Student arrested for having an abortion

574
Malawi Abortion

The arrested student Suzen Chinkhokwe

Malawi Police officers in Nkhotakota district are keeping in custody a 22 year-old student at Nkhotakota College of Education Private Secondary School for having an abortion.

Nkhotakota police public relations officer Williams Kaponda said the suspect, Suzen Chinkhokwe, gave birth to the baby in one of the school’s bathroom.

“Some students were shocked when they went to the bathroom and saw blood in the bathroom and a foetus lying lifeless on the ground,” said Kaponda.

The incident was reported to the school’s matron and she told the police who arrested the suspect.

Health officials confirmed that the girl was recently pregnant and said the foetus was about four months old.

Meanwhile, the suspect is in hospital where she is receiving treatment after a medical examination revealed that she took an overdose of DCN capsules.

Meanwhile she has been charged with the offence of concealing birth of child and is expected to appear in court soon.

The suspect hails from Kalunkhulu village, Senior Traditional Authority Kanyenda in Nkhotakota.

(Images credit: Williams Kaponda)

Share.

574 Comments

 1. M’kwiyo wa mulungu ugwele pa iye vuto mukumapanga ziwelewele zopanda nazo sogolo ukanakhala iweyo amako ndi abambo ako anakupanga khalidwe limeneli bwezi ulipo padziko pano .

 2. Atsikana chonde tiziyamba taganiza Kaye kuti bwanji ifeyo makolo anthu sanatitaye koma kusungabe pathupi mpaka miyezi 9 mzimu umenewu uzamudandaura ntsikanayu mpaka kale ndipo alibe mwayi

 3. Symon moto uzikhala serious wandisangalasa jwambiri nanga chotaila mwana ndi chain uziwa ma results omwe upeze mukagonana osaziteteza kudonthatu kumeneko

 4. Symon moto uzikhala serious wandisangalasa jwambiri nanga chotaila mwana ndi chain uziwa ma results omwe upeze mukagonana osaziteteza kudonthatu kumeneko

 5. Iye amaonangati chani zimakoma popanga komatso atulusidwe pomwe anatengela mimba palibe akuziwapo musiya muzikapanga za ndalama zobedwa

 6. Everything in lyf hv its meaning……dnt say more bt jst say alowerere ambuye coz we can’t fight alone dis war coz we don’t hv sophisticated weapons

 7. Dat dae wil cum wen each man shal b judged..jxt imagine.Jah askin u about di kids u ave erased from ur wombs..oxanama,or mmatchalitchimo kumangkhala ngati kokaphunzitxana uchimo…wonder wat ana amene ama bosholao analakwa chan….bt EVERYONE WILL MEET HIS/HER END ONE DAY….#Jah_knws

 8. km anakupatsa mimbai ndimuthu wa mamuna nanga chochotsela ndichan mesa udakabala mwana kapena udakabala Galu?kapena adakuchinda ndi Galu

 9. km anakupatsa mimbai ndimuthu wa mamuna nanga chochotsela ndichan mesa udakabala mwana kapena udakabala Galu?kapena adakuchinda ndi Galu

 10. km anakupatsa mimbai ndimuthu wa mamuna nanga chochotsela ndichan mesa udakabala mwana kapena udakabala Galu?kapena adakuchinda ndi Galu

 11. Akazi chonde osamachita zimenezi,mukatenga mimba basi berekani mwanao osachotsa.Simungakhale oyamba inuo azanu anazichitapo ndipo adabereka mwana.

 12. Akazi chonde osamachita zimenezi,mukatenga mimba basi berekani mwanao osachotsa.Simungakhale oyamba inuo azanu anazichitapo ndipo adabereka mwana.

 13. Akazi chonde osamachita zimenezi,mukatenga mimba basi berekani mwanao osachotsa.Simungakhale oyamba inuo azanu anazichitapo ndipo adabereka mwana.

