President Peter Mutharika has said that government will continue upgrading road networks in the country to boost social and economic activities.
Mutharika made the remarks on Monday in Blantyre where he was inspecting new road projects in the city.
“We will work on all roads leading to the townships. Malawi needs good road infrastructure to ease access to public services such as hospitals, schools and markets among others. That is why my government put road infrastructure as one of its priorities,” Mutharika said.
He added that Malawi needs a good road infrastructure to spur economic growth.
“We want to make life comfortable. We want to make driving and travelling more comfortable. We are upgrading these roads to reduce congestion and ease smooth flow of traffic. Besides, good roads reduce vehicle maintenance costs,” the state president said.
He further said that this is good news to minibus operators too as they will benefit from the new roads and Blantyre will be a new city.
“Government plans to upgrade more roads within and on city boundaries to facilitate social and economic activities,” he said.
The inspection exercise took Mutharika to Limbe, Bangwe, Manja and Chilomoni Townships.
Dnt wstng money for mkng shit Rd you dnt wnt to hlp pple at thy hms
Please mukhozenso mzuzu to Nkhata-bay road.
Tamuuzani mkuluyu akagwele uko
wosatiwatu amavota ndi anthu tizaonana 2019 basi
You worried about Roads, instead of solving hunger in our country @stupid decision Mr Pitalaaaa
Puss
Pali anthu ena chimene amayankhula chomwe akunena chopsnda tanthaudzo ngati mnsogoleri wadziko akuyenda Madera kuksona Miseu kuti ikonzedwe ngati M bsli imodzi yokongoletsa dziko kutipangira ife kuti nptidziyenda mosavuta lero tikuti walakwitsanso koma anakagula chimanga tsopano ngati M atrack onyamula chimangawo ngati Miseu siilibwino akudutsa kuti muli ndinzeru zoputsa nonse amene mukuti walakwitsanu ngakhale mukufuna mundiudze kuti mwanawanu alindiutsiwa wakabudula amalephera kupita kuxool muli ndindalama yokwana thumba lachimanga mungalephere kudulako ndalama yathumba ndikugula half kwinako nkukagula kabudula wamawa azipita kusukulu?ziganizani guyz be4 u comment
Anthu akufuna chimanga osati misewu
Starving Malawians must use that road
Point of correction Mr Writer. Anati mwaiu ukhala wa mma city anai, osati Blantyre yokha.
legacy, Bingu’s vision. nice work better you fullfil your gurantees Mr President
we need to eat b4 moving. palibe cha nzeru apa.
Bravo APM
Kodi athu akumudzi akwanitsa kugula fetelizer pamtengo wa k32500 thumba limodzi.
They have left to help people to control the hungry but is waist money for nothing
Term yonse ithera campaign
Paja mwati misonkho mupangila miseu siyazungu kapena athu akuda Koma albino
Ok
Kod mkuluyu lilongwe amamuiwala et……..fumbi lili ntown lonseli
nanga sugar wopanga pa Dwangwa
nanga sugar wopanga pa Dwangwa
ife tikufuna mbewa bwana
guys pali chifukwa choti munenere munthu apapa zolakwika tsutsan komaso zabwibo yamikilani kodi tikamat chitikuko timanena chakudya chokha?I thot wina aliyese kut akafike kumwe amapezela ndalama zake ku tchito o business mesa ayenela kudusa museu so munthu wabweresa miseu ya tala fo easy n fast transportation for ur gudz walakwisaso? ??Malawians Malawians Malawians moyo uwu suzatithandiza Mpaka kalekale instead tizingosaukilasaikilabe
Thats a joke right? Can some1 pliz tell me what this man has achieve so far?
This President is not fit even to be a village headman.
Ife pano sitikufuna misewu Koma fertilizer subsidy
Its suprising to see how pple fail to understand the agenda of a meeting. Some meetings have a specific agenda e.g when the tour is for road inspection, do we expect to be told about maize? Government has more pressing issues and all cannot stop bcoz of one. Yes, food is very important now and has been spoken about over and over again. We have been assured that nobody is gonna die bcoz of hunger so many times. I wud rather want action than hear the prezident talk all the time. Lets be objective and try to understand issues in broad sense.
