Mutharika challenges Chakwera

210

Malawi President Peter Mutharika has challenged that he will never bow down to the demands of leader of opposition Lazarus Chakwera to appear in the national assembly for questioning.

During the recent Parliamentary session, Chakwera said he could not ask questions to government ministers arguing that his questions were to be answered by the head of state.

Peter Mutharika and Lazarus Chakwera

They never cease attacks on each other.

“I demand that the president should come in Parliament to answer questions because he is part of us, we do have government ministers all the times but this time we needed him to answer questions” said Chakwera.

However, speaking at the official launch of Buy Malawi Strategy, Mutharika said he will never go to Parliament to answer questions from opposition members of Parliament.

“They want to put Presidential powers on scale, I cannot appear in parliament because of someone, they were defeated they should wait for 2019,” said Mutharika.

The opposition have been grabbing the government by neck to explain on issues that are affecting the country including on the shortage of maize in Admarc depots across the country.

Share.

210 Comments

 1. Stupid should go 2 L.Chakwer susiya za umulungu kuyamba ndale! aaaaaa amene ali ndi xoka xangawine chixankho ameneyo bola N.L.P.basi awo azipanga zawozo amusiye Big man-yo ananale.Ngat akuona kut pali bvuto anene ife a N.L.P. led by Friday Jumbe tithandizepo

 2. we malawians lets committed ourselves on scene of constitution if we really know dat each & every country has constitutions lets all centerd on the law, laws never minds the position of ahuman being wherever is prezdent law must on him/her if our constitution allows that the prezdent must go under questioning he suppose to do so,no matter he can hire someone else but the government surely knows dat mthalika was under questioning,don’t beat about the bush mthalika has no leadership in him,he is just aprofessor in education not in human emotional as such he is also athug of malawian

 3. I should thank Peter for taking a new step. Opposition imafuna kumamutola. atleast if he continue with strong Leadership in this way. he will take over again in 2019.

 4. What is the connection between appearing in Parliament to answer questions and 2019? I am 100% made to beleive that this man is really dull and has no bit of intelligence in his Mulhakho brains.

 5. John Dale you’re the kind of Pipo who are killing Malawi! What do you have here or what does your president have that can stop him to be questioned in pubulic? Have you seen South African parliament how it is doing in parliament? Haven’t you seen Zuma being questioned or told in parliament that he is under performing? Now you are saying Peter can’t appear in parliament becoz he is a president are you sure or serious? Don’t be self-centered with your president! It’s something of national interest! If he cares he have to!

 6. Pitar yo ndi galu alibe uzimu wawu munthu miyoyo ya Malawi oculuka kwambili ikuvutika kamba ka munthu modzi vuto samava zonena azake

 7. Kodi bambo chakwera mulibe kuganiza kodi? Kodi inu mudasankha kukhala mbusa nokha mwasintha mwati ai ndikufuna ndale kodi chikhala kuti amalemba baibulo lina mukanakhala mneneriwake uti ?or mukwiye mcp sizalamulanso umbavawo mukutionongera nawo zinthu kuno mudziko lathu anzanu akalamba nazo zimenezo munthu wamphongo sanyanyala

  • Mukadziwa kuti munthu amene ali ndi U Mulungu ndiamene angakhale ndi utsogoleri wabwino chifukwa akhoza kumva chisoni ndi anthu ake osati nati Peter

 8. Mchifukwa chiyani Mulungu munandilenga limodzi ndi anthu ochimwa ongoziwa kutukwana,kunyoza,umbuli ndikudana ndi munthu yemwe sanawambe?

 9. Ndale zophusa zimenezo ,,,kodi atsogolerinu mudzasiya liti kuphwanya malamulo,kodi mesa aPhungu wo akugwiritsa ntchito lamulo lomwe likuwapatsa mphamvu kukokera yense ofunikayo Ku Nyumba yamalamulo

 10. kodi bwanji Chakwera sakamba zabwino zokhazokha za Peter koma zoipa basi? Adakhala bwanji? Tiziti zabwino sakuziona? Chili kwa mzako umati chigwire nyanga iwe utabisala ngati dolo. Akadakhala dolo akadazindikira kuti action speaks louder than words. Iye akupangapo chiani ngati m’malawi?Kumango nyoza.kulalata.k uyalutsana basi, ndi mzeru chomcho? Utsogoleri ndi umenewo?Amusiye PETER ndi nthawi yake apange zimene amatha. Ife timamukonda PETER, WOYEEEEE! DPP WOYEEEE!

 11. Ochakwera Ofuna Chan Ku Politics Mesa Ndiobusa Zachamba Mayaz Iwe Chakwera Mafunso Achan Zapatundu Wakwanu Komanso Pamacheza Panu Ndi Chabwera Zisatkhuze Wamva!?