 14. ubwino wake kwathu kuno malamulo ndisaopsa ndikanali ine ndikulamulira dziko opeza atapanga izi kunali kumangowapha mahulewa akuipitsa dziko

 15. ubwino wake kwathu kuno malamulo ndisaopsa ndikanali ine ndikulamulira dziko opeza atapanga izi kunali kumangowapha mahulewa akuipitsa dziko

 16. Ena akisowa chibelekelo ena akulepela kukala ndimwana kma ena akutaya mwana ndithu tinenekuti ndizibwanabwana zimenezi atsikana wina azapita nayo mimba ndithu kugonana ngati kwakoma osangotengana bwanji muzikagonana bwino mnyumba mwanu zoputsa

 17. Ena akisowa chibelekelo ena akulepela kukala ndimwana kma ena akutaya mwana ndithu tinenekuti ndizibwanabwana zimenezi atsikana wina azapita nayo mimba ndithu kugonana ngati kwakoma osangotengana bwanji muzikagonana bwino mnyumba mwanu zoputsa

 18. Kkkkk koma nde chi dzina.., Nkhotakota college of education private secondary school?? Is it college or secondary?

 19. Nkhotakota college private secondary xul,wat does dat mean? En 4 agal to abort it means the man has forced,maybe kumukana kumene,men u r weeked

 20. Ukupha pamene azako aku chitila k mwela z wawa bwaji ukanangondipasa ndipanga adopt w chitisa manyazi xool yathu y kale kale

 21. Mmmmm guys it wasn’t her fault plz don’t Luk 1 side apa u can see mukuti ndi students kodi mamuna amanamuvomera akanapanga zimenezo?. Guys sindikumubakira koma inuyo amuna amabanja anu ndiomwe mukupangitsa izi mumati mkaziyu mwanayu akanatani naye anamamuthandiza zikatero?. Its true walakwa kutero moti God will judge her on last not u and me plz musakhalire Mulungu pa mpando komanso moti mumve both side of Story inunso atola nkhani tafufuzani mutiuze zoona plz

 22. Ngati mukulephela kulela pitani kuboma mukawapasi aboma akalela kusina ndimumene mukuchitia mo kodi simunziwa chifunilo chamulungu chonde muziweni mulungu pephani akupasani zeli .pepani kwambili chifukwa muli ndiphavu yamdyelekezi muthamangiseni oyipa yo chonde.

 23. Ukamadya munthu umayembekeza kukhuta nde ndizimenezi,,,and mwawi sumabwera kawiri u will never have a child no more chifukwa mwana ndamene wachita abort’yo

 24. fotsek that lady why at first was she having unprotected sex or go to the clinic for contraceptives let the courts give her a death sentence rot in hell

 25. “Mtsikana iwe” amene waphawe kaya anzako anakunyenga kuti uphe dziwa kuti uli ndimulandu pamanso pa yawe. Mulungu chitanayeni mtsikana ameneyu kuti adziwe ukulu wanu.

 26. ano poti amateteza ufulu wokhala ndimoyo wa akupha anzawo. Ndikanakonda kuti osata lamuloli aphedwe ndi munthu wopanda mantha chifukwa iyeyo sazaphedwa lizamuteteza ndi lamuloli. Apo biii lamuloli alichose ayikepo lakale la diso kwa diso muzaona kuti mchitidwewu uzachepa kapena kutheratu. I mean wakupha munthu. AUZENI A BOMA ACHITEPO KANTHU. TILI CHETEE PA RUMPHI. TIKUYAMIKILA NTCHITO ZA APOLISI KUGWIRA ALIYENSE WOPHWANYA MALAMULO.

  • I agree with u Edie they shouldnt have put this pic on social netwk cos coz the under age children r on social netwk.but anyway that student shame on her for killing an innocent umborn child she must face the law

 27. Tikamalangiza munthu wolakwa tisamanyozane nyozane olangiza tokhatokha monga zoti:- atumbuka, achewa kaya mtundu uli wonse chifukwa sizizatithandiza ayi. Kulibwino kunyoza wolakwayo koma momuphunzitsa. Iwe mtsikana wapalamulawu ndi mlandu wakupha munthu ndipo chilango chakupha munthu umachiziwa kale akakumbusa ku khoti. Wachosanso ufulu wamunthu wokhala ndi moyo. Fox walesa mwana kukhala ndi moyo nawenso akuletse kupitiliza maphunziro pokukutumiza kundende kaya akakunyonga. ungoyamika makhoti asop

 28. Because of your #COMMENTS, can any one of you know the last destination of my dear sister, either hell or heaven? God is slow to anger. #totallyAgainstABORTION

 29. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 30. Kodi atsikana, NDE uhule ndi zisembwerezo mkumapangiranji? Inu mumaganiza kuti mvula ingamagwe mtsinje osadzadza? Uhule wachuluka kwabasi. Koma kuti upite mmatchalichi ambiri upeza akuoneka ngati ma holy holy. Today virginity is being exchanged for Christmas, parties, jobs, school, money and nobody wish to protect it. Koma kumwamba kuli zoopsa. Atate khululukani!!!

