Sulom fails to vacate Dedza’s injunction

Advertisement
dedza young soccer

The 2016 Super League playoff match involving Dedza Young Soccer and Airborne Rangers at Civo Stadium failed to take place on Saturday after the Super League of Malawi (Sulom) did not vacate the court order which was obtained by Dedza on Friday.

dedza young soccer
Dedza Young Soccer: Against play offs.

Dedza took the injunction to stop Sulom from proceeding with the Super League playoffs.

On Friday, there was drama at Civo Stadium when Wizards were playing against Airborne Rangers as Dedza Young Soccer’s lawyers stormed the stadium to issue the injunction to Sulom officials.

They began moving around with the court injunction, looking for Sulom officials in order to issue them the order and stop the playoffs.

But Sulom officials were nowhere to be seen as they were hiding and only got the injunction after the first playoff game involving Wizards and Airborne Rangers was over.

It is now not clear whether Sulom will take Wizards as the 16th team in the 2016 Super League because they won their game against Airborne Rangers or if they will try to vacate the court injunction and continue with the playoffs.

Dedza however want to be promoted automatically since they finished higher than Wizards and Airborne Rangers last season.

The first playoff match between Wizards F.C and Airborne Rangers saw the Blantyre based side win 2-1 with goals from Bernard Chimaimba and Patrick Phiri while Stain Malata scored the consolation goal for Airborne.

Advertisement

85 Comments

 1. Sulom members ilibe nzeru nthawi yoxeyi be4 league kutha y oxanena kuti tikhala ndi mateam 16 pano awaxumir zamanyazi, mukhalir yomweyo ife kwa2 nkumva mukamapanga zachikape zanuzo

 2. SULUM OFFICIALS,
  Apa mene ziliri musatenge timu ili yonse kupita kuti Super league chifukwa Dedza zomwe adandaula kwa iwo ndizoveka komanso FISDS nayoso idawina ngati mungatenge Dedza ziwani kuti Fiti za pira nazo zimang’ala. Nde musatenge timu ili yonse. Injuction yawo muisiye ikhale chomwecho tione kumene akaponye mpira wawo. Nkhani izi ndi zamasewere cholinga kuthandiz ana athu kuti azipeza zochita.

 3. Plays offs for what.
  Super league separate weak from strong through full season performance not plays.
  Mukuonatu mvuto la umbuli.
  Dedza deserve it
  Why harassing them like that
  Shame on you

 4. Plays offs for what.
  Super league separate weak from strong through full season performance not plays.
  Mukuonatu mvuto la umbuli.
  Dedza deserve it
  Why harassing them like that
  Shame on you

 5. chifukwa chokusapanga dzinthu mwa u professional nkani matimu amapita kokamangala. nde Dedza sinalakwise oyendesa masewero muziko muno ndiandale kwambiri. ndipo deza musaipange nkhaza siyolakwa

 6. Sulom is not helpng our soccer. They kno truth why kumakakamira mtunda opanda madzi? Imene mukufunayo idakanika basi. Dedza ipite basi.

 7. PALIBE ZOLOWA CHAMUTU MA PLAY OFF OMWEWO NDIZA MPILATU IZI SIZANYAWU TIYENI UKOOO APA!! KODI IKAKHALA CUP AMATANI MESA AMASEWELANSO MA BEST LOOSE KUTI APEZE WAPA NAMBA 3?? NDE AMATI POTI UYU ALI NDIZIGOLI ZAMBIRI BASI AKHALA NAMBA 3??? NDIMPILATU UWU SIGULE OHOOO?

 8. PALIBE ZOLOWA CHAMUTU MA PLAY OFF OMWEWO NDIZA MPILATU IZI SIZANYAWU TIYENI UKOOO APA!! KODI IKAKHALA CUP AMATANI MESA AMASEWELANSO MA BEST LOOSE KUTI APEZE WAPA NAMBA 3?? NDE AMATI POTI UYU ALI NDIZIGOLI ZAMBIRI BASI AKHALA NAMBA 3??? NDIMPILATU UWU SIGULE OHOOO?

 9. Malawi is a very pathetic country bkoz all the leaders in influencial position done know what are doing. Very true one observer said this country it’s rotten from the head thus there can’t be anything positive from office bearers. Fam and Sulom is just one vivid example of such incomptent leaders! Do you expect Malawi for forge ahead with its football! No wonder Malawi football is 30years backward thus even Supersport doesn’t want to beem our superleague it doesn’t want to be party to incomptences! DYS automatically qualified nontheless!

 10. abvubwe ena ake mukuyakhula motubwa kut za mpira sidzifika ku court ngat anyapala asulomu akulephera kudziwa chilungamo mukufuna atani sumudziwa kut ena anapita nazo ku manda za mpira zomwezi nde uzinena zaku court

 11. Inu a Sulom, system imenei mwaitenga kuti? FIZD mukufunayo ife sitikuona phindu lake. Timafuma team imene imachita zakupsa pa ground like Dedza. Ganizani bwino osatengera kudzika koma chilungamo chiyendepo

 12. sometimes we have to be serious,asulom tinene zoona kt munali ndi team yomwe mumafuna kut isatuluke.Panalibe chifukwa cha ma play offs,Dedza ndiyomwe inakwaniritsa team ya 16.koma mudziwe kuti mmene mukuchitiramu mpira sungatukuke,even national team yathu singapite patsogolo.Lero ndiizo kungochinya azam,koma dziko lonse kudziwa ngati ayichinya Ghana,eee mmhi what a shame enerst.