 12. the ministers he delegated were ready with answers.we all know mcp and their loser CHAKWERA.they are happy when things go wrong and then blame government.their criticism is full of badmind.they just want to divert the presdents mind from other issues….moti akonze kae mavuto a munyumba mwawo akuthamangila kuitanisa Presdent?koma mfiti yopemphera iyi.mfalisi weniweni chakwera

 13. In 1993, malawians voted for democracy. We didn’t know its meaning then, and we still don’t know now. Most of the time even learned leaders to do the opposite. At that time, Salim wa Salim advised that to run a democracy, the people must be knowledgeble. In malawi many people do not understand the workings of a govt. We vote for wakwithu, gifts and not mfundo.

 14. A malawi chipani chimene sicigwilizana niboma chifunsa bwanji mafunso,chifukwa ndizoziwikilatu kuti mafunso ake ndiwo masula osati kumanga UDF it is a good example that ni imene ina bwelesa D

 15. Is it Chakwera or the Constitution. I have to read a clause where it says a winning candidate is barred from being called to answer some questions in Parliamenr.

 16. Chakwera ndiwe wabodza ukumana kt ukumenyera amphawi pamene ukufuna akuwonjezere allowance ndakutulukira. Si ndingakukhulupilire chot ndikuwuze

 17. Mmmm mr president akuopa chani kukayakha mafuso amalawi? you have to go koma mwampini sadzathekasotu uyu aaaaaaa malawi ali pavuto akulu life yake imeneyi isheee.

 18. Apresident apite asapite kuparliament ndi chimozimozi. MUTU UMOZI SUSENZA DENGA. Achakwelawo ndi ndale chabe. Mafunso awo angayankhidwe bwino ndi nduna popeza ndi mitu ya anthuyo yomwe yapanga boma. Mutu umozi sungapange boma ndiye amafuna mitu 193 against mutu umozi. Ndindale chabe president sapanga boma payekha koma anthu.

 19. zovuta. MCP ikuti Achimwene Lazalo akukana konveshoni so ndi dikiteta. Naye Lazalo akuti Malume Pitala ndi dikiteta coz akukana kuyankha mafunso chifukwa amalume alibe pulobulemu kuchipani chao. Kaya Lazalo zikuthela bwanji coz ndikuona kuti udasankha molakwika ndi namondwe akutchaya bad. Chilichonse ukukhalira kulira. Think twice my brother. Pitala wachita bwino kukana paja ndi alongo awo amakupanganira. Akukuona nthawi yao yatha. Koma nawe Pitala watani wangokhala osafufuza kuti za Brother zidakhala bwanji? Mulungu akuika pamene kuti amalawi adziwe zoona zenizeni thats why abusa olosela imfa aja nawonso akukumana ndi namondwe oopsya zeni. Usaope tiyenaye. Nthawi yake yatha. Mademoni ake alankhula atopa koma usafoke Mulungu akumenyera nkhondo

 20. Mind y our tongues. He is still a president. He is still ruling. A person who loves you does not wait to question you in public. No body is happy to be undressed in public. Can you take the advice from a person who is proporsing your wife?? And the one who is seeking your death to grab your position is as well an enemy. Malawi first.

 21. To be apresident it doesn’t mean u a right or u know every thing no. Let me remind u 4u to be apresident its bicoz of us who vote 4u to be at de high rank so its only de opposition leader who can come and ask u questions on be half of us .So if u dont want 2 appear in parliament and ans some questions concerning ur and our country u a selfish and 1 day is 1 day u will be ex president.

 22. Its nt Chakwera who wants Pres Peter to answer questions,but Voters who Employed Peter and Chakwera is our MouthPiece.Mesa pamenepa ndi pamene Mukawonese Upulofesa wanu .Mafuso amene tatuma aChakwera ndi a577bn, 92bn, za maTractors, za Njauju ndi Chasowa,Nanga ndalama apereka Japani ndi China zagwira ntchito yanji ? Pano tikuva za 3Trillion not counted for.Nanga 3bn za MERA, Nanga za ATI Bill,musathawe aPresident pitani ku Parliament next sitting mukayankhe mafunso athu tatuma aChakwera.

 23. Its nt Chakwera who wants Pres Peter to answer questions,but Voters who Employed Peter and Chakwera is our MouthPiece.Mesa pamenepa ndi pamene Mukawonese Upulofesa wanu .Mafuso amene tatuma aChakwera ndi a577bn, 92bn, za maTractors, za Njauju ndi Chasowa,Nanga ndalama apereka Japani ndi China zagwira ntchito yanji ? Pano tikuva za 3Trillion not counted for.Nanga 3bn za MERA, Nanga za ATI Bill,musathawe aPresident pitani ku Parliament next sitting mukayankhe mafunso athu tatuma aChakwera.

