Nyasa Big Bullets have warned vendors in Malawi against selling products that have the club’s name without proper authorization from the team.
According to the team, many vendors are benefiting a lot by using the name Bullets on their products.
Among the merchandise that have been selling like hot cakes are scarfs, calendars, stickers, and posters.
Reacting to the illegal use of Bullets name, the team’s deputy head of finance George Ndindi said the vendors risk arrest.
“We have noted that some are using the team’s name and they are making profits while the team is not benefiting anything I think that’s unfair,” said Ndindi.
He warned that the management will involve the police to arrest any person found selling any product with Bullets branding.
The team has since appealed to the general public to follow proper procedures when they want to use the Bullets name.
Bullets ndiyama vendor ndiye akuliranso chani ndi zawo zomwe izi…..
kkkkk mungoti yachenjedza mavenda amzawo tikanamva
Mwaiwala kuti masapota anu ambili ndi mavendawo?Timu iyi sizatheka,imakonda zamakangano.Umbuli too much!
tsono venda vs venda angagule nzake ndani
tsono venda vs venda angagule nzake ndani
ndeuchitsilu osawasiya mavendor bwanji,iyaa akugulitsa maina a azikazi amabwana mu bullets?nxaaaa
Mmesa team ndiyamavenda kumene
Ure Talking Of Chamba Or What?
Neba Wayamba Kutuma Mavenda Kuti Azitibera Tikuphwasamulira Pa Stadiam Uone Polekera Maule Ndi Maule Umwa Wa Nchere Ndi Nakamula Wa Bpyo
Mavendawo ndiye masapota abullets nangamuwaletsa dwanji kugulitsa? Timu yamavenda!!!!!…….
kkkkkkkk muzngothokoza kut mavendor ndiomwe akupangsa kut makaka amaule azpezeka palipose not to warn vem
Mwaonjeza gys bwanji samagulisa jenzi ya noma ndiye kuti bullest ili ndi masapota ambili?
Za kubanja izi kaya muona mmene mupangire poti mumati ndi people’s team
mmmm keep fightng coz dis is our proparty
Mavendor okha okha kuletsetsan kk
Mavenda kuchenjezana hahaha
How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

Neba milandu iiiiiiii umayikonda bwanji
Neba milandu iiiiiiii umayikonda bwanji
Koma. Ma vendor siazungu akulodzani ndipo simudza winanso.inu pangani zanu zabwino muzigulitsa
Koma. Ma vendor siazungu akulodzani ndipo simudza winanso.inu pangani zanu zabwino muzigulitsa
hahahahahah! Neba ukuti chani apa! Nokha nokha mukubelana ku bullets,,,u mbuli sudzathaa ……. Mbuli ndi mbuli basi
Asiyeni azigulitsa kodi ayipa lero chifukwa kwabwera nyasa mwayiwala kuti ndi amene akusamalani mbuyo mosemu
INE NDIMATHA KULUKA ZINTHU ZOSIYANASIYANA. MOTI MUNTHU WANDIUZA NDIMULUKIRE SIKAFU/CHISOTI CHA BB, NDIZIKANA/CHILOLEZO MLACHITENGA KUTI?
INE NDIMATHA KULUKA ZINTHU ZOSIYANASIYANA. MOTI MUNTHU WANDIUZA NDIMULUKIRE SIKAFU/CHISOTI CHA BB, NDIZIKANA/CHILOLEZO MLACHITENGA KUTI?
Team yovutika tikakudyerani kut? Mavenda azanga osasiya akadzatopa okha adzatisiya kkkkkkkk simunati musova
Team yovutika tikakudyerani kut? Mavenda azanga osasiya akadzatopa okha adzatisiya kkkkkkkk simunati musova
Neba sungalimbe pa vendor!waiwalanso kuti ndi team yama vendor nthawi yomweyi?kupanda vendor ukadakhala ndana?
chongofunika aliyese okonda maule akhale mulonda wazake.zikhoza kuchepa,chonde tiyeni tikonde TEAM yathu.MOO!! FIRE
Nkhani ya chande yomweyi mpaka mihawu kkkkkkkkkkkkk
Mayoo !! Nyasa BB mwatani kodi limenelo ndivuto. Tamangosutani fodya wanuyo
ZAONETSELATU KUTI BULLETS NDIYOVUTIKA
https://video.xx.fbcdn.net/hvideo-xpf1/v/t42.1790-2/13077521_278804699122696_325147942_n.mp4?efg=eyJybHIiOjM0MCwicmxhIjo3MzksInZlbmNvZGVfdGFnIjoic3ZlX3NkIn0%3D&rl=340&vabr=189&oh=cf437803ced7df077b08999bc80e938b&oe=571CE507
kkkkk neba wayamba kulimbananso ndi mavenda kkkkkkl koma iwe suzathekadi sheeeeeee. chiwanda cha ndlama chakukamiladi basi kkkkkkkk USOVENGE
Aziguritsa mamerycad anyimbo kare ndi chingambwe kkkkkkkkkkkkkk
its not gud to do dis they hav to stop dis
Gud move bullets ,,,koma muzipanga zinthu zambiri ndipo mtengo uzakhala ochepelako
Do they have copyrights?
Koma ngati ndiumphawi team iyi hahahaha yaonjeza kulimbana ndi tizinthu tama K100 zoona
Kkkkkkkkkk kodi nonse ndinu ma vendors how can u stop them doing it
Kkkkkkk chingambwecho ndimalima ndekha ndiye pali vuto?
Tikadyera ku hospa ifeyo axova
Hahahaha…. Asaletse coz the cant manage kupanga zinthu zoti ma supporters azigula zokwanira. Tiye nazoni ma vendor osasiya.
The people’s team remember.kkkkkkk