Renowned actor and comedian Eric Mabedi popularly known as Jakobo has called on Malawians to desist from rumour mongering days a death hoax about his longtime John Nyanga populary known as Izeki hit the social media lately.
Mabedi called on Malawians to verify information before posting on social media.
“I remember last year when he was also admitted, people were all over the social media saying that he is dead. This time is the same, I have received many phone calls and up-to-date, the phones are still coming,” said Mabedi.
Mabedi has disclosed that Izeki was admitted at Queens Elizabeth Central Hospital in Blantyre on Monday.
“He was in the Intensive Care Unit but now he is in ward 3B. His condition has slightly improved,” said Mabedi yesterday afternoon.
He further asked online publications to always verify their stories.
“Let me also call upon some online platforms who take up the leading role of posting information without verification to always verify,” said Mabedi who is the Director of Kwathu Drama Group.
Kkkkkk kkkkkk tsono iwe ndioweluza milandu?ngati wafuna kufa musiyeni afe basi wadyelera kokwana,mwina tizionako 4th_generations monga kado ndi Mr jokes,paja nonse mukuchokera kwa anyamata oyenda ndi mipeni mkathumba(kadyeke)
Plz let love lead!!What kind of joke is this.
amalawi tiziwopa mulungu,
Jesus name Amen
Malume anthu amenewa akumalemba zopusawa kugowaloza basi
Malume anthu amenewa akumalemba zopusawa kugowaloza basi
,ine ponva kuti izeki wamwalila kuena zoona zinandiwawa kwambili ndipo Sindinatskiminze koma kufusa kwa ena omwe Ali BT koma umboni omwe anandipasa ndinali ndi chikhulupilo kuti ambuye ayikapo nzanga ndipo ndingoti zikomo ponziwa choonadi ambuye akuonjezeleni pomwe mulipo ofunila zoipayo manyazi kwa iye ndingoti zikomo pephelo kwa izeki ambuye ndikukupephani kagwileni nzanga izeki aka the kupeza bwino inde ndinziwa pomwe pali chabwino Samara amakhalaso pompo kufuna kusokonensa koma inu nokha ndinu ammene m ukunziwa choonadi ndipo ambuye mukakhale naye izeki pomwe akunzuka mmawa aka the kupeza bwino ndikafika APA ndingoti zikomo

May the lord remember his son john nyang.,and heal completely in Jesus name.
May the lord remember his son john nyang.,and heal completely in Jesus name.
May the lord remember his son john nyang.,and heal completely in Jesus name.
What’s wrong with John nyanga wathu?
What’s wrong with John nyanga wathu?
anthu ena mumalakhula motumbwa apa uzimu waumunthu mulibe go 2 hell kod Ali mai ako or bambo ako or mwana wako or mkaz wako or mamuna wako or wekha ungaulule kt HIV postiv? ?????? ambuye akukhudzen kuthup ndi muzimu momwe
anthu ena mumalakhula motumbwa apa uzimu waumunthu mulibe go 2 hell kod Ali mai ako or bambo ako or mwana wako or mkaz wako or mamuna wako or wekha ungaulule kt HIV postiv? ?????? ambuye akukhudzen kuthup ndi muzimu
Masalmo ananena kale wokumbira nzake dzenje alowemo yekha,,,,,
Masalmo ananena kale wokumbira nzake dzenje alowemo yekha,,,,,
Zisirudi zamalawi
Zisirudi zamalawi
Kodi amalafe bwanji ndi umbuli kapena kuchenjera mopusa ? Nchifukwa chani munthu otchuka akadwala mumapeza zokamba instead of kuti mulembe pa fb kuti abale akufuna kwabwino tiyeni timupemphelere nzathu sali bwino koma inu dairy wakuti ndi wasatanic wakuti watisiya, mumapindulanji? Let’s wake up Malawians love each other no body knows about tomorrow its only god,we are alive in God’s mercy, I WISH U ALL THE BEST MR JOHN, GET WELL SOON .