 24. Economic problems are all over but our president and other ministers are foolish how can he fear to answer Malawians in parliment yet are failing to ease the problems on their own

 25. Economic problems are all over but our president and other ministers are foolish how can he fear to answer Malawians in parliment yet are failing to ease the problems on their own

 26. Akuziwana zasatanic zokhazo kha TB wanuyu amati akayambana ndi azakewo pansi panyanjapo amadalira kulosera azake azitipusisa apa mukutinyasa ife bola kumawotca cimanga

 27. Akuziwana zasatanic zokhazo kha TB wanuyu amati akayambana ndi azakewo pansi panyanjapo amadalira kulosera azake azitipusisa apa mukutinyasa ife bola kumawotca cimanga

 28. APM thats good osamangosekelera zilizonse, ndipo chakwera even ku mcp your days are numbered akuthotholako a kabwila ndi anzawo kumeneko kaya uloweranso kuti?

 29. These politicians they take us for granted,why they don’t respect voters ? I have never here them coming together to discuss how they to improve the life’s of poor Malawians

 30. These politicians they take us for granted,why they don’t respect voters ? I have never here them coming together to discuss how they to improve the life’s of poor Malawians

 31. Akuopa chani APM kukayankha mafunso, apa iye ndipamene akanaonesadi kuti ndi mtsogoleri wa dziko popita ku parliament konko nakayankha mafunso amene anzake ovoteredwanso ngati iye amkonzera. Chifukwa mkatikati m mafunso omwewo iye (APM) akanatengeramo mfundo zina zoyendetsera bwino dzikoli, koma kukana kokhako kukusnyeza kulephera kumva za anzao, kufooka komanso kusalabadira za anthu. Bwana APM pepani mkanakhala ena otifunira zabwino ife okuikani pampandowo,mkanapita ku parliament kuja nakamva zomwe ma duty bearers anznu akukufunirani, pajatu boma timayendetsa limodzi ndi osutsa boma amene, ndiye tiyeni pamodzi ngati tonse a malawi, osayiwala nyimbo ya late state president Bingu wa Mthalika yoti “tiyende pamodzi ndi mtima umodzi”, nanga inu zanuzi bwanji, loreranani ndipo gonjeranani after all nonse kumeneko muli after ifeyo anthu.

 32. Akuopa chani APM kukayankha mafunso, apa iye ndipamene akanaonesadi kuti ndi mtsogoleri wa dziko popita ku parliament konko nakayankha mafunso amene anzake ovoteredwanso ngati iye amkonzera. Chifukwa mkatikati m mafunso omwewo iye (APM) akanatengeramo mfundo zina zoyendetsera bwino dzikoli, koma kukana kokhako kukusnyeza kulephera kumva za anzao, kufooka komanso kusalabadira za anthu. Bwana APM pepani mkanakhala ena otifunira zabwino ife okuikani pampandowo,mkanapita ku parliament kuja nakamva zomwe ma duty bearers anznu akukufunirani, pajatu boma timayendetsa limodzi ndi osutsa boma amene, ndiye tiyeni pamodzi ngati tonse a malawi, osayiwala nyimbo ya late state president Bingu wa Mthalika yoti “tiyende pamodzi ndi mtima umodzi”, nanga inu zanuzi bwanji, loreranani ndipo gonjeranani after all nonse kumeneko muli after ifeyo anthu.

 33. Anthu enanu sindimaziwa kuti mumaganiza bwanji? Anthu ngati achina Tripple kumachita kufunsa za nzanu kuti kodi afa liti?Dziwani kuti imfa ndi mdani wathu wankulu ndipo ndizoona kuti mutha kumafunsa chifukwa nzanuyo analotseledwa. Inuyo mulibe mbiri ina ili yonse mdziko kuti mungaloseredwe za imfa yanu, koma sikuti ndi inu amuyaya ayi. Za mmawa siziziwika nkuthekanso kuti mungayambe ndi inuyo ngakhale nzanuyo analotseredwa.Wina ali yense ndi ofunika pamaso pa Mulungu choncho sibwino kusangalala ndi kufa kwa nzanu. Kunena zoona nkhani yokhuzana ndi imfa sibwino kumangoikamba kamba chifukwa angakhale akunyanseni koma kumtundu kwao ndiofunikira ndipo ndikukhulupirira kuti angadandaule zedi atafa nsanga monga mmene zingakhalirenso kwanu mutafa inuyo.Kanthu n’kako uvundukula nupenya.Kamba amam’nyera amene wam’tola. Kwatsala tchire ndi komwe kupita moto. Tisamale ndipakamwa pathu popeza mau amalenga.Ndikudziwa kuti Peter simukukondwera naye koma imfa ndi nkhani zina palibe amakondwera nayo.

