a lesson.. Allah bless Nyasaland that’s why i always pray for Christians to accept Islam,, Simungamve msilamu akupanga nawo zimenezo.. Anyway am not here to preach am only concern for what dey did to ma innocent mother,, alima bwanji amayi awa? Pepani zinthu zikuvuta chfukwa chakumipandowa so let’s not kill innocent pipo leavin achina Balaba dere smh!!

 6. Muzimu wamalemu bingu uwuse ndi ntendele anati mudani wawo ana umphawi ,njala ,komaso chitetezo chokwanila amalawi ndikhulupilila kuti mwakumbukila bwino lomwe mawu ake a mose walelo.

 7. If i can catch one of those who are killng my blovd albnoz i cant totaly stink a sharp knife in his useles head bcoz we r tired of u bullshit ppo!! and GOD wl set fire on u bad ppo!!.

 8. Amene agwidwawo ngati ndi iwodi avulaza mzimaiyu,”chilungamo chiyende ngati madzi”DISO KULIPA DISO”Nawo adulidwe nkono komanso aseve jere.Apo bi! kulibwino anyongedwe chifukwa zomwe apangazo apha.!!!

 9. Pls pls asatuke ameney akhale moyo onse asangachte bwno kamba kot waxowetsa moyo wanzake choncho sibwino pls mpandeni mbuzi yamunthu imeneyo

 10. Uku kosakondana ndi bwino boma liike lamulo wokupha zake aphedwe mwina athuwa angachite matha apo ai akagwidwa muthu woterei aphedwe pompo or pakhale police ndibwino kuwaphera limodzi baaasi ndiye tidzaone kut boma izalakhulapo chan sii boma lakanika aasiye athu agwire tchito bas pafika zithupa ndi wokupha nzake aphedwe basss

 11. mmmmm koma anthunu khalidwe lapipi ngat limeneli mwalitenga kuti,koma ngat akukutumani akupweteketsani ndthu mulungu akuona ndpo sazakusiyan chabe anthu oipa inu

 12. We should deal with the source not the ones that do the job their rules says f u have caught dot mention me and all u put in jail are the poorest villagers big boss are still out do u think they wul stop demanding 4 more,deal with de source then u wul c that problem solved am just passing through.

 13. Koma Munakakha Kut Mumaona M’mene Kumawawila Potchima Sibwez Pano Mukutelo Kubeleka Ndikowawa ABoma Mutengepo Mbali Mukuyenela Kutenga Malubino Onse Ali Maboma Ndikuwapezela Camp Ndikuyikako Chitetezo Chokwanila Ngat Sizitelo Mukudziwapo Kathu Athu Amenewa Mukawagwila Choncho Akumadisha Mukumawatutsa Cashgate Ndimene Munayitha Kufufuza Mukukanika Kufufuza Kumene Kuli Msika Wa Albino Mulungu Adzakulangan.

 14. Why MALAWI why? Albino is a Human like, have a mercy please. Amene mukumapanga chipongwechi ndinu Amuna anzathu, mukutichititsa manyazi. Shame on you #Stupid people. Curse is upon your head and the hole of your family. Anthu osafuna kugwira ntchito inu kungokhalira kukhetsa mwazi wa Anthu osalakwa, #GOD will punish you.

 15. ine omwe akumazenga nkhanizi sindikutha kuwanvetsa. kodi sangawapane anthuwa? kuti awulule yemwe akuwatuma komanso komwe akumakagulitsa ziwalozo? zitipidulira chani kumangopukuta mafinya osazula mingayo? ndakwiya nanu

 16. Abale ndi alongo,Mulungu watiwonjezera timasiku pang’ono kuti mwina tingalape, koma ayindithu.Apatu bola MULUNGU atiweluze coz patokha talephera.

 17. ineyo ndikuona ngati kuti anthu amenewa akagwidwa mphamvu zisamakhale ndi a police iyayi koma ku anthu azithana naye wokha azingopheratu anthu awa akuwononga mtundu wosalakwa. nanga amai awa alakwa chani mpaka chonchi. chisoni chandigwira. pepani amama.

 18. I love Malawi and I want to live there when I retire there! But with all these stories I am now scared to think about ever living in that country. This is inhuman, and a disgrace because I have known Malawians to be very humble and loving people

 19. Satana ali ndi njira zake chonde tisiyileni azibale athuwo ngati ziwalozo nzaphindu ndipo nzopindulitsa bwanji musayamba mwadula zanuzo zatikwana ompezayo aphedwe osati kupita naye Ku police apolisi amakhala akuziwana ndi zigawenga zotchuka ndziko lina lililonse nde sangasove

 20. Yense opezeka akufuna kupha kapena wapha kale basi tizingolanga tokha basi coz kundende azikadya nsima albinsm kuno ndikwawo mdziko lawo lomwe asasowe mtendere ngati ali dziko la eni.