 31. Am vry much touched with the torture this girl z going through in the custody.Her only sin z her excersize of her originality and deciding what z best for her and not everyone else.my fellow narrow minded malawians let embrace individual autonomy ide

 32. Ana Ndiawa Mukutaya Nthawi Yolowa M’banja Isanakwane, Ndiye Muzizanena Kuti Mwamunanu Ndiosabeleka Vuto Uli Iweo

 33. Chimkana wachitonga waku Dwangwa.Ambiri amakhara maHule..Atsika apa Nkhotakota Colege pvt se xool ambiri ndiwoyaluka mahule amangoyenda yenda usiku pa Nkk Boma.ndipo ine sindikuona zachilendo izi

 34. Atumbuka what’s wrong with u guyz?? Y are responsible 4 every bad newz??chimakhala chili chani kodi??kapena tiziti oipayo wamanga madziko kumpoto kokha bass??

 35. Yooh dziko lapansi eish zandipasa matha ine kod ameney makolo ake akadatero bwenzi alipo? Umuthu alibe zoti kunjakuno kuli yehova anaiwala aaaaaa zatiweluzeni yehova dziko lanu labwno lija munatipas lero iiiiii lanyasiratu

 36. amangiranji iye ndiye avutike ndimimba yopanda bambo apolice nanuso mupasuleni muthu she got rights for abortion mesa akatero apitiliza maphuzilo kkkkk leave her

 37. Osakabaisa.or kusekesa bwanji. Having unprotected sex…what were you expecting to have? A fridge? A plasma tv? Ladies even if we dump you after impregnating you….come on …raise the kid. You are part of creation….this dumping thing shouldnt be in a ladies mind

 38. when she wz avn sex we were nt dea bt today u av shwn d whole country dat u were enjoyn d stuff somewhere.shame on u diot.

 39. when she wz avn sex we were nt dea bt today u av shwn d whole country dat u were enjoyn d stuff somewhere.shame on u diot.

 40. Dis is too much!!!!!…nde nkumapangiranji ziwerewere ukuziwa kut u dnt need mwana??…she’s a 100% murder and she deserves jail!!…,some pple r strugling to hav dat precious gift,ena phiri akwera akweraso & wina nkupha innocent life mercilessly…,mtsikana wandiwophya uyu!!!..GOD can’t b happy with u!!!!!

 41. Dis is too much!!!!!…nde nkumapangiranji ziwerewere ukuziwa kut u dnt need mwana??…she’s a 100% murder and she deserves jail!!…,some pple r strugling to hav dat precious gift,ena phiri akwera akweraso & wina nkupha innocent life mercilessly…,mtsikana wandiwophya uyu!!!..GOD can’t b happy with u!!!!!

 42. Azibambo ena amangodziwa kufesa mbeu koma kuti asamale goo,they varnish but no man can ran away from his sins where ever you hide they will find you.

 43. Azibambo ena amangodziwa kufesa mbeu koma kuti asamale goo,they varnish but no man can ran away from his sins where ever you hide they will find you.

 44. You warn us for graphic image yet mwayika pa mbalambanda, how do you expect those who would be offended not to see? The warning has been put right where the graphic image is, such that when one is reading the warning their eyes have already been set on the images. Next time check with other online publications how they professionally handle such issues.

 45. You warn us for graphic image yet mwayika pa mbalambanda, how do you expect those who would be offended not to see? The warning has been put right where the graphic image is, such that when one is reading the warning their eyes have already been set on the images. Next time check with other online publications how they professionally handle such issues.

