Mphatso Chinguwo, 38 from NKhotakota district has died after drinking too much alcohol without eating any proper food.
Chinguwo was working as a tailor in Mng’omba village, Traditional Authority Mwadzama in Nkhotakota and his sudden death has shocked residents in the village.
According to the deceased’s workmate, Alfred Green, the two were working at their tailoring shop when Chinguwo suddenly collapsed.
Green called other villagers for help and together they took Chinguwo to Alinafe Hospital where he was pronounced dead.
A post-mortem conducted at Alinafe Hospital revealed that the deceased died because he took too much liquor.
Chinguwo hailed from Undi village, Traditional Authority Kalonga in Salima.
Zomwe amadzala zomwe ayenela ku kolola amadziwa cocita ameneyo
Gud photo ya uchimo
Eish… imfa sithawika mpakana mowaso kutipha koma abale
Inu mukuwona ngati akadadzamwalira litiro ndipo ndi chiyani kodi?…
Tisonkhe limodzi limodzi si mzathu nanga uyu biggie
Nanga inu mwadya kale tiuyambe
Nthawi yakwana yakwana ngakhale anakadya anakaduwabe.ifeso tilimmbuyomo chifukwa ife ndiye timamwa kumwa.R I P
Ali bho ameneyo…ndamumunyadira
Kukhala ndi 5 pin yomwela koma kulephela kudyela chips ndi kanyenya wa 5 hands kuwopa kuti siwuledzela,,,R I P
Kukhala ndi 5 pin yomwela koma kulephela kudyela chips ndi kanyenya wa 5 hands kuwopa kuti siwuledzela,,,R I P
wafika kumwamba ndi masile alibo maniwo
wafika kumwamba ndi masile alibo maniwo
Timayamba tayiteleka kaye tisanayambe kumwa.
dot blame beer blame him iyeyu ndiamene adalondola mowa komaso iyeyu adali munthu wosusuka
mowa umakoma kumwa otsadyela inu
ntchito zake zamuchitira umboni
So is alcohol improper food or no food at all?
wajanduka ndi kachasu lkklkk
guyz nditsaname bawa nsindingasiy! wachita kufuna
guyz nditsaname bawa nsindingasiy! wachita kufuna
Kkkkkkk. Koma inu. Walupanga amafa ndi lupanga lake lomwe
Eeeish thought anamwa osadyera …RIP BAXI
Anamudza ameneyo
woow amen R.I.P
Drinking and driving
Tikamamwa zofewa mumati ndife zitsiru,RIP
Mmmmmmmmmm for WHAT ! Lets think and dadecate befor doing things
The danger of alcohol cannot be over emphasized.
Ntchito zamanja ake zamusata zamuchitila umboni akapume tikamupeza
Ntchito zamanja ake zamusata zamuchitila umboni akapume tikamupeza
just say rest in peace cz zofuna
Bola iyeyo wafa ataledzela
Zosadandaulitsa….
Kkkkkkkk osationongera Dzina ife
Vuto ndiwokumwayo coz bawa ilibe problem
Kumaliro kwake umwedwenso basi
Mmmmm R. I. P Take Note F This Don’t take alcohol in an empty stomach
Kkkk mmalo momakalima uku aaaa
Conz zoona mwapitadi? Apolisi chitaponi kanthu coz mowawu waonjeza kkkkk beer at mob justice
Mamane, mpaka pamenepo?
Kkkkkkk koma zinazi
bola ameneyo akapitilizebe kumwa kumka iyeko.
Rip.man palibe wambeu,tonse tiri padepot koma manyamkidwe ngosiyana
takulandirani Kuno kumanda man
Wopanda ndalama amamwa zedi koma omwela zake ndi chetechete amagulilidwa uyu DYELA KUPHA!
why taking too much mowa ?
Kkkk,alibo kufa ata blaka
Sikokhako ku Chikwawa wa Ngabu akwana awiri tsopano amamwa mowa osadyera nde palibe kuchitira mwina koma Kutisiya basi
foolish man! h 4rm Nkhota1/4 osamango suta chamba bwa? cant kil u no mata hw much u smoke on an empty stomach
This is nothing but the truth bra!! gud comment, braaaaavo dude!!!! kkkkkkkk
thanks fam. real recognize real
zachamba bax
akut mowa man. OSAT chamba
hiii;;;;;;;;;;;;;;ok
Good trust alcohol you end like that.
Aziyika mu ukapolo pa kukonda za pamwamba.
Munthu wopusa ameneyo.
Its ol about tym
yense ofuna kufa amwe mowa wawukulu
Zisandikhuzeee
anamwa WIN ameneyo mowa ndichibuku.
Rest in peace braz see u later.
Its 2 bad
Kutopa ndi moyo et
See you there man, it`s one way better to die
Thawi yake yakwana ameneo ine singasiye bawa
Oooooh…oooh…ok…
Oooooh…oooh…ok…
May his so rest in peace
May his so rest in peace
tchito zamanja zamuchitila umboni
tchito zamanja zamuchitila umboni
anauyamba atakula uyu iii sorry fo dat
anauyamba atakula uyu iii sorry fo dat
I can’t say sorry we know beer it’s another rubbish stuff u can’t drink without eating.
I can’t say sorry we know beer it’s another rubbish stuff u can’t drink without eating.
mowa koma uwu…. ameneyo wamamwa kachasu.. icant blame bawa bawa alibe chifukwa koma munthuyo sakhutitsidwa.. ineso ndimwamwat koma ndikakwana ndimavomeleza kut tanki yazaza ndimaona nsana wa njira nde pali mamwedwe ena osaganiza bwino… shame kwao kwa chamba ku KK
chikakhala panzako umatenga madzi ndikumua koma chikakhala paiwe umayiwala ndipomwe madzi amakhala wapha angati green several pple
man vuto la anthu ena samakhutitsidwa zot mimba komaso mutu wao wakwana ndipo mowa wazaza mthupi mwao amafuna kumamwela mwelabe can u tel me kut utat uvomeleze zot walezela vuto lingakhale pat

Nanji kachasu wanzimbe ndikawawa ndeotsamudyera mapeto ake ndikuzimwanayo basi
Nanji kachasu wanzimbe ndikawawa ndeotsamudyera mapeto ake ndikuzimwanayo basi
RIP mr tailor cases like dis are on increase guyz tizidya tisanauyambe
RIP mr tailor cases like dis are on increase guyz tizidya tisanauyambe
Ok