 21. Kodi boma likutipo chiyani pankhani ya ufulu waanthuwa? Bola mu 2019 muzavotere bwana EVANCE MAZANGO PHILIH, muchipani chotchedwa people’s human Rights in Malawi PHRM, chomwe chiyambe mu June next year. Lidzakhala Boma la chitetezo kwambiri.

 22. Bon Kalindo akati ayende maliseche nkumati mawaya anaduka. Nanga chochi kumulumalisa zimayi wokongola ngati ameneyi. Pepa mayi wanga GOD LOVES YOU THATS WHY YOU’VE SURVIVED

 23. DEVILS CHILDREN, WHY NOT LEAVE THESE EVIL ACTS? WHY BEHAVING LIKE WILD ANIMALS? YOU WILL NEVER PROSPER IN LIFE WITH YOUR WICKED MINDS.

 24. Amalawi tiyeni tikondane wina ndi mzake poti tonse ndife zolengedwa zamulungu, ndichenjezo langa kwa nonse mukuchita izi kuti muyenso womwe umamuyesa nawo mzako ndiomwe umazayesedwa nawo ena mukuchita izi muli ndi ana, zizukulu mudziwe kuti zizakuchitikirani zimenezi kwa ana anu atabereka albino palibe amasankha kuti abereke mwana wanthundu wina ulionse koma ndichikomzero chamwini mlengi

 25. +260972036211: CALL DR. OKWITU LUBANGA IN LUSAKA /ZAMBIA/

  LETS, THANK THE MANAGEMENT OF ZAMBIA TRADITIONAL HEALERS ASSOCIATION COMMITTEE TO BRING DR OKWITU THE STRONGEST MAN IN AFRICA:
  SPECIALIST IN : RE-UNITING LOVERS 24HRS AND MAKE HIM/HER LISTEN TO YOU, WIN TENDERS / CONTRACTS,
  – RECOVERING STOLEN PROPERTIES , COURT CASES AT ANY STAGE, BUYING/SELLING OF PROPERTIES, PASS EXAMS, LUCKY CHARMS TO REMOVE BAD LUCK, PROMOTION AT WORK , CUSTOMER ATTRACTION (BUSINESS), DELAYED PENSIONS, RESTORE A JOB OR GET A NEW ONE, CD4 BOOSTERS, DIABETES,
  -MARRIAGE/PREGNANCY ISSUES, QUICK MARRIAGES, DIVORCE, MANHOOD RELATED ISSUES 4 IN 1 PACK, HIPS AND BUMS ENLARGEMENT, BREAST FIRMING, -FINANCIAL PROBLEM,/GET RICH WITH CHITAKA WALLET OR HIRE SHORT BOYS TO BRING MONEY IN YOUR HOUSE /ACCOUNT 24HRS, POWERFUL SPIRITS TO CONNECT U TO YOUR GRAND ANCESTORS (K500)
  WE DELIVER +260972036211

 26. Papita nthawi pamene mchitidwe wopusawu unayamba ndithu! Kodi ku Malawi kuli president? kapena tinene kuti ndiamene akutuma zigawengazi? Sorry my beloved country that was once called “the warm heart of Africa” bt now its the warm heart of Criminals.

 27. Anthu azikhala ndimantha mudziko lawo zowona??kukacha aziti amen sanatigogodere,kodi nthawi ya Kamuzu zinalikoso?Albino ndimunthu ngati ine,mayi wa albino anamva kuwawa ngati mmene amayi anga anamvera kuwawa pondibeleka ine,anasiyiranji mwini mwana kumupha atabadwa kumene kuti ndimu albino ndingomupha???oziwa kuchosa moyo ndinu anthu ofuna kulemera???chonde tiyeni tikonde chilengedwe chamulungu,mulungu polenga mu albino amakondwera,pa ten commandments pali mau oti,konda muzako mmene udzikondera iwe,mwaphwanyiranji lamulo abalaba inu????nanga mukanakhala kuti mu albino ndinu mukanatani????less hold hands to love our albino’s.

 28. Boma Liloleze Kuti Akapezeka Otelowo Apolisi Azipeza Titalanga Kale Tokha Osatinso Akalowe Kaye Khoti Ayi Koma Aphedwe Pompo Pompo Bola Umboni Weniweni Uzikhalapo Basi Mwina Zingathandize

 29. Pakuganiza panga ndikuona kuti boma likudziwapo kanthu zankhaniyi,the only way to solve this problem is throu god the almighty lets just pray hard so that we should find solution!! Kaya ndi mob justiceyo tiyambepo!!!

