Thugs kill Lilongwe woman


Chikwawa

Thugs in Malawi’s capital, Lilongwe have killed a business lady who owned a shop in Area 36 in the city, police say.

Lilongwe police spokesperson Kingsley Dandaula said the woman was murdered in her shop.

Blood.“At around 17:00 hours we received a report that a woman has been killed in her shop so we rushed to the crime scene,” said Dandaula.

At the shop, the police noted that the deceased had serious head injuries which suggested that she had been beaten with a metal object.

Post-mortem results from Kamuzu Central Hospital revealed that the woman died due to the head injuries.

The police believe the thugs stole cash amounting to K9,000 from the shop but the motive of killing the lady is yet to be known.

Meanwhile the law enforcers are investigating the issue and are appealing to Malawians to report to police if they know any person involved in the murder.

104 thoughts on “Thugs kill Lilongwe woman

 1. mmmmm guyz malawi wafika pena last of last week @ chipasula river eeshh!

 2. Mmmmmmh, zikumvetsa chisoni. Kupha munthu wosalakwa??? Mmmmmm, abale, ganizani bwino. Peter Mutharika uyu, dziko ili, sanalitenge bwino. Ikanakhala nthawi ya Kamuzu, bwenzi wakuphayo, akanapezeka kalekale. Lero, titengerepo phunziro, kuti si bwino kumangovomereza zina zili zonse kuti tizivoteranso zimatchona zoti zakhala zaka zambiri, kunja.

 3. Munthuyu sanali wakuba koma ndi chibwenzi chake chamkaziyu ineyo only kuti ndinali nditadutsapo pang’ono pamalopo ndipomwe ndinangomva galimoto ikupanga spininga matayala nditatembenuka ndimomwe ndinaona kuti anthu akuthamangila pamalopo munthu uja wathawa ndi galimoto lake komabe anakazipeleka yekha ku area 3 police station,mkaziyo sanali mu shop amachokera mbali ina yamseu wa M1 kumapita komwe kunali shorp yakeyo kumeneko ndikomwe addah amenewo anali ataima ndigalimoto yawo mkazi uja kuti azifika pagalimoto paja mwamunayo anangotuluka ndimpeni ndikumubaya mkaziyo pa phewa

 4. Kuba ndalama Mpaka kumchotsera munthu moyo wake zooona? Mmmmmm zandikhudza hevy! May her soul RIP

 5. Okuba ake ndi osadziwa ntchito yawo,chifukwa okuba ndimamudziwa ine sangalimbane ndi moyo wa zimayi malo mongomubela nkumusiya akulira.koma chongochotsa moyo wakewocho mwaputa tsoka lalikulu zeni ndipo multi ndi nsambi

 6. I personally knew this lady ndamva chisoni kwambiri and wasiya kamwana close to 2 years amakhala nako mu shop mo, mulungu azilangiratu anthu achomcho, komwe akukhalako ajumva bwanji mumtimamo, she was so quite samayambana ndi munthu, God should punish these criminals right away eeeish

 7. Mbava zochitisa manyazi izi kumupha munthu chfukwa cha change chakubeer aaaa i think kaguluka mayi wophedwawa amawaziwa ndiye mbavazo zimaopa kuti zigwidwa akaziulula thas why anapanga zoipazi chonde ambuye mwambamo ukhuzeni mzimu wamayiwu kuti uwuse muntendere ameena.

 8. Gayz ,tsono ndatha kuona kuti ufulu umene tili nawo pano tikugwiritsa ntchito molakwika. Malemu Dr Kamuzu anali tsogoleri wa luntha pogwiritsira mawu oti ,WAPHA, APHEDWE.Umbanda unali osowa ndipo kunalibe kuphana. Taonani tsono ufulu ukutisowetsa ntendere ,tingophana .FOSEKI!! Apolice nawo mzitsiru angoti akamva zoterezo ndiye mwetu tiyi tapeza. Futso kwa achitetezo ndiloti,kodi ophedwayo mwana obeleka inu mungamve bwanji ,chingachitike mchiyani kapena mungapune bwanji?

 9. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 10. Anthu oterewa akapezeka tziweruza tokha coz apolice amapanga zachamba chomwe amachifuna ndi ndalama akatero chigawenga mkuchitulutsa chikaphe anthu ena zmene szli zabwno.

 11. IZI NDIZOMWE KAMUNZU ANALOLA LAMULO LOTI WAKUPHA MZAKE APHEDWE AMAKANA UTSILU NGATI UWU. ~~~~~~~~~~~~~~~~~~~~ IZI ZIKAMACHITIKA NGATI MAIKO A MARABS NDIKUMATI ASLAM AMALOLA BWANJI LAMULOLI KUGWILA NTCHITO AMAKANA NYANSI NGATI ZIMENEZI.

 12. Apolice mfuti ntchito yake sayidziwa….zipolopolo kuapasa amakapanga na decolations kunyumba kwawo. Asaaaaaa #tired mbava zivutise kupha anthu….. Via ma albihno nawo kuphedwa akapezeka basi ali awamanga afta a week ati atuluka kukaoanganso zina. Now hope anthu tiziweruza tokha akapezeka oterowa! Anyway RIP

 13. Ndiye wina nkumachita commend Malawi Police, pakufunika death penalty, enough is enough. To loose life in this way becoz of these fucken people.

 14. Ndiye wina nkumachita commend Malawi Police, pakufunika death penalty, enough is enough. To loose life in this way becoz of these fucken people.

 15. WTF! taking somebody’s life jst coz of k9,000. osangopepha bwanji! God .

Comments are closed.