Thugs in Malawi’s capital, Lilongwe have killed a business lady who owned a shop in Area 36 in the city, police say.
Lilongwe police spokesperson Kingsley Dandaula said the woman was murdered in her shop.
“At around 17:00 hours we received a report that a woman has been killed in her shop so we rushed to the crime scene,” said Dandaula.
At the shop, the police noted that the deceased had serious head injuries which suggested that she had been beaten with a metal object.
Post-mortem results from Kamuzu Central Hospital revealed that the woman died due to the head injuries.
The police believe the thugs stole cash amounting to K9,000 from the shop but the motive of killing the lady is yet to be known.
Meanwhile the law enforcers are investigating the issue and are appealing to Malawians to report to police if they know any person involved in the murder.
mmmmm guyz malawi wafika pena last of last week @ chipasula river eeshh!
Mmmmmmh, zikumvetsa chisoni. Kupha munthu wosalakwa??? Mmmmmm, abale, ganizani bwino. Peter Mutharika uyu, dziko ili, sanalitenge bwino. Ikanakhala nthawi ya Kamuzu, bwenzi wakuphayo, akanapezeka kalekale. Lero, titengerepo phunziro, kuti si bwino kumangovomereza zina zili zonse kuti tizivoteranso zimatchona zoti zakhala zaka zambiri, kunja.
shameful
A Malawi ndichan aaaaa
Mchiani Kodi A Malawi
Sad
But guys people can take someones life just because of 9000?Kupedzeka anthu ngati amenewa aphedwe basi
Dpp boma fucken bastered, mapazi anu this is bad
A Dpp nonse ndinu mbuzi ndi galu wanu yemweyu wamagweruyuu wheres the govt here
Sad news………….may her soul rest in peace
Area 36 its not aplace to stay 11 bongoz!! iz still existing…Mbavaa inuuuu tamangobani mkumapita osati kuchotsa Moyo.
Area 36 its not aplace to stay 11 bongoz!! iz still existing…Mbavaa inuuuu tamangobani mkumapita osati kuchotsa Moyo.
Munthuyu sanali wakuba koma ndi chibwenzi chake chamkaziyu ineyo only kuti ndinali nditadutsapo pang’ono pamalopo ndipomwe ndinangomva galimoto ikupanga spininga matayala nditatembenuka ndimomwe ndinaona kuti anthu akuthamangila pamalopo munthu uja wathawa ndi galimoto lake komabe anakazipeleka yekha ku area 3 police station,mkaziyo sanali mu shop amachokera mbali ina yamseu wa M1 kumapita komwe kunali shorp yakeyo kumeneko ndikomwe addah amenewo anali ataima ndigalimoto yawo mkazi uja kuti azifika pagalimoto paja mwamunayo anangotuluka ndimpeni ndikumubaya mkaziyo pa phewa
Akagwidwa asawasiyesiye plz
RiP mama
Kuba ndalama Mpaka kumchotsera munthu moyo wake zooona? Mmmmmm zandikhudza hevy! May her soul RIP
Choncho muziti tikagwila mbava tibweletse ku police demet
Bwanj osangoba nkumusiya ndi moyo muxafa imfa yowa agalu a dpp inu
Okuba ake ndi osadziwa ntchito yawo,chifukwa okuba ndimamudziwa ine sangalimbane ndi moyo wa zimayi malo mongomubela nkumusiya akulira.koma chongochotsa moyo wakewocho mwaputa tsoka lalikulu zeni ndipo multi ndi nsambi
Mchiyani kodi a Malawi?
Pepani A malawi tisamatero
Koma apeter wo zimenezi akuzinva tikamayimba nyimbo ndiye muzitipha ngati Lobati chasowa komanso Evison Matafary
I personally knew this lady ndamva chisoni kwambiri and wasiya kamwana close to 2 years amakhala nako mu shop mo, mulungu azilangiratu anthu achomcho, komwe akukhalako ajumva bwanji mumtimamo, she was so quite samayambana ndi munthu, God should punish these criminals right away eeeish
ukav nawo knokmalawi
Mbava zochitisa manyazi izi kumupha munthu chfukwa cha change chakubeer aaaa i think kaguluka mayi wophedwawa amawaziwa ndiye mbavazo zimaopa kuti zigwidwa akaziulula thas why anapanga zoipazi chonde ambuye mwambamo ukhuzeni mzimu wamayiwu kuti uwuse muntendere ameena.
Great said
kulakwa kuchotsa moyo wamuthu chifkwa cha k9000 mwatenga nsambi amene mwapanga zmenez
kulakwa kuchotsa moyo wamuthu chifkwa cha k9000 mwatenga nsambi amene mwapanga zmenez
kulakwa kuchotsa moyo wamuthu chifkwa cha k9000 mwatenga nsambi amene mwapanga zmenez
In malawi …. Which way malawi..
In malawi …. Which way malawi..
In malawi …. Which way malawi..
death penalty indeed
death penalty indeed
death penalty indeed
Mwapindulanji crime to christ
Insecurity is high
Anthu opusa kwambiri oyipitsa mbiri ya umbava bwanji osangopita ndi ka 9 grand ndi ku siyila umoyo wake malemu no good.