 13. Zina Zinthu Mukamapanga, Osamapanga ngati anthu Oduka Mitu. Kodi mufuna kusonyeza kuti Sulom Ndi Fam, Atsogoleri ndinu Okonda Chinyengo kwambiri? Mungatiuze Ife aMalawi Chomwe Dedza Young Soccer Simukuifunila? Musaganize kuti Mukalowetsa Team yomwe inu mukufuna mu Supper League, Ndiye kuti mwakoza Mpira muno ayi. Zimenezo ndizobweretsa phokoso M’masero. Chitani Manyazi anthu akuluakulu inu. Tere ndipoti mudwepo apa. Be Ashamed of yourserf.

 14. Dedza more fire,zinali zodziwikiratu kt Dys ndi imene idakatha kulowa mu super league becz ndi Mzuni adangosiyana zigoli koma all they got 29 points each,ndiye iwe mtsongoleri wa sulom kaya mumati Botowoman zimenezi umazidziwa kale kt Dz young Soccer ndi imene inayenera kutsala ndiye iwe ukuti ma play off a chiyani? Kodi ndimayesa kuli odziwa malamulo kumeneko? Chonde usamautenge mpira ngati wakunyumba kwako, u r there becz of us people,be carefull wamva!

 15. Aaah!pamene a sulom amalengeza kut asitha kut matimu atatu ndiomwe atuluka bwanji sanapite ku courtso kapena kunena kuti sanatuluke mu ligi? basi asewere ngati asafuna asiye

 16. Kkkkk Mpira Pa malawi a sulom mukuchitayo ndindeu yogwililira kuti wina adzimenya pamapeto nkumati wawina ndiyemwe sanagwilidweyo DYS aliyense akuziwa kuti ndiyomwe inali team #16 Ma Playoff Achani ngati mateam amafanana ma points.mwachitilanji izi wina andiunikile coz mwina sindikuziwa chifukwa chomwe apangila

  1. inu ku jolozi amamenya ndi omwe achoka ku division amaphatikiza not okhaokha achoka mu Premier

  2. The setup is different and the circumstances are different. It’s simple you want to increase number of teams by one then relegate two only. That’s the point.

 17. MMPIRA PA MALAWI PANO SUDZALONGOSOKASO CHIFUKWA SULOM NDIIMENE IIMAYAMBITSA ZANYASI APAPA DYS NDIYOFUNIKA KULOWABISI AKUFUNAKUPANGA CHAN ASULOM OOOO ZACINYENGOZO AONINGETSA MPIRA

 18. Dedza Young soccer Isagonjere zofuna za Sulum. Dedza Isasewere mpira umeneu. A Walter Nyamilandu muli ndi vuto lalikulu kwambiri ndipo chinyengo chanu mulibe nacho manyazi. Tonse tikudziwa bwino kuti D Y S ndiyomwe ikuyenera kulowa mu super legue pachilungamo. Ngati DYS silowa mudziwe kuti National team yanu idzingomenyedwa ndi mphwephwa zomwe chifukwa mizimu siyimasekelera chinyengo. Mwanva agaru achinyengo a sulum inu?

  1. Dzina la peetteer liipati pa mayina a anthu odziwa kapena kutsata mpira? ngati palibe You ARE AN EDUCATED FOOL!!! & no explanation can affect my brain from your mouth

  2. Nkhani yake iti yotukwanayo apa? Ndinu makape amene mukutukwananu, ganizo loti pakhale ma play offs si la munthu mmodzi anthuwa anakambirana ndiye sindikuona choti muzinyozana apa

  3. Nkhani yake iti yotukwanayo apa? Ndinu makape amene mukutukwananu, ganizo loti pakhale ma play offs si la munthu mmodzi anthuwa anakambirana ndiye sindikuona choti muzinyozana apa

 19. dedza shud be the 16th osati zama playoffs zanuzo! ikanakhala wizard inamaliza the position inamalizira dedza last season simukanamenyesa ma playoffs koma poti ndi dedza ya ku central region ndiye kumaikhomelera??? rubish zokondera basi

 20. zankutu ma playoffs achiyani? Ife tikufuna maplayonns,Dz yachitabwino isasinthe maganizo.ganizo loti atuluka matimu awili lidaperekedwa then ndikumati atuluka atatu pambuyo pake ndikumati ina iloweso,apanjira imaonekeratu kt ilowe ndi dz basi.sadalakwitse a DZ kwakhala ndikutenga chiletso cha Lig ngati dz siilowa,ma lawyer apezeka a Caf.

 21. Malamulo ndi umunthu zigwire ntchito.
  You yourself create problems that you will fail to solve.
  The truth is that the team that was behind the last team in the supper league, should be included to make it 16, nothing else.

  1. malamulo akuti amenewa ongoloza chalawo.kamenyeni ma game basi mesa munatuluka super league and mulandila religation letter now you kuti mungolozedwa chala.thats childish and selfish.

  2. Ntchito inagwirika kale musamalankhule ngati mulendo.
   Pakati Pamatimu atatuwa, wina anali patsogolo pa anzake & that one deserves respect if we are to follow good procedures.
   All the teams are comming from the last seaso and we all know how they performed.

 22. Ku SULOM uko chinyengo sichikuthandizani mukubwezera mbuyo mpira ngati mwadya kena kake musanza.mufuna za mpira kumazitenga ngati zakunyumba kwanu bwanji? SULOM amayendetsa munthu m’modzi? mxiiim…

 23. wizards yapita basi enanu badikirani mwina akuthandizani asulam muzamenya 2017.

Comments are closed.