God right hand is on your chest.u will be healled soon
God right hand is on your chest.u will be healled soon
God right hand is on your chest.u will be healled soon
Dzulo wina watumiza ixi kumatiwatisiya ndiye tive zitichondo
Dzulo wina watumiza ixi kumatiwatisiya ndiye tive zitichondo
Guys pls l don’t understand what going on pls
Guys pls l don’t understand what going on pls
In jesus name amen
koma inu sanamwaliredi????? winawake kuchita kulemba kuti brother tikusowani ….ine kufunsa akuti eya ndi malume anga amwalira usiku maliro akupita kumudzi mawa……koma athu abale
A Malawi ndife osowa chikondi panzathu ndipo ena samamvetsa thathauzo loti munthu wagonekedwa kuchipata amakuuza zina zamutu mwao akudziwa mix matama kwambiri ngati iwo ndi amuyaya get well soon #John_Nyanga
kusanduka kokhakokha anthu okonda kudya maliro amasangalala ndi imfa,mufa ndinu odwala alipheeee ,stupid pipo
Get well soon, we have missed u in action.
amalawi usilu umeneu mmaukonda ofcoz nane ndi mmalawi koma amene mmakonda kumwalilitsa anzanu inu kamoyo kanuko mukut mwasunga mmakhala mukuganiza bwa?musiye ndi mchitidwe opusa umeneu…u think death is simple?!
Upole bwangu izeki
Eish amalawi,ndimaona ngati ndizoonadi
Moyn Ndi Wa Chauta,get Well Brother
guys tidziopa mulungu izek watisangala zaka zambiri.tikumufunira imfa chifukwa chani.sherm on u.
Eeeeeee NDE akuthatu iiiiiiii
Eeeeeee NDE akuthatu iiiiiiii
Amalaw mwatani kodi????
Amalaw mwatani kodi????
bola iye ndi Born-again’tu…kumwalira lero akalowa ku moyo wosatha,nanga iweyo ulipat?
bola iye ndi Born-again’tu…kumwalira lero akalowa ku moyo wosatha,nanga iweyo ulipat?
This Is Atragidy Rumour. Whats Wrong With You People?
Kudwala sikufa amalawi tizikondana
Amfiti opemphera amenewa
Is not good
Ndimoyo wazibwana kwambiri okhalira kudikilira kumati kodi wamwalira lero mwa anthu otchukawa ndindani, i must be on top one kulengeza on social medias. Kusafunilana zabwino kumeneko kumationetsanso anthufe kuti mzeru ndi chikondi zikutisowekela. Tikudikilani inu mukadzamwalira mudzatidziwitse nokha kuti mwamwalira,,,,, chifukwa yomatidziwitsa za ena nde mukuitha.
Am praying Izeki to get well soon
Okufa sadziwika ndipo kumanda kulibe khuto mulingo umene ungamuyedzele zako mawa ndiwako
Wakufa sadziwika
Amalawi iiiiii simuzatheka basi maboza eeeiiish tiyeni timfunile nzathu kuchira kwansanga
Mulungu amuptse moyo wa utali.
All men die
I wish Izeki a speedy recovery for more dramas
“Amalawi , moyo umene tikuchitawu siwabwino.
Get well soon brother
Kuchila kwa msanga Izeki! we love you body!
Okumbila mmbuna nzake,amagwelamo yekha,kodi sunawelenge iwe????? okufa samadziwika,kuli ngozi,zivomelezi,kudya poison mwa mistake etc ndiye think twice befole you talk,our life is in the hands of God
This is true we don’t know who’s gonna die.
This is true we don’t know who’s gonna die.
This is true we don’t know who’s gonna die.
Okufa sadziwika. Nowadays we can witness deaths of those people who never knew what it means to be sick. But in a brink of the eye, they die.
LONG LIFE TO OUR DEAR BROTHER!!!!!

get well soon!!
get well soon!!