Gayz ,tsono ndatha kuona kuti ufulu umene tili nawo pano tikugwiritsa ntchito molakwika. Malemu Dr Kamuzu anali tsogoleri wa luntha pogwiritsira mawu oti ,WAPHA, APHEDWE.Umbanda unali osowa ndipo kunalibe kuphana. Taonani tsono ufulu ukutisowetsa ntendere ,tingophana .FOSEKI!! Apolice nawo mzitsiru angoti akamva zoterezo ndiye mwetu tiyi tapeza. Futso kwa achitetezo ndiloti,kodi ophedwayo mwana obeleka inu mungamve bwanji ,chingachitike mchiyani kapena mungapune bwanji?
Its bad
A Malawi mwatani kwenikweni? munthu amazithandiza yekha iye ndi banja lake mpaka kumumpha chonde Yehova akukhululikileni.
Thugs kill a woman in Lilongwe
Aphunzitsi hahahahaha
Bola wanva what matters is uthengao
How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.
ndizimezo,,apolice maso alipachamba basi, koma anthu akuphedwa
Anthu oterewa akapezeka tziweruza tokha coz apolice amapanga zachamba chomwe amachifuna ndi ndalama akatero chigawenga mkuchitulutsa chikaphe anthu ena zmene szli zabwno.
RIP
IZI NDIZOMWE KAMUNZU ANALOLA LAMULO LOTI WAKUPHA MZAKE APHEDWE AMAKANA UTSILU NGATI UWU. ~~~~~~~~~~~~~~~~~~~~ IZI ZIKAMACHITIKA NGATI MAIKO A MARABS NDIKUMATI ASLAM AMALOLA BWANJI LAMULOLI KUGWILA NTCHITO AMAKANA NYANSI NGATI ZIMENEZI.
Repports of killings are recieved everyday,but our government still reluxing,i cant believe this.
Apolice mfuti ntchito yake sayidziwa….zipolopolo kuapasa amakapanga na decolations kunyumba kwawo. Asaaaaaa #tired mbava zivutise kupha anthu….. Via ma albihno nawo kuphedwa akapezeka basi ali awamanga afta a week ati atuluka kukaoanganso zina. Now hope anthu tiziweruza tokha akapezeka oterowa! Anyway RIP
Wina waphedwa ena akuchita like zikugwilizana bwanji ndi nkhaniyi?
Pepani man anthuwa ndamalawi like nchichewa ndekuti ku khuzidwa kikkkkkkkk
Ine kukhala président nditha kulola law into your hands
Iiiiiih United States Of Malawi(USM) vuto ndichani kwekwen?? RIP Innocent lady.
This is too much now…
Choncho kugwidwamo anthu ndikumuocha ndiye mukumazuzula kuti mob justice yabwino Zoona
Its too bad….
tit for tat is the only best way of resolving such crimes
Zonvetsachisoni malawi akupitakuti #eeee}
Xo bad
Its 2 bad R.I.Peace
Its 2 bad R.I.Peace
Mulungu akuwona zonsezi
Mulungu akuwona zonsezi
Ndiye wina nkumachita commend Malawi Police, pakufunika death penalty, enough is enough. To loose life in this way becoz of these fucken people.
Ndiye wina nkumachita commend Malawi Police, pakufunika death penalty, enough is enough. To loose life in this way becoz of these fucken people.
mbola
mbola
End times,murders will be common.today killing z in fashon,just matching the scripture
End times,murders will be common.today killing z in fashon,just matching the scripture
Ndi chiyani kodi amalawi?
Ndi chiyani kodi amalawi?
Koma mesa #DPP imkati ikadzawina idzabweletsa chitetezo nanga lero ziii muli kuti anthu akungophedwa ngati nkhuku
Koma mesa #DPP imkati ikadzawina idzabweletsa chitetezo nanga lero ziii muli kuti anthu akungophedwa ngati nkhuku
The Last Dayz
The Last Dayz
WTF! taking somebody’s life jst coz of k9,000. osangopepha bwanji! God .
kupha munthu chifukwa cha 9000 basi malawi akulowela kuti?
whats the full story /Singano/ more details if u hv.
kupha munthu chifukwa cha 9000 basi malawi akulowela kuti?
whats the full story /Singano/ more details if u hv.
Oh….. ma country
Oh….. ma country
Nkhani zamasiku ano ndozophana basi
Nkhani zamasiku ano ndozophana basi
Woyenda ndi lupanga azafa ndi lupanga. Ooooo!! my God, do something to them within this week.
Woyenda ndi lupanga azafa ndi lupanga. Ooooo!! my God, do something to them within this week.
God of mecy do something
amen
Pliz God anthu ngati awa ndiofunika akumafa imfa yozuzika yopweteka pang’onopang’ono
Kma chifukwa chan apanga zimenez anthu amenewa? Ndithudi mulungu achite nawo mwapaderadera!
Kma chifukwa chan apanga zimenez anthu amenewa? Ndithudi mulungu achite nawo mwapaderadera!
R.I.P
R.I.P
To bad
What happening malawi each and everyday we must hear abt somebody kill someone nononono
What happening malawi each and everyday we must hear abt somebody kill someone nononono
mmmh why malawian tdzipangirana zimezi..so bad.
mmmh why malawian tdzipangirana zimezi..so bad.
Lets God punish them
Lets God punish them
Too bad!
Too bad!