NTCHITO YA UTSOGOLELI ANTHU AMBILI SIMUIDZA. IWO AMATI DPP M’THETSA NJALA LELO NJALA NDI IMENEYI NDIKUMAWAUZA WANTHU MUDZIDYA ZIWALA NDI MBEWA PALI MZELU??? AKATI KUDYETSA WANTHU M’DZIKO SIKUWAPATSA ANTHU CHAKUDYA CHAULELE CHOKHA AI. BOMA LIYENELA KUGULULA CHAKUDYA CHAMBILI KUNJA CHIMANGA CHIPEZE MMISIKA YA BOMA CHIKHALE NDINTENGO UMODZI OKHAZIKILA OSATI CHIMANGA CHIPEZEKE NDI MA VENDER BOMA LILIPO AI. ~~~~~~~~~~~~~~~~~~~~ NDIYE MUNTHU AKAMADANDAULA ZA NJALA WENA MUMANGOGANIZA KUTI ANTHU AULESI AMADALILA BOMA ANTHU SAKUDANDAULA DZAULELE KOMA BOMA LIPANGE KANTHU KUITANITSA CHAKUDYA CHOWAGULITSA WANTHU MMISIKA YAKE.
Amalawi chenjerani,bodza ili sidzatha palibe chimene chikusintha pa Malawi.President akamaliza term lake adzasowa kukadya ndalama ku maiko akunja moti anthu amenewa akapempha ndalama ku maiko akunja amasiya ku acct lake,ena ndi aja asowetsa ndege ali kuti pano.
In your dreams
Pple should work hard in industries where they are in order to find their own basic needs.Your president won’t help you .Tt’s his time to cheat pple abaut developement of some areas of acountry while he is putting more money into his pokect.You and me starving outside there!.
Good move Mr president. Inu kuberekana ngati makoswe nkumati boma Iizatidyesela ana.mkapeza ka K 500 wakumowa anzanu Ali yakaliyakali.bola amene adayesa yavuta ndi mvula pepani.koma enanu ndima daily complainers.
Njala ndichinthu chchitika nthwi ndi nthawi,mseu 4 ever.Njala sichitukuko ,tiwona mmene tipangire nkhani yanjala kwinaku chitukuko chikuyendà monga miseu ndi zina :Ine Mneneri woyima pandekha waboma loramula.Zikomi.
Bamagula meno inshi kumalawi kulibe iwe kaili
Anthu azyenda misewumo ali nd njala?
Amalaw tikulimbana nd piter kut satithandiza kod azitiyendela makomo mwathu kumatipasa ndalama
We are hungry we don’t need roads now
Maize in Admarcs sheeee
Tidya misewu tikufuna nsima
Thanks mr president but hw far is the road of thyolo makwasa thekerani road its long i never hear anything since bingu left the mission
Mmmh maboza basi akukanika kukhomza msewu wa chingeni-zomba mseu ofunika kwambiri
misewu yachani malo molimbana ndijara yavuta kuno ku màlawi
Wow! Ix dat all abt,gud story, Xo wat next??
Mr. President, I thnk dat is gud decission, coz Malawi is luks like its not a cntry own its whn we see our poor roads. But am urging with u just becoz u cnt solve dat prblm while we got a critical stuation in de cntry like hunger. Mr prsident try 2 tackle dis situation 1st. And Mr president, things are high in our cntry cnt u fnd da way to reduce dis prblm. We knw its hard 2 tackle with bt, as u’r a leader of da national u cn find loophole, 2 stablelise da situation. Luk da poor r getting poor and poor, it doesn’t mean dat de cnt change life but things are going worse each and evry time which drag down their efforts. Luk Malawi is very gud cntry 2 live as we got fertile land and the citizens are wrk harders, but the our leaders, ‘r da ones who make da cntry 2 be like Hell 2 live. Just take a luk, becoz of da road, Pulezident mpaka kupita yekha kukawauza anthu. Zosenzo chifukwa choti zinthuzo sizimachitikachitika ndiye yakhala ngati label kwa iye. Mayiko azathu sizimachitika ngati zimenezo komaso president sangakwanitse kumakawauza zimenezo coz museu imakhala kuti ikumangidwa everyday. SORRY MY MOTHERLAND
KUNKHOTAKOTA NAKOSO MISEU IPEZEKEKO ABALE PLZ KKKKKKKKKKKKKKK
Anzake anali pompo. Sanakwanise lonjezo lao usati pake manyi
Palizina akulakul tienela kumanvachisoni ndidzikolathu.ngati kulinjala tikuenekakuimitsa zina kuti tisove vutolanjala miseu bingu anakonza apeter sanakulile kumalawiawa sakudziwa chilichonse chammalawi.ganizilani wanthu osauka mukulanhula zotumbwa chifukwa mukugwila timaganyu tama 5, 000 kuyambakutukwana osauka.mudzafachoncho mulibekanthu.
