In a bid they say is to reduce road accidents in the city of Blantyre,police this week impounded up to 40 minibuses on miscellaneous traffic offences in the commercial city.
According to police, the operation saw commuters under offences of exceeding seating capacity, expired insurance and certificate of fitness (CoF) and road obstructing, among others being impounded.
Blantyre police Public Relations Officer, Elizabeth Divala told the media that at the moment, half of the owners of the commuters have since duly paid fines to their various offences.
But some of the minibus owners said police did not provide vivid ground on why they impounded the minibuses arguing it was only meant to dupe them off their ‘hard earned money’.
Minibus drivers have been accused of careless driving in Malawi and police believe that enforcing such laws would see the reduction in accidents in the country.
ngati ikumakafika ku ndix ndikubweleranso,ili bhoo imeneyo,mapepala sayendetsa galimoto koma munthu,ngati waledzerd mugwireni,ngati ali bho basi
tangotchizulani magalimoto anuwo,muzikwera kabaza basi tiwone kuti azigwira chani
ma minbus a mabwana a police sagwidwa, ku Lilongwe a kwa Phwetekere ndi Chinsapo
Extra care is needed every where in the world when driving people
Say taxis not minibuses. Kkkk
Zachamba izi
Zachamba izi
hhhhhhh!!!!! iyaaaaaa!! ndalama ndiimene yalowesa anthu kumanda mtopesa zati bb! kufa siwalesa manje kafeledwe!.
Good development koma mmbweleso Ku karonga ndi Chitipa amanyamla anthu ngati chimanga kuno pliz pliz
How Did They Got COF
then next step?what about if my offence gets a fine of k50 pin and l bribe you with K20 pin then back into the road?hahahaha!tricks to get bread are many.
Chambatu ichi amatero??? kubera uniform eti..
Zatchito mabig osawasekerera amenewa.
Mareceipts aoneke ndalama zipite ku boma osati mmatumba awanthu take care
Mareceipts aoneke ndalama zipite ku boma osati mmatumba awanthu take care
Paja ndikukhara kwao zikakhara kuti sizinalowe
Paja ndikukhara kwao zikakhara kuti sizinalowe
Dziko ndilimenero.sometimes police have their target of making money.sorry to vehicle owners.
Dziko ndilimenero.sometimes police have their target of making money.sorry to vehicle owners.
Ok…
Komadi ntchito igwirike ku ma minibus anzathu awa apolicewa ngti alibe zowayenereza
CHILUNGAMO CHIYENDE NGATI MADZI
Akungofunapo ndalama basi palibe nkhani apa
Akagule magalimoto awo apolicewo azipanga nawo zimenezo.Akuuziwa mtengo wake?
Koma kuba2 uku ndalama ikuvuta kale komaso akufuna kumangowabera anthu
Mubwerenso ku lilongwe kuno apolicenu. Kma bola wosakondera palinso apolice ena ali ndima minibus akungoyenda wopanda misokho town muno mugwire wonso