Police in Ntchisi have arrested three people for allegedly cultivating indian hemp.
The incident happened on Sunday April 3 2016 in the villages of Chikowa, Kawenje and Kachirandozi in Ntchisi.
Police have identified the three suspects as Davis Mzunga aged 38 from Chikowa Village, Austin Kambewa aged 37 from Kawenje Village and Petro Kadam’manja aged 40 from Kachirandozi Village, all from Traditional Authority Chilooko in Ntchisi.
Police report indicate that Malomo Police Unit got information from respective village heads and detective Sub Inspector Orphan Mkhalipi together with other police officers went to the respective village heads and uprooted the indian hemp with most of it at maturing stage.
The three suspects have been charged with the offence of cultivating indian hemp which they admitted and will appear in court soon to answer the charge.
most of are able to support their families trough ganja farming. fight against Gayism and leave ganja farmers that’s how they make a living. free them up
Eieeesh nde mwati anthu osalakwawo amangidwa ndithu?? Kkk
Ngati analibe fertiliser othilira chimanga option ina yabwino ndi imeneyo kaya ndiye mukuwagwiriranji apha munthu mmalo momakayang’ana aja akupha albino aja apa kulimbana ndi za zii
Ngati analibe fertiliser othilira chimanga option ina yabwino ndi imeneyo kaya ndiye mukuwagwiriranji apha munthu mmalo momakayang’ana aja akupha albino aja apa kulimbana ndi za zii
ameneyo atayeni alibe chifukwa.
i can see no reason of arresting them,indian hemp should be legalised so that farmers shld cultivate without fear of this poor regime
Alibe problem let yhem out
Morgan Heritage will not be able to like this.
palibe chamzeru malo mothana ndinbavaa mukulimbana ndi munthu wosalakwa zichepe kumanga alimi
palibe chifukwa chot muziwamanga anthu olima ganja ndipo zomanena jut ganja amachitisa misala ndizaboza lakukhuniza amachita kulozedwa ndi athakat osat gamja
Nanga mumanena kut aku Nkhotakota ndio amalima ganja ,nanga awa ?
Babelon agwe! kadziko kosauka kwambiri dziko lose. sikuti ndife aulesi koma ukati uyese babelon yusokoneza.moti ine munda wanga mbeu imene imalola ndi ganja emweyu basi.
Babelon agwe! kadziko kosauka kwambiri dziko lose. sikuti ndife aulesi koma ukati uyese babelon yusokoneza.moti ine munda wanga mbeu imene imalola ndi ganja emweyu basi.
Apolici kusuta ndiye eishi,koma akachipeza ndimunthu wina ndiye lamulo ligwire ntchito.
Atulutsidwe pasanathe 1to2minits changu
ndapezanso musika waganja amene alinacho in box me.apolice omwewa amatigulisa iwowo kumanga anthu.kagwileni mbamva ndi komaso ndi anthu obela boma kuti chuma chizikwela,fuseki!
Cuma Cobisika Tingakhale Odzidalila Bwanji? Indian Ndiye Kuti Ku Indiako Amalima Kuno Tina Zolowela Kusaukitsana Amasuleni Alibe Kalikonse Anthuwo
still not in love with popo
Nde mwateromo mutaya kuti?tifuna tione mukuotchadi zimenezo
Fuck dem police thats brutality u shown us
Police smoke it too!!
Kodi anthu aja akumaba kuma office aboma moopseza ndimfuti agwidwa kapena ayi? Zukudabwitsa apolisi kugwira anthu oti avutika kulima mbewu zawo kuti mwina akagulisa apeze kangachepe.Should i see the police officers arresting my relatives they will know what shaved the guinea fowl
Free up due herbz ……
Apolice apanyasa thats y dema amadana nanu. Vuto nchani kumamanga anthu olima zomera?
free ganja Free de pippo dont criticise ganja
Our MP Requested This In Pariament And If Any Thing We Are Just Experimenting. Whats Wrong With Experimentation? Escot Them Free!
Our MP Requested This In Pariament And If Any Thing We Are Just Experimenting. Whats Wrong With Experimentation? Escot Them Free!
Well processed Ganja..
Well processed Ganja..
Lets use it.
Lets use it.
LEGALIZE IT!
ndiye mwapindula chiyani?
ndiye mwapindula chiyani?
Kkkkkkkkkkkk ma ganja planter kukolola pomwe analima basi
Kkkkkkkkkkkk ma ganja planter kukolola pomwe analima basi
@
nyasa big bullets behind this
Kd Mmesa Mwati Tisamagule zakunja Tixipanga tokha ma business konkuno ku mlw ndie awa agwidwawa alakwa cha`kd mmesa ndi business
I want to give a testimony on how I get cured from HIV/AIDS. As I was browsing through the internet on how to get cured, I saw a lady testimony praising DR Williams I never believe it before until I tried it and it really work for me am very happy right now may God bless him. this is an opportunity for you to get cured contact him via [email protected]….. and also you can contact on whatsapp number +2348143143878 THESE ARE THE DISEASE Dr.DR WILLIAMS CAN CURED. HERPES. HIV/AIDS. CANCER. LOVE SPELL VIRUS.
They are doing a research, free them!!!!!!!!
Kukabwera akuba amfuti nde kukhala pa easy anthawe nde kubwera kuli kuwopa koma kungomva zachamba nde komweko kufwenkheza ngati agalu shupiti
Ligalisation
legalize it Ganja is harmless , police and soldiers smoke it , lawyers and doctors take it politicians also smoke it
industrial hemp.
Fire burn them bomboklaaats police
But it is legalised.
Mgcini Maseko
Akhaulitseni imeneyo sintchito yawo eni ndi a fwaka bb.
inu ganja? malawi24 you not serious how can you use the word ganja mmmmmmh? it dilutes the importance of the story. sitingakudalireni eti?
Zaziiiiiiiiiiiiiii mukumanga mlimi koma okuba ndalama za boma ku ministry of Agriculture akukukanikani. Fodya osuta ena akukupwetekani inu.
Apolice akumalawi akulephera kugwira okuba kulimbana ndi anthu osalakwa
Pitani ku mgozga ngati simkaphedwa mwawapezerera akuntchisi?
Wamuvifyontha nadi
sangapiteko anzawo anakalodza miyendo sakufunakonso
sangapiteko anzawo anakalodza miyendo sakufunakonso
Ha ha ha ha
udzadya thukuta lako” mawu amatelo sono anthu alakwa chani? ???
Chowamangiranso ndi chani’Mesa amati Chuma chili Nthaka,ife zamathanyula ayi,bola kulima ganja mwina kupindula akabe alakwanso
ok chabwino
Akanangowa cya madoloo..! Alakwxa apolice o.!