 30. THE NIGERIA CUSTOM SERVICE AUCTIONING OF DIRECT TOKUNBO CARS ARE NOW ON SALES!! AT CHEAPER AND AFFORDABLE PRICES, INTERESTED BUYERS SHOULD CONTACT THE CUSTOM MARKETING DEPARTMENT FEMI BELLO ON (09039549935) THOSE VEHICLE AREACURRENTLY AMIABLE AT THE CUSTOM WAREHOUSE AT SEME BORDER LAGOS AWAITING REMOVAL BY CLEARANCE AND CUSTOM DUTIES ‘EG; Golf 1,2, 3, 4, 5, 6,from N200, 000-N300, 000. Toyota Camry big. daddy=N400,000. Honda accord baby boy=N400, 000. ToyotaMatrix=N400, 000 Toyota Prado=N600,000 Toyota. hiaceBus=N450,000 Toyota Avalon=N 400,000. ToyotaCorolla=N400,000 Mazda=N 350.000 HondaAccord end of discussion =N400,000 Honda Evil Spirit =N400,000 ToyotaCamry. 2.2(Tiny Light)=N350,000, Toyota Avensis=N400,00. 0, Rav4=N500, 000, Toyota Seinna=N400,000, Highlandzxer=N550,000. ,Murano=N500,000, Pathfinder=N500,000, Infinity Jeepfx35=N500,000. & fx45=750,000 Mercedes Benz ML350=N500,000. ETC

 31. I prefer to concur with George,it’s not the govt alone that is better placed to cub this atrocious deeds,we need to unit and say one voice as brothers and sisters.We can’t afford to allow the minority to keep terrorising and butchering us precisely because they want to get rich swiftly.Lets wake up from slumber and depict the police where they getting it amiss

 32. IT IS VERY PATHETIC THAT THE GOVERNMENT IS TURNING A BLIND EYE ON THESE INHUMANE ACTS.

 33. We have no choice nw, its enough nw, our goverment is doing nothing to end up this situation, let us take the laws in our hands, mob justince will help to deal with the sitiuation, we can’t stand idol and waite for the goverment to decide what to do while our relatives are living in fear, its enough now!

 34. Zoona anthu amenewa anja omwe timati anja ankhalidwe lonyatsa ndi lonunkha ofunika akangwidwa nawonso alandile chilango chomwe iwo akuwa chitira adzanthuwo anthu oputsa opanda chisoni moyo ngati ziweto nawonso akangwidwa nawo aphedwe nawo

 35. Ignorance is proving to be expensive and the sooner we deal with it the better.This is the best time for NICE Trust to make noise in the remotest parts of the country where supernatural beliefs reign supreme.

 36. Mmmm nanga choncho ndichilungamo ichi tikuchita a malawi fe? Boma ndye lidzisekelera zimenezo? Tiyeni timange umodzi abale or mutapanga zimenezo sikuti umphawi wanu utha ayi, ndipamene zipitilire kuonjezeleka coz Allah(Mulungu) akwiya nazo zimenezo. Palibe kothetsera umphawi koma kungogwada ndikumupempha Namalengayo amapatsa kusiyana tidzilimbana ndi ndalama za magazi, remember ndi masiku omaliza ano

 37. Mmmm nanga choncho ndichilungamo ichi tikuchita a malawi fe? Boma ndye lidzisekelera zimenezo? Tiyeni timange umodzi abale or mutapanga zimenezo sikuti umphawi wanu utha ayi, ndipamene zipitilire kuonjezeleka coz Allah(Mulungu) akwiya nazo zimenezo. Palibe kothetsera umphawi koma kungogwada ndikumupempha Namalengayo amapatsa kusiyana tidzilimbana ndi ndalama za magazi, remember ndi masiku omaliza ano

 38. boma likufunika lipangepo Kathi mama kupereka chilango chachikulu kwaemwe akukhudzidwa mwachidule akuyenera naye aphendwe km sanaphedwe ayenere afotokoze bwino komwe amafuna apite nazocho ziwalo zamuthu zikatero boma lipeleke chilango chokwanila

 39. Don’t kill him first he must tell all people involved in this evil act, I wish I was there my God , FRIENDS OF ALBINOS MOVEMENT kill the killers

 40. Kodi lamulo wokupha zake naye amphadwe munalichoselanji akuluakulu inu mukudziwapo kanthu koma chauta akuona tsiku ndilimodzi mwini namalengayo azakuoneselani poyera chuma chanu chamagazi

 41. Shaliya low wakupha nzake aphedwe kodindende imeneyi inapita kuti? Thats why masiku ano anthu akumati akapeza wakuba akumuwotya kuli kutopa nawo malamulo aboma amalawi kumpeza munthu opha alubino osampanga lipoti ku police tiyeni timpachike mateyala awotchedwe basi nayeso

 42. Vuto ndi boma zonsezi .lamulo loti opha mzake aphedwe lilipo koma mukulimbana ndi zokhomera minda popeza mukudziwa kut pali cholowa koma kuteteza mizimu yosalakwa simukufuna

 43. Olamulira a dziko lathuli akulephera kupeza njira zothana ndi uchigawenga woipawu, tiyeni a Malawi tiyang’ane kwa tate wathu wa mwambamwamba atipezera njira zothana ndi zonyasazi!