I hate you mutharika
Sopano iwe ediot umafuna kuti kusakhale nseu okongola iwetu ndiwe munthu ovuya maganizo wanva
bwana dzanjala mukuti nazo bwanji
tidye makoswe basi amalawi
Thanks mr President
Tamva mwanena zija Mr President kt tizidya mbewa ndi uzuu dzikomo mulungu atidyetsa ndife ana ake for ever no election
zaziiiiiiiii!!! malo mopeza njira zothesera mavuto ajara m’ziko bas .
Ndikutha kuona miseu ya makono kwathu ku Mw maka ku btz kkkkkkkkk
Zitete ndi mbewa kenako more roads in Blantyre. Nanunso mwakodwa ndi nkhani yopanda pakeyi. Mudzavotenso 2019 anthu opanda nzeru ngati inu a Malawi sinawonepo ai.
Wy a only blantyre? Wat about lilongwe? Mzuzu when? May God help us and hav mercy on his people
Ndiye za njala mukuti nazo bwanji bwana nanga???
Zikuwoneka kuti mwa anthu ena apapa simakhala mudzi muno mudakagwira ma ganyu ndi mapakistani ku jozi yogulitsa zama 4n koma mudzabwela ndithu.
Keep up! good job sir.
nanga ma kansala ntchito yao ndi yotani? zoona ndalama zambirimbiri kuonongeka chifukwa chokayendera misewu? ( feeder roads ) Anzathu apatu umunthu sukuoneka chifukwa ndalama zimene boma lamawononga pa m’bikiti wapulezident zimakhala zambiri zedi moti mbali ina zikhoza kuthandiza anthu kumbali ya chakudya kusiyana ndi kumapha mbewa ndi ziwala kuti anthu azidya kuti njala ichepe. Ndikudziwa kuti boma iri ndi lachikuko koma chonde a president azikhala ndi ntchito zoyendera, (kukaona) zinazi makansala akhoza kugwira, kodi kapena zinazi mukuchitira dala ndi cholinga choti ndalama zizingoonekabe anzathu akunja aziona kulephera kwathu?
azidya misewu yomweyotu aaaa pitala ndakaika za 2019
http://mypipcoins.com/[email protected]
Idiot
Where did this farm man come from?
Koma yah mmalawi sazatheka,kod paja zoti uzadya thukuta lako zinalembedwa buku liti?ndikanakonda tikanawerengera limodzi km nanga tikumana bwanji.komabe ena zongowerenga samazinvetsabe ndye tiyeni tilimbikire zomwe zingatithandize osati kutaya nthawi ndi anthu oti satipatsa or loboola khobili.
Bwanawo achita bwino akatelo kunotu ku juberg kuli miseu yopangisa chidwi
Thax
Anthu akungofa Ku BT koma anyapitala mahala yamala imwe sibweni
PALI ENA AMENE MUMALANKHULA ZAMBA MMALO MOLANKHULA ZA UMUNTHU. ANTHU AKAKOLOLA CHIMANGA ANDALE OMWEWA AMACHITILA CAMPEN MPAKA KUIKA CHIMANGA PA SALU ZA CHIPANI. KUKAKHALA NKHALA KUMAWAUZA WANTHU INE NDIMAGWETSA MVULA??? KUTITOLA UTSILU.
J
High way not single lane.Kodi mukamayenda maiko anzanu mulibe manyazi
Thumb up Mr President……step by step here we go as a nation
Tizikadya talayemweyo
Amene muli ndi njala mmakwanu, yesetsani muzilima. President sagawa Chimanga. Zitsiru.