 34. Anthu enanu sindimaziwa kuti mumaganiza bwanji? Anthu ngati achina Tripple kumachita kufunsa za nzanu kuti kodi afa liti?Dziwani kuti imfa ndi mdani wathu wankulu ndipo ndizoona kuti mutha kumafunsa chifukwa nzanuyo analotseledwa. Inuyo mulibe mbiri ina ili yonse mdziko kuti mungaloseredwe za imfa yanu, koma sikuti ndi inu amuyaya ayi. Za mmawa siziziwika nkuthekanso kuti mungayambe ndi inuyo ngakhale nzanuyo analotseredwa.Wina ali yense ndi ofunika pamaso pa Mulungu choncho sibwino kusangalala ndi kufa kwa nzanu. Kunena zoona nkhani yokhuzana ndi imfa sibwino kumangoikamba kamba chifukwa angakhale akunyanseni koma kumtundu kwao ndiofunikira ndipo ndikukhulupirira kuti angadandaule zedi atafa nsanga monga mmene zingakhalirenso kwanu mutafa inuyo.Kanthu n’kako uvundukula nupenya.Kamba amam’nyera amene wam’tola. Kwatsala tchire ndi komwe kupita moto. Tisamale ndipakamwa pathu popeza mau amalenga.Ndikudziwa kuti Peter simukukondwera naye koma imfa ndi nkhani zina palibe amakondwera nayo.

 35. As the matter of fact peter he mustn’t take for grated it his responsibility to appear in parliament don’t deceiving us by saying that he can’t give up to chakwela thats not true chakwela has got nothing to do with that stupidity gay presi its pple who need him to answer for himself not by sending some one like said in his coment above

 36. I am not an MP. I am not MCP, I am a simple retired person with a big heart for my grand children and their future. I want the president to go answer questions that I have for him, channelled through my MP. I am fed up with those kindergartten questions and answers on MBC

 37. Is it chakwera or constitution? Parliament needs the president to answer questions from mps.NOt from Chakwera. Apresident asawonesere kt akuopa chakwera ku parly

  • It means there’s some of majority support Peter?many pple still blinded in Malawi. Peter is there not for the development but for to hinder Malawian’s. Oh crying for my country, we should be out side till wen? Running poverty from our country

 38. It is constitutional to appear in parliament to answer question but it is not a “MUST”.. He can deligate any minister on his behalf the President is only exercising his powers within the constitution radius.

 39. Mutu umodzi susenza denga ngakhale utakhala ngat wanuwo.never cal pple opp. We are all malawian.we need 2 tak action 2 develop our nation through u de president.so dont divide us into grps.

 40. peole are taking him for granted and for fun ndye sakuyenera kumapezeko inu mavuto achuma ali kuno kokha why are u blaiming on things which are affecting the whole world senseless

 41. Agalu awa, bwanji osampatsako mpata woti izaganiza za mzeru zoyendetsera dziko. Iwe Chakwera ndiwe mbusa and chilungamo ukuchidziwa bwanji mudikire term iyi ithe?

 42. Ine Dzandale Sndmazitsata Komatso 2019 Tsindizabvotela Munthu Aliyense Ubwana Ine Ai……Aooooh Mbole Yaoo Mwauzeso Amzawooh Mbole Yaoooh,,,,,,

 43. Vuto kumalaw kuno munthu wna akamakuthandza maganizo umawona ngat zopanda mzeru ! I don’t knw may b coz ov our education, but we hav to remember “mzeru zayekha adaviika msima mmadzi”

 44. Vuto kumalaw kuno munthu wna akamakuthandza maganizo umawona ngat zopanda mzeru ! I don’t knw may b coz ov our education, but we hav to remember “mzeru zayekha adaviika msima mmadzi”

 45. Vuto kumalaw kuno munthu wna akamakuthandza maganizo umawona ngat zopanda mzeru ! I don’t knw may b coz ov our education, but we hav to remember “mzeru zayekha adaviika msima mmadzi”

 46. Mtsongoleli satero iyeyu wapambana bwanji ZUMA Amapezeka unyumba yamalamulo ; utathauza kuti akutumikira anthu iyeyu bwanji , m’masomwake chikondi cha khwagwa.

 47. It is only the Malawian president who can celebrate this mediocrity. To him he thinks it is a personal attack to be called to parliament but presidents all over the world worth their salt go to parliament to face tough questions from MPs on various issues affecting their countries. Ambush him with questions when he comes there to open the parliament kkkkk.