Gyz let’s love one another, don’t be heartless
Gyz let’s love one another, don’t be heartless
Gyz let’s love one another, don’t be heartless
who dnt no who iz going to die. pofera salambula. ife tmankonda kma that time adzakhal kut mulung wamukondetsetsa.
Guys m’mbuyomu ndinamvapo za kudwala kwa mkuluwina ogwira ntchito ku radio/tv koma boma linapereka thandizo kumutumiza chippatala chakunja mpaka anachira but why not this comedian plz plz plz chitanipo kanthu musamadikire agone.
Khati wafa ause mutendele!!
Thanks
Upita kuli chete ndiiwe bigyo yakana
Amen
zimapepuka zkakhala kwa wina.i wish hm well,GOD z great.
kodi aMalawi tinatani kukonda kumwalinsa anzathu akatu sikoyamba kumumwalirinsa muthuyu koma choti tiziwe ma plan amuthu simaplan amulungu ayi.tatiyeni tinkhale okondana ndikufunirana zabwino coz siku la kufa siliziwika.
Wish u quick recovery,,,,,stay blessed izeki
Anganga get well soon.
wishing u aquick recovery
wellwishers can you send him abroad please
Ndikuwafunira zabwino zones komanso kuchira kwasanga,moyo ndiofunika kwamunthu wina aliyense,sibwino kulemba nkhani zili zaboza ayi kutheka inu mukumufunira imfa muzamwalira ndinuyo iyeyu akadali moyo,
Wishing you good health.
ukamafuna kuti mzako achosedwe pa ntchito ndimeneumanva kuti wakwezedwa. akuluwaalipo mpaka ambuye azawaitana osati woipawe zikomo
You never know who will die soon,kwambiri anthu inu odziwona ngati alungalunganu ndi opemphera(kwa masiku anoku).You think ndinu oyeretsedwa,go to your nearby hospital and check,you will realise real life & that those who are dying are not all HIV+ve.Opanda chikumbumtima,eeesh! Lets have & show some moral pliz.
Nwadays pipo dnt think of others,
Nwadays pipo dnt think of others,
Nwadays pipo dnt think of others,
nde poti amafa ndi wosadwala mukungompa tsa moyo wautali munthuyu
Y do u hate this man so much get a life pls stop this nosense
Malawi pipo…frustrated pipo….
amalawi kupepela kaya munatengela ndani penapake kumaganiza muli inu mzanu akudwala inu mkumatchukisa kuti wamwalila moyo oyipatu umunewo muziziganizila muli uni umbuli suzakuthelani muzingokhala ovutika choncho I wsh izek qeak recovery and my God be with him timakukonda koposa
Koma atisiya eti?
Very sad
Get well soon isaac
Get wellsoon Zecks,wishing u good health n quik recovery in Jesus name.
may god do sam thing on izeki body
Mwaphakale mukale sachedwa kumbukilani mhone zinaliso chomwechi sanachedwe.
Kuli anthu opanda chikondi shame on you gayz muziganizile nokha pazomwe mwachita shame…….
Nde malawians amenewo, ther r best liars eva
get well soon Mr Nyanga. Trust in the Lord for he is always with you. Amen
mayendawa amukakamila ezeki kodi mankhwala samamwa? penapake vuto ndife amalawi munthu ali ndi HIV mmalo monena chilungamo timapita mmbali. sindiyambe nditamvapo kumalilo kuti pamalilo kuti mzathuyu wapita ndi Edzi pamene mbiri ikuti Edzi ikutha anthu
Or Muli Inu Mungakonde Anthu Azikutchulan Wa Edzi Iwe Mungamve Bwanji? & Wakuuzan Ndan Kut Iyeo Alinayo?
Adzayamba kuulula paiwe
shut up
sindikuyankhani koma mthupi last Izeki mulizilombo sizobisaizi
sindikuyankhani koma mthupi last Izeki mulizilombo sizobisaizi
kuyankhula mopusa!
kuyankhula mopusa!
inu ndachitsiru kodi et?
inu ndachitsiru kodi et?
