Izeki not dead! Malawians get cautioned on hoaxes

Izeki

Renowned actor and comedian Eric Mabedi popularly known as Jakobo has called on Malawians to desist from rumour mongering days a death hoax about his longtime John Nyanga populary known as Izeki hit the social media lately.

Mabedi called on Malawians to verify information before posting on social media.

Izeki
Izeki is not dead.

“I remember last year when he was also admitted, people were all over the social media saying that he is dead. This time is the same, I have received many phone calls and up-to-date, the phones are still coming,” said Mabedi.

Mabedi has disclosed that Izeki was admitted at Queens Elizabeth Central Hospital in Blantyre on Monday.

“He was in the Intensive Care Unit but now he is in ward 3B. His condition has slightly improved,” said Mabedi yesterday afternoon.

He further asked online publications to always verify their stories.

“Let me also call upon some online platforms who take up the leading role of posting information without verification to always verify,” said Mabedi who is the Director of Kwathu Drama Group.

Advertisement

259 Comments

 1. Kkkkkk kkkkkk tsono iwe ndioweluza milandu?ngati wafuna kufa musiyeni afe basi wadyelera kokwana,mwina tizionako 4th_generations monga kado ndi Mr jokes,paja nonse mukuchokera kwa anyamata oyenda ndi mipeni mkathumba(kadyeke)

 2. ,ine ponva kuti izeki wamwalila kuena zoona zinandiwawa kwambili ndipo Sindinatskiminze koma kufusa kwa ena omwe Ali BT koma umboni omwe anandipasa ndinali ndi chikhulupilo kuti ambuye ayikapo nzanga ndipo ndingoti zikomo ponziwa choonadi ambuye akuonjezeleni pomwe mulipo ofunila zoipayo manyazi kwa iye ndingoti zikomo pephelo kwa izeki ambuye ndikukupephani kagwileni nzanga izeki aka the kupeza bwino inde ndinziwa pomwe pali chabwino Samara amakhalaso pompo kufuna kusokonensa koma inu nokha ndinu ammene m ukunziwa choonadi ndipo ambuye mukakhale naye izeki pomwe akunzuka mmawa aka the kupeza bwino ndikafika APA ndingoti zikomo

 3. ,ine ponva kuti izeki wamwalila kuena zoona zinandiwawa kwambili ndipo Sindinatskiminze koma kufusa kwa ena omwe Ali BT koma umboni omwe anandipasa ndinali ndi chikhulupilo kuti ambuye ayikapo nzanga ndipo ndingoti zikomo ponziwa choonadi ambuye akuonjezeleni pomwe mulipo ofunila zoipayo manyazi kwa iye ndingoti zikomo pephelo kwa izeki ambuye ndikukupephani kagwileni nzanga izeki aka the kupeza bwino inde ndinziwa pomwe pali chabwino Samara amakhalaso pompo kufuna kusokonensa koma inu nokha ndinu ammene m ukunziwa choonadi ndipo ambuye mukakhale naye izeki pomwe akunzuka mmawa aka the kupeza bwino ndikafika APA ndingoti zikomo

 4. anthu ena mumalakhula motumbwa apa uzimu waumunthu mulibe go 2 hell kod Ali mai ako or bambo ako or mwana wako or mkaz wako or mamuna wako or wekha ungaulule kt HIV postiv? ?????? ambuye akukhudzen kuthup ndi muzimu momwe

 5. anthu ena mumalakhula motumbwa apa uzimu waumunthu mulibe go 2 hell kod Ali mai ako or bambo ako or mwana wako or mkaz wako or mamuna wako or wekha ungaulule kt HIV postiv? ?????? ambuye akukhudzen kuthup ndi muzimu

 6. Kodi amalafe bwanji ndi umbuli kapena kuchenjera mopusa ? Nchifukwa chani munthu otchuka akadwala mumapeza zokamba instead of kuti mulembe pa fb kuti abale akufuna kwabwino tiyeni timupemphelere nzathu sali bwino koma inu dairy wakuti ndi wasatanic wakuti watisiya, mumapindulanji? Let’s wake up Malawians love each other no body knows about tomorrow its only god,we are alive in God’s mercy, I WISH U ALL THE BEST MR JOHN, GET WELL SOON .

 7. koma inu sanamwaliredi????? winawake kuchita kulemba kuti brother tikusowani ….ine kufunsa akuti eya ndi malume anga amwalira usiku maliro akupita kumudzi mawa……koma athu abale

 8. A Malawi ndife osowa chikondi panzathu ndipo ena samamvetsa thathauzo loti munthu wagonekedwa kuchipata amakuuza zina zamutu mwao akudziwa mix matama kwambiri ngati iwo ndi amuyaya get well soon #John_Nyanga

 9. amalawi usilu umeneu mmaukonda ofcoz nane ndi mmalawi koma amene mmakonda kumwalilitsa anzanu inu kamoyo kanuko mukut mwasunga mmakhala mukuganiza bwa?musiye ndi mchitidwe opusa umeneu…u think death is simple?!