 46. Vuto la chigololo limabweretsa zoipa ndi machimo ena. Kupha, usakhulupirika, unama, chinyengo ndi umbanda. Kuwonongeka ndi kuwola kwa dziko. Sexual abuse and exploitation by men who sponsor prostitution. The guy who impregnated the woman must be hunted and arrested to answer charges of conspiracy to murder!

 47. Vuto la chigololo limabweretsa zoipa ndi machimo ena. Kupha, usakhulupirika, unama, chinyengo ndi umbanda. Kuwonongeka ndi kuwola kwa dziko. Sexual abuse and exploitation by men who sponsor prostitution. The guy who impregnated the woman must be hunted and arrested to answer charges of conspiracy to murder!

 48. Vuto la chigololo limabweretsa zoipa ndi machimo ena. Kupha, usakhulupirika, unama, chinyengo ndi umbanda. Kuwonongeka ndi kuwola kwa dziko. Sexual abuse and exploitation by men who sponsor prostitution. The guy who impregnated the woman must be hunted and arrested to answer charges of conspiracy to murder!

 49. Chitsitsi chamulungu kuli azimayi okulupilira iye ndipo akumasara kudya week ndi week kufuna mwana ena kupita kumene kwa sing’anga koma osampeza ayi, wina ndiye akuchita kutaya, mulungu wanga ine matembelero ochuluka agwere iye ndipo usayembekezere kupita nawo maphuzilo ako pasogolo ndi galu wamunthu, pamene ukunyengedwapo somaziwa kuti zosatila zake ndi mimba, uzamulila mwa ameneyo, apolice tiye nayeni amangidwe bas.

 50. Chitsitsi chamulungu kuli azimayi okulupilira iye ndipo akumasara kudya week ndi week kufuna mwana ena kupita kumene kwa sing’anga koma osampeza ayi, wina ndiye akuchita kutaya, mulungu wanga ine matembelero ochuluka agwere iye ndipo usayembekezere kupita nawo maphuzilo ako pasogolo ndi galu wamunthu, pamene ukunyengedwapo somaziwa kuti zosatila zake ndi mimba, uzamulila mwa ameneyo, apolice tiye nayeni amangidwe bas.

 51. Chitsitsi chamulungu kuli azimayi okulupilira iye ndipo akumasara kudya week ndi week kufuna mwana ena kupita kumene kwa sing’anga koma osampeza ayi, wina ndiye akuchita kutaya, mulungu wanga ine matembelero ochuluka agwere iye ndipo usayembekezere kupita nawo maphuzilo ako pasogolo ndi galu wamunthu, pamene ukunyengedwapo somaziwa kuti zosatila zake ndi mimba, uzamulila mwa ameneyo, apolice tiye nayeni amangidwe bas.

 52. Is a foetus human being? it has never been and it will never be.Stupid law enforcers why arrest her if a foetus is not a human being? After all she is in charge of her body and has the right to decide with what shd happen with it(archaic law)

 53. Is a foetus human being? it has never been and it will never be.Stupid law enforcers why arrest her if a foetus is not a human being? After all she is in charge of her body and has the right to decide with what shd happen with it(archaic law)

 54. Is a foetus human being? it has never been and it will never be.Stupid law enforcers why arrest her if a foetus is not a human being? After all she is in charge of her body and has the right to decide with what shd happen with it(archaic law)

  • mm tangoganizani mpaka lero akuyenda free bt otaya mimbawo nde pompompo.nonsese! en wy ar thy arrest hr? I thought nw abortion is legalised in malawi

  • Murder case happens when u kil a human being.in this case,she gets rid of a foetus.is a foetus human being? no.therefore, it z not a murder case. she is a complete owner of her body arresting her is gros violation of human dignity

  • Murder case happens when u kil a human being.in this case,she gets rid of a foetus.is a foetus human being? no.therefore, it z not a murder case. she is a complete owner of her body arresting her is gros violation of human dignity

  • #Aluzioh..,aise ukunama!!…if dat is da case nde y do doz pple hu hav been rescued in d process of committing suicide face the law??…mesa nawoso amalakwira thupi lawo..komabe amatsegulilidwa mlandu..

  • #Aluzioh..,aise ukunama!!…if dat is da case nde y do doz pple hu hav been rescued in d process of committing suicide face the law??…mesa nawoso amalakwira thupi lawo..komabe amatsegulilidwa mlandu..