Samara poti mawa ndiwe
Samara poti mawa ndiwe
kkkkkkkkkk man rich
sikuti ndikumuseka, ndikumuseka.ndimatenda inenso atha kundipeza ndipo sindikuopa koma zimakhala bwino kumamasuka cos ma Celebrity ngati Izeki ayenela kukhala olimba mitima kumaulula cos itha kukhala campaign yabwino. Sindikunyoza mundimvetse amalawi anzanga cos ndaona mukundipysela mitima kundinyoza simmene mukuganizila cos ngakhale in you know kuti natenda ndiamenewa koma kubusabisa penapake kumanena chilungamo
Munthu was Edzi akaulula kuti alindikachilombo amakhala ndinkhawa zochepa pamene ukamabisa mapeto ake ndiizo moti Izeki nkhawa zamupweteka tsono musanditenge ngati munthu wamisala I know chimene ndikunena am a normal person ngakhale inuyo anzanga mukapezeka nao subwino kubisa. apa zikuonetsa kuti Izeki sakumwa mankhwala cos olo inu mundivomeleza kuti masiku ano zomazubzika ndi AIDS monga Izeki ndimboriyakale
zikugwilzana?
iwe ulinao bwanji ukubisa mot uyambe iweyo kuululako
Ukufuna kunena kuti chani? Iwe ndi wamuyaya?
Zinazi ndibwino osamangokomenta nawo kumangoyang anako, nanga nkhaniyi ndi za edzi zikugwirizana? Mind ur bussness
ndikufunira kuchira kwabwino kochokera kwa mulungu akhuze nthupi lake kuti woyipa chite manyazi amen
Mmmmmmm shem
Apo nde ndikunva noo sopano otsat makape kumaremba pa fb kut wavaya
True
We wısh you quıck recovery.To my fellow Malawıans let love each other.Don’t wısh a bad luck to your frıend please Manyasa ımwe mbwe nkhanı nkhutınkhana waka nawanyınu mukuphındulapo vıchı when you hate your frıend.I beg your once agaın Don’t wıch your frıend a bad luck.
But he’s almost neh
Das bad story wina kumasangalara ndi kuchukisa kuti wakuti wakuti wamwalira zimenezi zikuchilukira bwanji amalawi azanga kumakhara kusowa chikondi mutima chan don’t take life eazy
Get well soon
Nthawi zonse amalawi sitimafunilana zabwino,tinakhala bwanji?tiyeni tizikondana.nkhani yamaliro siyamasewela.kodi inu ndiye ambeu?In u mukamatsogoza anzanu akupuma inu mudzanka kuti?
To brother, the more they are casing you the more life you are getting God heal your pains now in Jesus name

Tikufunila kuchira mwansanga Izeki,palibeso amene amatisangalasa pamalawi oposa iwe.
Tikufunila kuchira mwansanga Izeki,palibeso amene amatisangalasa pamalawi oposa iwe.
Tikufunila kuchira mwansanga Izeki,palibeso amene amatisangalasa pamalawi oposa iwe.
Mukayambe mwawaduwitsa achagogo anu kae b4 uyu wankulu uyu
Mukayambe mwawaduwitsa achagogo anu kae b4 uyu wankulu uyu
Mukayambe mwawaduwitsa achagogo anu kae b4 uyu wankulu uyu
Malawi woyeeee dziko ndi anthu ake
Malawi woyeeee dziko ndi anthu ake
Malawi woyeeee dziko ndi anthu ake
MULUNGU AMUSANJIKE DZANJA NDIKUMPATSA MASIKU OCHULUKA KUTI SATANAYO ACHITE MANYANZI. ~~~~~~~~~~~~~~~~~~~~ ABALE KUDWALA SIKUFA TIDZIKHALA NDI MOYO OKONDANA. NDICHIFUKWA CHACHE SANAKUPATSENI MPHAMVU ZAKUPELEKA MOYO.

Mulungu muchilisen zexy kut woyipa ayaluka ndinu mulungu wamphavu munazusa akufa ambuye khalan naye lzek kut achile musanga muzina la mwana wanu yesu AMEN

Anthu oipa
Anthu oipa
Anthu oipa
Amalawi mutani mabonza basi
Amalawi mutani mabonza basi
mulungu yekha ndiye aziwabasi
mulungu yekha ndiye aziwabasi
mulungu yekha ndiye aziwabasi
Long live man of God
Long live man of God
Long live man of God
Mutafe ndiinu, mukulemba nkhani zabodzanu… Mahule achimunanu, iyeyo ali pheee…..
Mutafe ndiinu, mukulemba nkhani zabodzanu… Mahule achimunanu, iyeyo ali pheee…..
Mutafe ndiinu, mukulemba nkhani zabodzanu… Mahule achimunanu, iyeyo ali pheee…..
wakufa sadziwika big man ananena okha kamba ka faz imene simafunila xabwino get well soon nebar
wakufa sadziwika big man ananena okha kamba ka faz imene simafunila xabwino get well soon nebar
wakufa sadziwika big man ananena okha kamba ka faz imene simafunila xabwino get well soon nebar
unfair tendency…..lets have diligence
unfair tendency…..lets have diligence
unfair tendency…..lets have diligence
Mulungu okondeka amuonjezera zaka zina. Long live. Mr
Mulungu okondeka amuonjezera zaka zina. Long live. Mr
Mulungu okondeka amuonjezera zaka zina. Long live. Mr
Izeki ndi munthu ofunika ku mtundu wa amalawi tonse timpemphelere
Izeki ndi munthu ofunika ku mtundu wa amalawi tonse timpemphelere
Izeki ndi munthu ofunika ku mtundu wa amalawi tonse timpemphelere
Moyo wanga unaasweka nditamva ngakhale sinzanga simbale wanga iye sakundiziwanso ndipo sakuziwanso kuti ndiliko koma a malawi sitizatukukadi ndintima wopusa wansanje wopanda nzelu anthu oti ofunika pachitukuko chadziko lathu lino kusintha myoyo ya anthu koma osayamika ngati ndimawudani konko kwa ena ndiwofunika chitsilu chili ndimwini long live mabedi shame to the mediocrity
Mmmmmm Chonde Amalawi Tatieni Tikondana , & ndikumbuse ntundu Wa Malawi kuti imfa sizoloweleka komanso sichinthu choti nkingolankhula ngati mukukamba zakumpila , ndipo ndikumbuseso kwamene anakhala pansi nkumalemba nkhani yoti I saac wamwalila kuti imfa sinzathu ndipo simasankha sibwino kummampasa malile nzanu mukufuna kuseleula seleulani zina koma nkhani yokha ya imfa usamale nawo, komansotu palibe amene azalumphe dzenje LA manda tele usazimve Sugar iweyo amene unapanga post zinthu zosakhala bwino we , ngati zolemba mulibe chonde chonde zisungileni Ulemu kungosiya osati muonekelepo kupepela kwanu Mulungu tu, amakonda wina aliyense ndipo ndiimene smaziwa kutisamala kwake.
God sees u bro
kumene kwatsala tchile ndikomwe ukupita moto muli inu mungamve bwanji m’bale wanu akuganizilidwa kuti wamwalira koma ali moyo
Nganga ndi kukufunirani kuchila mwa msanga, mupitilize kwa phunzitsa aMalawi get well Mr J Nyanga (Izeki) kowona odwala satenga satenga nkhata koma Duwa
Iyaaaaaa!!!! Iyaa!!!. Komatu Inu abale Inu?
Ufe ndi iwe
Anthu ndiwoyipa get wel soon
Kkkkkkkkkkkkkkkk
Heaven father will deal with that one who spread that long life im wishing to john nyanga
Ameneyo nde Malawi kukonda kusaongozana kumanda basi kufunilana zoipa nzomwe malawi amadziwa:dziwa ichi malawi palibew wa mbeu en wakufa sadziwika:zabwn zonse Izeki
Sibwinozomwe tichitaife Amalawi
A malawi24 yesterday you told us of death news and today you tell us that he is alive. First how is your journalism? 2nd how do you view a human being? 3rd how do you sensor the news you tell us? 4th do you know the people who read your articles. Don’t take us for granted. Not Long you will pay bcoz of your carelessness in reporting. Get well soon Izek. God is with you.
Akumupasa moyo wawutali.
Akumupasa moyo wawutali.
God! remember your servant, show him your mercy oh Lord! In Jesus name……
Asangotsekula m’mimba mwamutsogoza kale u pipo kkkkk
Chifundo makina i agree with your comment
Failing to think,,,humanity guys,,,pissed
Amalawi nchifukwa chiyani sitifunilana Zabwino maka munthu akangochuka ???! long life and quick recovery Mr Nyanga
Kulakwa abale nanga walakwa chani munthu kuti mumukankhire ku dzenje la imfa….
Long live prophet Z. Wakufa sadziwika, ankadziwa ndani.
God will jugde you for spread false story jacob alimoyo
Come guys.He deserves our love and respect.Get well soon.
wokumbira nzake mbuna azagwelamo yekha
wokumbira nzake mbuna azagwelamo yekha
Wakufa saziwika mwina ndi ine kapena ndi inu……
Wakufa saziwika mwina ndi ine kapena ndi inu……
Guyz please live this man alon
Guyz please live this man alon
Get well soon baba
Get well soon baba
may gud Lord add him 20 yrs more to live healthier & stronger.
may gud Lord add him 20 yrs more to live healthier & stronger.
Kukonda kulengeza za imfa ya anzanu inu yanu bwanji
Kukonda kulengeza za imfa ya anzanu inu yanu bwanji
Long live izeki umatidalitsa ndi phweteee
Long live izeki umatidalitsa ndi phweteee
Long live Bro
Long live Bro
Get well soon, Mr izeke.
Get well soon, Mr izeke.
kod m’bale wathuyu akudwala chiyan?ndikufunira kuchira kwamsanga
kod m’bale wathuyu akudwala chiyan?ndikufunira kuchira kwamsanga
Mmmmm….. Two bad Malawians
Live Long Mr “am The Road You Walk” God Continue Adding More Years To Your Existence!
Live Long Mr “am The Road You Walk” God Continue Adding More Years To Your Existence!
sibwino guys
sibwino guys
tikumufunila kuchila mwachangu
tikumufunila kuchila mwachangu
God knows get well
God knows get well
Long live
Long live
A Malawi ngafiti kaa
Amalawi sitidzatheka ndithu
Back fire,ufe ndiweyo munthu opanda phindu idiot.
Back fire,ufe ndiweyo munthu opanda phindu idiot.
Sibwino man mupemphelereni nzanu achire mwansanga
but even if pipo spread rumours that i have died, i cannot get worried at all. It can be my opportunity to surprize them.
but even if pipo spread rumours that i have died, i cannot get worried at all. It can be my opportunity to surprize them.
get well soon
get well soon
Dont worry John Nyanga okukumbira dzenje adzagweramo yekha
Dont worry John Nyanga okukumbira dzenje adzagweramo yekha
Eeeee koma Amalawiii..
Eeeee koma Amalawiii..
Amalawi anzanga tiyeni tikhale ndi chikondi, mzathu akadwala amasowekera chilimbikitso chathu osati kumuonjezera nkhawa or mantha, muganize muli inu. May the almighty God touch him body and soul IN JESUS NAME.

Get well Zex and continue your good work
Get well Zex and continue your good work
Long live
Long live
My favourite local comedian…live long izeki…
My favourite local comedian…live long izeki…
oh oh
oh oh
Anthu a Malawi sadzatheka
Anthu a Malawi sadzatheka
Long live Izeki
Long live Izeki
Lets Have Humanity As Malawians, Why Spreading Some False Issues? Lord Have Mercy On Us.
Lets Have Humanity As Malawians, Why Spreading Some False Issues? Lord Have Mercy On Us.