Kulima timalima koma ngati mvula sinagwe bho president ayenera kuchitapo kanthu bakha iwe people have got money no maize whr a we going to buy futsek wena uyahlanya kanti
If u got money come up north to buy, u mean every year a kongoresi muzingolira njala. Ingofani
Why insulting if u want to raise a better point. What u are talking is kak now. They is aid which came in due to hunger. And that money is diverted to roads and other social development. Think b4 u write. This president is using poor pple to beg funds 4rm donor they misuse it. That why other donors stopped helping. Watch sky news not Malawi 24
Do u have evidence?so u mean Gvt with the taxes we pay can’t manage a road. Check with ur local admarc, how much maize has been bought with that money u r saying. We can’t stop developing the country because of perennial hungry families. Ulesi too much. Mayi uja anapundura anthu kwambiri
I concur wit u Prince , a Malawi amzanga chakudya sinsima yokha lets change our mind set.
Mr president I won’t be happy with you this year to starve with hunger while I have money in my pocket, what are you doing about maize?
How many roads have been constructed since he began promises? I wonder how politicians look into it keeping malawians full of inept promises bt no succes. And what makes us the citizens clapping hands for something we know wont happen. I wish our president would have a daily diary for the promices he makes to the country and thumbs up or down where full filled and where not.
Tizidya misewu????? Sangaone kuti tili pamavuto achakudya……..#malawia…..ndichani????
Zikomo masende mtharika
Anayamba wadyapo ndi kukhuta mbewazo?????,,,,,zitete,,,,, munthu uyu iiii ayi satithandiza!!!!
People dont need roads at this time around instead you must order more maize so that people would not starve mr president
Nanhala collns its not me koma headline ikuti chani
azidya. tala paja
Stupid! Why not 4the whole malawi?
People have enadquate food mr president
tizikayenda mmisewumo tisanadye? nanga mbewazo tizingokhwasula opanda nsima? za ziiiii !!!!!!!
Bola akananena za chimanga2 kkkk koma ziliko
mukamangokha manja lende kuleka kulima ndikugwira ntchito molimbika mumayembekeza kuti azikudyetsa ndi Peter….musiyeni akwanilitse zomwe analonjeza mwaufulu….mukati aganize za mimba zanu amagwetsa mvula ndi iyeyo?
Iwe kuli anthu akuvutika ndinjala
tikunena anthu omwe ali homeless
anthu okalamba inde ena mwayiwo ngamasiye. ..iwe nsewu ndikudya chabwino nchani. .? watopa ndimaperiod’ye
awuze….alankhula ngat mwanatu
Zoona anthu angatafune tala?
Mwana wa hule idiot
Amayi deborah paja muli kuwu unduna wutiwo kwathu kuno mpaka kulankhula choncho zikuyenda.
Choncho
Choncho
chonsecho pa kwawo pali mbuuu ndichisonokho chomwe palibe cha chimanga hahahahs
vuto la anthu osutsa boma simuona zosutsa….amene ali ndi njala adye talayo kumene…mumati azikudyetsani ndani…amene timalimbika kugwira ntchitofe tilibe pulobulemu
kaya ukudziti Ramzey…hule ndi amako ndichifukwa ukulira ndi njala kusowa mtengo ogwira sananga anapita kuuhule kukusakula chakudya kuuhule….inetu ndakhuta pano mawanso ndidya chimodzimodzi
Ine iwe mpaka nditakulemba ntchito you yoyeza ntchigayo changa ndithu bitch
Mulungu amapatsa olimbika sikadza kokha kaopa kulaula……olimbika sitikuona vuto komanso vuto la anthu osowa dzokwelanu simukudziwa ubwino wa misewu
chigayo chake chojambula pa pepala…..musavutike timalima ndipo timakolola…timatumikila Mulungu wa moyo
Ndikadati Ndiwe Mbuz!
Koma nde kumuikira kumbuyo mfumu wanuyi…mbuzi yama president togetha with his frnd mgabe.
Nkhope dzina ndi zokonda kufanana nde ndi prezident wanu wankhope ngati bwampiniyu pa kwanu mumamutcha nda? ??….D PP is an average party mayiko opepusa
mungozivuta kumayankhula chifukwa sasintha maganizo ndikukubweletserani chithandizo anthu ozolowela kudya zolandilanu…..ndipo ife tikumva kukoma ndi tala wathu yemwe ataikila tawanyadila kwabasi uncle Peter
kkkkk koma abale…musananyoze nkhope za amzanu muziyamba kaye mwafunsa athu odutsana nao kuti yanu ndiyotani? Chifukwa mukafunsa a chibale akunamizani inunso ndi nkhope yanu ngati kuphazi yo mungakhale ndi mphamvu yonyodza nkhope ya mzanu?
Pamtumbo pako! Ulimmalawi muno koma galu iwe??
Isaacs ngati amako alibe ndiopunduka…ndichifukwa anabala chitsiru ngati iwe…mbuzi ya munthu kuzolowera kunyengana ndi amako ndiye umapaonaona ndichifukwa ukupatchula….pali chifukwa chotchulira maphuzo apa umbuli ndiumene ukukupangitsa…chifukwa aliyense ali ndi ufulu opeleka maganizo ake ndye iwe kavuchete ngati iwe ukuti chani?
Derbora asiye alibe chochita amenewo ayamba kukulakwisa, azazindikira bwino pasogolo.
Stupid president
kkkkk mpaka mbewa ndi ma grasshopper kkkk uyu sakusiyana nfi hitler ndithu
chitute uyu akut chan apa
hahaha
Wlcm mr president
Bola akananena kuti “more roads, ADMARC deports & enough maize coming.
…. Ayi,,,, chitukuko chimakoma ndi njala…..
Not roads,but humps & patchs ishiiiiii Malawi yose bwana mukutionongera magarimoto……!!!!!!.
Kambuku wachabe chabe uyu mbudzi yamunthu galu watha ntchito. ..tell him to bring mice and grasshoppers instead of those roads
…. Kuti chimangacho chiziyenda mosavuta etiiiii……?
We need new infrastructures in Blantyre
Osamagotukula ku Lilongwe ayi
You pipo if you go to pairament you mean to say that youre just discusing about road networks how can road help pipo while they are staven?
Tell him that we are waiting for these infrastructures: Stadium, Peter international conference Centre PICC, 5 Star Hotel, by pass Roads and irrigation systems in lower shire.
Nanuso inu mungayende mumisewo muli ndinjala? Chofunika anthu akhute kaye ndiye zinazo pambuyo.
Malawi24 Ndiya Boza Post Ina Anenakuti Chaka Chino Kulibe 6 July Koma Zodiak Online Anenakuti Iliko Aaaaaaa Ma Page Enawa Kaya Osathamangira Ku Panga Post
Only good news for blantyre pipo, what about entire Malawians excluding blantyre shame
mmmm man lets be honest ku north zikuchitikaso
Gud decision,,pro Peter
Inu ndinu opusa
Akanati wayankhula kuti azigawa chimanga bwezi tikuyankhulaso zamwano, kodi dziko lilephele kupanga zitukuko zina chifukwa kuli njala?
Koma iweyo siutamba? hw can you work if u r nt strong? strength comes from food
Bro chitukuko chadziko chikamabwela mbali ina imakhala ikufooka,, ndiye mukuganiza kuti dziko lathu njala izatha liti?
President amapereka chimanga? Muzilima mwanva
Munthu uyu sanalakwe ,ndizoona president ofunika anthane ndi njala
Koma anthu angwira ntchito ndi njala mwaganiza bwanji tafufuzani kaye muliko ngati zimatheka.
Penatu tizithaso kuona mbali zose, chitukuko chimmakhala ndi ndalama zake za padela, mavuto ogwa mwazizi amakhalaso ndi ndalama yapedela, tafufuzani kuti kodi bageti yathu imapangidwa motani,,
Ngati atafooke anthu ndi kufa chitukuko anyadire ndani????,,, zonse ndizofunika koma atsogoleri aziti zikadyani makoswe ndi aphananawo,,,,, musavutitse ine as njala yanuyo!!!!,,,, palibe nzeru APA!!!,,abweretsa njala ndi atsogoleri omwewa mdziko!!
Hah Misewu yache yopita kuti ambwiye…..!! Isi……!! Am all eyez..
Njala kuno bwana
People are about to eat mice and grasshopper, handle the stomach first sir!
kkkk that’s point
Akuti kukhonza misewu, kuyika ma patch, mabampu iyi kwa iye ndi development, ena amapanga misewu yamakono,
Zero pa hundred!!
I like President Mutharika, his eyes sees far things, he is instituting this project because he knows that it is only two handful years before 2019. I think this is one of his campaigns—-cub reporter
Ngati ali dolo ayambe kumanga misewu yamwamba in our city’s.
zachamba akalime kundatako
Chipitala,,,,,,ichi
abantu alalye misewu?
akagwere uko, akuganiza kuti tidzidya misewu ife..
Roads,not food as ppl are hungry