 44. Peter zikomo kwambiri patchito yose
  Ukugwira tinakuvotera kuti uzituma athu adzipha alubino omwe safunika kukhala padziko lapasi ndiwe wekha amene ukufuna moyo zikomo mulungu akudalitse ndimwazi umene ukukhetsa kwa ma innocent people

 45. Fellow Malawian its only mob justice can solve this problem,not a president, Judges or Organizations,when we hear about these killers they no need to call Police,we should call police when the problem is solved.

 46. Why are these thugs breathing free oxygen?Am very sorry.God is always by the side of the poor,vulnarable and the ompressed.Get well dear Lucia Kayinga.

 47. musavutike guys nkhani yofunika ndi demo achoke peter chifukwa ndiemwe akudziwa msika,mmalo motuma anyamata ake kosaka mbewa&zitete akuwatuma kosaka maalbino asowe watikwana

 48. Apolice achita bwino kumugwira kuti akamuteteze kuopa anthu okwiya angabweze chipongwecho coz ameneyo nde mmalawi amene ali ndi right to life okhapidwayo ayi if not so then why saying no to death penalty?

  • Baba sizikugwilizana lets fire those who are doing this and we together with the government we may have one root which can end is obstace not pointing a party.

 49. malawi akupita kuti ?ndalama basi mabanja kuonongeka kamba kandalama pano ndimuthu mzakono mkumati ndalama ok….!

 50. Amene analakwitsa ndi President akulamukla panoyi akananena poyera kuti ndikulamula opha anthu amenewa akagwidwa naye aphedwenso.Nkuyamba kuphadi zikanasiyika.Koma president makayo akuti ayi kuli kuwapasa mphamvu kuti ziphani.Chofunika kwamiri amalawi tiyeni tiyike malamulo manja mwathu basi kugwira nayenso nthawi yomweyo afe imfa yowawa kwambiri

 51. Aka pezkea anthu oterowo , zakupolice ayi ,chifukwa chake azikatulusida pa belo but the best way kumudulanso ziwalo nayenso aziwe kuti ndi tchimo

 52. munthu anabadwa wabwinobwino uyu lero mukudula zanja ngakhale achile muzimuthandiza kulima? Muzimuchapira kapena kumuphikira? chomwe mukuchitachi ndiye sichilungamo . Boma likuziwapo kanthu zakuphedwa kwa anthu amenewa. Anthu ayendapo maliseche kukwiya ndi nchitidwe umenewu ndipamene wina akupitiridzabe kudula anzake manja chonchi Jodi mphamvu wayitenga kuti? chikhala anakomana ndi ine ku police ko sakanapita tikanangompanga timtini!. zatopesa izi shupid!

 53. In his manifesto he was preaching abt the security tight. Fenx mr President for doing nothing while our brothers en sisters are butchered daylight

  • He should not be granted bail. Let him rot in jail. He should also tell the nation at large where there is a market for these people so that it is demolished

 54. Anthu nkumawagwira zilango zake zotiphimba mmaso! Dziko lathu tikumangopeza atsogoleri ake opusa, akumidima komanso osaopa MULUNGU. Tisayembekeze malawi kutukuka akutsogoleledwa ndi mbuzi zozikundikira chuma komanso kuzunza anthu ake kut zilemere.

 55. So sad Mulungu adati aliyense adzadya thukutalake osati kumpha muthu kapena ziwalo zamuthu,chotitidziwe malubino ndi muthu ngatiifetomwe.

 56. Kodi nsika wake ulikuti, ndipo akumagula ndani? Chofunika ndikuthana ndi nsika wawukuluwo zikatelo malonda amenewa atha. Kuwononga moyo wamunthu sibwino zimenezi zitheletu ndithu, Mulungu singapange munthu kuti adzidzaphedwa ngati nkhuku.

 57. God will add a stiffer punishment to Malawi nationals,if this does not stop!You are in hunger attack and still adding on more hunger!God must judge mercilessly over you Malawi.
  That’s a crying oracle from a man of God in fasting!

 58. these people are sick, There is no short cut Riches. Work hard don’t. be lazy butchering people thinking success wil come like magic

%d bloggers like this: