Regina Nsona, a Malawian woman in South Africa has been listed among the most wanted suspects in the rainbow nation.
According to South African police, Nsona was a domestic worker and is believed to have assisted other criminals to steal from the house of her boss.
Meanwhile, the law enforcers have asked the general public to help them locate the suspects.
Police said all the wanted suspects have appeared in court before and were either released on bail or on warnings.
“We need help locating Nsona and other people as they have been linked to crimes. In most cases they have missed their court appearances,” a police spokesperson said.
Amalawi kuchitixa manyazi!
how much that money they steal
Mabwana enawa amaonjeza, timalipilo ngati pocket money yamwana wa ku primary xool. Waitha ameneyo.
wel done azichangamka…..
Wakhwana bwera ndizakuchekele mankhala kuti usagwidwe bola chipita mthengo.
Malawi 24 u r very stupid! Don’t you know that stealling is our custom here??
Wakula watha uziona, osalimbana ndi ntchito bwanji, mwana opusa kwambiri. Uzapeza mavuto moyo wako onse
Thats not good what ? Malawian girl .
Umakwana
Iye kusakhala mmalawi watani? Munthu aliyense atha kulimba mtima basi posatengera kuti ndi mkazi kapena mamuna. Anthu akulimba bwanji mtima kuchotsa ziwalo za amzao? Adaotchedwa kwa Tengani aja ndi Ma Nigeria?
Azibweradi ameneyo
Nkazi wachangamu pitani sister kumudzi mukathandize ana Mulungu wakuyankhani
Kaya ndi Malawi or not komabe wakuposani, inu paja mmafuna u gudu boyi kkkkkk shameeeeeee
Mungaphata Mugase Moto Mwapomva Mwalonga Ndinsena Biiiii
I thought she has killed the President, lol
chifukwa chani amalawi timaipitsa tokha mbili?
Wabwera bho sister azichenjera
Wabwera bho sister azichenjera
Akazi ochongamuka ngati amenewo ndi abwino
Akazi ochongamuka ngati amenewo ndi abwino
Poti ndimsena mukukana mwaymba kunamizila chinyengo chaku immigration Koma akanakhala Chirwa or Mkandawire Mkanati a Tumbuka,,,,, mlomwe akuyipisa dziko mwakana zoti ndi mmalawi
Do Or Die game
Plz call me ndakuona kuti ndiwe wachangu another mission is loading
Plz call me ndakuona kuti ndiwe wachangu another mission is loading
Angofuna kutionongela mbili yathu dzina ngati ili sikumalawi ayi
Mbuxi simadya nyama
atleast amalawian is making headlines abroad
Aziona
Ndakayika ngati ndim,malawidi ameneyo
yaaa,uyu nde mai wachangu than kumaphedwa ndi ka k300yauhule changu zibwera undiimbire pa 0888…..tigawane
Fake malawian girl you are damaging our image here, I hope the cops must arrest you and rot in jail
Mmmmh ayi
kkkkk malawi 24 be serious most wanted for aiding criminals to steal I thought u will say she killed the whole family
Zinachitikadi & ndizoona
Usatiyipisile mbiri galu iwe.
Kutipangitsa manyazi mxiew
Ta thamangira kumudzi msanga ngati munabadi ndalamazo,aliyense akhoza kumubera bwanayo,if u have got chance pliz amalawi anzanga just take the money and go back home immediately
Kkkkk koma iwe!!!
Angofuna kuononga CV yathu. Si mmalawi uyu
Kuipisa mbiri ya a amalawi kumeneko, choncho anthuena aziopedwa kulembedwa ntchito za mnyumba kujoniko chifukwa chaiwe.
oky
Leave her alone maybe she was reacieving meagger salary….
Leave her alone maybe she was reacieving meagger salary….
Sizoona kuti ndi M’malawi ameneyo.Changu chili ku Immigration poperrkera pa window owooooo! Kaya!
Sizoona kuti ndi M’malawi ameneyo.Changu chili ku Immigration poperrkera pa window owooooo! Kaya!
she cannt be a malawian this ready it mt be someone bought a passport from malawi
she cannt be a malawian this ready it mt be someone bought a passport from malawi
Aaaaa wasowa zolembapo eti?
Aaaaa wasowa zolembapo eti?
ndimdaphunzira naye ameneyu,koma i cnt believe this,ndi wachisena
ndimdaphunzira naye ameneyu,koma i cnt believe this,ndi wachisena
Ma passport amene mngogawa kwa aliyense awa. Mwaona tsopano mnapasa passport wakuN…. Ayamba ktiipisira mbiri pano. Mmalawi wenwen,maka wankazi, sangapange zimenezi
Ma passport amene mngogawa kwa aliyense awa. Mwaona tsopano mnapasa passport wakuN…. Ayamba ktiipisira mbiri pano. Mmalawi wenwen,maka wankazi, sangapange zimenezi
Ukanena kuti passport mukungopatsa aliyense ndindani anayamba wapatsidwa passport yaulele? Ulemu ndiumene umatipweteketsa. Ndichifukwa kuli mau okuti gender kupalamula ndi kwa aliyense.
Azimayi ojijilika
Azimayi ojijilika
My sister?
My sister?