 10. Ndimoyo wazibwana kwambiri okhalira kudikilira kumati kodi wamwalira lero mwa anthu otchukawa ndindani, i must be on top one kulengeza on social medias. Kusafunilana zabwino kumeneko kumationetsanso anthufe kuti mzeru ndi chikondi zikutisowekela. Tikudikilani inu mukadzamwalira mudzatidziwitse nokha kuti mwamwalira,,,,, chifukwa yomatidziwitsa za ena nde mukuitha.

 11. Okumbila mmbuna nzake,amagwelamo yekha,kodi sunawelenge iwe????? okufa samadziwika,kuli ngozi,zivomelezi,kudya poison mwa mistake etc ndiye think twice befole you talk,our life is in the hands of God

 12. Guys m’mbuyomu ndinamvapo za kudwala kwa mkuluwina ogwira ntchito ku radio/tv koma boma linapereka thandizo kumutumiza chippatala chakunja mpaka anachira but why not this comedian plz plz plz chitanipo kanthu musamadikire agone.

 13. kodi aMalawi tinatani kukonda kumwalinsa anzathu akatu sikoyamba kumumwalirinsa muthuyu koma choti tiziwe ma plan amuthu simaplan amulungu ayi.tatiyeni tinkhale okondana ndikufunirana zabwino coz siku la kufa siliziwika.

 14. Ndikuwafunira zabwino zones komanso kuchira kwasanga,moyo ndiofunika kwamunthu wina aliyense,sibwino kulemba nkhani zili zaboza ayi kutheka inu mukumufunira imfa muzamwalira ndinuyo iyeyu akadali moyo,

 15. ukamafuna kuti mzako achosedwe pa ntchito ndimeneumanva kuti wakwezedwa. akuluwaalipo mpaka ambuye azawaitana osati woipawe zikomo

 16. You never know who will die soon,kwambiri anthu inu odziwona ngati alungalunganu ndi opemphera(kwa masiku anoku).You think ndinu oyeretsedwa,go to your nearby hospital and check,you will realise real life & that those who are dying are not all HIV+ve.Opanda chikumbumtima,eeesh! Lets have & show some moral pliz.

 17. amalawi kupepela kaya munatengela ndani penapake kumaganiza muli inu mzanu akudwala inu mkumatchukisa kuti wamwalila moyo oyipatu umunewo muziziganizila muli uni umbuli suzakuthelani muzingokhala ovutika choncho I wsh izek qeak recovery and my God be with him timakukonda koposa

 18. get well soon Mr Nyanga. Trust in the Lord for he is always with you. Amen

 19. mayendawa amukakamila ezeki kodi mankhwala samamwa? penapake vuto ndife amalawi munthu ali ndi HIV mmalo monena chilungamo timapita mmbali. sindiyambe nditamvapo kumalilo kuti pamalilo kuti mzathuyu wapita ndi Edzi pamene mbiri ikuti Edzi ikutha anthu

  1. sikuti ndikumuseka, ndikumuseka.ndimatenda inenso atha kundipeza ndipo sindikuopa koma zimakhala bwino kumamasuka cos ma Celebrity ngati Izeki ayenela kukhala olimba mitima kumaulula cos itha kukhala campaign yabwino. Sindikunyoza mundimvetse amalawi anzanga cos ndaona mukundipysela mitima kundinyoza simmene mukuganizila cos ngakhale in you know kuti natenda ndiamenewa koma kubusabisa penapake kumanena chilungamo

  2. Munthu was Edzi akaulula kuti alindikachilombo amakhala ndinkhawa zochepa pamene ukamabisa mapeto ake ndiizo moti Izeki nkhawa zamupweteka tsono musanditenge ngati munthu wamisala I know chimene ndikunena am a normal person ngakhale inuyo anzanga mukapezeka nao subwino kubisa. apa zikuonetsa kuti Izeki sakumwa mankhwala cos olo inu mundivomeleza kuti masiku ano zomazubzika ndi AIDS monga Izeki ndimboriyakale

  3. Zinazi ndibwino osamangokomenta nawo kumangoyang anako, nanga nkhaniyi ndi za edzi zikugwirizana? Mind ur bussness

 20. We wısh you quıck recovery.To my fellow Malawıans let love each other.Don’t wısh a bad luck to your frıend please Manyasa ımwe mbwe nkhanı nkhutınkhana waka nawanyınu mukuphındulapo vıchı when you hate your frıend.I beg your once agaın Don’t wıch your frıend a bad luck.

 21. Das bad story wina kumasangalara ndi kuchukisa kuti wakuti wakuti wamwalira zimenezi zikuchilukira bwanji amalawi azanga kumakhara kusowa chikondi mutima chan don’t take life eazy

 22. Nthawi zonse amalawi sitimafunilana zabwino,tinakhala bwanji?tiyeni tizikondana.nkhani yamaliro siyamasewela.kodi inu ndiye ambeu?In u mukamatsogoza anzanu akupuma inu mudzanka kuti?

 23. MULUNGU AMUSANJIKE DZANJA NDIKUMPATSA MASIKU OCHULUKA KUTI SATANAYO ACHITE MANYANZI. ~~~~~~~~~~~~~~~~~~~~ ABALE KUDWALA SIKUFA TIDZIKHALA NDI MOYO OKONDANA. NDICHIFUKWA CHACHE SANAKUPATSENI MPHAMVU ZAKUPELEKA MOYO.

 24. MULUNGU AMUSANJIKE DZANJA NDIKUMPATSA MASIKU OCHULUKA KUTI SATANAYO ACHITE MANYANZI. ~~~~~~~~~~~~~~~~~~~~ ABALE KUDWALA SIKUFA TIDZIKHALA NDI MOYO OKONDANA. NDICHIFUKWA CHACHE SANAKUPATSENI MPHAMVU ZAKUPELEKA MOYO.

 25. MULUNGU AMUSANJIKE DZANJA NDIKUMPATSA MASIKU OCHULUKA KUTI SATANAYO ACHITE MANYANZI. ~~~~~~~~~~~~~~~~~~~~ ABALE KUDWALA SIKUFA TIDZIKHALA NDI MOYO OKONDANA. NDICHIFUKWA CHACHE SANAKUPATSENI MPHAMVU ZAKUPELEKA MOYO.

 26. Mulungu muchilisen zexy kut woyipa ayaluka ndinu mulungu wamphavu munazusa akufa ambuye khalan naye lzek kut achile musanga muzina la mwana wanu yesu AMEN

 27. Mulungu muchilisen zexy kut woyipa ayaluka ndinu mulungu wamphavu munazusa akufa ambuye khalan naye lzek kut achile musanga muzina la mwana wanu yesu AMEN

 28. Mulungu muchilisen zexy kut woyipa ayaluka ndinu mulungu wamphavu munazusa akufa ambuye khalan naye lzek kut achile musanga muzina la mwana wanu yesu AMEN

 29. Moyo wanga unaasweka nditamva ngakhale sinzanga simbale wanga iye sakundiziwanso ndipo sakuziwanso kuti ndiliko koma a malawi sitizatukukadi ndintima wopusa wansanje wopanda nzelu anthu oti ofunika pachitukuko chadziko lathu lino kusintha myoyo ya anthu koma osayamika ngati ndimawudani konko kwa ena ndiwofunika chitsilu chili ndimwini long live mabedi shame to the mediocrity

 30. Mmmmmm Chonde Amalawi Tatieni Tikondana , & ndikumbuse ntundu Wa Malawi kuti imfa sizoloweleka komanso sichinthu choti nkingolankhula ngati mukukamba zakumpila , ndipo ndikumbuseso kwamene anakhala pansi nkumalemba nkhani yoti I saac wamwalila kuti imfa sinzathu ndipo simasankha sibwino kummampasa malile nzanu mukufuna kuseleula seleulani zina koma nkhani yokha ya imfa usamale nawo, komansotu palibe amene azalumphe dzenje LA manda tele usazimve Sugar iweyo amene unapanga post zinthu zosakhala bwino we , ngati zolemba mulibe chonde chonde zisungileni Ulemu kungosiya osati muonekelepo kupepela kwanu Mulungu tu, amakonda wina aliyense ndipo ndiimene smaziwa kutisamala kwake.

 31. kumene kwatsala tchile ndikomwe ukupita moto muli inu mungamve bwanji m’bale wanu akuganizilidwa kuti wamwalira koma ali moyo

 32. Heaven father will deal with that one who spread that long life im wishing to john nyanga

 33. Ameneyo nde Malawi kukonda kusaongozana kumanda basi kufunilana zoipa nzomwe malawi amadziwa:dziwa ichi malawi palibew wa mbeu en wakufa sadziwika:zabwn zonse Izeki

 34. A malawi24 yesterday you told us of death news and today you tell us that he is alive. First how is your journalism? 2nd how do you view a human being? 3rd how do you sensor the news you tell us? 4th do you know the people who read your articles. Don’t take us for granted. Not Long you will pay bcoz of your carelessness in reporting. Get well soon Izek. God is with you.

 35. but even if pipo spread rumours that i have died, i cannot get worried at all. It can be my opportunity to surprize them.

 36. but even if pipo spread rumours that i have died, i cannot get worried at all. It can be my opportunity to surprize them.

 37. Amalawi anzanga tiyeni tikhale ndi chikondi, mzathu akadwala amasowekera chilimbikitso chathu osati kumuonjezera nkhawa or mantha, muganize muli inu. May the almighty God touch him body and soul IN JESUS NAME.

 38. Amalawi anzanga tiyeni tikhale ndi chikondi, mzathu akadwala amasowekera chilimbikitso chathu osati kumuonjezera nkhawa or mantha, muganize muli inu. May the almighty God touch him body and soul IN JESUS NAME.

Comments are closed.